Amen mtumiki Twaibu Tinakusowani ife mwezi wa juni zachitika zambiri ku malawi taluza oyimba komanso Atsogoleri ambiri koma inu mwasakha kukhala chete Mu odio yanu ina munanena kuti tiyembekezere kuluza oyimba ochuluka mmalawi Now I believe it True we are in end time
Ulendo uno mwatenga nthawitu atwaibu tinadikilira koma opanda ma aufio mapeto ake timangonveseta ma aufio akale,bwanji simukukambapo zazomwe zikuchigikazi ?
Mmh koma ku Limbe cathedral kuli mphanga ina yake imene timati kuli Mai Maria 😢😢 tikapita back in the days kukapemphela I hope it's not one of those 32 pit's😢😢
Amen mtumiki Twaibu
Tinakusowani ife mwezi wa juni zachitika zambiri ku malawi taluza oyimba komanso Atsogoleri ambiri koma inu mwasakha kukhala chete
Mu odio yanu ina munanena kuti tiyembekezere kuluza oyimba ochuluka mmalawi
Now I believe it
True we are in end time
Amen ndipo tinakutsowani mpaka ife daily kuvera uthenga wanu wakale kale
Mulungu akutetezereni mumatiphuzitsa ndikutsekura maso Amen
Amen, mumatisegula mmaso a mbuye apitilize kukutetezelani
Amen... Mudzutulutsa tulutsa ma audio chifukwa ife timadikila inu
Mulungu akutetezeni mtumiki. Tinasowa chitsogoleri chanu.
😢😢😢 finally
😢😢😢😢😢😢
Koma asamasowe choncho please
Ulendo uno mwatenga nthawitu atwaibu tinadikilira koma opanda ma aufio mapeto ake timangonveseta ma aufio akale,bwanji simukukambapo zazomwe zikuchigikazi ?
Kodi whatsap forum ya a Twaibu bwanji,tigaileni
Ambuye andichitile chifundo
Amwene tinakusowani ise amwene, ambuye akhala nanu
Mmh koma ku Limbe cathedral kuli mphanga ina yake imene timati kuli Mai Maria 😢😢 tikapita back in the days kukapemphela I hope it's not one of those 32 pit's😢😢
Amen🙏🙏
Mulungu atipulumutse😮😮😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢
Alipo ali ndi phone number ya atwaibu guys andapatseko
Munthu uyu koma amandidalitsa
Amenman of God
Zovutatu koma Ambuye atithandize
Amen
Zooona kama kusaziwa ndikufakomwe
Chisilamu ndi ufiti
Ndezikutheka bwanj malo oti pamatchulidwa mau amulungu patheka bwanj kunkhala ziwanda
Eyetu nthawi yakisadziwa mulungu afaileketrta
Zimatheka ngati athu ambili pamalopo Ali okuda mu ntima
How can we contact twaibu
I can give you access
You have his contact?@@romanmanjolo1991
Ziwanda ku mpingp uli ose zilipo, even ku chichristu
Nde ukufuna kutanthawuza chani ?
Akuonekakuti akususana ndi uthengau koma chilungamo chimamasula my God bless Mr twaibu
@@romanmanjolo1991 Christianity kuli ziwanda inu simukuona zomwe akupanga ma prophet
@@AlliSaiti vuto simukufuna kuvesesa malume sanati Ku chi,christu kulibe ai koma nkhaniyo isateni muvese sanapatule
@@AlliSaiti vuto simukufuna kuvesesa malume sanati Ku chi,christu kulibe ai koma nkhaniyo isateni muvese sanapatule
Zikomp
Nkulu uyu😮 mutu wake sugwira ndi wamisara 😂😂😂😂😂😂
Olo nowa posema chombo ananenedwa kuti ngwamisala sizinayambire pa ATwaibu ,, God bless you brother
Ambuye akukhululukire
Paja mdima umadama ndi kuunika
Kuyankhula kotan uku
Because your religion is exposed?
Kodi ndi ipeza bwanji Whatsapp group kapena phone number ya a twaibu? Please help me
Amen
Amen
Amen
Amen