Living for Christ - Malawi
Living for Christ - Malawi
  • Видео 133
  • Просмотров 931 716

Видео

Umboni wa a Twaibu - kufotokoza za Black & White Pit, Shire Valley, ndi zina zambiri
Просмотров 7 тыс.2 месяца назад
Mu umboniwu, a Twaibu akufotokoza zambiri zobisika pansi pano. Mverani...
Umboni wa a Twaibu - Kufotokoza zambiri za ma PHONE games, komanso MANDA ngati dzenje la ZIWANDA
Просмотров 5 тыс.3 месяца назад
Mverani a Twaibu akuyankha mafunso okhudza ma phone games komanso manda ngati dzenje la ziwanda.
Umboni wa a Twaibu - Za chikumbumtima cha machimo a "HARD PLATE"
Просмотров 2,9 тыс.4 месяца назад
Mu uthengawu, a Twaibu akofotokoza za chikumbumtima cha machimo a "Hard Plate" poyankha funso.
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza za 'MALO OKWERA'
Просмотров 8 тыс.4 месяца назад
Mu utumikiwu, a Twaibu akufotokoza za 'Malo Okwera'
Utumiki wa a Twaibu - Kufotokoza za ku chigwa cha SHIRE - 30/04/2024
Просмотров 6 тыс.4 месяца назад
A Twaibu akufotokoza zambiri zokhudza ku chigwa cha SHIRE. Mverani anthu a Mulungu ndipo tipemphere ndithu.
UMBONI wa a Twaibu - ZA SATANA SI ZAULERE
Просмотров 15 тыс.4 месяца назад
Mverani a Twaibu kuchitira umboni pa zinthu zosiyanasiyana.
Umboni wa a Twaibu - Kufotokoza za maukulu a dziko la pansi
Просмотров 5 тыс.5 месяцев назад
Mverani a Twaibu kuyankha ena mwa mafunso a zobisika za dziko la pansi.
Umboni wa a Twaibu - kufotokoza zobisika za bwalo la mpira
Просмотров 6 тыс.5 месяцев назад
Mverani a Twaibu akufotokoza zobisika za bwalo la mpira
Umboni wa a Twaibu pa Lunzu - March 2024
Просмотров 11 тыс.5 месяцев назад
Uwu ndi umboni wa a Twaibu womwe anapereka pa msonkhano wa pa Lunzu, Blantyre womwe unachitika pa 17 March 2024
Utumiki wa a Twaibu - CHIYERO pamwamba pa SATURDAY/SUNDAY
Просмотров 3,2 тыс.7 месяцев назад
Mu utumikiwu, a Twaibu akufotokoza za CHIYERO pamwamba pa Saturday/Sunday
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza za chikhristu cha mphamvu
Просмотров 6 тыс.7 месяцев назад
Mverani a Twaibu kufotokoza za chikhristu koma cha mphamvu
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza zambiri za zakumwa zoziziritsa kukhosi
Просмотров 13 тыс.7 месяцев назад
Mverani a Twaibu akufotokoza zambiri za zakumwa zina zoziziritsa kukhosi
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza zambiri za chaka cha 2024
Просмотров 15 тыс.7 месяцев назад
Mu uthengawu, mverani a Twaibu akufotokoza zambiri za chaka chino cha 2024 ndi zina.
Umboni wa a Twaibu - Kuyankha mafunso pa documentary ya B.BC yokhudza TeB Joshua
Просмотров 14 тыс.7 месяцев назад
Mverani a Twaibu kuyankha mafunso pa zomwe documentary ya BC yatulutsa zokhudza TeB Joshua
Utumiki wa a Twaibu - zokhudza achinyamata komanso magazi a anthu
Просмотров 8 тыс.8 месяцев назад
Utumiki wa a Twaibu - zokhudza achinyamata komanso magazi a anthu
Umboni wa a Twaibu - "Mudzayilira nthawi yotereyi."
Просмотров 4,6 тыс.8 месяцев назад
Umboni wa a Twaibu - "Mudzayilira nthawi yotereyi."
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza za chinsisi za pa 21 December 2023
Просмотров 12 тыс.8 месяцев назад
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza za chinsisi za pa 21 December 2023
Umboni wa a Twaibu - wa pa 9 December 2023 pa Chichiri ku Blantyre
Просмотров 10 тыс.9 месяцев назад
Umboni wa a Twaibu - wa pa 9 December 2023 pa Chichiri ku Blantyre
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza za ma aliens, nthawi yomwe tiri ndi zina zambiri
Просмотров 3,7 тыс.9 месяцев назад
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza za ma aliens, nthawi yomwe tiri ndi zina zambiri
Utumiki wa a Twaibu - za LCD ya pa 10 Nov. 2024; CHIYESO cha OYERA MTIMA mu 2024
Просмотров 8 тыс.10 месяцев назад
Utumiki wa a Twaibu - za LCD ya pa 10 Nov. 2024; CHIYESO cha OYERA MTIMA mu 2024
Utumiki wa a Twaibu - za MAUKONDE a mulengalenga ogwira MAPEMPHERO. Zolepheretsa kulandira mayankho.
Просмотров 2,6 тыс.10 месяцев назад
Utumiki wa a Twaibu - za MAUKONDE a mulengalenga ogwira MAPEMPHERO. Zolepheretsa kulandira mayankho.
Utumiki wa a Twaibu - “Kodi inu mudzakhalako?” …ndi zina zobisika m’Malawi
Просмотров 9 тыс.10 месяцев назад
Utumiki wa a Twaibu - “Kodi inu mudzakhalako?” …ndi zina zobisika m’Malawi
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza za nkhondo yomwe ikuchitika ku Israel - PART 1 & 2
Просмотров 20 тыс.10 месяцев назад
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza za nkhondo yomwe ikuchitika ku Israel - PART 1 & 2
Utumiki wa a Twaibu - za UFITI ndi zoipa zina pa ANA M'MASUKULU - zoyenera makolo kudziwa
Просмотров 3,6 тыс.10 месяцев назад
Utumiki wa a Twaibu - za UFITI ndi zoipa zina pa ANA M'MASUKULU - zoyenera makolo kudziwa
Utumiki wa a Twaibu - Njira 6 za SATANA pa mpingo wa Mulungu masiku ano
Просмотров 3,7 тыс.10 месяцев назад
Utumiki wa a Twaibu - Njira 6 za SATANA pa mpingo wa Mulungu masiku ano
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza za IMFA YA OYIMBA M'malawi...
Просмотров 52 тыс.11 месяцев назад
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza za IMFA YA OYIMBA M'malawi...
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza zambiri za chiwanda cha ajiba, pa ana komanso akulu
Просмотров 5 тыс.11 месяцев назад
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza zambiri za chiwanda cha ajiba, pa ana komanso akulu
Utumiki wa a Twaibu - zochitika pa 2 OCTOBER 2023 pa tsamba la internet la satanic - MALAWI wavomera
Просмотров 11 тыс.11 месяцев назад
Utumiki wa a Twaibu - zochitika pa 2 OCTOBER 2023 pa tsamba la internet la satanic - MALAWI wavomera
Utumiki wa a Twaibu - ma plan a satana osokoneza matupi a anthu komanso chilengedwe
Просмотров 3,2 тыс.11 месяцев назад
Utumiki wa a Twaibu - ma plan a satana osokoneza matupi a anthu komanso chilengedwe

Комментарии

  • @FrancisYohane-t6o
    @FrancisYohane-t6o 4 часа назад

    Mulungu akupase mabvumbunso ochuluka

  • @user-hh9us2ee9c
    @user-hh9us2ee9c 4 часа назад

    Kwa amene ali ndi link ya brother twaib ya watsap chonde taponyan

  • @NovemberMmangathayo
    @NovemberMmangathayo 7 часов назад

    Mukuti analakwitsa kuphatikiza ma kalazi

  • @NovemberMmangathayo
    @NovemberMmangathayo 7 часов назад

    Munasowa tinalindimafuso pa zayimfa yachilima panatuluka odio yomveka ngati yanu yoti chilima anafa chifuka Chama calazi azipani kodi odio yi munatumizadi ndinuyo?

    • @EvelynChitsonga
      @EvelynChitsonga 3 часа назад

      Aaa ine sindikhulupilila kut ndi brother twaibu anayankhula zimenezija

  • @LINELYBISANI
    @LINELYBISANI 9 часов назад

    Asamasowe choncho munthu wamulungu

  • @VioleBandason
    @VioleBandason 9 часов назад

    Zoona achimwene nthawi zina umangoona wayankhula mosayenera kenako kumaganiza kt km ndione ndemwe zili ziwanda Mulungu atilanditse maka azimayife

  • @RyleChole
    @RyleChole 11 часов назад

    Aliyense amene amakhulupirira chipembezo mmalo mwa mau si mkristu chifukwa ziwirizi siziyenderana

  • @RyleChole
    @RyleChole 11 часов назад

    A Twaib,vuto nloti inu mmaganiza kuti Pali chipembezo chomwe chimatsogozedwa ndi Mulungu,kulibe chipembezo choterocho pansi pa thambo,Mulungu amatsogolera mpingo basi,osati chipembezo ayi.

  • @RyleChole
    @RyleChole 12 часов назад

    Zoona ziwanda zimakhala mwa munthu

  • @Idadube
    @Idadube День назад

    Ambuye atithangatire tataikadi. Tikonzeni Yehovah wathu kuti tiyendenso ndiiinu muuzimu ndi muchoonadi. Amen

  • @RyleChole
    @RyleChole День назад

    Ndithudi timvere Bible chifukwa Mulumgu anayi,lolani mau anga akhale Oona koma aina aliyense abodza

  • @Prophet-Ian-Ntaba
    @Prophet-Ian-Ntaba 3 дня назад

    God bless you for the revelations

  • @Prophet-Ian-Ntaba
    @Prophet-Ian-Ntaba 3 дня назад

    ndipo aliyense owonera ndi kusewera mpira masana ku thupi amachitanso chimodzimodzi ku uzimu. Ambuye anandionetsera zimenezi. Achibale nzophya kwambiri

  • @Prophet-Ian-Ntaba
    @Prophet-Ian-Ntaba 3 дня назад

    praise God. ine ndi mboni za mpirazi. Ambuye Yesu anandionetsera kochululuka kuti mpira ndi woima. ma demons amalemba aliyense osewera ndi kuonera mpira. No heaven for onse owonera ndi kuonera mpira. Ever since, ndinasiya kuonera or kutsatira mpira. Ndimakhala ngati ndikukhala dziko landekha lopanda mpira. Achibale, onse owonera mpira ndi kutsatira mpira, ali pa ndandanda wopita ku gehena akapanda kulapa. Izi nzoona.

  • @jonesmwengo6127
    @jonesmwengo6127 4 дня назад

    Amen ndilowetseni pa group yanu a Mtumiki anga. Glory to God!

  • @FrancisYohane-t6o
    @FrancisYohane-t6o 5 дней назад

    Ambuye alkudaliseni

  • @SamuelLiwonde
    @SamuelLiwonde 5 дней назад

    amen

  • @FrancisYohane-t6o
    @FrancisYohane-t6o 8 дней назад

    Tathokoza tatsisimuka

  • @frodgermakwa5973
    @frodgermakwa5973 10 дней назад

    Amen

  • @nicolauvirgiliolanguitone5041
    @nicolauvirgiliolanguitone5041 11 дней назад

    Kodi Alípio apa amene anakwanisa kupeza number ya mtumikiyu?

  • @Lawrencenkhoma-b2s
    @Lawrencenkhoma-b2s 11 дней назад

    Nanga mayiko enawa? Ndosiyana bwanji

  • @ChingahPetros
    @ChingahPetros 11 дней назад

    amen amen

  • @RyleChole
    @RyleChole 12 дней назад

    Ayuda lero Sali ndi kuwala chifukwa kuwalako anakukana ndipo kunaza kumadzulo komwe nkwa mitundu,ndipo panopa Mulungu sakuchita ndi Ayuda koma amitundu

    • @RyleChole
      @RyleChole 12 дней назад

      Doctrine iliyonse si chokera kwa Mulungu kuphatikizapo ndi sda yomwe mmaigomera.YESU ndiiye chomwe chikuchitika koma vuto nloti Inu simudziwa kuti Yesu nndani,Yes7 ndi mau a Mulungu.Pachiyamb8 panali mau ndipo mau anali kwa ndipo mau ndiye Mulungu,ndipo mau anasanduka thupi nakhala pakati pathu,Ndipo Yesu anati ndi choonadi,njira ndi moyo.kutsatira Yesu nkutsatira mau omwe Yesu adanena

  • @RyleChole
    @RyleChole 12 дней назад

    A Twaib,koma mudziwe kuti lero kuwala sikuli kummawa koma kumadzulo, ndipo mudziwe kuti mbali za dziko lapansi anthu amakhala kummawa ndi ku madzulo

  • @RyleChole
    @RyleChole 12 дней назад

    Kuibweretsamo ku njira zakalekale ndiko kubwerera ku zomwe Mulungu adanena

  • @RyleChole
    @RyleChole 12 дней назад

    Kummawa,Yesu ndi nyenyezi ya kummawa,nhanda,zonse zomwe mungatiuze mchipangano Chakale zinkaimirira KRISTU.

  • @RyleChole
    @RyleChole 12 дней назад

    Kristu nde chiphunzitso chomwe chidachokera kwa Mulungu ndipo Yesuyo anati mau a Mulungu nde choonadi,yYohane 17:17

  • @RyleChole
    @RyleChole 12 дней назад

    Ngati mukufuna mukhale ndi Lexicon chifukwa mmenemo muli ziyankhulo zitatu, Hebrew language,Greek ndi English.komabe ine sindimachitira kuti munthu amamvetsa mau a Mulungu chifukwa timamvetsa ziyankhulo koma chifukwa tili ndi Mzimu Woyera chifukwa wokhawo ndiye Mzimu wa choonadi Basi,komanso a Twaib musamakhulupirire zomwe anakuitanirani satana koposa zomwe Mulungu ananena, chifukwa funso lililonse bible Lili ndi yankho koma vuto nloti Inu mmachita refer nza satana lomwe ndi bodza chifukwa mau a Mulungu okha nde choonadi.

  • @RyleChole
    @RyleChole 12 дней назад

    A Twaib,njira zakalekale ndi mau a Mulungu nchifukwa chake ana a Israel skachimws amakhala kuti asiya njira imenyi nkani MULUNGU amawapempha ana a Israel kuti azibwerera kwa Mulungu chifukwa njira zakale ndi mau a Mulungu Basi.

  • @RyleChole
    @RyleChole 12 дней назад

    Komanso ku college sikuphunziridwa mau a Mulungu

  • @RyleChole
    @RyleChole 12 дней назад

    Koma okhulupirira sakhala ndi doctrine chifukwa iwo amatsatira mau basi

  • @WatsonManusha
    @WatsonManusha 16 дней назад

    Mulungu atithandize ndithu tidziwe zenizeni

  • @PreciousKamban
    @PreciousKamban 17 дней назад

    But you are too slowly straight to the point

  • @stephanoabraham6345
    @stephanoabraham6345 17 дней назад

    Basi ndasiyaa

  • @ShieldHenryHills-nm2wt
    @ShieldHenryHills-nm2wt 17 дней назад

    Ndine APOSTLE SHIELD HENRY PHIRI ku Zambia PETAUKE district. Ndine ofunitsitsa ku kumana ndi inu mtumiki wamulungu....ndilaka laka kwambiri mudzina la yesu khristu..mundi thandiza bwanji?

  • @GetruedAusten
    @GetruedAusten 17 дней назад

    Zikumandipsa coz anthu timaona nga zimene tikupanga ndizabwino kma palibe chi mene tichita nothing tingopepha molimbika kut tikule muuzimu

  • @RyleChole
    @RyleChole 18 дней назад

    Anthu anene amapitikiteidwa ndi ma Israel bible limati anali akuluakulu chifukwa Cain anali wa hybride yemwe anali mwana wa chigololo yomwe inali njoka.

  • @RyleChole
    @RyleChole 18 дней назад

    Mau oti Canan anapangidwa kuchokera ku dzina loti Cain chifukwa iwowa anali ana a Cain.Werengani Genesis 4:16...kenako muwerenge Gentiles 5:1...Mudzaona kuti pa Cain sipakuikidwa Adam monga bamboo kwa Cain koma pa Seti paikidwa Adam monga nakubala.werengani Genesis 3:20 Adam adamutcha mkazi wake Hava chifukwa ndi Mai wa amoyo onse nchifukwa Adam sakuikidwapo pa Cain ngati nakubala.

    • @RyleChole
      @RyleChole 18 дней назад

      Bible Ndiye choonadi chifukwa ndi zomwe Mulungu ananena osati zomwe zinachitika ki satnic ayi.Ana a Cain ndi omwe amatsogolera dzikoli mpaka lero ndipo satana amalamulira dzikoli kuzera mwa iwowa malemba amatero koma ngati simmaona kuti malemba akutero nthawi zonse muzikhulupirira zomwe nzonama.

  • @TrebuMalunga-sr2rz
    @TrebuMalunga-sr2rz 18 дней назад

    Mulungu akhale ndi inu pamodzi ndi ife

  • @TrebuMalunga-sr2rz
    @TrebuMalunga-sr2rz 18 дней назад

    Zabwino zonse atwaibu

  • @RyleChole
    @RyleChole 20 дней назад

    Ngati satana anakuuzani zimenezo amakunamizani,ndipo mudziwe kuti choonadi ndi mau a Mulungu lomwe ndi bible.werengani pa Genesis 5 pomwenso npamene akulondola za ana a Adam ndipo likukamba ndi Set yemwe anali mulowammalo was Abele koma Cain sakupezekapo koma ndipo Adam akuikidwapo ngati nakubala koma osati pa 4,,16 pomwenso akukambapo za Cain ayi.kawerengeni Genesis 3.20 akuti Adam anamutcha mkazi wake Hava chifukwa ndi Mai wa amoyo onse,mukawerrngenso pa 4.25 pomwenso akukambapo zakubadwa kwa Set ,makolo anati,Mulungu watilowezeta mbeu Ina mmalo mwa Abele, chifukwa Abele anali wosiyana ndi Set.yKofi Yesu sananene za chinthu chomwechii mfanizo la namsongole ntirigu kuti mbeu zonafesedwa ndi Mulungu komanso satana ndipo mbeuzo ndi anthu.,Kodi bible komweko silimalowedwa likukamba zoti ana a njoka Inu kapena ana a chigololo Inu.Atwaib ziulullani za ku satanic koma osati

  • @BeautyMtambo
    @BeautyMtambo 20 дней назад

    Mulungu alemekezeke kumwamba mulungu azikudalitsani kutiwulilila ku mwamba

  • @LontiaZimba-z4d
    @LontiaZimba-z4d 21 день назад

    Amen

  • @BrianDambula-b5g
    @BrianDambula-b5g 21 день назад

    Zikomo potichenjeza

  • @BeautyMtambo
    @BeautyMtambo 21 день назад

    Mulungu adzikudalitseni baba Twainu apitilize kikuwulilani zaku mbwamba

  • @BeautyMtambo
    @BeautyMtambo 21 день назад

    Ababa Inu mulungu azikuwululilani za kumwamba tiyeni tigwilanene manja

  • @BeautyMtambo
    @BeautyMtambo 21 день назад

    Mulungu atithandize ana Ake Apulezudenti athu tdegula maso baba mulungu akuyendeleni

  • @PróprioCassinganoCassingano
    @PróprioCassinganoCassingano 21 день назад

    Amen

  • @GenitoBento
    @GenitoBento 22 дня назад

    AMEN AMEN

  • @JamesChidothe-g6u
    @JamesChidothe-g6u 26 дней назад

    Amen