Utumiki wa a Twaibu - zokhudza achinyamata komanso magazi a anthu

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 19 сен 2024
  • A Twaibu akufotokoza zambiri zokhudza achinyamata komanso magazi a anthu

Комментарии • 28

  • @shakiraameen8001
    @shakiraameen8001 8 месяцев назад +5

    May our living God continue blessing and keeping you healthy for us in jesus name Amen 🙏

  • @EstaiajoaoveremosJoaoveremos
    @EstaiajoaoveremosJoaoveremos 8 месяцев назад +2

    From Moçambique beira amen

  • @BensonTembo-q4g
    @BensonTembo-q4g 6 месяцев назад

    Pastor twaibu you are doing a very good job you have transformed my spiritual life

  • @user-xh4bu5he9r
    @user-xh4bu5he9r 8 месяцев назад +2

    True massage Mr twaibu go ahead

  • @VioleBandason
    @VioleBandason 8 месяцев назад +1

    Amen ndithu brother mm tadutsamo m'menemo ngakhale mkazi amapanso zozigona yekhazo Mulungu atikhululukire

  • @dorothykalanda1742
    @dorothykalanda1742 8 месяцев назад +1

    Appreciate you thanks for your ministry.
    Kalanda Dorothy South Africa 🇿🇦 ♥️

  • @CosmasChikwindi
    @CosmasChikwindi 3 месяца назад

    Zomwe akulankhulazi inenso ndikudusamo😭😭😭😭

  • @SaraihKambatata
    @SaraihKambatata 8 месяцев назад +2

    Ineyo mulungu andikhuze chifukwa uthenga mwatengawo ndayendamo ndipo masiku akusaziwa muli ifa yamuyaya chifukwa muli uchimo

  • @Sonye-h9f
    @Sonye-h9f 4 месяца назад

    Uthenga wabwino ambuye akudalitsen 🙏

  • @LoseBauti-ju9ze
    @LoseBauti-ju9ze 7 месяцев назад

    Ambuye alemekezeke tadziwa kmanso taphunzilaa ambuye akudaliseni munthu wa mulungu

  • @isaackinod1256
    @isaackinod1256 7 месяцев назад

    True man of God

  • @ShentrycChinoko
    @ShentrycChinoko 2 месяца назад

    Abusa chonde gvm nambala komeleni mtima

  • @successngoma
    @successngoma 8 месяцев назад +1

    Amen

  • @Nadeon-y2k
    @Nadeon-y2k 4 месяца назад

    Ndimatsatila ma uthengawa koma ulilakiwu kuchokera kuno ku South Africa

  • @joeecoolkenzo7396
    @joeecoolkenzo7396 8 месяцев назад

    Twaibu I'm from Zambia 🇿🇲 was TB Joshua part of you guys 😢

  • @LysonZulu-p5r
    @LysonZulu-p5r 8 месяцев назад +1

    Nimayamikila kwambiri kuno ku Zambia

  • @AlexJosua-x2r
    @AlexJosua-x2r 8 месяцев назад

    From Mozambique Maputo ❤❤❤

  • @user-ei2yt3kf4x
    @user-ei2yt3kf4x 8 месяцев назад +1

  • @christophersankhani8635
    @christophersankhani8635 8 месяцев назад +1

    ❤❤❤

  • @Yabwata
    @Yabwata 8 месяцев назад

    Fusa pazakulela , timati kulela ndi oipa ndee tigwiliskenge tchito vichi .. to avoid preg..

  • @DilaGerald
    @DilaGerald 6 месяцев назад

    Bwana twaibu, ndakupezani mochedwa pa nkhani iyi ya chinyamata, ndaphunzira zambiiri, koma Izi Za menstruation, ine ine, zandichitikira Kwa Zaka zambiiiri pa umoyo wanga, Moti zanditengera mu mabvuto ambiiiri, mu zigololo zomwe ndachita mu Zaka zambiiiri, Kwa Zaka 50 Moti ma bizinezi anga asweka , Moyo wanga Uli chose kamba ka dzigololo dzosatha , ndachita dzigololo ndi akazi ambiiiri, chinthu Ichi ndikufunitsitsa chitandichoka, zonse mwachezezera ndi anyamatawa, ndazinva, Ndipo ndimakutsatirani mu ma Audio Anu onse, Ndipo NdadzIWA mochedwa, Ndipo ndikuoneka ngati watsoka. Ndipo ndanvetsa kwambiiiri, Mdikudzinvera chisoni Kwambiiiri. Ndine Gerald Dilla, Ku Lirangwe

  • @christophersankhani8635
    @christophersankhani8635 8 месяцев назад +1

    Mumanditsitsimutsa kwambiri

  • @reginajames5351
    @reginajames5351 7 месяцев назад

    Nanga anthu oti ali moyenda ngati maiko akunja koma mpata oti angaotche pad kuti atetezeke angamatani ???

  • @KeffasSimion
    @KeffasSimion 7 месяцев назад

    Fuso langa tsiku la lero nari.
    Kodi visible church ija munkanena titha umakumana bwanji, poti ndikaona ku 7 mitundu ya athu iri momo, ccap iri momo, ndingoti mipingo yambili mitundu ya athu yadzadza nditani kuti ndipezeke pa visible church?
    Monga atumwi adakhara oyera ntima nayenda mu mzimu umodzi, please please help me.
    Ntima wanga usautsika kuno ku kasungu west kamboni tc

  • @user-gp7tj4eg9o
    @user-gp7tj4eg9o 8 месяцев назад

    Ndili ndi fuso ....what if munthu walota kuti mnyamata yemwe ukundeta nayo wamulota katatu kuti siwako ndiye upange bwanji....umusiye kapena utani? Please please help