Nde makolo akudziwa 90 days anatani kukasuma pachiyambi Kufika pokhala ndi phone number ya bandela makolo mitu siwathandiza nawoso amangidwe amawonerela zopusa Vuto amuna ndi anthu odedwa hvy kusiyana ndi akazi 😊
Inu zopusa mwanakumalawi aliko anazipereka bwanji ali mwanakomaso bandera uzikhara serous boma lake ili unya nawe kuonjeza sikamba lot samakukana akazi Komatu ku ndende kuli sikizi uonapwanga
Aaaaaazh mutulusen bandera apo bii tizagenda😮😮😮
Zosayenda et eish mmmm❤ bandera
Aaaaa zaziiii tsikana WA zaka 14 ameneyoyooo zaugalu
Bandela mwayalukha
Kwaliji unyagotu kweleko baba chebandela wakasa ntesa
Inu zachamba zanuz ife ay wav et mwana amawoneka chocho Ife tikudauula zina ndy muztimwana za Ziii
Nde makolo akudziwa 90 days anatani kukasuma pachiyambi
Kufika pokhala ndi phone number ya bandela makolo mitu siwathandiza nawoso amangidwe amawonerela zopusa
Vuto amuna ndi anthu odedwa hvy kusiyana ndi akazi 😊
Mai opusa kwambiri,ngati chili chibwezi ndipo amadziwa kwa miyezi iwiri bwanji sanakamang'ale same time.
Kusonyeza kuti ntsikanayo akadabwelera kunyumba tsiku lomwero Amai wo analibe nazo ntchito eti?
Atsikana ongokhala onsewa?
Uchawa, kumusiyirira mwana kumapanga zauhule
Ndil ku court live ndi Bandera apapa MH court
Mwanayo mmayesa anasankha yekha,,nawonso makolowo
Mwamanga chinkhoswe pamenepo
Let's pray for him hope some hrs akhal mfulu
Bandera atuluke mwana
Mwana wachepa kwambiri akuyenera kumangidwa
Mwamuona mwana yo koma???
Kanema mpk 2days 😂😂😂😂
Inu ndiachisilu mwamva mwana wa zaka 14 ankhala bwanj ndi digree
Jeledyo dyausilu mwana amakhala chomcho
Atuluka
Inu zopusa mwanakumalawi aliko anazipereka bwanji ali mwanakomaso bandera uzikhara serous boma lake ili unya nawe kuonjeza sikamba lot samakukana akazi Komatu ku ndende kuli sikizi uonapwanga
Mtsikana wamkulu
That's not wat really happened
Pomumanga bandera awonese kut apeza umboni weniweni woveka ngati sikana yemwe akuweneka kuti ndiwakulu kaleyu àngonedwa koma ngat zili zaboza pofuna kuyipisa mbili yàke wachiyawo ziñdikilani kut ifeso malamulo tikuwàziwa ndiye kut khani ivuta chifukwa aliyese Ali ndi ufulu samalani
😂😂😂😂Pepan
Zausilu bas khalambayo imene ija ingakhale yazaka 14 kagwilen uko
A police akumalawi ndi agalu
Uchitsilu
Ndimamufila