We thank God to bring Mr Kabambe I think you're chosen by God Please Mr Kabambe Don't change because of people Rescue Malawians becoz they're suffering 😢😢🙏🙏
Nanga apitesotu azikwanje aja amavala gule aja.Aone akasendedweko mphuno kumeneko......!!!! I never ever seen a woman like you more specially for what you have done Thanda. You're a really freedom fight. Congratulation to you Thanda 🎉🎉🎉🎉❤❤❤
From Thabwa, Fatima Road in very bad shape. Nthanda, a star illuminating lower Shire development. You deserve to be called a Grand Lower Shire Development. Representative.
Let me tell him mr kabambe mene mukuwonese kwa a Malawi and sitinawonepo or mozi akupanga ngat iweyo koma apapa next year inu nd Boma people come and join UTM ❤❤❤❤❤
ku Malawi kuno for anything to work zikungoyenera kutopa basi kuuzana reality akwiye akwiye. people in offices dont work for the people but for their mimbas
Nthanda wishing you well as you keep on pushing this Roads Authority to make sure that Chapananga bridge , Gwanda Chakwamba etc has to be fixed properly,,,, She's one of those interigent in Malawi let her represent youth in Mw
Akabambe woyee I like mr Kabambe because everything in there position Akabambe ndi munthu olimba mtima Ndichifukwa chake china chilichonse chimamupeza mu nthawi yake A good leader is like that
Muuzeni uyo akalire Kwa Peter Mutharika ndiyemwe wakhala akumupangira campaign, nanuso a times mwasowa Zochita, wakhala akutukwana Boma pa Tik tok ameneyo,
My home needs development sure; big up Nthanda, Proud of you!!!!
Very intelligent girl deserve to be MP into Parliament. Keep up girl
Dr Kabambe mwayankhula bwino tu...bwino tu akubelani nzeru zanu ...........ndazikonda❤❤❤❤❤
Akut mwana opanda nzeru or umuuzile amaluzabetu paja😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
We thank God to bring Mr Kabambe
I think you're chosen by God
Please Mr Kabambe
Don't change because of people
Rescue Malawians becoz they're suffering 😢😢🙏🙏
Dandawulo limveke mwanayi akudandawula zona
You have inspired me young lady, keep the fight.
No matter that they have coached her but what we need is serious solution as she said, big up sister.
No one coached her but she stands for the people from her Area so don't say what you don't know.
Dr kabambe iweyo ndimuthu osazikonda akanakala wina sakanayima pamenepo koma mulungu Ali ndcholinga pa Dr kabambe god bless you ❤❤
Nsikana olimba ntima mwanzelu God bless you
Bravo kabambe bravo Fredokiss Bravo Khumbanyiwa❤❤❤
Kabambe woyeeee ndiwe Muthu ozichepesa
More fire Thanda, Kabambe and your team
Kabambe wawina vote yanga bc ❤❤❤
Our next MP, Thanda
Dr Kabambe is deserve to be a Malawi next President he has good idea
Koma ndalira ine kukumvera kwathu chisoni Given our fighter keep it up
Great work girl
When Dr DK steals Nthanda's show ❤❤❤❤❤❤ Bravo vote my support
🎉🎉🎉🎉🎉🎉viva Malawi viva freedom fighter
Bravo Nana iweyo ndi 1 palibeso ..big up 💪
❤ mbambandetikufuna anthu ngat awa
Nanga apitesotu azikwanje aja amavala gule aja.Aone akasendedweko mphuno kumeneko......!!!! I never ever seen a woman like you more specially for what you have done Thanda. You're a really freedom fight. Congratulation to you Thanda 🎉🎉🎉🎉❤❤❤
Ndalowa UTM lero
Welcome dear❤❤❤❤❤❤
Ine ndinalowa after convention ❤
@emmanuelkenneth4768 zamphavu❤️❤️❤️❤️
Wafika iweyo🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Ife tinalimomo kare sitinagwedezeke.... More 🔥 utm osaopa osatopa osafooka...kc mau. Anatisiyila💪
Thanks sister you share mind to people and encouraging fight to them corruption 😂😂😂😂😂 kabambe woyeeeee😊
Dr kabambe deserve to be next prezdent💕💕 Nthanda my Daughter Big up never give up
From Thabwa, Fatima Road in very bad shape. Nthanda, a star illuminating lower Shire development. You deserve to be called a Grand Lower Shire Development. Representative.
What a brave girl,,liked ur bravery ❤
Nthanda congrants to what you have done we need good girl like you
Izizi 😂zipangitsa Amalawi kuzindikira
generally kkkk
Usamati a Malawi uziti amalafe uzazichoso😂😂😂😂
Kkkkkk ali ku America. 😅😅😅😅😅 Ameneyu
Let me tell him mr kabambe mene mukuwonese kwa a Malawi and sitinawonepo or mozi akupanga ngat iweyo koma apapa next year inu nd Boma people come and join UTM ❤❤❤❤❤
Koma cameraman 😂😂😂 wamuzumulatu mkazi wa ma hip wa miyendo yotambalalayo 😂😂
We need people like her
Nana, mwadokera. A big hand to you.
Rumphi nyika we are the next tikubwera konko
😂😂😂😂😂😂😂😂🎉🎉🎉🎉🎉
Sounds great, really their is potential for development in the lower shire, kudos for excellent argument
Thanda I'm so proud of you keep it up UTM more fire 🔥
Bola Asasowetsedwe🤢
Malawi Waipa pano......we dont know who Trust anymore..
Malawi is Doomed..
And t needs a serious deliverance....
Am crying for her strength. She is a freedom fighter.
I like the courageous in her! We citizens need to demand what we deserve
Ndakomerwa maningi nana. Pyachita iwe nkutumbula nyamkalimbwi na munga wa kanjona! Thimiza kugogoda nyoka pa msolo! Maji akwathu kuno ambawera akunjipa maningi, tinaphata muti upi mvula akatoma kudima??❤❤
Ameneyitu ayankhidwe zomveka izi ndiye zikufunika munyengo ino
Akufunika mumupase u MP mwina azagwilisa bwino ntchito CDF
Federal system of government, ikufunika ku Malawi kuti mu dzigawo mudzikhala mpikisano wa dzitukuko.
Amen.
🙏🏾❤️🇲🇼.
Kabambe akangoyamba Campaign ambiri alira😢😢
Ndipo osakaika😂😂😂😂
Ngati akabambe alondola achita bwino kwambili tiyeni timupase molalo amalawi tiziphuzila
Congrats for what you have done Nthanda keep it up ❤
We need pipo like you to be with us in UTM❤❤❤❤❤❤❤
Proud of you nthanda God be with you always
ku Malawi kuno for anything to work zikungoyenera kutopa basi kuuzana reality akwiye akwiye. people in offices dont work for the people but for their mimbas
Government of Malawi imatisala kwathu and we don't deserve to vote any political candidate because of that ndikanakonda nditampanga join koma nana
Dr kabambe is very clever big Bren
Nthanda wishing you well as you keep on pushing this Roads Authority to make sure that Chapananga bridge , Gwanda Chakwamba etc has to be fixed properly,,,, She's one of those interigent in Malawi let her represent youth in Mw
Mitsonkho ya Malawi izioneka kagwilitsidwe kake Ntchito.zomankhala chete ndi izo akungonkhutitsa mimba zawo.keep up the good work nana tili ndulimo
Akabambe woyee
I like mr Kabambe because everything in there position
Akabambe ndi munthu olimba mtima
Ndichifukwa chake china chilichonse chimamupeza mu nthawi yake
A good leader is like that
DR KABAMBE 2025 BOMA UTM MY VOTE ❤❤❤❤
Sister inuyo kulimba tima kumeneko musasiye pali anthu ena atengelepo nzeru
Be careful azitsogoleri generation ino yabwera mwa coming 🔥
Chemwali anga mukukhala ndinzelu ngat mamuna koma osati mamuna wake ogodomala ❤❤❤
My sister tell them
When they like it or not
They must do something
Take it or leave it they must do something
Bola asakufinyeni sister proud of you
Mantha amenewo?
Kuyankhula tu mchizungu ndi chichewa same same ,,he has not missed any point spoken in Chichewa to English....
Dr Kabambe❤
Mr kabambe deserve to be next prezdent
Izi zithandiza azingozizimuka mademo ayambika .sister ulemu wanu
Mmene akugwetsera kwacha,sakunena Ife kumangomvera kushop Kut yagwatu usiku wathawu nafenso mademo azingoona Gululu ngat pa mikozi kkkkk
Kodi ineo sindnamumve Dan Lu akutchula Za chapananga bridge Kuti amanga Adadi munyimbo ya winanso Ayi?
Bravo koma azumula mkazi wa shape eeee😂 camera man salibwino
Msikana uyu sakufuna ndalama akufuna chitukuko mwana uyu ndi wamaso mphenya a malawi enanu simuganiza za pasogolo ndichifukwa chake mukuthandizila kugwetsa dziko ndinu posapota chakwera
We need young presidents like him ,,new blood not going back to Egypt,,,nooooooo
AZIKWANJE AJA ALIKUTI 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Am very impressed
Big up brave lady
💪💪💪💪💪💪thanda 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
We must also hold accountable to our MP, they just chop our taxes
Zili bho sister mwatipatsa nafe nyonga nseu wakwathu nafe mavuto Makanjiea road nafenso tipita konko ipatse moto 32:44
UTM❤
This guy is a genius
I'm proud of you my sister I am from Chapananga
Achinyamata tidzuke it's our time bravo Nthanda
A minister Ali konko koma tulo
Big up nana❤
Ulemu wanu sister osawaopa anyaniwa anavoteredwa ndi mmalaw aliyese osat akwao
I like it that you can speak fluently your language, enatu mmm sangathe
Let's be proud of our roots.
Ne soti nulawira ngako chakwasu.
We need pipo like you daughter
This government is finished
Thy don't know what thy are doing
Muuzeni uyo akalire Kwa Peter Mutharika ndiyemwe wakhala akumupangira campaign, nanuso a times mwasowa Zochita, wakhala akutukwana Boma pa Tik tok ameneyo,
Usova ,chimene ukuziwapo ndichimenechoncho?
Nyapapi mzanu akupanga za mzelu inu bizy kutsutsa vuto lokonda kuzikonda wekha phwala iwe
Aka tear gas lero kulibe?
Bravo bravo bravo Khumbanyiwa umakwana iweyo
Ine ndingoseka Kaye 😂😂😂😂😂
Dr. Kabambe ndi Pangolin 🔥
Bravo Thanda this country need courageous people like you
Ndizoona wosamaletsana mademo ndimangoponya matiye gasi kumangodya ndalama
Azikwenje lero bwanji,koma Malawi akufunika anthu alikonda ziko NGAt inuoo
💔🖤💚 Nzika Patriots indeed 👏🏾👏🏾👏🏾👌🏾
Ntanda ndili pa mbuyo pako Kuno kumangochi❤
Ulem wan cct mumatiimilila thanks
Did she submit the petition..??
Good idea
Big up Nana nthanda iweyo ndi 1
Mulungu akumbukile Malawi 😢😢
Need more supporters this girl please Malawi workup
Aglades Ganda alikuti,nanga Mandevana alikuti ,nanga Dosi alikuti,Chomanika yudasi alikuti,nanga Khumbanyiwa alikuti, Bagass alikuti, nanga Abida mia ulikuti nonsenu ndakutchulani ndinu anthu omvesa chisoni kwambiri mukutaniko kuparliament mumagwirako ntchito yanji musazabwerekonso Kuno mwamva
Malawian Cameras ur great
Kwathuku ambabwera amadungwe nakupasani ma water pump amajambula chimanga chawanthu kukhalangati kuti anthuo anawathandiza zimbava zikuxikulu ,
Usaiwale pa phanga bridge Kms pamkombedzi pa mchalo
Koma kungotheka misewu imeneyo komaso ma bligewo zikwangwani zankhope yanthanda zisadzalephele akumenyela ufulu oopsa
Nthanda zikomo kwambiri mulungu akuthandizire mu dzikhumbokhumbo zako
Great point.....
Great mind...
Mindset change....
Big up.