BON KALINDO - ATUPELE MULUZI + UDF - UTM YONSE YAFIKA KU AREA 30.

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 24 окт 2024

Комментарии • 68

  • @HaleemaAllie
    @HaleemaAllie 3 часа назад +8

    Atupele muzipanga zimenezo anthu akundani kwaabasiiiiii❤❤❤❤❤❤❤❤❤ bonikalindo motooooo kuti buuuuu

  • @SaudhaKatete
    @SaudhaKatete 3 часа назад +3

    Aaaa I salute u the DC may Allah reward n bless you

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 3 часа назад +2

    The dc mwana wolimba mtima malema wa kumalawi 😂😂😂😂❤❤❤❤❤

  • @UncleShopRite
    @UncleShopRite 3 часа назад +1

    Kalindo our president

  • @AustinNangwale
    @AustinNangwale 3 часа назад +1

    The true definition of friend ❤❤❤

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 3 часа назад +1

    Kaya Kalindo ndizampase chani kaya Ambuye sogoleren Kalindo

  • @Mohammed-sk1fy
    @Mohammed-sk1fy 3 часа назад +1

    The Pangolin Dangerous Child Bon Kalindo ❤❤❤

  • @amontchuwa6876
    @amontchuwa6876 3 часа назад +2

    Bon kalindo more fire 🔥 ❤❤❤

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 3 часа назад +2

    Atupere pamenepo wayambapo mkupasa vote ukapitiliza

  • @ChristopherKawilam
    @ChristopherKawilam 3 часа назад +2

    Our own DC 💪💪

  • @AkibuMdala-sr1dy
    @AkibuMdala-sr1dy 3 часа назад +1

    The DC umatiyimilila❤❤❤❤❤❤❤

  • @McMillanChikalasa
    @McMillanChikalasa 3 часа назад +1

    More fire mr kalindo mumatiyimilira!!!

  • @EvanceHorresie
    @EvanceHorresie 2 часа назад

    Machine mumakwana big musadzafe bon kalindo

  • @FlorenceDouglas-x5c
    @FlorenceDouglas-x5c 3 часа назад

    Kalindo anakoza 💞,,,mwaitha🙏🙏

  • @MacleanManda
    @MacleanManda Час назад

    Solidarity ✊

  • @miriammvanda3404
    @miriammvanda3404 3 часа назад +1

    more fire Kalindo

  • @LindaChikwawa
    @LindaChikwawa 3 часа назад

    More 🔥🔥🔥🔥Mr dc

  • @amontchuwa6876
    @amontchuwa6876 3 часа назад +3

    Wayamba umnthu sopano Atupele

    • @DOLADAUSI
      @DOLADAUSI 3 часа назад

      Wabwerako🤣🤣🤣

    • @omardyman8083
      @omardyman8083 3 часа назад

      Kaya amwene anthu sakuwafuna ndikale kumazipalamulilabe basi uku kwangozazana anthu amamina mmitu okhakha

    • @WisdomChimalizeni
      @WisdomChimalizeni 3 часа назад

      ​@@DOLADAUSIanali kuti????samangopanga zinthuti ameneyo

  • @DanielJuwawo-s5n
    @DanielJuwawo-s5n Час назад

    Kalindo kuchita kuposa chakwera ma sapota

  • @MagretSaizi
    @MagretSaizi 3 часа назад

    Koma kwayakakat ku 30 mpaka ku court woooo

  • @MikeLodzi
    @MikeLodzi Час назад

    BON KALINDO
    MWANA OWOOPYA KWAMBILI

  • @HadijaKamwenendo
    @HadijaKamwenendo 3 часа назад

    Ine chonena ndilibe abale😢😢malawi malawi

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 3 часа назад +1

    Koma chakwela akuva kupwetekani ndi ulamuliro wakewu

  • @PatriciaAlomwe-oz8wc
    @PatriciaAlomwe-oz8wc Час назад

    Kalindo bwelan kwathu muzatenge kalongonda mwana wakwathu iwe

  • @getrudeminikwa9636
    @getrudeminikwa9636 3 часа назад

    More fire ipatse moto

  • @BerthaMkwinika
    @BerthaMkwinika 3 часа назад

    Dziko lonvetsa chisoni kwambiri,anthu ena azimangidwa ena ayi chonsecho onse alakwa

  • @MustapherLino
    @MustapherLino 3 часа назад

    Chikangawa akumva bwanji

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 3 часа назад

    Ok ndafunila mafuno abwino mai kalitati boma

  • @WestonOzuwell
    @WestonOzuwell 48 минут назад

    Nchto ipitilire timakunyadan ma bigy

  • @lacksonsiyadi943
    @lacksonsiyadi943 3 часа назад

    The dc mmm ndikatundu

  • @WhyteSmart
    @WhyteSmart 3 часа назад +2

    Mukuzipalamuliranji izi inu A MCP,kkkkk

  • @ChindikanChipeta-f3u
    @ChindikanChipeta-f3u Час назад

    Koma inu a MCP tikangowina kuyambla president tizumumanga mpaka kumusi mbuzi inu

  • @sthoramexjrsa902
    @sthoramexjrsa902 3 часа назад +1

    Madala madara😅😂😂😂😂🔥🔥🤣🤣😹💪💪💪💪💪

  • @EmsAdam-c1i
    @EmsAdam-c1i 2 часа назад

    Zilibwino kwambili anthu kumakungana choncho asakatitole

  • @LetshaChirwa
    @LetshaChirwa 3 часа назад +2

    MCP ziwan KT Malawi si wachakwera

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 3 часа назад +1

    Mcp chipani chopanda nzeru ichi

  • @StephanoChimwala
    @StephanoChimwala 3 часа назад +1

    😂😂😂😂😂😂kwamvuta kumalawi

  • @WilisonWilliam-d9j
    @WilisonWilliam-d9j 3 часа назад

    ❤ the dc ichi sichiopa.chapit.koko.

  • @EvanceHorresie
    @EvanceHorresie 2 часа назад

    Good luck

  • @ELLENZAPS
    @ELLENZAPS 2 часа назад

    Zkm kwambili akalindo ambuye azikutsogolelani

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e 3 часа назад +1

    ❤❤❤

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 2 часа назад

    Osati onse otsutsa ayi koma ya mmalawi aliyese,amene anabadwa ndi umunthu.police, imeneyi amalawi tagawanani wache wache kuwatyola apolice a usilu

  • @HassanTwaibu-c6h
    @HassanTwaibu-c6h 3 часа назад +1

    tiyeni guys tili limodzi pakana pamapeto

  • @mbaliehaward947
    @mbaliehaward947 3 часа назад

    Koma the DC umakwana

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 2 часа назад

    DC ❤😂😂😂

  • @nicolamarr7420
    @nicolamarr7420 2 часа назад

    Tikudikila ma repot akucourt

  • @KingsleyufuluChawawa-xx2qn
    @KingsleyufuluChawawa-xx2qn Час назад

    Osamatinamiza inu mwamva

  • @kangungufoundation2020
    @kangungufoundation2020 2 часа назад

    Ignorance will not rule our good country

  • @AgerbonMaulana
    @AgerbonMaulana 3 часа назад

    Malawi okomaaaaa😂😂😂

    • @HabrilMalaya
      @HabrilMalaya 2 часа назад

      😂,😂😂 okomera tonse 😂😂😂

  • @TiamikeMbalati
    @TiamikeMbalati 2 часа назад

    Moto kuti buuuuuuuuu

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 3 часа назад

    Tupere boma likumvunika 2025

  • @mphompho6652
    @mphompho6652 3 часа назад

    Where is Manganya??????

    • @WysonChilonga
      @WysonChilonga Час назад

      Manganya manyazi bwa?,dyera likuphetsa,usamale😢

  • @IbrahimJasiten
    @IbrahimJasiten 3 часа назад +1

    Koma

  • @RuthTungande
    @RuthTungande 3 часа назад

    Kumalawi mkokoma athu timakondana mwachisisi

  • @kekeaufi9834
    @kekeaufi9834 3 часа назад

    🎉🎉🎉🎉🎉

  • @TamandaniMaseya
    @TamandaniMaseya 3 часа назад

    The Dc

  • @ChixomoPeter
    @ChixomoPeter 2 часа назад

    Km ziliko

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh 3 часа назад

    The fall of mcp

  • @PriscaMussah
    @PriscaMussah 3 часа назад

    Kod akut alakwa chan

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 3 часа назад

    The DC

  • @ChembeWaimba
    @ChembeWaimba 3 часа назад +1

    Timve kaye kuti anatani

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 2 часа назад

    The DCCCCCCCC

  • @IbrahimJasiten
    @IbrahimJasiten 3 часа назад +1

    Koma