Chipani Cha PP chati report la ndege Lawanamizira pa nkhani ya ndalama.

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 19 дек 2024

Комментарии • 51

  • @LucksonChipofya
    @LucksonChipofya День назад +10

    Basitu ayamba okha kuziwulura zotsekana pakamwa ndalamatu zimenezo koma ayi ndithu kulikumangidwa chaka cha mawa ine pheee kudikira

    • @ronaldordinga6537
      @ronaldordinga6537 День назад

      Ku Malawi zomangana ngati andare sizimatheka pokhapokha achina alexicius kamangira alimbikire kumenyera katangare

  • @AaronPaulos-j7g
    @AaronPaulos-j7g 22 часа назад +1

    It was a good move by Government to support political parties during the vp funeral koma zonamazo mmmh zitha kukuganizista pambali kapena Pali report yina ya 9.5 million

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda День назад +2

    Mulungu si James ayamba kubwebwetuka okha ..tiziona chaka chino mpaka 2025

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx День назад +6

    Pp kusava chokan kumeneko osava mwaon ayambakjkunamidzilan

  • @BerthaWasi
    @BerthaWasi День назад +2

    Kod chipepeso chowapasa a PP kut atani? Anakhuzidwapo bwanj pamaliropo?

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v День назад +1

    mtima wanga dekha aka sikoyamba kumangisa katundu chakwera ndi gulu lake kuchosa ndi mvote yanga

  • @mwale86
    @mwale86 21 час назад

    Zinthu zimenezi zimachitika with all state funerals with Kamuzu etc nkhani ndiyakuti akuti pp inalandila 15 million pamene sizinali choncho

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel День назад +2

    Imfa ya SkC anthu anadyera nazo ndalama

  • @WonderfulChibisa
    @WonderfulChibisa 20 часов назад

    Anthu akuba awa akuyaluka nazo izi.

  • @FosterZulu-b3j
    @FosterZulu-b3j День назад +5

    Ndalama imeneyi amati ndiyachani kodi powapatsa app ngati chipani?

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj День назад +1

    School ndi yofunikadi Mesa pamenepo anthu ena akuchipaniwo ndiye akuziwa za ndalama zomwe adalandira ndiposo ndalama zomwe adatenge chilima ngati chipepesa zonse zidasowa not kuti adapezapo zina English anthu sakuivetsa

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr День назад +1

    Kuba mudzina la MALIRO, shame. Komanso mwina za 5million zija angonama powona kuti SKC kulibe kuti asutse izi.

  • @patassonelucaszovuta3431
    @patassonelucaszovuta3431 День назад +3

    Kodi mukuti pp idalandila mdalama zinali zachiyani amawapatsa kuti ndiza chiyani tapitilizani bwino bwino

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  День назад +1

      @@patassonelucaszovuta3431 Chipepeso

    • @HanifaAdam-tm9yv
      @HanifaAdam-tm9yv День назад +1

      Amaapepesa kt atani??​ bwanji sanapepese UTM?? Kapena mu ndege muja munalinso wa pp???

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 День назад +2

    Aaaa kodi ndalamayi nkhani yake yamalilo achilima NGATI NDIKUMVAPO BWINO NANGA AMAPATSA CHIFUKWA CHANJI KWASEKA PAKAMWA NKHANI ZAKE SINAMVEPO BWINO

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  День назад +1

      Akuti Yachipepeso

    • @BerthaWasi
      @BerthaWasi День назад +1

      Chipepeso kut atani?​@@MalawianCamera

    • @MosesDicostar
      @MosesDicostar День назад

      Chipepeso chimayenera kupita kumabanja ofeledwa

    • @MemoryZiyaya
      @MemoryZiyaya 22 часа назад

      Nane ngt mkuzivesa...anthu awawa ndioononga ndithu..chipepeso chotani chopasana azipani. Kuti atani iwowo..mxiim atichimwisa

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy День назад +1

    Khaniyi sikumveseseka kod muthu uja anali wa pp??

  • @ZaharahYusufu-i9l
    @ZaharahYusufu-i9l День назад +1

    Ndalama zidapezekazo sizidali za chilima zidali za anthu enawo zachilima zonse zidasowa

  • @dianachabs
    @dianachabs День назад

    Ndinu opusa , Kodi osamatuluka muzigobamo bwanji kuti miziyankha bwino ? Moti ngati kangawude

  • @peterkakhome6976
    @peterkakhome6976 День назад +3

    Ndalama zantchito yanji pa maliro a eni?

  • @chiletsokazembe-ri4ic
    @chiletsokazembe-ri4ic 15 часов назад

    Koma ma channel anuwa mumangotsula mulibe ma program et

  • @twaibupatrick-k1n
    @twaibupatrick-k1n День назад +1

    Komano ndalama zimenezi amati ndizachani

  • @listonnantapo1670
    @listonnantapo1670 День назад +1

    Ndalama zomwe zinapezekazo sizikukhuzana ndi K5,000,000. Yonse anapakula.

  • @RitaNyaude
    @RitaNyaude День назад

    Osabwera pano without clear evidence, pp yalakwa chani ah

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg День назад

    Kodi ndalama zomwe zimapasidwa zipanizi zinali za chani? Ali ndi mayankho ogwirika ndiyankhen

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani День назад

    Bola Mulungu atisungre moyo timva zambri ndpo sikunati muuluran enati akupemphera zolimba ndpo Mulungu avumbulusa ndt bola moyo guyz

  • @innocentlipita3630
    @innocentlipita3630 День назад

    15million 700 million kwacha doesn't make any sense

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i День назад

    Azanga mwafunsa bwino kobili imene inapatsidwa a PP ndi ya cani? Ngati cili cipepeso amamupepesako ndani? Cifukwa cilima anali wa utm. Kalipo, kalipo tiunikepo gys omangidwana achuluke.

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe День назад +1

    NDÀLAMAZI ZOKWANIRA K15 MILLION KWACHA KWA PP KWA AMAI JOYCE BANÐA YANTCHTO YANJI? KUTI AMAIWA A JOYCE BANDAWA NDIOMWE ANATHANDIZIRA KUPHA A DR KLAUS SAULOS CHILIMAYU.? AFOTOKOZERE AMALAWI CHIFUKWA CHOPATSIRA NDALAMA YONSEYI KWA JOYCE BANDA WA CHIPANI CHA PP..

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 20 часов назад

    NKHANI NDI YOTI KODI NDALAMA ZOMWE ZIPANI ZIMAPATSIDWAZI NDI ZACHANI ? APAPA PAKUONESA KUTI ZIPANI ZIKUDZIWAPO KANTHU PA IMFA YA CHILIMA ZIULULIKA KALIKONSE TIKAONA EEEEEE OSADZAKHULUPIRIRA ANDALE GUYS

  • @peterkakhome6976
    @peterkakhome6976 День назад +1

    Maliro a utm, pp ikhuzidwa bwanji?

  • @JasonMailos
    @JasonMailos День назад

    Ose amapanga kafuku fuku Aja anili a MCP tinakuuzani

  • @MariaNkhata-i9q
    @MariaNkhata-i9q День назад

    Boma la anthu opanda nzeru ili

  • @alickmathias2097
    @alickmathias2097 День назад

    Ndalama ndiyovuta

  • @mkajikosya-uq5hs
    @mkajikosya-uq5hs День назад

    Si PP yokha angakhalenso UDF inalandira

    • @chifundocharles2348
      @chifundocharles2348 День назад

      Kod UDF inalandira kut yatan? Coz zikudabwitsatu😢😂😂

  • @FrankFrancis-ch3xv
    @FrankFrancis-ch3xv День назад

    Dziko lazibwana kwambiri zoona boma lingapereke ndalama ngati imeneyo kuchipani cha pp for the chilima's death condolences,for what

  • @IBRAHIMRAJAB-l3c
    @IBRAHIMRAJAB-l3c День назад

    kkkkkk ok

  • @IgnatiousFote-i7g
    @IgnatiousFote-i7g День назад

    fifteen million and seven hundred kwacha osat mbwelera zakozo ai

    • @EmmanuelGasiten-fo5dr
      @EmmanuelGasiten-fo5dr День назад

      Ayi iwenso mbwelera, ndi fifteen million and seven hundred thousand kwacha.