AKU DPP NDI AFITI GUYS...MPAKA CHAKWERA KUMUTELE KU PARLIAMENT ABALE?

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 19 дек 2024

Комментарии •

  • @Steven-q4u
    @Steven-q4u 23 часа назад +14

    Chule iwe chizungu ndi nzeru yoyendetsera dziko umbuli okha okha akulu inu !!!

    • @HenryBanda-wh6gg
      @HenryBanda-wh6gg 21 час назад

      Chile ndi amako anakuberekawo

    • @kechu289
      @kechu289 3 часа назад

      Nsanje iyooo. Chakwera, osanama, amayankhula monveka bwino. Ndiye akhale chule chifukwa chamomwe amayankhulira? Nanga in Mujahideen mumayankhulira muja mukhala chiyani?

  • @BakhePaliso-h8h
    @BakhePaliso-h8h 21 час назад +5

    Mukutiuzakut tigulise chimanga tigule fetereza chimanga tichitenga kut anthu tikusowa chakudya

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 21 час назад +2

    AAAAAAS IWE UKATI A DPP NDI AFITI UFITI WA DPP UNGAPOSE UFITI WA MCP WAKUPHANAWO CHILIMA MULIBENZERU AGALU INU ANA ACHIKANGAWA ,CHAKWERA NDI MCP NDI AFITI OTHERATU ANTHU OPANDA CHIFUNDO NDI NZIKA ZAWO ANTHU ONGOFUNA KUKHUTITSA MIMBA ZAO , MUMAIKIRA KUMBUYO MCP CHONSECHO MUKUDYA CHITEDZE , FERTILIZER MULIBE , MUKUTUPIRANA NDI NJALA KOMA KUMAKAMBA ZOPUSA KUIKIRA KUMBUYO AFITI A MCP MUNYATU SIMUNATI NDIYE WAKANIKATU KUFOTOKOZA KUTI KODI NJALA INGATHE BWANJI KUSONYEZAKUTI MUDAKADYABE CHITEDZE NYEKWE YENIYENI

    • @RichardHetekere
      @RichardHetekere 15 часов назад +1

      Ine ndilibe chipani komano chikangawa no no no non no 😂😂😂😂😂

  • @Marymahendra
    @Marymahendra 11 часов назад +1

    That’s his job not just getting paid for nothing by the law he should go to permanent every day

  • @KalimaImedi
    @KalimaImedi 11 часов назад +2

    Mmmm Achakwela Kupha chilima chifukwa cha ndalama. Ayi zikomo popeza ndiwe wamuyaya Zonse tisiyila mmanja mwa Mulungu mwini wake 😢

  • @michaelkunje5370
    @michaelkunje5370 11 часов назад +2

    Mbuli ya president 🚮

  • @RuthJopilo
    @RuthJopilo 21 час назад +3

    Mfiti ndi chakwera ndi boma lake.

  • @KalimaImedi
    @KalimaImedi 10 часов назад +1

    Mukamat ku oposion kulibe oziwa chingelez Anthu amadya chingelez? Anthu akufuna mafuta,chakudya feterizer osat chingelez chanucho ayi .Zija zachitika ku chikangawa zija zabwino? Kupha chilima zabwino? Oziwa chingeleziwo amapha Anthu mmbusa otan

  • @EnifarSeleman
    @EnifarSeleman 12 часов назад +2

    Ine ndikuona kuti mr pule apite kaye ku Zomba mental sizikuyenda taa

  • @PaulChibakuwa
    @PaulChibakuwa 5 часов назад

    Chakwera should change his mind set if he wants to gain people's attraction

  • @danielstorey5655
    @danielstorey5655 4 часа назад

    What I know Chakwera mngobgoyankhula pa ground zimamuvuta... dziko likufunika munthu ngat Chilima yemwe sadzapezekanso tiyen tibavutika ndachewa osaphunzirawa akutilamulira demet

  • @JohnChitsulo-q6f
    @JohnChitsulo-q6f 18 часов назад +2

    😂we don't have leadership in our country

  • @IvyMkhura
    @IvyMkhura 3 часа назад

    President wakoyo ndamene alibe mzeru, umafuna opposition izisekelera zopusazo?

  • @JimmyMaster-l1x
    @JimmyMaster-l1x 21 час назад +1

    Chakwera mutu wake sukugwila kuyankha mafutso si solution yothesera njala

  • @EDGARMPIKAMEZO
    @EDGARMPIKAMEZO 23 часа назад +2

    Ndale za ku malawi ndi nthabwala zeni zeni 🤣🤣 President wadziko kukayankha mafunso kunyumba ya malamulo yomwe mtsogoleri wake ndi wachiwiri wa president ku chipani. 🤣🤣🤣 A Malawi tilinso ndi vuto losadziwa malamulo athu a dziko

  • @FelixMakumbi-r6k
    @FelixMakumbi-r6k 13 часов назад +1

    2bags yachimanga ichokela kuti akulu igwa kumwamba

    • @benjulius6070
      @benjulius6070 8 часов назад

      Guys chakwela ndiochimwisaaaa😅😂😂😂

  • @fulbertkalongonda5171
    @fulbertkalongonda5171 5 часов назад

    Mr President, be able then to let Malawians now that you are been sponsored on your trips

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august Час назад

    Dr Lazaro Chakwera do you now meaning of the name of Lazaro it mean waumphawi osauka opanda nzeru osaganiza bwino ndiye tathauzo la dzina limeneli musazayese kupasa mwana wanu dzinali pankhomo sipangayende olo banja ngakhale ku tchito palibe chingachitike chilichonse chimakhala chokanikani

  • @zamanmwachumu554
    @zamanmwachumu554 17 часов назад

    The sound from the house is very poor sitikunva BS plz

    • @bs-malawi
      @bs-malawi  17 часов назад

      @@zamanmwachumu554 Oooh sorry, next time we will try to improve

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo Час назад

    Chiphaphalitseni ndi mafunso chimenecho

  • @wisdom20mkango49
    @wisdom20mkango49 22 часа назад

    dpp ikawina will be a mistake of malawians....this guy is humble forget what propagandas

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 2 часа назад

    Linda yo ndiye akumveka kuti ndi mMalawi kusiya ndi winayo omveka ngati mulendo .

    • @bs-malawi
      @bs-malawi  2 часа назад

      Amene amalankhulira ma video wa ndi mmalawi koma wakhalisa ku Japan. Chichewa chonse amatha koma lilime linapindika

  • @phillipkazembe7281
    @phillipkazembe7281 21 час назад

    Ben NDI machine 🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @AlumakioChingalu
    @AlumakioChingalu День назад +7

    Ku opposition kulibe wodziwa kuyankhula bwino chingerezi ngati chakwera

    • @CvgGgbnb
      @CvgGgbnb 23 часа назад

      Kulimbedi simukunama kkkkk

    • @Shariffsa
      @Shariffsa 21 час назад +1

      Iweyo ukudya chizungu?

    • @HenryBanda-wh6gg
      @HenryBanda-wh6gg 21 час назад

      Komaso amenewa akhala ku opposition mpaka kale kale asathamangire kukwiya

    • @HenryBanda-wh6gg
      @HenryBanda-wh6gg 21 час назад

      Awonda asanati

    • @gkay-striker
      @gkay-striker 20 часов назад

      ndipo ​@@Shariffsa

  • @FrankChimphepo
    @FrankChimphepo 13 часов назад

    Boma ndilomweli palibe kusitha opposition yomweyi.....namalomba uzingovutika ......boma ndilomweli anthu sitikusitha

    • @Steven-q4u
      @Steven-q4u 12 часов назад

      @@FrankChimphepo Koma utsilu uwu si utha boma Lake liti kkkkkk Koma Zina izi ndi mphwepa !!!!

  • @ChristopherManase-s1f
    @ChristopherManase-s1f 14 часов назад

    Chakwela wayankha mafuso ndipo moveka bwino kwambiri. Macadet akungopanga phokoso basi. Kkkkk

  • @MolesBrown
    @MolesBrown 23 часа назад

    Ndi afiti kumene nkhalamba zokhazokha muziwona nkhupe zija nkhope zoyipa sizisowa nte umadziwika ndichipatso chake

  • @EmmJay931
    @EmmJay931 13 часов назад

    Boma ndilomweli la MCP lotsogozedwa ndi Chakwera ndipo palibeso kusintha olo pang'ono... Dpp never again

    • @EnifarSeleman
      @EnifarSeleman 12 часов назад

      Anthu onvesa chisoni Inu ,nde muthawatu next year

    • @KalimaImedi
      @KalimaImedi 11 часов назад

      AAAA akulu please Anthu 9 anafa ndi chilima Aja amafuna Moyo mukamat boma ndi lomweli mukufuna kupha Anthu ena? Ndale zakupha Anthu zinatha kale ndi kamungu

    • @GodfreyWhayo-hh1dm
      @GodfreyWhayo-hh1dm 2 часа назад

      No to once tried and tested political parties that have failed us , MCP & DPP never again to lead us. Let's try the untested parties

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 22 часа назад

    Chakwera is a democrat. A Peter Muthalika anakhala zaka 6 koma ku parliament sanapiteko kukayankha mafunso. Kukula mtima ndikutsatsata malamulo.

    • @JohnChitsulo-q6f
      @JohnChitsulo-q6f 18 часов назад

      For ???

    • @MaryMlomba
      @MaryMlomba 13 часов назад

      Ndiye kuti zinthu zimayenda bwino nthawi ya dpp ndi chifukwa samaitanidwa ku parliament kukayankha mafunso. Munthu amene amayankha mafunso ndiye kuti ndi olakwa.

    • @EnifarSeleman
      @EnifarSeleman 12 часов назад

      Mumafuna azikataniko , fertilizer otchipa,sopo otchipa school fees yotchipa ,osati ndikubwera ngati adya nyama yagaru

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 23 часа назад

    Abwana bwanji kungosiya kupitako? Siulemu umenewo. Akungofuna kupedzelapo zoyankhula pa compen yawo.Muona mtsogolomu zimene atayambe kuyankhula
    Tiyeni tilitose pano.

  • @AgnesNjikho
    @AgnesNjikho 23 часа назад +1

    Kkkkkkkkk sikidi munthu woziwa kiyankhula komwano ndindewo amafuna palipose pakhare ndeu or chipongwe kumeneku skukula muzeru choti tiziwe nichakuti chikondweresa muzinda sichikondwrresa aliyese ndiye awaa abambo awawa mwina akufuna achuke pazoyipa

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 17 часов назад

    President uyu mutu wake wapoila bas 😂😂😂😂

  • @PhillipMacheso
    @PhillipMacheso 13 часов назад

    Aaaa DPP akeeee

  • @ThomChirwa-py8xo
    @ThomChirwa-py8xo 18 часов назад

    Kod akuyankhula chani uyu

  • @CvgGgbnb
    @CvgGgbnb 23 часа назад +1

    Wojambula mukunama mukutengela Mbali Koma Chakwera ndi BOMA basi mpaka a Malawi azavoteso mwamwayi Chakwera kuzawinaso ndiye muza lira chifukwa Mulungu amakonda aliyese❤❤ Chakwera

  • @hagayichiluwe
    @hagayichiluwe 12 часов назад

    Basi ukatelo watsuta boma? Ponyelela Palo garu

  • @phillipkazembe7281
    @phillipkazembe7281 21 час назад +1

    Kkkkk koma chakwela kulephela kuyankha mafuso ngati Mwana choncho 😂😂😂😂

  • @FrancoKaunga-rq2ki
    @FrancoKaunga-rq2ki 13 часов назад

    Chakwera you must be mad enough! How dare you speaking stupid facts like that?

  • @EdnaChidyaudzu-fx5eo
    @EdnaChidyaudzu-fx5eo 12 часов назад

    Ndipo opposition youma mitu ngatiii iyiii sindinaioneko akuvaaa kuwawa kwambiri en zakuti mutenga mpando umeneu ndi kuopseza mukunama pezani za zeru zopangira campain not the way u are doing

    • @YamikaniMsosa
      @YamikaniMsosa 2 часа назад

      Zanuziso nde ayitu😂😂😂😂

  • @Bernarddavide-e1o
    @Bernarddavide-e1o 15 часов назад

    Chakwera watiponyadi ku chile