kwavuta Chimwendo Banda Vs Norman Chisale Mesa munakhapana nokhanokha mesa munandiimbira phone?

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 29 сен 2024

Комментарии • 101

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 6 часов назад +10

    Nanga why galimoto yomwe anagwiritsa ntchito mwini wake ndi WA MCP?

  • @PreciousDouglas-d7v
    @PreciousDouglas-d7v 6 часов назад +8

    Awa amayamkhla izi akakhala pa camera kom kumbaliko amatuma anyamata azikasokoneza, sangakaneso ai ma audio tilinao

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 6 часов назад +7

    Iwe ndwe munthu wabodza chimwedo Banda unazolowera mabodza galu iwe

  • @Drmuhammadchiwona
    @Drmuhammadchiwona 5 часов назад +10

    Mutu ngati papaya

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 5 часов назад +5

    Chimwendo iweyo ngati sumatamba chilipo chilipo paja mwatchuka ndi kunamiza a malawi ndiye utulutse umboni osonyeza kuti chisale adakuimbira phone kmso iyeyo akudziwa za pa mbowe galimoto inali ya member wa mcp imene anakwera okhapa anthu mwangoyaluka za chilima sitinaiwale .

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 5 часов назад +5

    Achimwendo ndinu chitsiru kwambiri lwe mesa ndamene ukumatuma anyamata kut azimenya anthu

  • @Kabwilachikangawa
    @Kabwilachikangawa 4 часа назад +4

    KOMA NDE ZAFIKA POTOPESA BWANJI,ZAKWANA.TIKHALIRA ZIMENEZI BASI MOTI TIZIMVA MFUNDO ZENIZENI

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 4 часа назад +3

    Kodi iwe Chimwendo kupanda nzeru bwanji, olo atakhala kut amapanga a DPP okhaokha ndie police ngat Boma bwanji sakuagwira omwe amapangawo popeza ndi ntchito yawo.

  • @UsLack-h5b
    @UsLack-h5b 6 часов назад +4

    Ndipo ndangoononga data yanga kumvera fundo zopeperazi

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 6 часов назад +8

    Iweyo ndie oyipa kwambiri chimwedo banda umatuma anthu kupweteka anthu azikwanje galu iwe

  • @HanafihYusuf
    @HanafihYusuf 5 часов назад +7

    Mmmm akuru mulungu akukhululukireni

    • @PatricaTchuwa
      @PatricaTchuwa 3 часа назад

      Chimwendo wabodza iwe muyaluka inuu

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 5 часов назад +4

    Nthawi yatha chimwendo

  • @PempheroAlli-v8y
    @PempheroAlli-v8y 5 часов назад +2

    Ife tikufuna report la ndege osati zanuzo mukuziwana Dpp mboma bas

  • @YasmeenYalabi-b2c
    @YasmeenYalabi-b2c 3 часа назад +2

    Iwe ndi chitsilu kwambili chimwendo banda dikila a Norman akuyankha

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi 5 часов назад +5

    Tikufuna report ife musanamizile chisale apa

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 6 часов назад +3

    Bwanji a police sanagwile athuwo kape iwe

  • @WinerdShadreck
    @WinerdShadreck 5 часов назад +2

    Ife tikufuna za report nkhondo inayamba kale kuno kumalawi

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 6 часов назад +3

    Nanga achipani Cha Afford nawonso anachitidwa chipongwe ndi a DPP?
    Inuyo nkukhala kwanu kukana pa zinthu zachionekere.
    Mmesa munankanso Chilima zokhudza mgwirizano kuti palibepo mgwirizano wina ulionse omwe mudasainirana

  • @MrMagombo
    @MrMagombo 6 часов назад +2

    Mawu amapita kwa IG oyankha akuyankha a Chimwendo.

  • @KENETHMAJASA-ud5ee
    @KENETHMAJASA-ud5ee 5 часов назад +3

    Chipani cha nkhanza

  • @BeckhamDavid-v6c
    @BeckhamDavid-v6c 6 часов назад +1

    Anthu mupwetekana inu chilungamo Kwaaliyese ngt Mungokanirana simuphana😅

  • @Yanjanani
    @Yanjanani 5 часов назад +2

    Mutuwu wangokula mzeru alibe

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 3 часа назад +1

    Eeeeeish achimwendo ngati ufiti alibe ndakayika

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali7401 5 часов назад +1

    Cha Richard Banda chopusa kwambili

  • @felixmaluku5077
    @felixmaluku5077 6 часов назад +3

    Kodi lwe wamkulu mutu lwe ndi I G

  • @FernasonMasiya
    @FernasonMasiya 5 часов назад +1

    Ndakamba zoveka bwlno ukunamatu zakozo

  • @ObentObau
    @ObentObau 5 часов назад +1

    Chimwendo mapwalako ndithu iwe

  • @TiyaMtete-o3h
    @TiyaMtete-o3h 5 часов назад +1

    Koma iyiiiii ndi mbuli machende amako

  • @OnexAliMwale
    @OnexAliMwale Час назад

    Anthu mukungoti ndichisiru komanso ndiwabodza chosecho munthu wanena kuti bweretsani mayina aanthu..Munthu opanda mfundo komanso wabodza amathamangira kutukwana kapena kulira chifukwa amakhala kuti alibe chonena...come up with ur point not kutukwana....

  • @JohnSoweso
    @JohnSoweso 3 часа назад

    Kodi ukutchatchalika bwanjii
    Bwanjii osachita zimenezo pa lmfa ya President wathu Chilima

  • @michaelkallyz2425
    @michaelkallyz2425 2 часа назад

    aChisale akupempha Apolisi kuti agwile anchito, Spokesperson waPolisi asanduka Chimwendo

  • @Mickeykasambula265
    @Mickeykasambula265 5 часов назад +1

    Kalikonse tikawona

  • @DavieKidison-p2t
    @DavieKidison-p2t 3 часа назад

    Zandale osagwilitsa dzelu zachibadwidwe ukhoza kuzitengela ndale ndi game 🎮 yauchikape kt uzitengele ukhoza kuzelezekapo chabe

  • @kerishalaston5650
    @kerishalaston5650 2 часа назад

    Chimwendo osagodwala kenako kufapo tipume kupusisa kwakeko anayenera kufa Mulungu akanayankha malawi Ali pamavuto chifukwa chameneyuyu

  •  3 часа назад

    Iwe chimwendo nthawi yonse ija sumanena bwanji waona kuti zafika povuta nde wayamba mabodza, zikusalira uona plus chikangawa uko zikudikila iwe

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 4 часа назад +1

    Aaaa MCP uchisilu uyi

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl 2 часа назад

    Kodi ntchito yofufuza anthu opanga chipongwe ndi ndani kodi anthu anagenda galimoto ya president kunapita president kukaloza anthu omwe anamugenda koma mfundo zinazi

  • @michaelkallyz2425
    @michaelkallyz2425 2 часа назад

    Kodi aChimwendo mwayiwala kuti munamugenda APM kuNdirande??

  • @patrickmatabwa5828
    @patrickmatabwa5828 3 часа назад

    Waonekera poyera wa Inkata coz ngakhale 2019 unali owotcha matayala mmisewu

  • @WorriedNdhlovu
    @WorriedNdhlovu 4 часа назад +1

    Galu chimutu

  • @MuhammadSamson-yz1kl
    @MuhammadSamson-yz1kl 3 часа назад

    Iwe chimwendo panyero pako anthu amene akakhape anzawo pambowe anali a MCP iwe chitsiru chodzadzamamina nkati

  • @HolickLemajomo
    @HolickLemajomo Час назад

    Chimwendo wangokula chimutu chakocho koma mzeru ulibe anankhumwa achani galu iwe

  • @LukaMankhwala
    @LukaMankhwala Час назад

    Koma Ngati Boma sitikuyenela kulekelela Kuti anthu okha adzimenyana police imayenela Ku chita kathu

  • @SimonBanda-b1f
    @SimonBanda-b1f 32 минуты назад

    Uyu mumati chimwendo amawoneka kuti ndiwochenjera
    Koma anyamata anu adzawona maloza

  • @khwimaBanda-s3u
    @khwimaBanda-s3u 2 часа назад

    ine ngat mmalawi ndikuona mbali zose kulibeko fundo akungonyozana bas amalawi tili pa vuto mwina kubwele a nyuwani osat kumene tadusaku ndi izi lelo

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 3 часа назад

    Wabodza uyu awa a mcp zinthu amayakhura okha, koma nso. pamawa nkhani yomweyi za amanthanso kukana awa alibe chilungamo or pangono kay amapemphera kay za malemu chilima bwanji. anapha okha koma amakana

  • @RaffickAllie
    @RaffickAllie 3 часа назад

    Mmmmmmmmm Mesa munatchingira panjira and zinatengera chisare kuonesa ukadauro .

  • @NickUpoche
    @NickUpoche Час назад

    Tikufuna report la ndenge ife osati za Achisalezo ife

  • @Jacksonmuhackeya
    @Jacksonmuhackeya 4 часа назад

    Kodi iwe umaziona ngati ndani muziko La Malawi umaona ngati dziko ndi LA amai Ako umadabwisa ikubwela nthawi uziona chimwendo

  • @HenderesoniNdau
    @HenderesoniNdau Час назад

    Muthu opusa kwambili chimuthu ngat pwala ranjovu

  • @BeautyGivenLupwayi
    @BeautyGivenLupwayi 35 минут назад

    Chimwendo Banda boza chimutu kukula🤣

  • @PetroJack
    @PetroJack 3 часа назад

    Uyu asamulidwe ponena kuti DPP idaotcha a Tambala

  • @AgnessKalindo
    @AgnessKalindo 33 минуты назад

    Apa nde kuyakha kma za ifa ya chilima osayakha. Chisilu cha muthu.

  • @ChimzyWesley
    @ChimzyWesley 3 часа назад

    Ndiye ngati anali onkhaonkha amene anayambisawo osawagwila bwanji olo ali a DPP

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 47 минут назад

    Chimutu eti kuyakhula moputsa chifamba chachikulu iwe

  • @ChimzyWesley
    @ChimzyWesley 3 часа назад

    Park and go your time is over chimwendo

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 4 часа назад

    Koma nkhani ndiyoti anakuuzani kuti yadzadza ndindani ndiye zimene tikufuna kumva apapa

  • @ElizabethAlick-e6b
    @ElizabethAlick-e6b 4 часа назад

    Umboni okuti achisale anakukumburani phone urikuti?

  • @FrankRabson-q6j
    @FrankRabson-q6j 4 часа назад

    Achimwendo kumeneko sikuchenjela ndikupusa

  • @AyandaPhungula-bg9ql
    @AyandaPhungula-bg9ql 2 часа назад

    Umazitenga Ngati ndi iwe dolotu komano one day is one day

  • @kenngondwe5698
    @kenngondwe5698 29 минут назад

    Youre very fair in this channel

  • @ChristinaChimombo
    @ChristinaChimombo 4 часа назад

    Nanga anachepa uja bwanji anthu anawatchura police inachitapo chani

  • @NabiuMatola
    @NabiuMatola Час назад

    Atu awaw ND oipa kd mulung osawalang buanj

  • @ShamilahSaizi
    @ShamilahSaizi 2 часа назад

    Koma achimwendo mukamayakhula muziziwa kut kuli mawa

  • @HamanjaManyela
    @HamanjaManyela Час назад

    Chimwendo Banda ulibe humanity

  • @ChikupizgaKajawaMkandawire
    @ChikupizgaKajawaMkandawire Час назад

    Ma cadet ma cadet kkkkkk ndinu osekesa mukufuna ndeu

  • @Dellingsmunthali
    @Dellingsmunthali 2 часа назад

    Apa obanda mwayankhurako zabwinoko🙏🙏

  • @MarthaChigonero
    @MarthaChigonero 4 часа назад

    Ambuye bwerani muweludze dziko lanuli

  • @PraiseKaliwo-x4l
    @PraiseKaliwo-x4l Час назад

    Kodi anthu akavulazana okhaokha samangidwa

  • @ZADOCKTEBULO-p8g
    @ZADOCKTEBULO-p8g 4 часа назад

    Boza ili ,, iwe Chimwendo panyopako

  • @Paul-q2p
    @Paul-q2p 4 часа назад

    Ndewu imayamba chocho ife o vota tili pheee

  • @JonathanMunthali-n3c
    @JonathanMunthali-n3c 4 часа назад

    Ngati anakhapana wokha wokha agwireni anthuwo

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Час назад

    Ngati anali a DPP bwanji osawamanga?

  • @Samson-ve5rs
    @Samson-ve5rs Час назад

    Taona macomment Chimwendo Banda

  • @Marymahendra
    @Marymahendra 51 минуту назад

    Chmwando ndi munthu wamboza

  • @NoohNowa
    @NoohNowa 2 часа назад

    Ndege inagwa chifukwa chani 😢?

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 3 часа назад

    His time is near chileg

  • @NyangwaKoma
    @NyangwaKoma 3 часа назад

    Chimwendo panyelo pako

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e 4 часа назад

    Apanika awa.ayankhe za ndege awa..

  • @MaggieBanda-ft5tu
    @MaggieBanda-ft5tu 50 минут назад

    Mayoopp data yanga ine😢

  • @LameckManuel-f3q
    @LameckManuel-f3q Час назад

    😂😂😂😂 koma dziko ili eeeee

  • @MCDONALDTHENGENDE
    @MCDONALDTHENGENDE 3 часа назад

    Chimwendo wa boza iwe ,,,

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Час назад

    😂😂😂😂 ndilibe lawyer

  • @NoohNowa
    @NoohNowa 2 часа назад

    Alani witika

  • @PaulFrank-tj2mc
    @PaulFrank-tj2mc 4 часа назад

    Kuyankhula ngat munthutu

  • @WorriedNdhlovu
    @WorriedNdhlovu 4 часа назад

    Mwapha bwanji chilima

  • @MosesTangwe
    @MosesTangwe 2 часа назад

    Mutu ngati vembe

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 2 часа назад

    Kodi mukuopana

  • @memorexinc8506
    @memorexinc8506 Час назад

    Adah wa nzeru alibe

  • @BrownMainje-sh7hj
    @BrownMainje-sh7hj 12 минут назад

    Mfiti

  • @NyangwaKoma
    @NyangwaKoma 3 часа назад

    Milomo yonyasayo

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wt 4 часа назад

    Ndalee anakonzaa

  • @KennethMugabe-f9l
    @KennethMugabe-f9l Час назад

    Bodza

  • @blessingssaiti
    @blessingssaiti 5 часов назад +2

    Mayina achoka kuti Mesa anyamata anu anathawa