2016 ambuye nakumana ndichosowa changa I remember I met the car advertising about this CD I said I have met my wish I purchased one and indeed God see me. Through and bless me wit a baby boy ❤ 2024 December 8 who is wit me ❤
Mukune ndi moyo wanga baba and mukumane ndi chosowa changa ambuye yesu.more grace and anointing upon your life brother king James Phiri.nyimbo zanu zimandidalitsa
2023, its a year I can testify about this song. The Lord Jesus played this song for me in the spirit and I danced to it. It was my first time experience to witness God's approval of a gospel song and anointing it. It was sung to me before my healing. It prophecied of my healing. Kings Phiri, just know this song was inspired to you by God and He ordained it. I am a witness in 2023.
Thank God for being faithful this song was a declaration but now a fulfilment of it Banja mwandipatsa Ntchito mwandipatsa ana mwandipatsa Yatsala galimoto tikukwerabe za eni I know you will not fail me simunalepherepo I LOVE YOU LORD
yesu mukumane ndi moyo wanga. ..mukumane ndichosowa changa.lero mundipatse umboni. ....nyimbo iyi imandilimbitsa mtima pamene ndili munyengo ya chitonzo mulungu adzikudalitsani brother king James phiri
Ambuye ndkumbukiren munyengozang ambuy chitan nane ambuy chitisan manyaz adani angawa sekan pakamwa pa adan anga is song will bless my life l thank god for is song ❤❤❤❤ndchosen manyaz ambuy
Maukwati aeni,magalimoto aeni,ma business aeni Ngongole zokhazokha Who is reading this comment in 2026 kno kut i have cars,bank balance is fat,am now married n i have built the elderly home that i was struggling to 3 years isn't long in God's goodness No more ngongole Ndikungongoza now Oh God 😢😅
2019 it was my prayer for the fruit of womb today I can testify that God come through for me🙏
8 years ago i found myself in Malawi, newly wed and jobless this song always ministered and still ministers to my soul!
Inu Munati olema aze Yesu Pamaso panu...
Lero ndi mtima wanga wosweka Ambuye ndabwera🥹🥹🥹
Ambuye...Mukumane ndi Moyo wanga...ndi chosowa changa🕯🕯🕯🕯
2016 ambuye nakumana ndichosowa changa I remember I met the car advertising about this CD I said I have met my wish I purchased one and indeed God see me. Through and bless me wit a baby boy ❤ 2024 December 8 who is wit me ❤
P
Mukune ndi moyo wanga baba and mukumane ndi chosowa changa ambuye yesu.more grace and anointing upon your life brother king James Phiri.nyimbo zanu zimandidalitsa
Mukumane ndi chosowa changa❤Ambuye
2023, its a year I can testify about this song. The Lord Jesus played this song for me in the spirit and I danced to it. It was my first time experience to witness God's approval of a gospel song and anointing it. It was sung to me before my healing. It prophecied of my healing. Kings Phiri, just know this song was inspired to you by God and He ordained it. I am a witness in 2023.
❤
Thank God for being faithful
this song was a declaration but now a fulfilment of it
Banja mwandipatsa
Ntchito mwandipatsa
ana mwandipatsa
Yatsala galimoto tikukwerabe za eni
I know you will not fail me
simunalepherepo
I LOVE YOU LORD
Mukumane ndi moyo wanga baba,ndatopa kukhara moyo ovutika komaso odwala dwala mwana wanga maria komaso mayi anga ambuye ayendelen ,ineso mundipatse mzeru amen
Ndatopa ndikunyamula Ana aeni mukumane chosowa changa ambuye😢
Mukumane ndi moyo wanga choonde Yesu😭😭😭😭 This year sizikuyenderatu
Mukumane ndichosowa changa❤ am still in love with this song
Indeed kumanani ndi zosowa zanga ambuye
I like the song it blesses me
yesu mukumane ndi moyo wanga. ..mukumane ndichosowa changa.lero mundipatse umboni. ....nyimbo iyi imandilimbitsa mtima pamene ndili munyengo ya chitonzo mulungu adzikudalitsani brother king James phiri
Yesu mukumane ndi moyo wanga mukumane ndichosowa changa 🙏🙏🙏
Mukumane ndi moyo wanga yehova 2024 mundipatse abwenzi onse anathawa amen
Ambuye zikomo kumani nane i first heard this 7 years ago and it is still ministering to me
Amen to the wonderful prophetic song ❤❤❤ I bear witness to this song.
Still here in 2024. A powerful song that still blesses my soul
Ambuye ndkumbukiren munyengozang ambuy chitan nane ambuy chitisan manyaz adani angawa sekan pakamwa pa adan anga is song will bless my life l thank god for is song ❤❤❤❤ndchosen manyaz ambuy
May the Good LORD Jesus continue to inspire your songs
Oooh this song is always powerful,,,,Jesus Christ is Lord
Mukumane ndi Moyo wanga Ambuyee🙏
Heard this performance at the Forward in Faith Ministries International Big Sunday ku COMESA Hall.....
Beautiful, highly anointed 🎉
Powerful song
Mukumane ndi chosowa changa ambuye♥️♥️
Maukwati aeni,magalimoto aeni,ma business aeni
Ngongole zokhazokha
Who is reading this comment in 2026 kno kut i have cars,bank balance is fat,am now married n i have built the elderly home that i was struggling to
3 years isn't long in God's goodness
No more ngongole
Ndikungongoza now
Oh God 😢😅
The number one gospel song no one else 🙏
Mukumane ndi chosowa changa, Amen
Kumanani ND moyo wanga Ambuye🙏
Grateful bro timakunyadirani keep it up and God should continue using you according to his greatness🎉🎉❤❤❤❤❤❤❤❤
Unmentioned wars,yesu mukumane ndi zosowa zanga
2023 still getting blessed
Mukumane ndichosowa changa yesu
Am tired mukumanena yesu napo ndi umoyo wa nkhongole
Mukumane ndichosowa changa yesu❤❤❤
Ndatopa ndikunyamula ana a anthu ena,naneso ena anyamule wanga
Eeeesh this track is still the best 💕💕
That's touchable song. Keep burnng
Thank my Brother this song is talking to my situation
Things song😭.yesu mukumane ndi moyo wanga
This song , okay u did it mmmmm
Mukumane ndichosowa changa ambuye😢😢😢😢
Mukumane ndi chosowa changa usiku uno Yesu wanga
You always touch my heart brother keep it up
Mukumane ndi mamuna wabanja kwaine ambuye
2021 it's my testimony , AMEN
Great song, I am blessed
Amen Mukumane ndine Yesu
Mukumane ND moyo wanga Ambuye
Mukumane ndi moyo wanga Mulungu
James pitilizani tchituyanuyabwino
Mukumane ndichosowa changa ndatopa
Amen best song
Powerful ❤❤❤❤❤
Mukumane ndi chosowa changa Ambuye nyimbo iyi imandilimbikitsa kwambiri
2023 it's my testimony
Amen and Amen eeeee
So powerful 5 yrs like yesterday
Anakumana nane ndithu🙏
Ndipaseni nyimbo ambuye
mukumane ndimoyo wanga
❤❤❤❤❤❤ nice song
Mukumane ndichosowa changa baba
Very powerful song
Ameen
Kumanani ndi zosowa zanga ambuye
evergreen king James
Nyimbo zina zilikutii
Amen
Nyimbo yachilimbikitso
🙏
Powerful 🙏
2024 Christmas ☃️
Ndili pano Baba
Kumanan nane yesu
Powerful
Jhooova is ky in my lifi
Kumanani ni chosowa changa, nkhawa zanga zotse
Emen
Muzabwera liti kuno kusouth
Kuimba molapitsa
Amen
Powerful
Amen