ANTHU ADABWA NDIZOMWE MCP YAYANKHA LERO PA ZAMPHEKETSERA YOMWE IKUMVEKA KUTI AKUFUNA KUBERA ZISANKHO

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 16 дек 2024

Комментарии • 162

  • @TrizaDzimbiri
    @TrizaDzimbiri 4 часа назад +10

    Zitsiru inu a mcp munapha chilima inu and mulibe manyazi mmene mukuyankhulira zopusa izizi,za ugaru basi anthu akupha inu

  • @abdullalajabu5871
    @abdullalajabu5871 3 часа назад +5

    Ife tikawona ngati sumawopatu ndimene mumazitamila muja kaniso nditu amantha musiye kwachocho azanu nawoso akasiyani💪💪💪💪💪

  • @LuciusPatrick-f2c
    @LuciusPatrick-f2c 3 часа назад +3

    Anthu akupha inu mizimu yanthu amene anafera kuchikangawa ija muzuzika nayo ndipo nonse amene munatengapo gawo pa ifa imeneija mtendere simudzaupezaso kuphatikizirapo mnsogoleri wanu chikangawa ndipo ena inu simufikanawo nthawi yo vota

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 3 часа назад +3

    Asatana ndi ziwanda zake zili pa meeting eeee ungodziwiratu apa sungamve chanzeru pemphero lathu ndiloti Mulungu atithandize pothana ndi ziwandazi mungoona nkhope zokhazo eeee ayi

  • @DamaliceWamalanguluko
    @DamaliceWamalanguluko 3 часа назад +2

    Kujala wanthu kumaso kose uku mkuchita apa wa mcp imwe yehova akuona ivyo muchita muona

    • @chrissyamanda5510
      @chrissyamanda5510 Час назад

      Nivindele ivi wose na catherine gotani wose vizeleza va wanthu vilije namahara

  • @EnerstManess
    @EnerstManess 3 часа назад +2

    Kod iweyo chimwendo zikukupweteka zongolankhula iwe ukutumiza zikwanje pa ground koma iweyo siunat iwe uva kuwawa koopya anthu akukufuna iweyo

  • @GeoffreyMarko-v3s
    @GeoffreyMarko-v3s Час назад

    DPP💙💙💙💙💙💙💙🔥🔥🔥🔥🔥

  • @BensonJamali
    @BensonJamali 3 часа назад +2

    Afiti awa + chakwera wawo

  • @CliveKelvin-o2s
    @CliveKelvin-o2s 3 часа назад +1

    Ngt simukuziwa za imfa ya member wanu uja,, anamupha ndi Moses kunkuyuyo chisilu iwe

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 3 часа назад +2

    Ndfe amodzi zolengedwa za Mulungu ndpo tonse pamaso pa Mulungu ndfe akapolo ake koma anthu ndinadana nanu kooooopsaaaaa pa 10 June zmwe munapanga ku Chikangawa aaaaa basi sndinunso anthu koma zilombo zeni zeni asatana opanda chison ngt anthu osabereka

  • @lovemorengwira
    @lovemorengwira 28 минут назад

    Mcp Kuba ndi kupha basi that's only thing thy know very well 😊

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Час назад

    😂😂😂😂 DPP kupangisa MCP press briefing. Kwachematu

  • @JemusHaji
    @JemusHaji 2 часа назад +1

    Chimangachotu tandandizibwa ndi maiko ena osati ndicha mcp

  • @JamesBrown-gx8my
    @JamesBrown-gx8my 3 часа назад +1

    The whole press briefing for DPP 😂😂😂😂 mukuiopa agalu anu

  • @SamuelThanganyika
    @SamuelThanganyika 3 часа назад

    This is good for our peace koma vuto ndi andalewa,mbali zonse zimasowa chilungamo pa nkhani zofunitsitsa ku malankhula zomanga dziko pa misonkhano Yao yandale.Chooonde Malawi is one our beloved leaders,dziopani mulungu pa zochita zanu.Dzipani dzimafuna anthu therefore tidzisamala kwambiri.

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 3 часа назад

    Tikumva kuwawa ife munatimphela ..... Anthu ofunikila.....mcp mumuziwe yesu ndi omphunzila ake onse 11 kupatula wa 12 yudasi😢😢😢😢😢😢

  • @BlessingsSeleman
    @BlessingsSeleman Час назад

    Taona nose mwatengana pamenepo nonse kamwa zanu kumalakhula zotani NRB musaiimile plz iwe Rish uli ndi vuto lalikulu uwononga chipani Cha mcp ngati sukuziwa anthutu sopano akumakuonatu usamazinamize bwanawe

  • @StevenJana-m2e
    @StevenJana-m2e Час назад

    Zitsiru inu a MCP,padzana paja muli pheee pankhani ya anyamata azikwanje,ndiye pano zikukuwawani pati

  • @JemusHaji
    @JemusHaji 2 часа назад

    Chimwendo kumunyenga nkaz wa lufan 😂😂😂😂😢 iweyo umakwana chimwendo umupatse mimba

  • @markanthony5402
    @markanthony5402 2 часа назад

    Komatu MCP ikazawina ine ndizalengeza kuti am no longer a Malawian

  • @JonathanMunthali-n3c
    @JonathanMunthali-n3c Час назад

    Chimwendo ukuyipisa chipani ukapangisa press briefing it means ukufuna a police amcp akamange anthu

  • @ZameersurathAnnubi
    @ZameersurathAnnubi 2 часа назад

    Ndimawu otsatsawo chimwendo patsana pako galu😊

  • @SteveZimba-e8s
    @SteveZimba-e8s 3 часа назад

    Inu mulibe manyazi zomwe mukulankhulazo nzopanda pake inutu mukuziwa Kuti bomali lapita basi ndipo Kwa munthu oganiza bwino sangazavotere mcp ndi chipani chovunda inu nkhaza simunasinthe kuzuza amalawi

  • @honmitrus
    @honmitrus Час назад

    Don't worry chimwendo mukuziwa yemwe anapha chilima, lwe simulungu wait for revenge

  • @EnockMawaya
    @EnockMawaya 3 часа назад

    Achimwendo , mutu wanu wangokula. Palibe Cha nzeru pazimene mukuyankhula. Nthawi yatha basi. Muwawuze ana about your party, mcp. Inu azipani Zina mukuwalora pa central region? Zikwanje mwakhala mukutenga Zija. Pa mbowe filling station munapanga Zija, a police anagwira ndani? Inu munadzudzulapo?

  • @Hannif-o2z
    @Hannif-o2z 2 часа назад

    Khondo munayiyambisa nokha inuyo a mcp osati zoomwe mukunenazoo bwanji tigogawana mitundu bwanji gati ndikotheka kutelo coz mene zikuyendelamu ndibwino wina aliyese aziona zakwao bas

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 3 часа назад

    Zokambrana zake za DPP ndye munyeratu sikunati mwalephera kupepera anthu asiye kukonda DPP ndpo mukuona nokha mene fanz ikukondera DPP ndpo even inenso ndi banja langa pompano talowa DPP pazomwe mwayankhulazo ndalowa DPP thanks guyz poyankhulira DPP

  • @CliveKelvin-o2s
    @CliveKelvin-o2s 3 часа назад

    Mumapha anthu inu osati kuopseza anthu inu Mumapha ndipo ine vot yanga ikupangisa kt APM aimeso

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t 2 часа назад

    Sochichitika chisakho chimenecho muwonaso sichizakhala cha Bata cz inuyo a mcp ndale zanu ndi za u savage 🤣 😂

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope 2 часа назад

    Aaaaa zeru zalutha zake ziti chakwera sadapemphe mulungu nzeru zophela chilima ndipo mulngu adapasa

  • @LysonMkomadzinja
    @LysonMkomadzinja 2 часа назад

    Musatinyasepo apa inu mukunena azanu kuti ankhaza mulibe manyazi mbuzi inu mukamati dpp siingabwelele m'boma inu mwabwelela bwanji m"boma anthu oipa inu fotseki.

  • @EnerstManess
    @EnerstManess 3 часа назад +1

    Shem on u chimwendo umunthu ulibe

  • @frankndawandawa6666
    @frankndawandawa6666 3 часа назад

    Mmalo mokambirana zanzeru busy kuzuzula DPP

  • @CarolineJohn-ue3tr
    @CarolineJohn-ue3tr 2 часа назад

    Nditukwanatu ine iwe chimwendo banda mutu ngati jungle ngati nafuko machende ako ndi azako womwewo amfiti inu a mcp panyapanu mwanva iwe undilakwinsa

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 3 часа назад

    Mcp kukhetsa mwazi ndi chikhalidwe chanu afiti inu oyipa .

  • @IshuBillalli
    @IshuBillalli 2 часа назад

    Mai otembeleledwa anabeleka iweyo chimwendo mulungu akuona chilichonse chomwe ukupanga

  • @GiftBonomali
    @GiftBonomali 3 часа назад

    Chipani chang,ona ichi apm my vote

  • @JonathanMunthali-n3c
    @JonathanMunthali-n3c Час назад

    Kukokomeza nkhani yopanda pake pamene iyeyo chimwendo anapha chilima.

  • @mickiaskumbasa136
    @mickiaskumbasa136 2 часа назад

    Iweso umawopa tithana nanu a emusipi ndipo kafukufuku wandege azachitikaso

  • @KumbukaniKadzuwa
    @KumbukaniKadzuwa 3 часа назад

    Ngakhale chakwera yemweyo azavotela dpp ndiye iwe manyazi bwanji

  • @WellodChagunda
    @WellodChagunda 2 часа назад

    Anthu amene adabwawo ndindani tiwadziwe

  • @clairemyegha4315
    @clairemyegha4315 4 часа назад

    We want solutions and not meetings please

  • @denndavie6041
    @denndavie6041 3 часа назад

    Chipani cha anthu oipa nkhope okha okha n🎉gati maliro. Kuipa ndi ntima omwe . Zikuonekelanitu

  • @fredgabrielnyangulu
    @fredgabrielnyangulu 3 часа назад

    Kodi zoti a chimwendo amkakuwa pa podiam kuti a mumtalika asowe akuwona ngati sitikudziwa osamasangalala chikakhala kwa iwe ai koma nzako akati abwenze kumamva kuwawa

  • @mikekaliza-bw4yg
    @mikekaliza-bw4yg 53 минуты назад

    patumbo panu ndi yemwe anakuberekani mukunamiza ndani inuyo lipoti mwabisa chilima ndi anthu 8 kuphatikiza kasambala sidiki miya ali kuti kusamala sasamala itasara ndiwa imodzi inu mwatilephera 2025 Dpp boma

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 3 часа назад

    Anakuuzani Chisale kuti lekeni izi chifukwa nafenso titenga malamulo mmanja mwathu. Pano mwaziona ndikummwera kumeneko Phalombe, Mangochi paja Chilima ankathamanga komeneko

  • @AlickMDayi
    @AlickMDayi 3 часа назад

    Anthu azikwanje oyipa inu ngakhale manyazi mulibe mphakana kumabwera poyera choncho mzimu wa Chilima ukusawutseni nthawi zonse

  • @AllanWyson
    @AllanWyson 3 часа назад

    DPP ilipobe ndipo sizatha akutha ndi anyamata a zikwanje,,,, zinyenganani nokha nokha kumeneko ndi Chakwera wanuyo pozinamiza kuti muzabera chisankho ndi mwana wa John tembo wanuyo.

  • @GreciousMbewe
    @GreciousMbewe 3 часа назад

    Press briefing ya mavuto Ali mziko muno muipanga liti pamene dziko likuzama mmatope a mavuto

  • @JamesBrown-gx8my
    @JamesBrown-gx8my 3 часа назад +1

    Press briefing ya zigawenga😊

  • @DalitsoMbewe-u1y
    @DalitsoMbewe-u1y 3 часа назад

    Musanamizile dpp kuti inapha munthuwanu,munaphana nokhanokha a mcp

  • @SirajuMasonga-h1u
    @SirajuMasonga-h1u 2 часа назад

    Palibe chomwe anayakhulapo ine ndikumva anthu awa ine ndikuona kut enawa nd matha chabe , muziona ndthu

  • @thomsonsuwedi
    @thomsonsuwedi 2 часа назад

    Anzako angoyankhula ndimawu koma iwe umatulusa zikwanje wayamba kunjenjemela kkkk

  • @Malekano-k3x
    @Malekano-k3x 2 часа назад

    Ife tikufuna utiuze amene adakuuza kuti ndege yadzadza

  • @BlessingsSeleman
    @BlessingsSeleman Час назад

    Guys kod chani inuyo ziyeleseni kaye osati zomwe mukupangazi inuyo nda amene munaziyamba musayese amalawi sakuona ndiposa samamva chosani maganizo oti amalawi sakukuziwani plz

  • @SOLDIERLOVE-e1q
    @SOLDIERLOVE-e1q 3 часа назад

    Mbuzi nonse palibe chimene mwayakhulapo chazeru apa zisilu zonse zakuba inu

  • @denndavie6041
    @denndavie6041 3 часа назад

    A fiti Mukuopa ndende? Munapha chilima, Mia, ndi anthu ena ochuluka. Mugwilatu ndende boma likasintha.

  • @JemusHaji
    @JemusHaji 2 часа назад

    Amalawi ake ati omwe ali osangarara ndi MCP

  • @crosbeygondwe5403
    @crosbeygondwe5403 3 часа назад

    Evn voice ndiyonya kwambili

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 2 часа назад

    Kuuzana chimfiti chigawenga ichi chomwe chumatsogolera zigawenga mulungu wake uti amene yu?????? Jahena Ikudikil.

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 3 часа назад

    Ineyo ndiye sindingavotele ndi chibekete chakwera .....munthu wolephela .....chakwera ndingamuvotele chifukwa chiyani munthu woti waononga ziko ....chakwera ndi mbuzi

  • @daviealabi
    @daviealabi 3 часа назад

    Boma ndilomweli kona tisintha president

  • @MilandaAyanna
    @MilandaAyanna 3 часа назад

    Athuwa ine amanditsetsa chisoni kwenikweni a jessy kabwira ndi achimwendo mukathera ku cell 2025

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d Час назад

    Boma lamangazi munampa anthu 8 osalakwa khani yake ufuma ufumu tiwonetsana 2025

  • @GoodsonNyakwawa
    @GoodsonNyakwawa 3 часа назад

    Kkkkk all the comments am reading here no any comment support MCP ayi zikomo chikangawa kwakodi kwatha

  • @NaomieBanda-t6g
    @NaomieBanda-t6g 3 часа назад

    Akufoyokozerani bwanj poti apolice akuziwa kuti mwapha nokha

  • @EviChio
    @EviChio 3 часа назад

    Inu ndi zitsiludi ndithu amcp, mulibe manyazi

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august 3 часа назад

    Koma mcp pempheroli silinayende Mulungu analanda kale nzeru kwa Chakwera nawapangisa kukhala wankhungu

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko 2 часа назад

    DPP ikukunvesani kuyabwa agalu inu 😂😂😂😂😂

  • @LucksonKumwenda-p2f
    @LucksonKumwenda-p2f 3 часа назад

    Kusowa Chonena Amaphwala Inu

  • @SteveNkhambule
    @SteveNkhambule Час назад

    Tikuonesani 2025

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar 3 часа назад

    Wina wangolakhula ndpo wina anachita Kodi oyipa nd uti pamenepo?? MCP kozekerani unyolo 2025

  • @Nathkala997
    @Nathkala997 Час назад

    Zakumtumbo zenizen...why mukuopa chiduswacho

  • @LottiAffati
    @LottiAffati 3 часа назад

    or mene ikuwonekera nkhope ya nzimayiyo eeeee yaufitifiti choncho eeeee tamuonesetsani guys nzimayiyo

  • @EnerstManess
    @EnerstManess 3 часа назад

    Kumbowe wayiwalako unamenya anthu kuphwanya ma galimoto lelo ukuva kuwawa ndi kulankhula kokha

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 3 часа назад

    NDIKUPEPHANI CHIMWENDO BANDA PANAFUNIKA KUWURURA PAZOMWE ZINACHITIKA PAKATI PANGOZI YA MR CHILIMA NDIKUNENA IZI KUTI NGATITU INU MUKUDZIWAPO KANTHU NDIPO NGATI DIMUNACHITE NAWO IZI PULANIYI YAKUPHA MR CHILIMA SAMBILATUNU MANJA NDIPO LIWUZENI DZIKO AMENE ANPHA MR CHILIMA CHIFUKWA ZIKUWONEKA NGATI THANO CHIFUKWA MULI BOMA KOMA MUKAVULIDWA PHAVU MUDZALILA MAYO PAMODZI NDAMENE MUKUMUBISAYO TONSE ANTHU TIKUDZIWA NDIYE INU MUKUCHEDWERANJI KUYERETSA MBILI YANU MUKUFUNA KUVALA MBILI YOYIPA CHIFUKWA CHOTETEZA CHAKWERA KOMASO NGATI MULI GULU APOSO EYA NDIZOWONA SIMUNGACHOKEMWE MGULU AI KOMA DZIWANI MUKATHERA KUNDENDE MUKATOZEDWA KWAMBILI KUMENEKO TIDZALIPEPHA BOMA WEEKEND ILIYONSE MUZIKAMENYEDWA NDI ANTHU KUMUNEKO KUFIKILA KUFAKWANU MACHENDE ANU AGALU OPUSA ODANA NDI ANTHU OPHUZILA OMWE ATHA KUYENDETSA DZIKO LINO MACHENDE MUFUFA IFA YOWAWA KWAMBILI AGALU INU

  • @ChrisMsonyo-yq2ko
    @ChrisMsonyo-yq2ko 3 часа назад

    All the comments no one is giving u support or the way anthu akwiila pamenepo manyaz ulibe kkkkk
    Mkanakonda muwaonetse ma comments awawa kut akumbukile😅

  • @TrizaDzimbiri
    @TrizaDzimbiri 3 часа назад

    Palibe munthu wanzeru amene azavoteleso mcp chipani chakupha ichi,munapha chilima anyani inu

  • @RexElsoni
    @RexElsoni 3 часа назад

    Dpp ikubwelela mboma mufune musafune

  • @BlessingsHarneck-p3y
    @BlessingsHarneck-p3y Час назад

    Koma mukawaona anthu omwe alipowo, zikuwakonda?

  • @MagieJames
    @MagieJames 3 часа назад

    Ukusowa zoyankhula galu iwe munthu anafa uja munapha nokha kuzowerewera kupakula nyemba umalimbana nd DPP chifukwa chani kuposa nkhanza

    • @MagieJames
      @MagieJames 3 часа назад

      Zimau ngt uli mutsuko wakupha iwe unakana kukwera ndege bwanji chitsilu ukubera mavote kudzera machine

    • @MagieJames
      @MagieJames 3 часа назад

      Uthe ndwe mukulimbana nd DPP bwanji kudalira machine obera mavote

  • @CliveKelvin-o2s
    @CliveKelvin-o2s 3 часа назад

    Km simukuwinat or mukapange sonkhano chifukwa ndinu mbuzi ndima hule anuo mmenemo

  • @EvanceKaira-w2f
    @EvanceKaira-w2f 2 часа назад

    Mbava za anthu inu chipani chosanganizila dziko la Malawi

  • @Amina-gg5gr
    @Amina-gg5gr 3 часа назад

    Iwe ndiwe chitsiru kobasi chimwendo

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx 3 часа назад

    Palibe mulungu pamenepo athu magaz alimamanja kumakamba za mulungu shem In u

  • @AkimumusaMusaakimu
    @AkimumusaMusaakimu 3 часа назад

    Please don't lie to say DPP there's bring violence in the country....no usatinamizepo ife Kodi violence ya zikwaje ndi anyamata Anu a MCP mukuyibisilanji????

  • @KettieNathaya
    @KettieNathaya 4 часа назад

    Mwadziwa bwanji kuti anali aDPP omugenda nkunkuyu.? naye mapwala ake pamodzi ndi chakwera

  • @AkimumusaMusaakimu
    @AkimumusaMusaakimu 3 часа назад

    Ndiye ifa ya chilima apolice apangapo chani

  • @DaudiLesta
    @DaudiLesta 2 часа назад

    Ooooo murungu wathu chonde mtengen chim wendo afe akuzuz a nthu anu kun chonde zatenge n

  • @Rasheedissa-f3q
    @Rasheedissa-f3q 3 часа назад

    awusen amallawi kt MPC innapha skc munapha ndinu

  • @MaliGomani-z4k
    @MaliGomani-z4k 3 часа назад

    Ndan okavotela chakwela 😂😂😂 kulozedwa 😅

  • @EmanuelPaul-io2hk
    @EmanuelPaul-io2hk 3 часа назад

    Chimwendo dzikoli silako udzaona polekera mzimu wachilima umakudandaulani agalu inu.

  • @VinciusmajiduMchepaanaffi
    @VinciusmajiduMchepaanaffi 37 минут назад

    Mcp ndie yankhaza yakupha

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc 3 часа назад

    Ana aberezebulo inu maka iweyo chimwendo Chaka chamawa uzapanidwa ma battery uzaulule Za imfa ya Chilima mmxwie 😑

  • @ibrahimJasten
    @ibrahimJasten 2 часа назад

    Kkkkk munasiya khaza kodi sitikuziwa kuti munasiya khaza

  • @BashiruAdamus-l2b
    @BashiruAdamus-l2b 3 часа назад

    Ndipo inuyo munya manyi chifukwa inu mcp anthu oyipa inu

  • @chrissyamanda5510
    @chrissyamanda5510 Час назад

    Mwayila yanu ya zikwanje ija agalu inu
    Munya muwona

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 3 часа назад

    Zisilu za anthu
    ...agalu enieni .....Muona chaka chake ndi chino

  • @MaliGomani-z4k
    @MaliGomani-z4k 3 часа назад

    😂😂😂😂pephero la munlo 😂😂😂 zalowa libolonje 😅

  • @daviealabi
    @daviealabi 3 часа назад

    Zitsiru zopanda mzeru