Kodi kutha kwa licence ndi nkhani yomwe tingati inathandiza kuti anthu aja aphedwe. Kwa ine pari zocuruka ndikungopukusa mutu komano yawe azakonza mosavuta
Nkhani la mkazi wa Kasambala musayitengere chifukwa ulendo wao unatheka, and there was no reason to waste time to interview her. The issue is where is the black box? Why did Chimwendo fail to use the aeroplane? Is it normal for a pilot to start flying without getting information from the control tower? Foolish report just like Chizuma's report, useless. I wish commissioners of enquiry should he held accountable should they come up with doctored report.
Ndili mzolankhula zambiri ,kma kwathu mkosaukaa sangandigulire lawyer ,but only God knows 🙌
Bakili Muluzi TV always tells us the truth than this political radio
Only God knows..... We can't say much
Za kumdima nzovuta fusani kaliyat ndi mai winayo ndi amene amadziwa chilungamo pazimene anapangana ndi god papa
Fist to watching ❤
Takambani za black box inu, report is incomplete without black box
Chilima anaphedwa bas ndipo one day chizavumbuluka
Aaa a2 amenewa akutiyesa ngat ife zitsilu et ife ndi omphunzila tipasen mwai kumeneko
Anthutu maumboni alinawo, koma a kuopa kuphedwa awateteze ndani.
Ineso ndikuti mufuse.kaliyati ndi ajenra akanenebwino
Mmmmm Nanu atolankhani lankhulani mosakondera mbali... Bwanji simukulankhula za black box? Nanga zopanga suspend searching ? Mmmmm no !!!!! no!!!! No!!!!! Let's be honest .
Mzuzu new airport ilikuti????????
Black box mu report muja sinakambidwemo
Ife sizitsilu
Public audiences could have given alot of people to give witnesses.
Don't overlook that.
Ma gyz inuyo ndi one ,2 ndiopotoka kkkkkkk
Kodi kutha kwa licence ndi nkhani yomwe tingati inathandiza kuti anthu aja aphedwe. Kwa ine pari zocuruka ndikungopukusa mutu komano yawe azakonza mosavuta
Nkhani la mkazi wa Kasambala musayitengere chifukwa ulendo wao unatheka, and there was no reason to waste time to interview her. The issue is where is the black box? Why did Chimwendo fail to use the aeroplane? Is it normal for a pilot to start flying without getting information from the control tower? Foolish report just like Chizuma's report, useless. I wish commissioners of enquiry should he held accountable should they come up with doctored report.
Ubwera bwanji ndi umboni ulibe lawyer and security. Akupha ngati nkhuku
Munali ndi Mwayi okapeleka Umboni wanu koma munasankha ochita nde Pano mukuti chani?
Munalandilazo ku dpp kabwezeni
Aaaa mumaganiza ngt chakwela mwaoneka 😅😅😅
Ndalama. Anatenga ndiyamene anawapanga chipongwewo osati a police, a police anafikapo mochedwa iya
Eya nkhani yo ndiyoona
Anthu akwanthu sazatheka amakonda kuba bas salabadira kuti apa Pali chani.
Zovuta
NKHANIYI KUNENA ZOONA MCP IKUZIWAPO KANTHU. KODI NKHARANGO YOKWITHIMAYO ZINARI ZOONA?KOMANSO WINA AKUTI NDENGE INAKAFIKA KUNZUZU POMWE WINA AKUTI AI. KOMASO ZOTI MUZIPEREKA REPORT AFTER 4 HRS NDI ZOONA? PAONEKA KUREPHERA NCITO KWA ANTHU ENA MWAPANGAPO CANI?NKHANI NDIOTI ENA AKUMWA WA MKAKA POMWE IFE TIKURIRA IZI ANACITA KUKONZA NDI CIFUKWA AKUNGOFUNA KUWAPARA AMARAWI NKAMWA IMENEITU IKUBVUTANI KURAPA KWAKE NDI AMBIRI OMWE ZIKUWA KHUZA NDI CIFUKWA AKUSOWA OMUVEKA BERO BWANA KOMANO BOMA RIKASINTHA TIZAZIWA ZOONA BASI
Penapake inu ndi program yanuyi mumapanga nayo ndale the fact is president and his Dogs killed Chilima and 8 others.