SAMEER SULEMAN NDI PETER MUTHARIKA SAKUGAWA MA SWEET KOMA AKOMETSA BLANTYRE - TAMVERANI DPP LIVE

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 8 янв 2025

Комментарии • 51

  • @ClementChilunje-k2c
    @ClementChilunje-k2c 16 часов назад +7

    Sumeer suleman ndi chilima wa lero 💪💪 akundipatsa feel ngati Dr SKC

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 16 часов назад +10

    Cikangawa lero nde akomoka tikamanena kuti mcp simungayime pa APM ndizimenezi 💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙boma!

  • @innokmw523
    @innokmw523 14 часов назад

    This suleiman guy....... uyuuu amayenela akaitenge utm ijaaaa the guy got energy yeeeses

  • @ComzySoko-c2y
    @ComzySoko-c2y 15 часов назад +3

    Replacement yathu Kwa SKC ndi Suleman bas God protect u Mr Suleman

  • @YamikaniYamikani
    @YamikaniYamikani 13 часов назад

    boma ndi dppppppp bansi💙💙💙💙💙

  • @YassenYasin-v6o
    @YassenYasin-v6o 13 часов назад

    😂😂😂😂😂 akuti chikangawa inuyo machine ❤❤❤❤

  • @Staphelsavimbindhlovu
    @Staphelsavimbindhlovu 16 часов назад

    Yaah Suleiman ndi akatundu eish 😂😂😂😂😂 ulemu wanu mr sule❤❤❤❤❤❤❤

  • @PatriciaAlomwe-oz8wc
    @PatriciaAlomwe-oz8wc 3 часа назад

    Wina Anya ampezeze team suleiman

  • @ModestaMlamba
    @ModestaMlamba 15 часов назад

    Chipani chosapangisa manyazi🎉🎉🎉❤❤ APM my vote 🎉🎉🎉

  • @AmosShadreck
    @AmosShadreck 14 часов назад

    Peter the most Loved president in malawi 😢 with joy

  • @MarthaGama-q1o
    @MarthaGama-q1o 16 часов назад

    😅😂😂 koma mwati ena sakomoka akamawona izii!! More fire a Malawi anzanga 🔥🔥🔥🔥✔️

  • @Staphelsavimbindhlovu
    @Staphelsavimbindhlovu 16 часов назад

    Adadi adadi more fire 🔥🔥🔥🔥🔥❤❤❤

  • @BobbyKabaya
    @BobbyKabaya 14 часов назад

    A.P.M is my vote ❤

  • @mphatsobwanali5981
    @mphatsobwanali5981 16 часов назад +1

    Apm azikuyang'anilani atate yahweh nthawi zonse,

  • @mphatsobwanali5981
    @mphatsobwanali5981 16 часов назад

    💙💙💙💙💙💙Apm my choice all the way

  • @KusalaMaganga-m2n
    @KusalaMaganga-m2n 13 часов назад

    Adad inuyo Mulungu anakusankhani kale mwainu muli otsongoleri, dpp woyeeeeee

  • @brightchataika
    @brightchataika 15 часов назад +1

    Suleman ndi SKC bas

  • @wayafrank2405
    @wayafrank2405 14 часов назад

    Boma ❤❤❤

  • @FrancisMalemia
    @FrancisMalemia 14 часов назад

    Skc no 2

  • @YamikaniYamikani
    @YamikaniYamikani 13 часов назад

    dpppppppp woyeeeeeee adad woyeeeeee adad kumenya kugwetsa ndi anyamata achina suleiman ndi achisale akumenya kugwetsa💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💯🎉💃💙💯💯💯💃🎉🎉🎉🙏💯💯💯💃💙💙💙💙🏃🏃🏃💃💃💯💯💯💯🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @EdwardSinoya
    @EdwardSinoya 16 часов назад

    Aona Nyenkhwe Chikangawa😂🙌

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 16 часов назад +1

    Kkkkkkk suleeman sazamva kkkkk umakwana mulungu azikuteteza

  • @DoreenMuhota
    @DoreenMuhota 16 часов назад

    Apm my vote 2025 😊❤

  • @VenusMataka
    @VenusMataka 15 часов назад

    Chikagawa lero akomoka katatu 😅 madala afika waimanya😂😂 chingawa mayoo!!! It's just beginning sunat chikangawa😂

  • @kekeaufi9834
    @kekeaufi9834 15 часов назад

    💙💙💙💙💙

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 16 часов назад

    Ulemu wanu adad mulungu akhale nanu

  • @MacxwellStuarts-h9r
    @MacxwellStuarts-h9r 14 часов назад

    Choona ndi choona simungachikwilire malonda abwino amakagulidwa ngakhale atayalidwa ku seri

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v 14 часов назад

    Koma muziyenda malawi yoseka kunoso ku Central region muzitiyendela DZ

  • @CharlesMateyaGospel
    @CharlesMateyaGospel 14 часов назад

    🍇

  • @ModestaMlamba
    @ModestaMlamba 15 часов назад

    Chikangawa anya manyiiiiiiiiiii

  • @PatriciaKapito
    @PatriciaKapito 16 часов назад +1

    Boma koma Dpp woyee

  • @BerthaAlfred-q5l
    @BerthaAlfred-q5l 15 часов назад

    🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @JoaneCarlitos
    @JoaneCarlitos 16 часов назад

    Chaka chino tiona zoopsa vuto ndiloti zipani zikupikitsana ndi Smart Matic zimene zizakhale zovuta kugonjetsa

  • @ajasikalonga3210
    @ajasikalonga3210 15 часов назад

    Kkkkkkkk chikangawa ndizomwezotu kkkk😂😂😂😂😂😂 upha tonse

  • @BistonMacheso
    @BistonMacheso 16 часов назад

    APM boma iloooooooo

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 Час назад

    Dpp ndi boma!!

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 14 часов назад

    Mdima ungakule bwanji Koma kumacha, masiku amatha ndi kugona

  • @MercyKziphondo
    @MercyKziphondo 15 часов назад

    Boma ilooo

  • @SamsonJoram
    @SamsonJoram 15 часов назад

    Akapume achikagawa

  • @GabieBlack
    @GabieBlack 10 часов назад

    Munthu woti sanazolepo manyi

  • @BashiruAdamus-l2b
    @BashiruAdamus-l2b 15 часов назад

    Adadi zowona chaka chofunika kwambiri mutipulumuse muwuvuni tilimu

  • @Margaret-b2m2w
    @Margaret-b2m2w 14 часов назад

    Amuna ogona kukhomo kosaseka

  • @NoahPhiri-f7m
    @NoahPhiri-f7m 16 часов назад +2

    Mufuniranji umboni wina kuti APM 2025 kuposa zomwe mukuona

  • @SamsonKhobiri
    @SamsonKhobiri 14 часов назад

    Km chimutharikachi ndi ntunda wina gyz, machinjiri ekha nde chatipula ee

  • @lacksonsiyadi943
    @lacksonsiyadi943 16 часов назад

    Uyu ndi katundu kaziotche

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 16 часов назад

    Chikangawa agwa nkhunyu basi

  • @Tawina0101
    @Tawina0101 16 часов назад

    16 spt,2025.

  • @ChuzyBoy-u1c
    @ChuzyBoy-u1c 16 часов назад

    Boma iroo 😂😂😂😂

  • @StevenDastan-f5y
    @StevenDastan-f5y 2 минуты назад

    Boma ilo

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 16 часов назад

    Mbambande ka