BON KALINDO LERO PA 13 JANUARY WAULURA CHIFUKWA CHOMWE WACHEDWERA KUTULUSA VN YA LERO NDIPO WATI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 13 янв 2025

Комментарии • 149

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll День назад +12

    Dzina Loti Valentino, ndikukaika ngati Ali mmalawi ameneyu, akuyenera kukhala waku Mozambique, kuchimake Kwa nkhanza

    • @RuthBeyala
      @RuthBeyala День назад +1

      Ukunena zoona tiyambe kumufufuza galu ameneyo

    • @FaroukSaliem
      @FaroukSaliem 18 часов назад

      Zoona dzina limeneli ndi lakumozambiq

  • @HildaLimbusha
    @HildaLimbusha День назад +9

    Koma a kalindo mumadalila chani,muyankula mofasa koma tima point towawa kkkkkkkkkk koma ya

  • @JorMan-x8e
    @JorMan-x8e День назад +4

    The DC ndinu number 1

  • @SadrackTseka
    @SadrackTseka День назад +6

    Ambuye ngati chakwera mudamulenga ndinu mulandileni ife sitikwanitsa kukhala naye watikwana eeesh mulungu wanga chakwera waonjeza lolani kumutenga asatipangitse kt tizichimwira inu daily

  • @Dayanschirwa
    @Dayanschirwa 10 часов назад

    Sitizasiya kuvesera bone kalindo mumaatiyimirira cifukwa mmanena cilungamo ❤

  • @mbonilekisebe2286
    @mbonilekisebe2286 День назад

    The DC mwana owoopsa kwambiri.... Long live the DC

  • @ChrispineMuzungu-l8h
    @ChrispineMuzungu-l8h День назад +3

    Ndipo munthu wina waphedwa mmmm zomvesa chison kwambr so sad in Malawi

  • @NkhomaFungo
    @NkhomaFungo День назад

    All the best DC❤

  • @WatsonMzava-k9f
    @WatsonMzava-k9f День назад +1

    Osasiya kufela Malawi❤

  • @wideafire9784
    @wideafire9784 14 часов назад

    ulemu wanu bwana DC

  • @ShamGabriel-j8x
    @ShamGabriel-j8x День назад +1

    Born kalindo the DC ❤❤

  • @YassenYasin-v6o
    @YassenYasin-v6o День назад

    Dc🎉🎉🎉🎉❤❤❤

  • @HopeLuwangakaunda
    @HopeLuwangakaunda 15 часов назад

    The DC mwana oopsa kwambiri President of the poor people

  • @victormaluwa6710
    @victormaluwa6710 День назад

    We're behind you the DC

  • @HabiboZimba
    @HabiboZimba День назад

    Boom boom ❤❤❤DC

  • @YassinzaoZao
    @YassinzaoZao День назад

    The DC 🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤

  • @SamuelBinton
    @SamuelBinton 12 часов назад

    Kuno taziwonadi ndithu ena mpaka kumalebetsa ana onse pakhomo kukaladila chimaga mpakana matuba 6 pakhomo zowona mpomwe ena olo thuba limodzi

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate День назад

    ❤❤❤ DC

  • @CrementiChilamwa
    @CrementiChilamwa День назад

    ❤❤❤ the Dc

  • @KennedyBanda-p9x
    @KennedyBanda-p9x День назад +1

    DC waromwe ndipitara ndikumuranje

  • @MozyDandawile
    @MozyDandawile День назад

    Fire 🔥

  • @HabiboZimba
    @HabiboZimba День назад

    DC ❤❤❤

  • @godfreyalberto7425
    @godfreyalberto7425 День назад +1

    DC , Venancio Mondlane wakumozambique

  • @ClementMachira
    @ClementMachira День назад

    Chipongwe chanji chimenechi, sangakhareko ndisoni zoona?

  • @MadaBlack-t8y
    @MadaBlack-t8y День назад

    Makwana DC

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi День назад

    DC ❤❤❤❤❤

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of День назад +1

    Zaziii zeni zenizeni

  • @samsonhavenoyayshonga2609
    @samsonhavenoyayshonga2609 12 часов назад

    Mcp ikuchosa ma vote yokha .panopa nkhatabay vote yawo ayichosa , pang'ono ndi pang'ono zizakhala bwino ku mbali yathu.

  • @NzeruNkosi
    @NzeruNkosi День назад

    Bon Kalindo think about kumaika ma videos or ma pictures kuti uku tikumvela VN bwezi tima video tikuonako.. Keep up the good work..

  • @GrantNkhoma-n3e
    @GrantNkhoma-n3e 20 часов назад

    The DC mumakwanisa inuyo tili mmbuyo mwanu

  • @KennedyBanda-p9x
    @KennedyBanda-p9x День назад

    Mwene mureke bodza muyambaso masewero

  • @Stretor
    @Stretor День назад +1

    Kkkkkkkkkkk eni ake achannel ino ndi 2025 not 2024 kkkkk

  • @MissyThobve
    @MissyThobve День назад

    Makwana

  • @BrightonKanyamula-i9i
    @BrightonKanyamula-i9i День назад

    The dc❤

  • @Rafick-jq8ts
    @Rafick-jq8ts День назад +1

    Malawi wanga ine 😢😢

  • @RoseChapinda
    @RoseChapinda День назад

    Osauka tonse kod malo okumanirana ndi atiwo tidzipita dziko lathu

  • @ShaibuSmart
    @ShaibuSmart День назад

    Dzoona Bon kalindo sukunama kkkk awazawavuta nyanja yapita uku

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i День назад +3

    Zonsezi dzikucitika coz uchisilu wa chikangawa ndi zache valentino anthu awawa nkhaza zawo dzinayambila pa ndege anapha kuchikangawa apapa angopitiliza .Ben longwe panopa wayamba kuima pachilungamo nde tikufuna adzithamang×2 naenso adzitipasila dzochitika kumeneko.Koma akupangazi caka cino dzitha 💙💙💙💙💙 DC MWANA OPANDA MANTHA.

  • @JohnPaul-r4u
    @JohnPaul-r4u Час назад

    R1475 pa week mungayambe kudabwa kuti akuti chani

  • @happynjikho4515
    @happynjikho4515 День назад

    This is bon kalinda mwana oophya kwambiri

  • @zayedmitawa8345
    @zayedmitawa8345 День назад +1

    MDF kumenya nzika zake sibwino.
    Anthu simungawasamutse musanapange arrange Malo oti akakhale.
    Ma notice azikhara at least a Chaka motsata ndondomeko osati kulamura asilikali kukapha mzika

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h День назад

    i think tayankhula kwambir let's take another step,,,,,anthuwa ationjeza kwambir😢

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl День назад

    Boorn kalindo 🔥

  • @JanatuCarlos
    @JanatuCarlos День назад

    Ndiye tiphanatu 😂 Ana azibwana amfiti

  • @mikelnorthern1911
    @mikelnorthern1911 2 часа назад

    Ulamuliro wa pharaoh plus dzaka 7 za njala

  • @NEBRA-lm7ji
    @NEBRA-lm7ji День назад +1

    DC amaponda paliponse

  • @EmilySalijeni
    @EmilySalijeni День назад

    Ndipo zoona nkhazazodi zikuchitika olo Thoylo panopa kwavuta kwambiri anthu akungomenyedwa ndi Ame akungozula chimanga kuno Ku Thoylo zomvesa chisoni zilikuno 😭😭😭

  • @RowlandAdinnie
    @RowlandAdinnie День назад

    The name Valentino the army general is a Mozambican it's what he says

  • @StandwellNjoka
    @StandwellNjoka День назад

    Koma mcp ikonjeza mukuwanyengerera munakangowaonetsa kamodzi kokha kongowalawitsa,mpaka kushuta mzimaiyu chonchi😢

  • @justinanyirenda6899
    @justinanyirenda6899 День назад

    Kasasire area

  • @EdwardSinoya
    @EdwardSinoya День назад

    Dolo ka 100🔥

  • @JimmyMzozoma-c7q
    @JimmyMzozoma-c7q День назад

    Tinadandaula chifukwa timaonadi kuchedwa tilinanu bwana DC

  • @KennedyBanda-p9x
    @KennedyBanda-p9x День назад

    Nanga pitara ubwino uripati muno mmarawi mavuto ngakarere kwambiri kuyamba.bingu anaguri ndege zomwe anagura kamuzu osati aromwe ayi muribe zeru mumanama ndiwazeru wawononga marawi

    • @EdythNamponya
      @EdythNamponya День назад

      Ubwino wake kulemba simutha komanso palibe chanzeru mwalemba apa

  • @StoniaMoyo
    @StoniaMoyo День назад

    Box 76 mwana wowopsa kwambiri❤❤

  • @frankfrankb8461
    @frankfrankb8461 День назад

    AMalawi tiyeni kunsewu

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 День назад

    History is the best Teacher.......osaopa..osatopa osafooka

  • @ElizabethMbewe-l2c
    @ElizabethMbewe-l2c День назад

    Umakwana DC

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe День назад

    A Bon kalindo musamati andale aiiiiiiiii koma chakwera ni mcp ndiamene akuzunza anthu

  • @veronicajana5225
    @veronicajana5225 18 часов назад

    Koma mwati ndi a police ndi amry eni eni kapena new fake recruit

  • @SildaKatundu
    @SildaKatundu День назад +1

    Mulungu alipo awakantha achina Chikangawa

  • @ChristopherManase-s1f
    @ChristopherManase-s1f День назад +1

    Kkkkk kodi Mesa unkati uchotsa chakwela muboma iwe? Zili Pati tsopano? Kkkkk koma

    • @GabieBlack
      @GabieBlack День назад

      Dikila nthawi ikubwela September uzaona ndmaso ako

  • @VINTRO-vw4ld
    @VINTRO-vw4ld День назад

    🎉❤

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe День назад

    Joice banda anakweza malipiro ama civil service ndi 57%

  • @MaggieCement
    @MaggieCement День назад

    Awatu olo Muthu atabvua ndikukhala mbuanda sangamve chifukwa azazidwa ziwanda zachuluka zochuluka kwambiri end panopa ndithawi yomwe tione satana uja adaponyedwa pnsipano uja thawi yake ndino kuti timuziwe

  • @ryanasandram65
    @ryanasandram65 День назад

    Zimvere mu mtolo ku Makande kkkkkkkk moni moni aphumzittsi a ku Ngabu Zone

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 День назад

    Chamba chimene akusutacho imfe timasuta chamba koma chaulele sichabwino

  • @rodrickmaster
    @rodrickmaster День назад

    Boma ndilomweli tingositha utsogoleri ndi chipanichi basi😮

  • @RoseChimbwefu
    @RoseChimbwefu День назад

    The DC Born Kalindo iwe siuwopa munthu

  • @Michaelaliemapira
    @Michaelaliemapira День назад

    BOSSMAN. MWAKUMBUTSESO
    PAJA ANANENA KUT ADZAPANGA RESIGNED. KOD LELO DZIKO PALIPONSE ANTHU AKUZUMA ZITHU SIZILIBWINO. LELO RESIGNED IJA ILIKUTI

  • @MosesJJ-d2p
    @MosesJJ-d2p День назад

    Ok

  • @ChimwemweMathyola-d1j
    @ChimwemweMathyola-d1j День назад

    Amalawi tikuvutika ngati sikwatu

  • @SilenceCryton-n9w
    @SilenceCryton-n9w День назад

    Akabwerezela kwa kadzake chakwerayo ndipo wandinyasa kwambiri tsogoleri osaganiza

  • @JafaliMataya
    @JafaliMataya День назад

    Without the DC Malawi 🇲🇼 tikanalandidwa kale

  • @AndreFretcher
    @AndreFretcher День назад

    Iiiii koma zimenezi zikuchitikadi, ndie azitsogoleri akutani??? Malawi tili be m'tsogoleri tiyeni tisankhe m'tsogoleri mu September

  • @BressingsNtambalika
    @BressingsNtambalika День назад

    Zonadi kuti anthu amenyedwa kapena na mungolakhula malingana ndi mene pagraundi ndimene palili

  • @KennedyBanda-p9x
    @KennedyBanda-p9x День назад

    Bon muribe zeru mabodza muribe aromwe karimenu nandoro

    • @SadrackTseka
      @SadrackTseka 10 часов назад

      @@KennedyBanda-p9x wadya nawo za kuchikangawa et ngat achakwera ndi uncle ako ukawauze kt pachipsenthe pawo ndiwe ndan kt ukanyoze alomwe ndiwe galu mvivi kapena kt tsetsetu ndiwe wakudowa et timuumbalitsa jando chakwera chakachino wandikwiyitsa bwanji ngt wadya nawo zophera chilima zija usanza wamva

  • @KennedyBanda-p9x
    @KennedyBanda-p9x День назад

    Ndiwe Kaya amakutuma uribe zeru unane mabodza ambiri ndiwendani mmarawi kape wenweni komaso ndi muribe

    • @HamuzahBamusi
      @HamuzahBamusi День назад

      Kodi inu mapwara ako ulibe nzeru Mai yako akunyera chiteze uko ukuyankhura chani apa panya pako

  • @GraceNdamuwa
    @GraceNdamuwa День назад

    Born Kalindo

  • @JumaEriya
    @JumaEriya День назад

    DC chonde boma ra chifunga rawojenza tiyeni pasewu mademotu basi

  • @IsabelLuka-i8f
    @IsabelLuka-i8f День назад

    THE DC ambuye adzikukutetezani ndikukupatsani moyo wautali,timanyadirani.

  • @EmmanuelLouis-t1x
    @EmmanuelLouis-t1x День назад

    Kuvotera mcp kuli ngat kulupha manyii kuponda konzo

  • @andrewmtendere3167
    @andrewmtendere3167 День назад

    Tiphane bas

  • @tambuwisick
    @tambuwisick День назад

    MCP mborazokhazokha 😡

  • @pharleykanyoni4517
    @pharleykanyoni4517 19 часов назад

    Koma abale kulakwa

  • @charityChindebvu
    @charityChindebvu День назад

    Ndipo ku kasasireko alanda Malo Oti a Zi Gogo a zigogo athu anankhalako karekale

  • @REXCHARLESKAJAWO
    @REXCHARLESKAJAWO 13 часов назад

    Mavuto alipo

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam День назад

    Chakwela ndi president ochitisa manyazi kwambili akukhawulisa athu kwambili why why anapha chilima iwe lazaro mulungu akusende iwe

  • @ChristopherKachepa-n4x
    @ChristopherKachepa-n4x День назад

    Asilikali onse ndi MCP mbuzi za athu agalu Malo ndi anu

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko День назад

    ndiposo sitingawavotere tapenga azawona kotere chavuta apo ndi azikhare anari konko ndachina mganda chiumia ndiye anthu wose sanapiteko kumusonkhano anakana ndiye amganda nda gotani hara anthu kukana kupita kumsonkhano ndiye avekere anthu akuno sitizakuthandizani ndinu wopanda nkharidwe anthu woipa ndithu nkhani iyi agotani azikhare amganda kotere anaretsa ndikujambura a time's kuti asajambure angapangike manyazi ndithu bon karindo mkunena zowona

  • @RejoiceMbewe-w5g
    @RejoiceMbewe-w5g День назад

    Chifukwa choti mbali imeneyo PP iliko

  • @IsiahChikwe
    @IsiahChikwe День назад

    IZIZI NDIZOONA KASASILE NDI BUNJI.ASILIKALI ALANDADI MALO NDIKUGUMLA MANYUMBA.

  • @blessingssilumbu2664
    @blessingssilumbu2664 День назад

    Katemera wa Johnson anayamba kugwira ntchito

  • @Samson-ve5rs
    @Samson-ve5rs День назад

    Ife timangomva ndi agogo athu Kuti MCP ndi ya nkhaza Koma lero tikuziona ndi Maso Vuto nkhwidzi Za a Timothy Ntambo ndi bungwe lija la HDRC, Zodiak radio, Times TV komanso inu a DC mudathandidzira kuchotsa Boma la mtendere la DPP mumafuna Kuti muphe mtundu wa a Malawi chonchi lero mwadzindikira Madzi Ali m'khosi

  • @JohnChiyazu
    @JohnChiyazu День назад

    The DC

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko День назад

    ndizowona ineyo ndikwagogo kotere mwezi watha ndinari konko nyumba zose anamphwanya zakudya kutayataya kukasasiri ndithu kotere ndinari Koko kotere chimene chikudabwisa ndiichi ari kutcharitchi kumeneko akupitaso kumeneko kukawamenya Kodi ziko iri ndi marawidi ambuye tiyendereni

  • @AliceChipeta-pc3nb
    @AliceChipeta-pc3nb День назад

    Ife kuno kumzuzu kulupaso primary school.
    1 ndi 2 3500
    3 ndi 4. 4000
    5 ndi 8 5000
    Yeyetu ma class ndimene ndikuyendela kuno ku mzuzu

  • @MussaAli-h4i
    @MussaAli-h4i День назад

    Mulungu tichtilen chfundo

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe День назад +1

    Tathokoza bwana bendolo ni ayuba James

  • @EusébioLucianoGaiondo
    @EusébioLucianoGaiondo День назад

    The dc

  • @KennedyBanda-p9x
    @KennedyBanda-p9x День назад

    Mabodza ureke karindo komweko kwaromwe kuno I we ndipitara takukana

    • @mozesjackson6328
      @mozesjackson6328 День назад

      Bon kalindo sanama amanama ndamako machende Ako wamva anthu akuvutikatu

    • @HendersonKapanda
      @HendersonKapanda День назад

      Kdi mutichani achitsiru inu...... Musamaikire kumbuyo zithu zopusa mwanva,,, dziko siliri bwino wanvaa kape iwe