Guys if we want Malawi to become a better country let's vote for this guy Enawa they will just waste our time We gave DPP 5 years they failed us MCP ndimeneyo they failed us again Who ever will vote for DPP or MCP again ndiye kuti mukufuna muzingovutika...let's think big guys for a better malawi
Dr.Dalitsa Kabambe is second to none in the field of economy in Malawi.Get rid of Malawian mendicancy when you enter your in your incumbency this year Dr Kabambe!!!
this country needs an economics and someone with financial management experience munthu okamupasa vote ndiyomweyi check how bingu hold economics ya dziko lino VOTE yanga watenga kabambe
Ukakhala kuja kwa boma ndichoncho ndithu, umayankhula zanzeru tiye ilowe hiiiiii palibepo chanzeru apa amene angathe kukonda dzikoli ndi Yesu Basi ndi Yehova woh. Awa anali mboma.momwemo lero siawa ali ndi milandu yambirimbiriwa
I have come to understand that, every politician is brilliant when he's not in power. When he/she is in power everything changes.......
Kabambe my vote
The man with wisdom it's my vote Kabambe UTM boma ilo
Well said mr Kabambe .
This guys has something to say
Alliance with Dpp and rescue this country
no we don't want alliance any more
@@Elizabethmanda-es7setell them😂
The president has talked
DK thus fantastic explanation thumbs up
People let's try to give him a vote
My, vote
Guys if we want Malawi to become a better country let's vote for this guy
Enawa they will just waste our time
We gave DPP 5 years they failed us
MCP ndimeneyo they failed us again
Who ever will vote for DPP or MCP again ndiye kuti mukufuna muzingovutika...let's think big guys for a better malawi
Listening from cape Town pa boma mr kabambe your chosen to be a leader of malawi not chikangawa❤
My vote
My vote is waiting for you
My vote for you DK is ready
I gave him my vote kale kale nthawi ya SCK. Take it DK.
My vote big up
My vote ❤
Uyu sangatichitise manyazi or pa debate nda china chikangawa wa!keep more fire burning 🎉
The guy is smart and has mfundo
He is sounding like a Plan🎉
Kabambe on 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Congrats Dr Dalitso kambambe you are good leader 2025 Boma
Ine nnalembetsa becouse of you other wise sikanapanga you deserve to be voted Mr dk❤❤❤❤❤❤
Ndipo zoona zake❤
Tikufuna kusitha pa ndale osati omweomweyo ayi ❤
Uyu akuyenela vote ❤
My president 🔥🔥🔥
UTM MY VOTE
Good messages mr kabambe😢
Chilima was something else
Good one.....
Boma iloooooo DK my vote
Dr.Dalitsa Kabambe is second to none in the field of economy in Malawi.Get rid of Malawian mendicancy when you enter your in your incumbency this year Dr Kabambe!!!
This is type of a president that Malawi needs. An economist that understands economy. Osati zinazi, let's wake up Malawians!!!
Kod background sound yi bwanji
Ndipo kabambe ali ndinfundo zogwira mtima uyu nde president isalute u Dr kabambe inu mukutipukuta misozi ya chilima
You have my vote #Dk2025
Big up kabambe chiyambikeni sindi danveko fundo zanu bwana SCKrest in peace😢😢😢😢 osatopa osafowoka🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
More fire kabambe,fundo zabwino.
Machine
DK 2025 bomaaaa🔥🔥🔥
aMalawi tigwirizane chimodzi, vote yathu tikapatse DK basi!
Eyo! Tieni !!!😂🎉🎉
We need such people like Kabambe. Keep on fire burning
Big man wulemu😢
Powerful
Mr president u need 100years to change malawi,
Tifuniranji wina apa a Malawi tapata basi❤
Genius
My President 2025 September.
Kabambe is my vote
Inu a Kabambe tiombolen
My vote kambambe
Politicians and lies😂😂😂😂😅
Every one come with a good idea but if they come in, they forgotten, everything. Is only let bingo was doing a good job.
I want to talk to him direct
Akabambe mkulankhula bw;i koma msathamangise kulankhula ; mzvala magekete kusonyeza kut ndiwe przdnt❤❤❤❤❤❤❤❤🎉:
Ndaseka😂😂 Dk 025🔥
Nice bro go l head
Bwana ndinuyo yankho....mutipeze tikupatseni mangolomera
This is our president moto kuti buuuuu Dr Kabambe boma ilo
Zofuka pa malawi sizingapose yapa. Go on papa tili pambuyo panu
DK MY VOTE
Utm❤❤
Munthu wa nkulu DK my vote
Big man 👨
Vote yako ndinayisunga pabwino heavy
DK…….SKC legancy
Alliance with dpp
No we don't want any alliance
@Elizabethmanda-es7se utm singawine yokha nde mukatero u mean Chakwera apitirize kuzunza anthu
vote yanga mwasunga bwana
Dk my vot
Dk my vote
Big up DR kabambe
UTM MWACEPA DZIKORI POMWE MCP YARI-IKAPA SIZIKUFUNIKA NSOGORERI OTI AZIKAPHUNZIRIRA PAUDINDO WAUSOGORERI AI ZIKUFUNIKA OZIWA ZOCITA .MAGANIZO ANGA MUSAKAKAMIRE KUKHARA PRESIDENT AI TAPANGANI CIMVANO NDI DPP PLEASE
🔥🔥🔥
this country needs an economics and someone with financial management experience munthu okamupasa vote ndiyomweyi
check how bingu hold economics ya dziko lino VOTE yanga watenga kabambe
😂 Anthu andale
APM SAMKABWEREKA MUNTHAWI YAKE.APM AOMBEREDWE MMANJA.
Voice imeneyi yofunika a church clerk osati abusa 😂😂😂😂😂
Mwayambapotu paja Peter mumkatiso ndiopanda mano koma Chakwera wachizungu lero ndizi 😂 tamaganizani guys
Bwana takambani ndi professor thalika mukoze dZikoli
Ine vote ya nikuvoterani komasamala ndi nduna zadyela zimene zimayenda yenda kuzipani zonse kumene kulindrama kusasamala ovota kumzi ovutika ndife ovota❤
Uyu nde wabwera tiyeni timutsatre
Tifuniranji wina apa a Malawi tapata basi
Auzeni bwana ,kumangokhalira kupempha pempha mmmmmm eish!!!
Utm my vote
Ukakhala kuja kwa boma ndichoncho ndithu, umayankhula zanzeru tiye ilowe hiiiiii palibepo chanzeru apa amene angathe kukonda dzikoli ndi Yesu Basi ndi Yehova woh. Awa anali mboma.momwemo lero siawa ali ndi milandu yambirimbiriwa
Machine opangila machine anzake
Koma kabambe iwe mmm titakuyesako mbambadi ndanena iweyo ukhara president ufune usafune vote yanga izapangisa kut bwana kabambe awine
Hear what the Holy spirit is Saying I warn and advice before September...
Auzeni kabambe ngatitisankhe mofoira tizariranso zaka5 zinazo
DK my vote
Mbambande tikufuna msogoleri WA Maso mphenye otere
Muli nzelu zakamunzu
Ndi bingo umu
Ine siwandale koma sindimanena
Pambali osamuluza utu
Angokhala opanda mzeru kwamtereyu apa ndie amuuzila mayesotu
Mugodi wakukasiya komwe kuchipinda kwa mcp tikauyanbe
Dpp+utm=boma
Kma ngat ukufuna kupanga izi wekh ndukuuza sudzamaka
Koma chilungamo chipose apa munthu uyu mumumvensese zose zoipa ndzake koma akuyankhuchi ndichilungamo
Tazivani ma follows anu akamayakhula tikutulukanitu
Ayi Alindimfundo zabwino
We need an economist not a theologian
😂eya not munthu oti amkagwira ku chipiku
Mbambande
Maboza okha okha awa, we miss you SKC continue rest in peace