NKHANGA ZAONA PA LIMPOPO FM NDI COMRADE NTANYIWA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 26 янв 2025

Комментарии • 16

  • @CharlesJames-f1w
    @CharlesJames-f1w 15 часов назад +3

    Mtawi.yamutera.chakwera.ntanyiwandi.ma.muna.weniweni.opsaopa.❤❤🎉🎉

  • @DavidChamani
    @DavidChamani 15 часов назад

    I love you so much My Elder Brother Tanyiwa

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso5062 15 часов назад

    Tamia Ja ndi nfana oganiza bho,, sangalore kugonana ndi ma members a Chikangawa party.

  • @MartinNice-z9n
    @MartinNice-z9n 8 часов назад

    Akunama nthaw yawo yatha respect ntanyiwa

  • @MathewsMakalan-l6v
    @MathewsMakalan-l6v 16 часов назад

    Big up Mr tanyiwa

  • @TasiyanaChinula
    @TasiyanaChinula 6 часов назад

    Eeeeee koma nkhani zake..
    Akumulakwira Tamiya....olo kugonanako basi zimaoneka zophweka kodi????

  • @KetrinaMpachika-c1p
    @KetrinaMpachika-c1p 4 часа назад

    Vuto ndroti mcp sikufuna kuti i vomereza kuti akupanga zinthu zolephera pachirichose

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 13 часов назад

    Koma kumeneko! A cina cimwendo ndi amene amafuna kunyengana nae nde yapheduka makape a mcp, nkhani ndimenei yoti akufuna kubela mavoti.Ndicifukwa cani amati sanagudwe pamene anali atugudwa cimene amabisacho chimenecho koma akunama sitisiyana umakwana comrade program ikhale choncho comrade manyo×2 basi palibe kubela.

  • @SteveMasuli
    @SteveMasuli 7 часов назад

    Kachasu wa kwachida kwa Bvumbwe anamukwana

  • @KetrinaMpachika-c1p
    @KetrinaMpachika-c1p 4 часа назад

    Zoti anapha chilima amakana zoti zinthu sizikuyenda bwino akukana ndakufuna chani aaaa

    • @MarthaMusa-j1w
      @MarthaMusa-j1w 2 часа назад

      Kodi ngati sanaphedwe black box akuibisilanji? Palibe chinsisi pansi pa thambo

  • @SteveMasuli
    @SteveMasuli 7 часов назад

    Chimwendo galu galu ndithu

  • @HanifuShaibu
    @HanifuShaibu 15 часов назад

    Mumakwana inuyo atanyuwa

  • @PatrishaMwale
    @PatrishaMwale 16 часов назад

    Tikaima pachirungamo chionrke

  • @MartinNgoma-tp2jk
    @MartinNgoma-tp2jk 2 часа назад

    Muulungu akafuna kuolosa anthu zigawenga zimasowa zochita mcp nizigawenga zisoba zochita shuwa bize kumanga anthu zikoyakanika basi

  • @AubMakwacha
    @AubMakwacha 16 часов назад

    🎉