Ambuye adzikupatsani mpweya wamphanvu kuti mudzilankhula. Koma inuyo a Boni Kalindo mudzidziwa kuti mavuto amene akukumana nao a Malawi 🇲🇼 munyengo inoyo ndi boma MCP. Zonse zimene zikuchitikazi ndi chifukwa cha inuyo a Kalindo pamodzi ndi Chilima ndipo ndi anthu inuyo amene munapangitsa kuti Malawi afike pamene alipa. Zonsenzi munachita chifukwa chakuti inuyo a Kalindo and Chilima ndi team yanu imene munayambitsa UTM munkachita nsanje kapena kuti jealous ndi a Peter Mutharika. ndiye pakuti munkadana ndi a Peter Mutharika ndichifukwa chake munawapeleka a Malawi 🇲🇼 ku MCP. ndipo sindikudziwa ngati Chilima ali ndi ntendele kumene aliko. Chifukwa anthu inuyo ndi amene munawaika a Malawi pa mavuto. chifukwa chimene ndikudziwa ineyo a Malawi anathana ndi MCP 1994 ndipo sankaifunanso ndipo anada nayo kukhosi. Koma iweyo Kalindo ndi Chilima ndi amene munawakakamiza anthu kuti avotele MCP. Ndipo inuyo a Kalindo pamodzi ndi team yanu imene inachita zimenezi mudziwe kuti milandu imeneyi mudzakayankha kumwamba chifukwa mwazunzitsa a Malawi 🇲🇼 osalakwa.
What Bon kalindo is saying is true
A south African friend was playing a narrative of this on his radio about Rwanda and the rebels in DRC
Seriously we thank this bcoz tikufuna zinthu zizifka poyera
Yaaah,uku nde kulankhula kwa khake kumeneko; Big brain.
Ntchito za MCP nzakumidima amakonda kumwa magazi
Kom Kalindo eshi ndagoma ine muli history too much ai chito yabwino the DC tingoti Mimosa Mulanje bas
May God bless you bon kalindo
Thanks Mr DC according to your information
Ambuye azikudalitsani a bon kalindo
Koma anamwiwa alipo muwawuzeko tawasowa
Bon kalindo ❤mwana oopsa aaa
Iweyonso Ndi Mbuli kalindo Anthu afa aku South Africa wo siamthu Iweyo suziwa kuti kjli maiko amu Africa onse
Chitsiru chimenechi, Kalindo ndimamuona ngati wanzelu koma ndichitsiru, akuona ngati akati nkhondo ndekuti asilikali amakhala akuvuna kumadya ma sausages, asilikali amafa kumene kunkhondo that's ntchito ya army
Ndi anthu km akudandaula, kd akudandaula nditchimo mpaka kumutchura mbuli muli mbali iti bwana tiuzeni mwina tiziwe 👂
@@BrendaJailosi aaaaaa Sadc meaning yake samadziwa angosunga tsitsi koma he dont know anything south Africa lose 9 soilders
@GiftMusorola-l2o komaso kupita ku Peace keeping zayamba lero?
Yabaya !!!!!!!
Thé Dc Bon kalindo ❤
Tamiaja osaopa akazingati inu ndiamene mumafunika ziko onena chilungamo pamenepo ndipomwe Unga ziwe kuti ndiwe ofunika ziko
Chipepeso kapena kt ndalama za anthu amenewa atenga chakwera ndi mkazi wake kapena kt kamajekete ndi kachimimba
MCP ndiyasamunda zimenezo tisiziwa guys
Ndiye chinacuilichose chikupanga Chakwela it's according what asamunda said to do
❤❤
Kuribeyi pindu kudrc tandizo ranji amathandizaro ziko rangondoro chiyani chakudya ndarama tandizorake kkkkk kusinthana ndiasirikari amarawi kupusa ETI
Maiko onse aku southern africa budget ya asilikili imachokera ku Britain that's why amatumidzidwa ku peace keeping mokakamidza alibe choice
Uuuuh nde kt Sitinatuluke be mu ukapolo wa samunda ooooh mulungu wanga tioneni ana anufe
Chamisala iwe asintha chani
Koma kuba misonkho kumamanga ma hotel ndimanyumba awo apamwamba kukanika ku manga zipatara
Makina
Awa ndakamuna amanena chilungamo
𝑩𝒐𝒓𝒏 𝒌𝒂𝒍𝒊𝒏𝒅𝒐 𝒎𝒘𝒂𝒏𝒂 𝒐𝒐𝒐𝒑𝒔𝒂 𝒌𝒘𝒂𝒎𝒃𝒓𝒊❤
Ambuye adzikupatsani mpweya wamphanvu kuti mudzilankhula. Koma inuyo a Boni Kalindo mudzidziwa kuti mavuto amene akukumana nao a Malawi 🇲🇼 munyengo inoyo ndi boma MCP. Zonse zimene zikuchitikazi ndi chifukwa cha inuyo a Kalindo pamodzi ndi Chilima ndipo ndi anthu inuyo amene munapangitsa kuti Malawi afike pamene alipa. Zonsenzi munachita chifukwa chakuti inuyo a Kalindo and Chilima ndi team yanu imene munayambitsa UTM munkachita nsanje kapena kuti jealous ndi a Peter Mutharika. ndiye pakuti munkadana ndi a Peter Mutharika ndichifukwa chake munawapeleka a Malawi 🇲🇼 ku MCP. ndipo sindikudziwa ngati Chilima ali ndi ntendele kumene aliko. Chifukwa anthu inuyo ndi amene munawaika a Malawi pa mavuto. chifukwa chimene ndikudziwa ineyo a Malawi anathana ndi MCP 1994 ndipo sankaifunanso ndipo anada nayo kukhosi. Koma iweyo Kalindo ndi Chilima ndi amene munawakakamiza anthu kuti avotele MCP. Ndipo inuyo a Kalindo pamodzi ndi team yanu imene inachita zimenezi mudziwe kuti milandu imeneyi mudzakayankha kumwamba chifukwa mwazunzitsa a Malawi 🇲🇼 osalakwa.
ℕ𝕕𝕚𝕡𝕠 𝕝𝕚𝕧𝕖 𝕞𝕣 ℝ𝕒𝕡𝕙𝕒𝕖𝕝𝕂𝕒𝕥𝕚𝕞𝕓𝕒 𝕄𝕦𝕟𝕥𝕙𝕦 𝕨𝕒𝕜𝕖 𝕟𝕕𝕚 𝕪𝕖𝕞𝕨𝕖𝕪𝕦 𝕒𝕟𝕕 𝕙𝕚𝕤 𝕗𝕣𝕚𝕖𝕟𝕕 ℂ𝕙𝕚𝕝𝕚𝕞𝕒 𝕞𝕦𝕟𝕥𝕙𝕒𝕨𝕚 𝕪𝕠𝕞𝕨𝕖 𝕒𝕞𝕜𝕒𝕡𝕒𝕟𝕘𝕒𝕟𝕒𝕪𝕠 𝕒𝕝𝕝𝕚𝕒𝕟𝕔𝕖 𝕄𝕔𝕡 𝕤𝕒𝕞'𝕜𝕒𝕕𝕫𝕚𝕨𝕒 𝕜𝕦𝕥𝕚 𝕟𝕕𝕚 𝕔𝕙𝕚𝕡𝕒𝕟𝕚 𝕔𝕙𝕠𝕚𝕡𝕒?? ℕ𝕕𝕚𝕡𝕠 ℂ𝕙𝕚𝕝𝕚𝕞𝕒𝕪𝕠 𝕟𝕕𝕚𝕘𝕒𝕝𝕦𝕟𝕤𝕠 𝕜𝕨𝕒𝕓𝕒𝕤𝕚
Live kumampandila ma demo peter muthaloka
Kkkkk km abale zinthu zake
The DC mukuyakhurazo zoona zokha zokha,yakhulani chilungamo cho mavuto kwa bas kudziko lathu.
Apa ndye wabwela bwino
Mesa amapanga makani Kuti akumapeleka 200million mma local government fund zapita Kuti Boma lapakamwaa miseche mabodza Kuba basii
Ndi u hure
Kodi munthu kungoyankhula maganizo ake ndimulandu? Momwe ndamvera zomwe anayankhula Tamia ja I think was just expressing her views.
MCP 😂😂😂 Agalu achiwewe angoluma aliyense.
KOKOLILIKOOOOOOOOOO KWADAAAAAAAAAA😂
🐓🐓🗡️🗡️
Osamangotchura Mulungu paliponse aaaaa
Ku Nkhondo anthu amafa kumene, sikuti anapita ku za tchalitchi kumaganiza penapake anthu inu. So cholowela ntchito yausilikali ndichani ngati mukuopa kufa? Akalindo mukuonetsa chitsiru apa
Gulu lachakwera losamva chisoni ndikufa kwa anzawo hehehe km muligulu
The DC ❤❤❤
Mbuyanga
Tamia ja tikukumpemphelelani nd Mr DC, mwana mulomwe umaintha
Kulibe chomwe mungane nkhondo ya Ku DRC inayamba kale kale kagame Sali president
Wayamwira 1983 anthu anaphedwa ku mwanza ndipo chipani chomwecho chikangawa kuyamwira za obaba
Kodi UN ili kuti
Nanga ndikuyamba kupita ku Drc asilikali aaaaa fundoless Nanuso maiko ena amatithandizawo amapeza chani ku Malawi
Inu ku drc amapezeko chani? Ndithandizo lanji lomwe amapeza ma banja awao
Iwe wa mcp war Ku DRC is multifaceted war among the tribes n funded by African leaders
❤❤❤