DR MICHAEL USI ZAWO ZADA KU UTM | NKHANI MADZULO APA 28 JULY 2024 |

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 7 сен 2024

Комментарии • 12

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v Месяц назад

    Lazaro Chikangawa Chakwera

  • @user-gd7xm7xr9v
    @user-gd7xm7xr9v Месяц назад

    Mungotenga nkhani za eni.osamati tikupatsirani nkhani..... Mudziti .....tikubwerezereni nkhani😂

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus Месяц назад +2

    Kulibe boma Ku Malawi
    Kuli chipani

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx Месяц назад +2

    Chakwera sadziwa kuyendetsa boma koma kugulitsa ku chipiku kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk

    • @robsontyg3928
      @robsontyg3928 Месяц назад

      Iwe machende ako wava, cadet chomwe mmadziwa ndikupha ma albino, pano sitikupatsan mpata

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r Месяц назад

      @@robsontyg3928nde MCP ndi yotani?? They’re no different than anthu a DPP. Muzingosauka mumtima nokhanokha

  • @YusufuUsumani
    @YusufuUsumani Месяц назад

    Okay katangale kapena kuti kalongonda ameneyi alibwino kwambili

  • @ChembeWaimba
    @ChembeWaimba Месяц назад +1

    Ovota Ali pa ground, inu mzilubwalubwa pa social midea pa ground MCP kuti buuuuuuuuuuuu

  • @jeffchikwapata6933
    @jeffchikwapata6933 Месяц назад

    Kulibe boma koma zigule zokha zokha

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope Месяц назад

    Tiyamikire kuti MCP ikuchita katangale kwambiri ndipo ilimbikire kwambiri kuti katangale apite patsogolo komanso tiyamike apolice polimbikitsa katangale pophatikiza ndi ant corruption mophatikiza ndi a MRA