Ulemu ku times, komanso chakwera ngati our president wathu koma tikasiyanisa 8yrs kuchoka 2014 to Pano aaaaah Chakwera and his government has failed us Malawian Pano walandisa immigration ku zigawenga chaka chamawa alandizanso intelligence agency tizitenge bwino izi si za ndale koma ma fact / Chakwera his 4yrs in Office scores 13% out of 100 Peter his 4yrs in Office scores 47% out of 100
You guys I just want to ask you this question, These politicians they can transform the country or they love their own country what's there are in power only, if so how can we believe them that they can do better yet nothing they did in their country
He was talking about Singapore in 12years not one, even u yourself u can see, so don't talk like u don't stay ing in Malawi, every one is crying in Malawi, so don't talk about Peter munthalika, he didn't take his son to give him any contract, so who's doing nepotism in Malawi right,be very careful. From johannesburg
Guy you are speaking openly and truly watching you live at SA Pretoria
This team add Brian Banda it will shake the whole national
Exactly brother
Ulemu ku times, komanso chakwera ngati our president wathu koma tikasiyanisa 8yrs kuchoka 2014 to Pano aaaaah Chakwera and his government has failed us Malawian Pano walandisa immigration ku zigawenga chaka chamawa alandizanso intelligence agency tizitenge bwino izi si za ndale koma ma fact / Chakwera his 4yrs in Office scores 13% out of 100 Peter his 4yrs in Office scores 47% out of 100
Ndipo Zoonadi uyu akuwonga dziko mwamva inu..
Akalowa mboma amakasandulila kukakhala ziwanda za pansi pa nyanja samamva chisomi kwan anthu osauka
😮Vuto la anthu amene akulamula ndiloti akangotenga ulamuliro amayamba kudziona ngati madolo omwe otsogoleredwafe singatsutsane nawo pamfundo zomwe akuzitsatira paulamuliro wao. Mwaichi amayamba kutenga maganizo awo ngati opamba kuposa a aliyense, ndipo satsutsika, satenga nthawi yodziunika okha pamomwe akulamulira, ambiri mwaiwo maso awo amakhala pakudyerera zipatso za kutinyengera kuti tiwavotere_ kuyiwala kuti mawa adzatifunanso.
Guys mm bola dpp basi siawa atabwaliwa ayi mcp kubin ikafik and asazazukeso
Program imeneyi yandtegula maso
I do agree kuti ma civil servants ndio amasithisa adale
Keep up 💯
Unless Boyz..
Welcome back
Dpp is better than mcp ndipo dpp imamva zomwe anthu akunena apapa mcp yafika potopesa chilichonse chili high
Sstana ndi satana ma guys palibe kusiyana
mutharika sazayima angopanga testing amene akufuna kuwawona ma presidents cadets
Kuona dzaka dza mbuyomo Malawi alibwino panopa. Ena aja anaononga kwambiri. Awawa mwina angophunzitsidwa kalembedwe ka malipoti a bodza kwa azungu.
You guys I just want to ask you this question, These politicians they can transform the country or they love their own country what's there are in power only, if so how can we believe them that they can do better yet nothing they did in their country
Choosing a better devil indee
DPP is the better devil is me from Soweto
Hot current 😂😂🔥🔥❤
According to the bible no matter how hard it was for the Israelites on their way to Canaan,they didn't go back to Pharaoh
mmati atsukuluza akuwoneka otopatu Mjamba rally imeneyo eti
Kodi zipani zilipo kumalawi ndi dpp and mcp bwanji osayakhula za udf ,afd and etc thawi yabakili bwanji
Inu ndinu madoro
These guys eeee mbambande
zitsiru izi takanyere uko mapwala anu
Achunga magalasi bwanj😂
Kikikikkkikiki choising the better devil
Komatu fusolo nde ndilovutadi kms mwafusa bwn kuti titseguke nawo mmaso ndipo kuti tsono titha kutani fukwatu ndie nchilungamo nayo dpp idabowaso kanthawi kenakake
He was talking about Singapore in 12years not one, even u yourself u can see, so don't talk like u don't stay ing in Malawi, every one is crying in Malawi, so don't talk about Peter munthalika, he didn't take his son to give him any contract, so who's doing nepotism in Malawi right,be very careful. From johannesburg
Chakwera is worse hummm
Mbwitu mbwitu
kkkkk wamutukwanatu akuwona ngati MCP ingawineso aja azikalima fodya basi
Dpp is better than mcp
Dpp ndiyabwino kusiyana ndi mcp koma iwe wakhala pakati ndiwe galu ndiwe wa mcp chisilu iwe
Ndipo live achisilu amenewo asiyen ziwavuta DPP is my vote
Komano vuto mbuli zaanthu safuna kusiyanitsa apa Chilima sakulamula muno aliyetse akudziwa maudindo kunchonsa sono bwanji until pano kukamba zachilima nonsense...
Iweyo ndi mbudzi chilima Sali mboma bwanji sakudzudzula bomalawoli
Ayambe kuyankha muzit ayamba kuwukilana onkhaonkha Chilima oganidzabho tasiyeni a dpp aziyambana ife mulibemo
Cinyengo cimatha ndi Yesu yekha osati bungwe
Amene sanacimwepo ayambe agenda mkaziyu
Koma mcp singafane ndi dpp ndichipan.chabwino peter muthalika woyeeeeeeee
Dpp is going to run the country again, from johannesburg cbd, DPP woyeee ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤