Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
I miss Zinaukamva.
😂😂😂😂😂waenda dziko lose simungamunamize monga kuzuzu 😂😂😂
Kod ndiye manambala awo bwanji?
Tingayankhure nawo bwanji ife kuno 🎉🎉
Munalibe ndalama..Mukanakhalanazo ndalama,, zikanatha zimenezo
❤❤ 5:54
Sing'anga wake kuyankhula izi kusiya kuyankhula nkhani iyi kusiya kulowanso nkhani ina
Akufa akuti angamvanewo
Iweyo umanisangalatsa kwambili komanso umayankhula mwaukadaulo ponya mbili zawanthu achina bingu Hussein ndionse odziwika bwino😊
Tandipaseni map ndikakumane naye sing'anga ameney.
Taponyani zina achelewuka .ndimakutsatani
❤❤
Alipobe😂😂😂
Awa akufa angavane zoona kkkkk
Mkaziyo munagona nayedi?
tiponyeleni zambiri zonse even ma audio achina bingu Albert muwalo sadam hussen Osama bin laden ndi zinazonse timasata zinaukamva
I like and love zinaukamva komano please tiponyeleni zambiri
Kodi Joy radio and TV inatha eti coz ine nasiya kuimva kalekale
Polisi ya kumalawi ndiyamanyi ndipo kwachuluka mbuli
Kudzitamilira awaa
Mbambande blessings
A bule sopano aaah man inuyo mmatha kwaabasi
Mulungu yekha bac namene amatetezela moyo wamunthu
Kkk
A Bule ulemuwako
Mli bho
Kodi ndiwe eti
Awawa aaa anagonadi ndi amaio aaaa
😢😢😢🎉😂
Kom zooona kut munasiya kugwila ntchito ku Joy Radio???
This guy is a womanizer I know him very well, he is in chikwawa Ngabu trading based
Ponyani zambiri man,
very pathetic
I miss Zinaukamva.
😂😂😂😂😂waenda dziko lose simungamunamize monga kuzuzu 😂😂😂
Kod ndiye manambala awo bwanji?
Tingayankhure nawo bwanji ife kuno 🎉🎉
Munalibe ndalama..
Mukanakhalanazo ndalama,, zikanatha zimenezo