BON KALINDO LERO PA 15 WAMUNG’ALURA CHAKWERA WATI JOHN CHILEMBWE NAYE ANALI BUSA KOMA SANALI CHISIRU

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 27 янв 2025

Комментарии • 134

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda 13 дней назад +3

    Bon kalindo same like chilembwe .kalindo zochita zake ndendende chilembwe

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d 13 дней назад +1

    The Dc 🔥🔥🔥🔥❤❤❤❤ tima kunyadilani more grace 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @StephanoKaunda
    @StephanoKaunda 13 дней назад +13

    Bon kalindo mo fire🔥🔥🔥

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 13 дней назад +2

    Eyaah DC izizi ndizomwe ndimanenazo kuti smart matic ichosedwe tisakhake ndi mtima oti yasiya kugwila ntchito chifukwa ikhoza kukhala filimu koma inu mabungwe ndi oposition iyiyi ndi nkhondo yomwe ikuyenela kumenyedwa pano.Icho chi DC kkkk iwe umandiwaza kwabasi.

  • @IsabelLuka-i8f
    @IsabelLuka-i8f 13 дней назад +2

    The DC tsopano,aaaah iweyo suopadi umakwanira akamuna bambo ogona m'nyumba chitseko osaseka,yonseeeeee!!!

  • @scoltenroma6240
    @scoltenroma6240 13 дней назад

    Kkkkkkk! DC iweyo unabwera kuzaomba lipenga,Oh Yes 🔥🔥

  • @rescoboardson-o3g
    @rescoboardson-o3g 13 дней назад

    Umakwana winniko 😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @GiftMatiki-q7s
    @GiftMatiki-q7s 13 дней назад +1

    The Dc timakunyadilani mulungu azikudalisani ndipo akupaseni moyo wautali

  • @ChrissySalimu
    @ChrissySalimu 13 дней назад

    More fire Mr DC

  • @PatriciaFund-n5r
    @PatriciaFund-n5r 12 дней назад

    The D.C. more fireeee🎉

  • @maxwelljuwaophiri
    @maxwelljuwaophiri 13 дней назад

    Ulemu wanu Honorable Kalindo

  • @MaryJamali-w7t
    @MaryJamali-w7t 13 дней назад

    Zoona bwana 🎉 congratulations 🎉

  • @sheilabanda7935
    @sheilabanda7935 13 дней назад

    Kkkkk mwana ooopsa kwambiri😂

  • @markanthony5402
    @markanthony5402 13 дней назад +1

    😂😂😂 komatu DC uli ndintopola

  • @Jamaat-m7l
    @Jamaat-m7l 13 дней назад +1

    The DC 🎉🎉🎉 you have a point

  • @JosephyMwale-u5y
    @JosephyMwale-u5y 13 дней назад +1

    The DC is best ever🤣🤣🤣🤣🤣

  • @MagretManase
    @MagretManase 13 дней назад +1

    Kuyakhula mosaona khope❤

  • @GrantNkhoma-n3e
    @GrantNkhoma-n3e 13 дней назад

    Born kalindo mmakwana boss man

  • @BerthaFriday
    @BerthaFriday 12 дней назад

    🤣🤣🤣🤣🤣 koma ndaseka eti

  • @jamesmasache3748
    @jamesmasache3748 12 дней назад

    Wayankhula zomveka bwino ndithu, chifukwa mavutowo ndiye alipodi mdziko muno eg kusowa Kwa madzi ku K C Hospital ndizinthu zoti za chilendo mu mbiri ya dziko lino

  • @ShylockBanda-o6u
    @ShylockBanda-o6u 13 дней назад +1

    Makwana big salute

  • @MerylKhamisi
    @MerylKhamisi 12 дней назад

    Born kalindo the DC

  • @lucksonmoonga4426
    @lucksonmoonga4426 13 дней назад

    😅😅😅 mwana oopyadi uyu.more 🔥.

  • @MozyDandawile
    @MozyDandawile 13 дней назад

    Born kalindo 🔥

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 13 дней назад +1

    Mcp yazazana ndi mbuzi zokha zokha basi chakwera number one chikangawa team imeneyo mulibe nzeru mcp ndi ma carward crocodile onse

  • @YohaneMabutao
    @YohaneMabutao 13 дней назад +2

    Bwana inuyo aiii ndithu ambuye azikusogolerani ndithuu makwana big

  • @CharityChirwa-v8v
    @CharityChirwa-v8v 12 дней назад

    ❤❤❤❤❤ moto 🔥🔥🔥

  • @WonganiJere-f8i
    @WonganiJere-f8i 13 дней назад

    I like this bon

  • @jameskadyaudzu3722
    @jameskadyaudzu3722 13 дней назад

    Hahahahaha🤣🤣🤣🤣🤣 Makape a MCP

  • @StandwellNjoka
    @StandwellNjoka 13 дней назад +1

    Ukunena zoona John chilembwe sanali mfiti,ndipo mwambo omukumbukila sunayenere kumapangidwa ndi anthu akupha,okhetsa mwazi mwadala

  • @FatimaHanifu
    @FatimaHanifu 13 дней назад

    My vote ❤

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 13 дней назад

    Koma ichichi amwene 😂😂😂😂😂❤

  • @JohnmjigoMalinda
    @JohnmjigoMalinda 13 дней назад +1

    Pamene mcp yafikapa ndikumafuna kuwinaso ndiye misalatu chakwera koma mutumo zikuyendamo 😂😂😂

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august 13 дней назад

    Mr Bon Kalindo president wa aphawi Malawi 🔥🔥🔥🔥

  • @WilsonFelix-j9n
    @WilsonFelix-j9n 12 дней назад

    Fire bon to bombclat chakwera machende aamake for two weeks

  • @NkhomaFungo
    @NkhomaFungo 13 дней назад +3

    Salute the DC

  • @FrankKadzuwa
    @FrankKadzuwa 13 дней назад

    I salute you DC

  • @Lucia-v3s
    @Lucia-v3s 13 дней назад

    More 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @enockjames3441
    @enockjames3441 13 дней назад +1

    Bon ulingati John chilembwe amwene

  • @HassanBabujr
    @HassanBabujr 12 дней назад

    The Dc❤❤❤❤❤

  • @dorothywillard2442
    @dorothywillard2442 13 дней назад

    Bon kalindo mwana woopsa kwambiri timakunyadiran

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope 13 дней назад +1

    Kalindo ukuyankhula zoona

  • @AubreyThom-h9g
    @AubreyThom-h9g 12 дней назад

    Indiye yake bg

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 13 дней назад

    🤣🤣🤣🤣🤣 kuyakhula Kwa president wathu

  • @ishmaelimedi7363
    @ishmaelimedi7363 13 дней назад +1

    Born saopa or ndipang'ono ndipo chakwera suzamuyiwala 😂😂

  • @ClementKamtema
    @ClementKamtema 13 дней назад

    Ndiwe mbuli bon kalindo,amene akulamulira ndi azipani 9 osat chakwera mcp sidawineko ngati ena amakutuma odzava kuwawa mcp ikadzawina mpaka 2030,palibe chimene ungapange atati ukhale president lero mupite kumaiko amene zinthu zawo zili pabwino.mcp my vote awinaso

    • @ChisomoYosefe
      @ChisomoYosefe 13 дней назад

      mbuli ndiweyo chifukwa sukudziwa chimene ukuyankhula udzakhumudwa koma mukutulukabe m'boma mufune musafune

    • @PatumaCassim
      @PatumaCassim 13 дней назад +1

      Hahahaha 😂mbuli ndinu simukuziwa chomwe mukulakhula nokha mukuti chakwera sanawinepo payekha nde angawineso bwanji mpaka 2030 😂😂😂😂

  • @GiftFrancesco
    @GiftFrancesco 13 дней назад

    The DC ❤❤❤❤

  • @JosephGabriel-y7w
    @JosephGabriel-y7w 13 дней назад

    Bon kalindo umakwana moto kuti buuuuuuuuuu mimba kuti swiiiiiiiiii

  • @TracyBanda-i2g
    @TracyBanda-i2g 13 дней назад

    Iiiii koma borni kalindo guys aaaaaa siyeni uyu wina capita naye ndaseka asaaa

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 13 дней назад

    Yakwiya ndi mizimu Mulungu salakwitsa akudzichotsa wokha pa mpando zochita zawo angokhala ngt a misala apule

  • @Samson-ve5rs
    @Samson-ve5rs 13 дней назад

    The D C❤❤❤❤❤❤

  • @henryTembo-n7u
    @henryTembo-n7u 13 дней назад

    The dc 💪💪💪💪

  • @GodfreyMatengo
    @GodfreyMatengo 13 дней назад

    The DC iweyo ndimsalamangwe sumaopadi.

  • @NdaonaChipwa-t7i
    @NdaonaChipwa-t7i 13 дней назад

    🔥🔥🔥🔥

  • @livingstonelangah3819
    @livingstonelangah3819 13 дней назад

    INE NDIMAFUNAKO PHONE
    YA THE DC❤❤❤

    • @I-Qz265Beats
      @I-Qz265Beats 13 дней назад

      Umveke audio yake ya pa 13 January I think. Yomwe amatokotela Army ndi Police. Anainena

  • @VictorJaphet-e6l
    @VictorJaphet-e6l 13 дней назад

    Kodi amipingoso ndiopusa inu ndi ozindikira èee muli nditsoka akalindo

  • @LaisanGoman
    @LaisanGoman 13 дней назад +2

    Zikuvekaz ndizionadi kut manganya wasowa ndi ndege

  • @LonjezoDivason
    @LonjezoDivason 13 дней назад

    Bosi ❤❤❤❤❤❤

  • @TechZaketa
    @TechZaketa 13 дней назад

    Ndimaona ngati contract imeneyo ikanakhala ya fuel koma ayi ndithu chakwera watilephera ndithu

  • @YahayaKondwan-mo8hu
    @YahayaKondwan-mo8hu 13 дней назад

    Kkkk iiii ama church mwanva ati agalu eeee katundu

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 13 дней назад

    Chakwera wake uti anabwera kuzapha kuzaba kuzagwetsa ndalama yathu yakwacha sitikumufuna ife chakwera wanuyo watikwana a

  • @ChrispineMuzungu-l8h
    @ChrispineMuzungu-l8h 13 дней назад

    🎉🎉🎉

  • @franktsoka
    @franktsoka 13 дней назад

    The boss❤❤

  • @ImminjaloImminjalo
    @ImminjaloImminjalo 11 дней назад

    Kutankhura kwabwino DC

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 13 дней назад

    Indeeeee ama church nawo

  • @AjanaChaima
    @AjanaChaima 13 дней назад

    Mo. Fire

  • @AlexanderTraffick
    @AlexanderTraffick 13 дней назад

    President waine ndameneyu

  • @PhilipCheuzi
    @PhilipCheuzi 13 дней назад

    Iwe ndiye umandimaliza mutima bwanji iwe ndiwed otimira ife osawuka

  • @MisheckKaseko-yb4cp
    @MisheckKaseko-yb4cp 13 дней назад

    Agalu inu mwatitora kkkk

  • @JamesYusuf-yc7cw
    @JamesYusuf-yc7cw 13 дней назад

    We need guys like you here in malawi

  • @KimmyIden
    @KimmyIden 13 дней назад

    Dc bwanji osangolitenga dzikoli ulilamulile tingamave kukomatu❤❤❤

  • @ChristopherChilambe-g4z
    @ChristopherChilambe-g4z 13 дней назад

    Akayendelenso chilembwe hospital ku phalombe

  • @JosephKwimbayani
    @JosephKwimbayani 13 дней назад

    Salute Boss ❤

  • @ChifundoFeston
    @ChifundoFeston 13 дней назад

    Ndiwe wa DPP Galu wachabe chabe

  • @HassaniHassani-yr2rf
    @HassaniHassani-yr2rf 13 дней назад

    The DC pangolin

  • @GREGORYBERNARDMATAMBO
    @GREGORYBERNARDMATAMBO 13 дней назад +1

    Wamisala uyu inu aaaaaaaa mutu wake unajama basi .

  • @MajiduNdiche-hl1ju
    @MajiduNdiche-hl1ju 13 дней назад

    Pena akumalakwisadi ndi azibusawa chikwa amafuna kuwachemelela andalewa ngt mwamboyo ndi wandale ndimayesa mwambowo ndiwamapemphelo ndiye chomalengezela chopeleka ndichani kusamankhalenso malonje aanthu andale azibusa apemphelese kumaliza pamenepo anthu ndi kumamwazukako bs

  • @PatrickKapendo
    @PatrickKapendo 13 дней назад

    Ngati pali chisilu cha munthu ndi winiko yemwe ndi Kalindo yemwe ndichisilu yemwe anawatenga amalawi kucholela ku dpp kupita ku mcp utm koma galu uyu amangolubwalubwa zausilu akuyesa kuvala dolesi iwe ndamane ukuyesa kuti tonse ndife zisilu m'mwaa aji

  • @ManuelJames-r5n
    @ManuelJames-r5n 13 дней назад

    The DC katundu wa amalawi

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 13 дней назад

    KAMPANI YAOYO IZIKAGWIRA NTCHITO MNYUMBA MWA MAKE A CHAKWERA

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 13 дней назад

    Koma ndiyed tu anachita kunena yekha Malawi likanakhala dziko lina chakwera atachotsedwa kale kale

  • @MussWalasi
    @MussWalasi 13 дней назад

    ❤❤❤❤❤❤

  • @JonathanMuhuwa
    @JonathanMuhuwa 13 дней назад

    Pangolini

  • @EnifarSeleman
    @EnifarSeleman 13 дней назад

    Chakwera ndiopusa 😂😂 kuno Ku Lilongwe sitikumufuna , fuel kulibe kuno

  • @harrisonmacheso
    @harrisonmacheso 13 дней назад

    😂😂

  • @livingstonelangah3819
    @livingstonelangah3819 13 дней назад

    ATI TILI KU KENANI APA ZOWAWA ZOKHA ZOKHA

  • @InnocentHassan-m3r
    @InnocentHassan-m3r 13 дней назад

    Big born kalindo inuyo palibeso

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 13 дней назад

    KATUNDU BAMBO 😂😂😂

  • @JorMan-x8e
    @JorMan-x8e 12 дней назад

    Ukali

  • @BravoGamah-n2t
    @BravoGamah-n2t 13 дней назад

    The DC

  • @JULIASKALITSIRO
    @JULIASKALITSIRO 13 дней назад

    Uthenga wanu ndi wachilimbikitso pitilzani abrazi

  • @NdaonaMsowoya
    @NdaonaMsowoya 13 дней назад

    Malawi ndi chililu chen chen olo maiko ankunja chifukwa samatituna grizano tilibe chisanzo anthu a ku south Africa amapanga umozi km malawi amasapota zopusa basi

  • @JuniorSaine-d6r
    @JuniorSaine-d6r 13 дней назад

    Nde mwat 0/10 😂😂😂...kma DC uli bho 🔥🔥🔥

  • @tambuwisick
    @tambuwisick 13 дней назад

    The Dc

  • @AssamMchenga
    @AssamMchenga 13 дней назад

    Mumakwanila bwana

  • @MaryPhiri-h6p
    @MaryPhiri-h6p 13 дней назад

    😊😊😊😊😊😅

  • @mikesandali8425
    @mikesandali8425 13 дней назад

    Inuso ndi achitsilu

  • @AyamiMustafa
    @AyamiMustafa 13 дней назад

    Osati galu alipanoyu munthu okuba kwambili

  • @JamesSingini-t4j
    @JamesSingini-t4j 13 дней назад

    No surname ya chtumbuka supporting this nosense,,,mtumbuka wenwen sangavotere DPP

  • @stormchatepa134
    @stormchatepa134 13 дней назад

    Nyo