SATANIC IKUKULA KU MALAWI KOMASO KUMANGA MAZIKO MOSAKAYIKA NDITHU

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 12 сен 2024

Комментарии • 209

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 20 дней назад +12

    What comes around , goes around ,
    No secret under the sun , may ALLAH bless our country MALAWl for ever .

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 20 дней назад +10

    Mkumabisala mu Dzina la Mtumiki wa Mulungu Koma zochita zake Nyansi zeni zeni.
    Mulungu akuyendere iwe Woyipawe ndipo uwone ukulu wa Mulungu.
    Brother Mtanyiwa keep it up.
    God bless and guide you in this evil World.

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 17 дней назад

      Ndiye choncho wina ndi uchitsiru wake aziti Chakwera 2025 Boma zoonaaaaaaaa???????

    • @kilt_la-flame265
      @kilt_la-flame265 17 дней назад

      ​@@VeronicaChirwa-ct4osndipo anthu alibe manyaz amwene, ambiriwa ndi okupha

    • @JamiluSunday
      @JamiluSunday 12 дней назад

      Koma abare inuyo aaaaa atimalizatu

  • @YusufuYunusuSavielMakey
    @YusufuYunusuSavielMakey 20 дней назад +6

    Vuto laife timasankha anthu okwaver koma onena analipo kuyambira Andale analankhurapo koma sitinawaver winaso Mr twaibu analankhuraso nkhan imenei koma timaona ngat akulankhura zogona lelo bwanji makosana but almighty Allah forgive us

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 20 дней назад +12

    The evil spirit is moving, eishhhhhh my Malawi where are you going. Our God who at in heaven please hear our cry

    • @MahometAli-e8w
      @MahometAli-e8w 20 дней назад +2

      Comrade Antanyiwa pls Malawi ipange strike kuti bushiri azipita ku South Africa amange

    • @MahometAli-e8w
      @MahometAli-e8w 20 дней назад

      Kmanso Chakwera akatuluka dziko zimachitikira zambiri

    • @MahometAli-e8w
      @MahometAli-e8w 20 дней назад

      Inu dziko sapangira mademo kuti utenge ai

    • @EstherDebwe
      @EstherDebwe 20 дней назад

      ​@@MahometAli-e8weti eti

  • @SAMARTEDWART-b1j
    @SAMARTEDWART-b1j 20 дней назад +8

    Inudi ndi 1 and ndikugwilizana nanu♥︎♥︎♥︎♥︎

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 20 дней назад +8

    Mufufuzeni bwino mwana ochedwa bushiri yo , akudziwana bwino ndi chakwela awononga dziko athu amenewo, musakaike bushiri chakwela mai joice banda

  • @Jabu-w8q
    @Jabu-w8q 16 дней назад

    We thank you as malawains who resides in south africa do be fear we hear you day and night we give you powers we thank you very much with the information for the plane. From Jawadu Majidu

  • @TimothyBomba-k7s
    @TimothyBomba-k7s 15 дней назад +1

    This is what Grace Chinga said about it only God knows
    At this time we need more Grace

  • @MatildahSianga
    @MatildahSianga 20 дней назад +5

    The,s no secret on earth , we are Ander the clouds , GoD protect you from these killers,

  • @InnocentGowelo-f9n
    @InnocentGowelo-f9n 20 дней назад +5

    We will meet on judge Ment day am swear for God

  • @user-st6bt5vv9c
    @user-st6bt5vv9c 20 дней назад +7

    Bushiri be aware choonde please choonde please choka mwamtendere ma Malawi 🇲🇼

    • @HappyAnt-uz5je
      @HappyAnt-uz5je 20 дней назад +3

      That's why Peter amamukanatu bushii eshiii Koma osavotera mcp

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 20 дней назад +4

    Lipopo FM number one

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl 20 дней назад +6

    Mumakwana guys ndi maumboni yoooo

  • @WizgskSoko870
    @WizgskSoko870 6 дней назад

    The world belongs to the most high nothing is hidden the bible talked about this already 😢😢😢

  • @user-ww4ei5fb7d
    @user-ww4ei5fb7d 19 дней назад +2

    God should protect our country Malawi

  • @COUVILLA11
    @COUVILLA11 20 дней назад +3

    Comrade Ntanyiwa with Lipompo fm 🎉

  • @ChikuMega
    @ChikuMega 20 дней назад +4

    God never fails

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl 20 дней назад +4

    Bushiri mutumizgani kuno wazakhare mundende chakwera tangomuyikani mu bini musekepo kwambiri

  • @ChristopherMakamo-ky4pq
    @ChristopherMakamo-ky4pq 20 дней назад +2

    Thanks my brother ntanyiwa ❤❤❤❤❤❤❤

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko 20 дней назад +4

    Koma mr ntanyiwa mulungu apiririze kukusungirani moyo wautali kuti mupitilize kutisegura maso😮😮

  • @EvanceRazaki
    @EvanceRazaki 20 дней назад +4

    Km Pete muthalika amamukana kulowa kumalaw

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 20 дней назад +5

    MANGANYA ALI BUSY KUDYA CHAKULAMBA 😂😂😂😂 MISALA YENI YENI NDITHU

  • @EuniseMasuku
    @EuniseMasuku 15 дней назад +1

    Eti eti Ngozi paliponse bushiri ndi wausiru eshii bodza Ngozi zikuonjeza

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 20 дней назад +2

    zoona zake. Mukunena zi athanyiwa Ambuye atithandize ndithu Ambuye azikudalisani inuyo athanyiwa

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope 20 дней назад +4

    Bushiri ndi Joyce banda samala

  • @AuphieBannet
    @AuphieBannet 20 дней назад +2

    Pambuyo panu AComrade 🙏

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 20 дней назад +2

    Pa dziko lapansi palibe chinsisi Mulungu kubvumbulutsa kumeneku

  • @WillmotChiuimia-vr6ou
    @WillmotChiuimia-vr6ou 17 дней назад +1

    Mmmm ndiye wapenga misala tu chakwerayu ndi zake wakudya mma restruant 😂😂😂😂😂😂

  • @EmmanuelMkata
    @EmmanuelMkata 20 дней назад +1

    Kumalawiko ndizabwera boma liri panoli likazachoka....

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 20 дней назад +3

    🔥🔥aululeni

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j 20 дней назад +3

    Mchifukwa chake mmayi uja anaphedwa Grace chinga esh akanaulula zambiri mu nyimbo muja esh

    • @MahometAli-e8w
      @MahometAli-e8w 20 дней назад

      Ambuye tagwada maondo pansi tiunikileni nyali yanu ikhale yowala kwa ife ana anu

  • @JasperKaleni-dx6nn
    @JasperKaleni-dx6nn 18 дней назад +1

    Same like bakili tv 📺 kuthoka ngamo

  • @GladysndilimbiraBonongwe-g6c
    @GladysndilimbiraBonongwe-g6c 20 дней назад +4

    Choyankhula chandisowa mmmm

    • @HappyAnt-uz5je
      @HappyAnt-uz5je 20 дней назад +2

      Ambuye atithandize tiyeni tipephere😢😢😢

  • @adilyseif2409
    @adilyseif2409 12 дней назад

    Mulungu ndiy aziwa bas

  • @SammieDickson-ln2hp
    @SammieDickson-ln2hp 20 дней назад +2

    There is no secret under the sun

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 20 дней назад +8

    GUYS BUSHIRI ABWELELE KOMWE ANALI KU SOUTH AFRICA PLEASE

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 20 дней назад +3

    Zoonadi mr ntanyiwa Zoonadi zimene mukunena

  • @KingDavedNkhata
    @KingDavedNkhata 6 дней назад

    A Malawi tili ngati mbuzi sitimamva ndipo timakhulupilira titavulala
    Onena analipo ndipo si munthu mmodzi
    Olo former president Dr Bakili Muluzi ankanena msonkhano wina ulionse kulikonse kuti a Malawi olo patavuta bwanji musazavotere chipani cha MCP mudzalodzedwa chokupha, cha nkhanza komanso cha sankho ndikumakumbusatso zintchito zake kumatchula onse anaphedwa mwa nkhanza
    Koma ata lero si izi zidathera mu nsinje wa tinkanena kusamva iiiii ayi ndithu

  • @HEROTHATNOBODYCANCELEBRATE
    @HEROTHATNOBODYCANCELEBRATE 20 дней назад +2

    To honest this guy say one truth kwinaku amakhala maboza chifukwa kwinaku amongopembembeza anthu open your eyes malawians kwina imakhala camghpain be mindful

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 20 дней назад

    Let's pray hard for our country again bad evil spirit

  • @finessechikaphonya2445
    @finessechikaphonya2445 17 дней назад

    Mr Ntanyiwa please pray hard ndi nkhondotu iyiyi..please

  • @JoyceBanda-k8t
    @JoyceBanda-k8t 16 дней назад

    Boma likangosintha 2025 bushili athamangitsidwe chakwera aphedwe chimwendo Banda mundende moyo wache onse mozes kumkuyu zikhale ngoma mdi ambiri amcp onse mundemde zanyanya

  • @DanielJuwawo
    @DanielJuwawo 20 дней назад +4

    Ndichifukwa chake Peter amamukana

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali 20 дней назад +2

    💔💔💔💔💔 chonena ndilibe ine

  • @LekkttarKhembo-or1tx
    @LekkttarKhembo-or1tx 20 дней назад +1

    Enanso kuno azimai akumalawi aku joina satanic kuno Ku Johannesburg azimai opusa ngati chakwera

  • @user-rt3nx4dx1t
    @user-rt3nx4dx1t 14 дней назад

    Bushiri u should be careful don't just think that God he is not watching u

  • @lyiemax
    @lyiemax 15 дней назад

    Satanism is really very high in this country, sizikukhala bwino

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 20 дней назад +3

    Mcp manyaka enieni basi bagamoyo

  • @harrisphambana4299
    @harrisphambana4299 15 дней назад

    Nanga ku SA kwachitika zingati ngozi , wa satanic ndi iweyo ntanyiwa

  • @JoyceLiwonde
    @JoyceLiwonde 20 дней назад

    Jesus name is the only way ❤❤

  • @AlickJota
    @AlickJota 13 дней назад

    Zovuta kwambiri koma Allah atiteteza ndithu

  • @DevisonHala
    @DevisonHala 20 дней назад +2

    Muwawuze zoona machende alinawo achakwera ,bushiri ndi mayi joice banda naye nyini yochotsera mwana alinayo asawononge m'mtundu wa anthu anyani amenewa fiti achoke m'malawi muno.

  • @EvanceRazaki
    @EvanceRazaki 20 дней назад +3

    Mbuzi zathu

  • @CorneliusSande
    @CorneliusSande 19 дней назад

    Number one nice man

  • @FarookLimula-v6r
    @FarookLimula-v6r 12 дней назад

    Tingolimba ndikupephela amaliwi tigonjese mizimu yoipayi

  • @user-hs4bm2yj8r
    @user-hs4bm2yj8r 17 дней назад

    Chakwera ndiye gwero la mavuto onsewa chifukwa pomuthawisa bushiri anali akudziwa chimene chingachitike,now abwerere bushiri adzamalize milandu yake ndipo chakwera atule pansi udindo

  • @JohnWame-u3l
    @JohnWame-u3l 16 дней назад

    Malawi ndi Munda WA azungu otiakafuna magazi,or chinachilichosechimene Iwo akufuna amadzipeza kumalawi,chifukwa audindo athu ndiowewo achitaizi

  • @julietmussa5103
    @julietmussa5103 20 дней назад +2

    Koma guys mmmmmmmm

  • @AgnessNdhlovu-xj3gn
    @AgnessNdhlovu-xj3gn 15 дней назад

    Mlungu atithandize atitumile mzimu oyera utifungatile ayikumbukile

  • @whatsonbanda4277
    @whatsonbanda4277 16 дней назад

    Cipani cinawina 2019 ndi DPP

  • @AnthonyChirwa-t4g
    @AnthonyChirwa-t4g 20 дней назад +1

    ndizona zake atanyiwa athuwa ndiwoipa kwambili chakwela ndichikangawadi

  • @PatriciaMbewe-xn7ke
    @PatriciaMbewe-xn7ke 20 дней назад

    Eeeee Limpopo ndi one ndipo anayankhuladi grace asanamwalire koma lero si iziii zikulumikizana kwathunthu

  • @SueWahna
    @SueWahna 20 дней назад +1

    😂😂😂 angokwera njinga ampanga withdraw kaganizidwe 😅

  • @GodfreySoko-c3l
    @GodfreySoko-c3l 20 дней назад +2

    mercy Lord🤦🤦

  • @PeterSuwack
    @PeterSuwack 17 дней назад

    Mbambande big man ❤❤❤❤❤

  • @OdettaLowrence
    @OdettaLowrence 14 дней назад

    Ndimanena kut bushili nzakudya akugawazi nzitha athu mwaona izi, achikangawa mukutitha plz, tisiyeni

  • @CathreenKadwala
    @CathreenKadwala 19 дней назад

    ANtanyiwa Ambuye azikupasani moyo wautali, mupitilize kutitsekula maso

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 20 дней назад +1

    Atimaliza agaluwa Achoke bas

  • @MatthewLameck
    @MatthewLameck 20 дней назад

    Pa dziko lapansi palibe chisisi ndakhulupilira ndithu koma zonse zizatha ambuye ndiwavhifundo khani ndiyoti tilimbike kupephela ambuye azatiyakha tisalimbane ndi kumenyana

  • @EmilyBanjachikwatula
    @EmilyBanjachikwatula 20 дней назад +1

    Lero madzulo omwe ano pa standard bank ku limbe

  • @MwaleMussa
    @MwaleMussa 17 дней назад

    Satanic wakula eeee ayi🙌🙌🙌 chabwino mwawina ndinu

  • @GiftManuel-er7yh
    @GiftManuel-er7yh 20 дней назад

    Ambuye MULUNGU atichosele chonyasachi

  • @LaynaAdam
    @LaynaAdam 20 дней назад

    Osamapeleka ana awo bwanji

  • @Failoss
    @Failoss 20 дней назад

    Tithatu kuno ku Malawi amwene 😱 chifukwa tinayamba ndi namondwe Zina ndi izi anthu angofa ngozi zimene zikuchitikazi haaaa😫😭😫😭😭😿

  • @BrinoMvula
    @BrinoMvula 17 дней назад

    Koma sakusaka iweyo mtanyiwa😂

  • @user-bn8hh2wb5b
    @user-bn8hh2wb5b 20 дней назад

    Bwana mthanyiwa nkhanga zaona limpompo fm mukunena zoona zinazi zikudabwisa kwambili komanso usogoleri omwe ulipo ukulekelera bushir kuti azitipha ife ngakhale mphepo yomwe inachitika kumalawi yamvula sizinachitikepo komanso amalawi tiyeni tisiye kulandila zinthu za ulele zochokela kwa mtumuki ameneyu atimaliza

  • @BigBangalala
    @BigBangalala 20 дней назад

    Ntanyiwa ntapangani zonteka bushili abwelele ku South Africa 🇿🇦 kuno

  • @JamesonPhiri-j7i
    @JamesonPhiri-j7i 20 дней назад +1

    So sad !!!

  • @user-sz6bi3tw5y
    @user-sz6bi3tw5y 18 дней назад

    Azitsogoleri anthu ali paubale ndi akumidima tiyeni tilimbikire kupemphara mu dzina la yesu kuti mulungu atichotsere anthu oipa ku parliament pachisankho chikubwerachi.

  • @davidsnkhomah2688
    @davidsnkhomah2688 14 дней назад

    Problem ndi DPP nkhani ya satanic akufuna ndalama zochitila campaign

  • @SandfordBanda-gk2dp
    @SandfordBanda-gk2dp 20 дней назад

    Zitukuko za Ku Lilongwe ndi dowa ndie ndziko lonse mwatha basi

  • @TUMISANGBOSILONG
    @TUMISANGBOSILONG 17 дней назад

    Asilamu inu tangokhalani chete this is not a time for Muhamadi its a time for jesus.

    • @kilt_la-flame265
      @kilt_la-flame265 17 дней назад

      😂😂😂😂 koma adah

    • @kimukamawe1591
      @kimukamawe1591 17 дней назад

      Amenewo ndiye manyi kod mmaonangati asilamu amapanganawo zamanyizo. Kungokula ndi umbuli basi muziona simunati Mesa inunso mulimommo zaumbulizanuzo ife ayi.

  • @petercheeseboymokoena8659
    @petercheeseboymokoena8659 17 дней назад

    Okupha alubino linali boma la DPP musaname inu

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q 19 дней назад

    Ok ok nichifukwa chake bushiri anathawa ku joni ndekuti kujoni bushiri amapha anthu basi taziwa kuti bushiri nisataniki ni chakwera ose nimasataniki ndipo kwabeba kumalawi ni usataniki mwava

  • @Eneth-w6l
    @Eneth-w6l 18 дней назад

    Mtanyiwa iponyera kwakuya, ng'alulani basi, Ambuye azikudalitsani kale kunalibe izi sitimadziwa zomwe zinsinsi zina zadziko muno panopa nthawi yatha satana ayaluke basi

  • @petercheeseboymokoena8659
    @petercheeseboymokoena8659 17 дней назад

    Makape a DPP mwayambapo kupanga ma fake report video imeneyi tipanga report sipezekanso apa for the next few hours

  • @fridaygonela
    @fridaygonela 11 дней назад

    Santhe ndi kasungu osati mchinji

  • @AustinMhone-r3s
    @AustinMhone-r3s 17 дней назад

    Ndare za panyasaland chilichose chalowa ndare sorry!

  • @DanielJuwawo
    @DanielJuwawo 20 дней назад +2

    Stanic iyi

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i 17 дней назад

    Yemweyo Chikangawa zakumidima zizaururika

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson 17 дней назад

    Tsoka ntunda ndi nyanja pakuti oyipa watsikila ku malawi 👿👿👿

  • @RyleChole
    @RyleChole 17 дней назад

    Ine ndi mboni ya zimenezi kuti nzoona chifukwa anadzandichita attack koma analephera ,nzambiri zomwe ndinganene, komanso ndichenjeze Inu a Mtanyiwa khalani mukudziwa chomwe mukudziwa

  • @EmilyBanda-xx8gd
    @EmilyBanda-xx8gd 20 дней назад

    Pa mtengo wanthenganso bus ya captain yagwa costor nso pompo zomvetsa chisoni kwambiri

  • @harrisphambana4299
    @harrisphambana4299 15 дней назад

    Dziko la umphawi basi nkhani zake zopusa basi kosowa zochita

  • @Shelifibraheem
    @Shelifibraheem 20 дней назад

    Kulichapwa Mr mtanyiwa kkkkkkkkk

  • @AnnieBanda-rb2dk
    @AnnieBanda-rb2dk 19 дней назад

    Iweyo iweyo mr chikangawa chakwera

    • @AnnieBanda-rb2dk
      @AnnieBanda-rb2dk 19 дней назад

      AGALU AMENEWO amaonjeza ndipo amandibowa basi chilichose mupaka ayikepo umbuli zazii, popeza anatiphera chilima ifeyo nde akuzitenga kut ndiophuzira iya akhalike agalu amenewo achina mr chikangawa chakwera fiti za anthu

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6no 17 дней назад

    Kkkk kuvina uli maliseche, koma ndalama

  • @MoosaSame
    @MoosaSame 20 дней назад

    Thanks big man we proud of you ❤❤❤❤❤❤❤.

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 20 дней назад +2

    Bushiri ndi munthu oyipa kwambiri satana ndithu

    • @jennyx6914
      @jennyx6914 20 дней назад

      bolani ali ndi ndalama amathandizanso amalawi omweo nanga iwe ndi ine

    • @WorriedNdhlovu
      @WorriedNdhlovu 20 дней назад

      ​@@jennyx6914 inuso kwanu mukuenela mumatamba

    • @WorriedNdhlovu
      @WorriedNdhlovu 20 дней назад

      ​@@jennyx6914kudalila zolandila zamagaz

    • @berlz12k
      @berlz12k 13 дней назад

      Ndipo sukunama oterewa amakhala anazama muufiti cos munthu wa normal sungamabakile zopusazi boss!.mxiew

  • @ChinsinsiChinsinsi
    @ChinsinsiChinsinsi 17 дней назад

    masiku otsiliza