Asilikali akuulula momwe anamuphera Chilima

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 24 июн 2024

Комментарии • 292

  • @user-bd5kw8oq1r
    @user-bd5kw8oq1r 23 дня назад +13

    Asilikaliwo amene akufalitsa bodzawo ndi a bodza ngati enanu bwanji sakupita ku court kukanena umboni wawo anthu mwazolowera ku pachika mayina a anthu apa cholinga wina ayipe inu mukome mukolola zomwezo bwanji osatchulako makolo anu mukunena anthu ena muferatu momwemo mu bodzamo ndiye pali phindu lanji zikuwoneka kuti ena 8 aja si anthu koma chilima basi kudafatu anthu enieni kunja kuno alikuti kili ziiii amapita kumanda nanga inu ndi ine mudzapita kuti kwa anthu andale kapena kumanda kumaganiza 😅😅😅😅😅 awa

    • @user-qb4pj5yy5b
      @user-qb4pj5yy5b 20 дней назад +4

      Apite ku khoti for what? Timapereka umboni popanda mulandu? Ku khothi siku polisi tu tizidziwa zimenezo! Pakuyenera pakhale mulandu ndiye iyeyo nkukakhala mboni

    • @user-bd5kw8oq1r
      @user-bd5kw8oq1r 20 дней назад

      @@user-qb4pj5yy5b ndiye siyani kulankhula zopanda umboni akutumani a ndale eti mukhalila yomweyio munthu anafa basi mwatsala inu ndi ine dzimvereni chisoni nanga bwanji asakatsegula mulanduwo mukungubwebweta pasi ngozi ya ndege mumayidziwa inu paja mkuyamba ku Malawi kuno eti ndiye ngoziyi yangokumaba ndi mbuli zomwe

    • @GrecianahmedMaulana
      @GrecianahmedMaulana 13 дней назад +1

      ndipo apite akamange palibe zoti akunama ndizoona zinachitikadi

  • @EnelessLundu-sn8om
    @EnelessLundu-sn8om 23 дня назад +8

    Uyu akuyenera kutengedwa ndi akubanja akalongosole bwino ...chifukwa ali nawo mu gulu lakupha

  • @user-xx4mt8ox8e
    @user-xx4mt8ox8e 23 дня назад +7

    Tell us where is blackbox?

  • @StellaKChicana
    @StellaKChicana 9 дней назад +1

    Mulungu amakanda munthu onena chilungamo iwe msilikali mulungu akukhululukile pazimenezi koma tikuthokoza ponena chilungamo usasiye pitabe chitsogolo oipa aoneke pa mbalambanda 😂😂😂😂😂

  • @kumbukaningambi4943
    @kumbukaningambi4943 13 дней назад +1

    Only JAH knows....everyone shall get paid according to works he has done🔥

  • @WycliffNkunika
    @WycliffNkunika 24 дня назад +5

    Limenelo ndi bodza lochita kupeka. Iweyo bewanji upite ku Police nkukaperekela umboni umenewo. Chimene ukuopa nchani? Wasowa chonena!

    • @paulinekayuni1621
      @paulinekayuni1621 22 дня назад +1

      Olo zimakhala zoona sangamusiyesiye atanena komano ndioipa yekha atinanalandira ndalama

  • @JosephKavalo-yx6xb
    @JosephKavalo-yx6xb 23 дня назад +6

    Uchitsilu mukananena anthu asanafe ndinu m'Modzi mwakuphawo

  • @GulliverTower
    @GulliverTower 22 дня назад +2

    Stop taking weed +Ambuye ntengeni Bro

  • @user-if3pe9mp4l
    @user-if3pe9mp4l 24 дня назад +8

    Udye ndalamayo usaope usachite matha nyani iwe unatani kuulura zisanachitike mwana wanjoka iwe

  • @DavidNundwe-k8r
    @DavidNundwe-k8r 11 дней назад

    Thanks for providing us you service

  • @DanielChipasula
    @DanielChipasula 13 дней назад +1

    MUZIDZIWA MULUNGU.. ZITICHEDWERSA IZO. MUBWERETSE UMBONI MWACHANGU... TIMVE # YANUYO. YA ZOMBA. PRAISE GOD

  • @racheallungu3939
    @racheallungu3939 23 дня назад +8

    Ndaika muzimu wa malemu Chilima manja wa Mai maria. Proud katorika / Lusaka Zambia

  • @MervisChiputula
    @MervisChiputula 23 дня назад +10

    Eshiiii mulungu amakondwera ndi munthu ovomera tchimo lake inutu mwayamba bwino ingomalizani Kuti anthu tidziwe chowonadi

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 25 дней назад +6

    Example kenya , anthu aku kenya anasiya kupembeza boma lakuba ,
    Ife amalaw wachuluka ndi umbuli .

  • @GodfreySibale-ry9ig
    @GodfreySibale-ry9ig 12 дней назад +1

    10 mita kupha munthu za Bodza ngat izi 😂😂

  • @user-dq8iq9bk7i
    @user-dq8iq9bk7i 22 дня назад +2

    Zopanda ntchito tonse timaziwa kuti tidzafa koma sitikuziwa mmene tingazafere

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 23 дня назад +3

    Tathokodza potiudza koma usanapite machende ako bwanji unalolera kuti chilima afe chotelo iwe pokhala nsilikari nyini yamako and u chakwera nyini yamako😢😢😢😢 RIP Chilima

  • @user-rg4du4vu9r
    @user-rg4du4vu9r 26 дней назад +5

    Zaboza ngat nkazi wako ndiwopemphera uma chitiranji zimenezo

  • @gwatandingo9502
    @gwatandingo9502 18 дней назад +1

    Koma munalakwa kwambili munapha muthu ofunika kusiya zitsilu komaso ndale zophana zinatha kale kale kupusa kumeneko adzakuvoteleni ndi Amanu😢😢

  • @WitnessPhiri-zr9uf
    @WitnessPhiri-zr9uf 24 дня назад +2

    Kabwezeni ndalama zo pemphelani pemphero lolapa lonsweka tima mulungu akukhululukirani mupite poyela kukabweza ndalamazo 😂😂😂😂😂

  • @humphreykalolo976
    @humphreykalolo976 10 дней назад +1

    Malankhulidwe anu zikuonetsa kuti ngakhale 8 simunafike, mumagwira ngati ndani ku airport?

  • @MackzainWhite-rj9tx
    @MackzainWhite-rj9tx 21 день назад +2

    Ndiwe chitsilu kwabas bwanji sukwatchula anzakowo nanga

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 23 дня назад

    Simunati mutuluka mizimu ya anthu amene Aja ikudzuzani zedi ndipo muulurana wat is 10 million after all ndalama malo moyendesera dziko mukupangira uchigawenga inu agalu kwambiri.

  • @ChiccoMabvuka
    @ChiccoMabvuka 23 дня назад +2

    Zikundimvekela ngati zaboza mukufuna kungotipusisapo

  • @DANIELMAGANGA-j7z
    @DANIELMAGANGA-j7z 23 дня назад +1

    mukusowa zochita mmene mumvekeramu mungakhale ten million kulira ndi umphawi

  • @Certified-Mbudede04
    @Certified-Mbudede04 20 дней назад +2

    Ngati mukufuna kutchuka muneneee

  • @BESTERMAYESO-r4v
    @BESTERMAYESO-r4v 12 дней назад +1

    iweyotu ukunama ndipo palibepo chikumveka panfundo zakozo usanamize ndipo usasokoneze anthu ndi bodza lakolo

  • @robertkalima874
    @robertkalima874 23 дня назад +2

    Akulu zopanda nzeru izi.

  • @SlyviaPhiri-bd9uu
    @SlyviaPhiri-bd9uu 24 дня назад

    Koma zovesa chisoni kwambiri kumpha anthu wosalakwa chifukwa chandalama Koma ndi zoonadi Kuti pamene pamphedwa munthu osalakwa mulungu amaulula zitsitsi. Zobisika 🙆🙆🙆🙆💔💔💔😭😭😭😭

  • @MuhammadKazembe-ot8sc
    @MuhammadKazembe-ot8sc 24 дня назад +2

    Alakhulayo panyepake

  • @user-iq5xk6ju7y
    @user-iq5xk6ju7y 24 дня назад +12

    Pitani ku TIMES TV on live interview ndi Brian Banda amwene

  • @LouisAndrew-jr1yj
    @LouisAndrew-jr1yj 26 дней назад +3

    We wish you well🙏

  • @user-lg1mc2ze2g
    @user-lg1mc2ze2g 24 дня назад +2

    Waboza kulankhula ngati wakurundi bwerani poyera kuti mumangidwe munthu oyipa iwe kumakapanga chiwembu

  • @SamuelMthengo
    @SamuelMthengo 24 дня назад +2

    Ngati ukufuna kukhululukilidwa,bwerani poyera.

  • @Owenmalunga-jo4iq
    @Owenmalunga-jo4iq 11 дней назад

    Vuto Kodi president ngati sakupanga zabwino osapanga Kuti achoke bwanji pa mpando

  • @christophergibson72
    @christophergibson72 22 дня назад +2

    Looking for 1M viewers

  • @GRACIOUSCHIDZANJA
    @GRACIOUSCHIDZANJA 19 дней назад +2

    Wow

  • @EversonGeorge
    @EversonGeorge 22 дня назад +1

    Chomwe mukuopa kut umbon ngat umenewu kukapereka poyera mukuopa andare coz aliyese Ali ndi mantha

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 23 дня назад

    😂😂😂 mulungu awakathe ndithu

  • @mussahalfraid6395
    @mussahalfraid6395 24 дня назад

    Kkkkk eeiiiiish koma yaaah. Zabodza izi akukamba uyuyuzi.

  • @user-hx6jl2jq9j
    @user-hx6jl2jq9j 26 дней назад +1

    Explain everything

  • @MeseMamba
    @MeseMamba 23 дня назад

    Keep it up

  • @JemimaNyirenda
    @JemimaNyirenda 22 дня назад +1

    Why is the government busy ku anga a Kaluw kusiya athu ngati a wawa why

  • @highcallingglobalministries
    @highcallingglobalministries 24 дня назад +1

    AM PASTOR CHRIS PLEASE BROTHER GIVE THEM BACK THEIR MONEY,

  • @user-et1tl1qs2j
    @user-et1tl1qs2j 18 дней назад +1

    Mulungu salephela tidziwa zonse pompano mu ukulu wake alibe othandizana naye

  • @GiftPhiri-f7i
    @GiftPhiri-f7i 23 дня назад

    God is great and the justice will be to an open❤

  • @chrissyamanda5510
    @chrissyamanda5510 9 дней назад +1

    Kupusa kwako galu iwe mxiiiii😢

  • @augustMag
    @augustMag 22 дня назад

    Mulungu wanthu sazagona tulo mpaka mwazi wa anthu omwe anafa pa ndegeyi utaonesa Chilungamo Romand Catholic Les prayers so hard mpaka Mulungu atationesa choona

  • @ChrisMroma
    @ChrisMroma 24 дня назад

    Ambuye akutezereni achimwene ,azikumangirani linga tsiku ndi tsiku

  • @JemimaNyirenda
    @JemimaNyirenda 22 дня назад +1

    Nde iweso uli mugulu lokuphalo

  • @user-ik5sz8hc6f
    @user-ik5sz8hc6f 11 дней назад +1

    Youuu!

  • @LindaMoffat
    @LindaMoffat 24 дня назад

    Nde osangozitchula dzina ngat mukunena zoona bwanj. Ndege yoti inaphulitsidwa ingawoneke chonchija? Komaso ndege yoti inatela inganyenyeka chonchija? Campaign yabwanj kod tiyiwone chaka chinoyi mwati

  • @JoshuaNyirongo
    @JoshuaNyirongo 26 дней назад

    Azikatenga iwe ku zomba all the way upto Chikangawa.....Pezani boza lina sir.

    • @mcsellahntv6896
      @mcsellahntv6896 24 дня назад

      Anatenga bwanji ma pilot a ku zomba nanga ?? Kumenwko kuyesela kuti muphuphe basi.

  • @LawrenceGolosi
    @LawrenceGolosi 23 дня назад

    1. Utchule dzina lakoo osati komwe uli.... Chifukwa komwe ulikoo ndikoti akafika sampeza munthu koma dzina lo akhoza kulipeza mosavutaaa
    2. Bweraani poyela bwino bwino kuti anthu ayitsate nkhani yi mwatsatanetsatane....
    3. Osamabwera ndi nkhani zabhoza apa where your facts are not straight!!

  • @SophieBanda-el8ri
    @SophieBanda-el8ri 23 дня назад +1

    Wabodza uyu, palibe chilungamo pamenepi

  • @kingsleyhopematchaya5184
    @kingsleyhopematchaya5184 7 дней назад

    Sunanene dzina lako bwanji kodi maliro mukuona ngati chithu choseweretsa kod atakhala bambo ako ungakambe zopusa kumanama ngati ukudziwa kathu uli jufuna kusikoneza athu iwe ngati unapha ndiwe osapita ku police kukadzipereka uzilakhula zophwisa apa malilo mukuyesa zoseweretsa kod

  • @ThokozaniJenala
    @ThokozaniJenala 10 дней назад

    Ambuye akuyendere mwapaderadera kuti unene zoona zokhazokha.

  • @DevisonHala
    @DevisonHala 11 дней назад

    Mudatani kumuthawitsa osamupha inu asilikali zovetsa chisoni😂😂😂😂

  • @augustMag
    @augustMag 20 дней назад

    Ambuye landilani mizimu ya abalewa amene mwawayitana kubwera Kwa Inu chitilani chifundo midzimu Yao pamozi ndi vice president Chilima Mulungu wamphamvuzonse landilani mizimu

  • @DanielLio-c6n
    @DanielLio-c6n 23 дня назад +1

    10million mungagule moyo wa munthu mulungu akukanthen nonse asasiyeko or modzi

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj 23 дня назад +2

    Tiutseni soona sandege live in the sauth Africa estan 😢😢

    • @esaMoha-dm4kj
      @esaMoha-dm4kj 16 дней назад

      Thank you so much for replying me your welcome

    • @esaMoha-dm4kj
      @esaMoha-dm4kj 16 дней назад

      Tell me all story from you soon side please I am Malawian

  • @user-gd6zb2bv8f
    @user-gd6zb2bv8f 24 дня назад

    Koma Razalo Chakwalayo samachita manyazi konse akamaona ndi kumva zimenezi,
    komatu mzimu wa munthu ndi oopsya, lero zili bwino koma mawa kaya

  • @TitusGoba
    @TitusGoba 15 дней назад +1

    Ndikuzimva mwabodza

  • @JackLuhana
    @JackLuhana 22 дня назад +1

    Inusotu ndinu abodza Inu, msilikali wake wakuti? Dzitchuleni dzina ndi unit yanu, msilikali ophunzitsidwa bwino angapange zimenezo ukukamba mlayiya iwe, umawudziwa uskali iwe?

  • @WysonJalamu
    @WysonJalamu 24 дня назад +3

    Boza ili, paja nvula ikagwa kuchuluka zoliralira, nanga ndege inachita kutela kapena kuphulisidwa? Mesa inagwa kusowa choyakhura eti amalawi tili ndi khwiyo pa ifa ya anthu amene aja ndiye osamatiuza boza ngati limeneri.

    • @mishecksipolo7153
      @mishecksipolo7153 24 дня назад

      Zowona ndiye ndiziti malume?

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r 24 дня назад

      ​@mishecksipolo71 mukavele yomwe watumiza lero mukhulupilila kuti ndiwaboza apa anati ndimusilikali anali kuchikangawa lero akuti anajambula dege ndiyeyo ku airport amalawi tiyeni tiseguke chonde anthu azikusewelesani chochi koma ambuye amukhululukile sakuziwa chomwe akupanga

  • @gregben7657
    @gregben7657 17 дней назад

    MA CADET MULI PA CHINTCHITO CHA SATANA MDYEREKEZI KWAMBIRI KOMA DPP CAN'T WIN BECAUSE OF PLANET CRASH OF VP.
    WE ARE STILL RECALL WHAT EVIL WORKS DPP HAS DONE TO INNOCENT BLOOD OF ALBINISM.
    GOVERNMENT VEHICLES WERE MISUSED TO AS POLITICAL PROPERTIES TO KILL THE OPPONENTS.
    SHAME ON YOU CADETS.

  • @DanKachikoti
    @DanKachikoti 25 дней назад

    Koma2 anthu inu mwasowa cholakhula 10 million ndi ndalama? 😂😂😂

  • @ShelaMsachi
    @ShelaMsachi 23 дня назад

    Once a snack always a snack. Sitinaiwale chipani ichi.

  • @Noelbanda-j1l
    @Noelbanda-j1l 23 дня назад +1

    Wa Dpp iwe

  • @user-dh1oi8mb4v
    @user-dh1oi8mb4v 21 день назад +1

    Rest in peace SKC

  • @Enjelinatembo-h9m
    @Enjelinatembo-h9m 22 дня назад

    Ukalapa mulungu amakukhululukila zoyipa zako bola ukayima muchowonadi ndipo mulungu amakhala kumbali yako mulungu ndiwazatheka bwanji pitilizani kuwulula kt satana achite manyazi

  • @ChifundoChicco
    @ChifundoChicco 26 дней назад

    Eish aaa

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti 24 дня назад +2

    Following 🙏

  • @AaronJaccob-us7xn
    @AaronJaccob-us7xn 3 дня назад

    Inu muli ndbodza Inu iwey sindwe msilikali ayi wangodzeramo ukufuna kungoypitsa munthu bas nde cholinga chako ife tikudzwa kut nd ngoz and ikanakhala fut anthu akanava kut akuombera nde pita nazo uko zamkutu zakozo usatiwawitse mutu apa

  • @anoldkapolo4493
    @anoldkapolo4493 20 дней назад

    Galu wachabe chabe uyu iwe umakatani kuchikangawa kuchoka ku Zomba? Bwanji osanena nthawi yomwe ija anthu tikusowa Mtengo ogwira? Ukamanama chonchi ukupempha tsoka kwa mulungu

  • @user-wk2is9bz8o
    @user-wk2is9bz8o 22 дня назад

    God is great

  • @franklinnyirenda8126
    @franklinnyirenda8126 22 дня назад

    Aaa 10 mita kandalama kochepachepa, kupha president kumafunika ma 50 mita

  • @wisemanmhango-t7o
    @wisemanmhango-t7o 24 дня назад

    😮

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 5 дней назад

    Munalakwisa kupha ose komanso ndiwe chisilu

  • @FiskaniTonymahone-vl3og
    @FiskaniTonymahone-vl3og 20 дней назад

    Anthu adyera awa oyiwara mwachangu,nawonso adzafa..

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j 23 дня назад +1

    Zomvesa chisoni kwambiri mmm

  • @rahimmard6617
    @rahimmard6617 24 дня назад

    Mmene umalandira umaona ngati mukukapha ziwala? Lero udziti ukulephera kudya ndalama 😢

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 12 дней назад

    NDIWE MUNTHU OPANDA CHIKONDI BWANJI SUNADZIWITSE NTHAWI YOMWEYO KUTI ANTHU APULUMUTSE MIYOYO YA ANTHU? KOMANSO IWEYO ULI NDI UMBONI OKWANIRA BWANJI OSAYITANA MABANJA OFEDWA NDIKUWAUZAKUTI TIYENI KU COURT NDIRI NDI UMBONI? MUNAPHANAWO CHIRIMA NDI ANZAKE,BAMBO MLANDU MULINAWO

  • @AndwatchMambo-gn5bs
    @AndwatchMambo-gn5bs 7 дней назад

    Mbuli yimeneyi yikupusitsa ndani APA.

  • @PicardolewisBismarck
    @PicardolewisBismarck 13 дней назад

    Anapha munthu ofunika kwambili,,ndipo the truth will come out soon

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani 20 дней назад

    Chikhala ndiwe oyima pa chilungamodi ukanadzutchula dzina

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz 22 дня назад +1

    Mmmmmm kaya God knows ife kunalibeko

  • @preciouskhombedza4456
    @preciouskhombedza4456 18 дней назад

    Bwanji wangotchula kuti ukupezekera ku zomba Barack while ku zomba kuli air wing kuli cobbe kulinso changalume and rank number Yako sunatiuze and why sunanene early because iweyo izizi ndekuti unazidziwa zisanachitike nde utha kuwauza anthu za Zina zimenene zikufuna zitadziwidwa kuti zili pati and zinaenda bwanji anatenga ndi ndani mafuso ngati amenewa utha kuyankha?

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y 23 дня назад

    Chakwera munthu wakupha uyo izi zayenera kuyamba ndinu bomwe asilikali.Mukusekelera zinthu zopusa kupha anthu amtundu wanu womwe mkwiyo wa Mulungu ukukanthani ndithu,Muuzane inuyo asilikali muyambe kukantha Lazaroyo ndi akubanja ake onse

  • @airtelteamleader
    @airtelteamleader 24 дня назад

    Atakumangani madzinvetsa chisoni Aaaaaa opusa iwe

  • @OdettaLowrence
    @OdettaLowrence 23 дня назад

    Nawe camba chakukwana, tinzakhulupilira ukapita ku khoti kukasuma mlandu wakupha, udye ndalama yo, ukananena time yomwe amakokedwayo😂 ndie kut iweso akanakupha, ndie ndipamene tikananziwa kut wafa bwanji pomwe ndege munakwela athu 9, iweo kukhala WA ten, zaziiiii

  • @andrewkalima
    @andrewkalima 22 дня назад

    Inu uyu ndi ndiwaboza mukumva akuti analandila ma 10 mita ndie ngati analandila avutikiranji kunena kuti amusake,koma munthu uyu ndiomvesa chisoni ndipo ndi kapunthabuye alibe chomwe akuziwa even malongosoledwe anta ongooneseratu kuti Ali blank,nkhani zongotolera kuti ena amakamba pena pake sizimasowa.Ukuona ngati akukondwa ndi angati ?ase samala ufera zaweni ngakhale ulibe gawo koma chokhacho chongobwelesa pa social media ukutitaisa time.

  • @LibelioZulu-n2o
    @LibelioZulu-n2o 13 дней назад

    Adanenakare achakwera Kuti alorela kukhetsa mwaz

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 26 дней назад +1

    Zoona izi ndithu

  • @DomMsiska
    @DomMsiska 5 дней назад

    Is this real?

  • @AlexHenere-r6l
    @AlexHenere-r6l 7 дней назад

    Audikira kufuza kwabomakaye akakanama bodza abomao ndipamene akapite kukhot

  • @PriscaChapsa
    @PriscaChapsa 8 дней назад

    Kkkk msilikalli opusa wapha nawo

  • @RightiousBright
    @RightiousBright 24 дня назад

    Iweso Sono ndwe wakupha ndye usawoneke ngt dolo ai chfukwa iweyo ngt umafuna kukhala Muthu wabwino ukanaulula pomwe amakupasa ndalamapo osati zithu zachitika kale ndikumaulula kungofuna kumuipisa Muthu bas ulibe umuthu iwe bwera poyera ngt ukukamba zazeru ukubisala bwaj

  • @philemontitusnkhoma7740
    @philemontitusnkhoma7740 26 дней назад

    Asilikali ake ambwiyako amene anakuphumzitsa kuuluka aja..

  • @jonathandaimon7996
    @jonathandaimon7996 12 дней назад

    Koma Chakwera why? Achewa ndithu ndinu oipa ndawonela Chakwera koma mulungu akukantheni tikuona ndithu