The closest thing that ever come to the likes of Winiko, Izeki, Jakobo and Manganya is Kunte. He is genuinely funny and unique. Osati munthu kungoguluka mano basi muli ndi wa Comedy. Ena kungoyankhula broken English Ali ndi comedian. Ena, basi ati chifukwa amayankhula chitumbuka, chi Burundi etc, ali koma comedian 😅
Mwazitengela kwina kunte aaaaasaaa zooona eeee ai😅😅😅😅😅😅😅❤❤❤❤❤❤❤❤❤😂
Aiiiiii kunte ❤🎉🎉🎉😂😢😮😅😊😊😊😅😅😮😮😢😢🎉🎉😂😂❤❤😂😂😂🎉😢😢😮😮😅😊😊😊😮😮😢😢🎉🎉😂❤❤❤😂❤❤❤❤❤❤😂
Welcome back
Koma nde ndaseka eeee mumakwanira big man
Inu anakonza bas😂😂😂🎉🎉❤
Kudya kunte ❤❤❤😂😂😂😂😂😂ai zimenezo
Eeeh man tikalibuseni, mzimbewo nde wandiwawa mix ma watermelon eeeh mnadya kale kkk
Mwabwera... Fridays, Kunte, Yawa, Kunte kumalizila Mark'
Kkkkkkkk😂😂😂 koma ndaseka mpaka kutsitsa mpweyaa
😂😂😂😂 mwabwela mwa finally kkkkkkkkkkk
Umakwana aseee🎉🎉
My favorite actor
The closest thing that ever come to the likes of Winiko, Izeki, Jakobo and Manganya is Kunte. He is genuinely funny and unique. Osati munthu kungoguluka mano basi muli ndi wa Comedy. Ena kungoyankhula broken English Ali ndi comedian. Ena, basi ati chifukwa amayankhula chitumbuka, chi Burundi etc, ali koma comedian 😅
Nyimbo ikhale ya Nyakwawa Matumbi
Mimba mukuwawa ndipambuke pompa 😂😂😂😂
Koma ndaseka eeeeeh nanga mmimba zingakhare bwanji zakudya zimenezi abale?😂😂
Ndangoona mzimbe ndy ndaseka😂
Ati wangondipeza ndikupephera 😅😅
Anthu amtima ogawa ngati inu amasowa paulendo😅😅😅
eti eti!
Madala kunte simusaza ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤aaaaaaiiiii
kunte nzakoyo ali boh he's always serious
😂😂😂😂😂😂 kumadya koma ena akuonjeza
😂😂😂 koma adah awa
Mavembe ngat juice wake kkkkkkk
😂 koma ndye kuyendera kupiliratu mpaka anthu kutsikatu kumusiya yekha
Welcome back Kunte 😂😂😂😂
😂😂😂 koma Kunte aise, kkkkkk
Kunte kudya too much 😂😂😂
😂😂😂😂😂Vuto lonyamupa dimba lonse pailendo ndilimero
Iwe ndi dolo kwabasi
Lero zandisangalatsa kwambili than ya last week ija
Iwe ndi dolo koma you only need a support
Iwe ndi dolo
Koma akulu inu😂😂
He is back....
Km xiliko kkkkk akazatiii heeeeee kunte😅
Wangonyamula dimba lonse
Ayiii zikomo 😂😂😂😂😂
Ati zimamixana mmimbamommu😂😂😂
kunte ndiwe mulomwe?
😂😂😂 kunte iwe nd nkhan zina mmmmm😅😅😅
Eee koma kunte kudya kumenekoooo
Kunte uimile u present kumalawiko ukhoza ku wina ndiwe oganiza bo ziko lathu likhoza kukhala mwana alilenji kkkkk zakudya zama gulu kkk
Mwadza Fada😂😂😂😂😂😂
madala tracks ijayi meachosa?😂😂
Ndipo sipapezeka pabwino kumene kk
Kunte ndiy kudya 😂😂😂
u are crazy
😂😂😂😂😂😂koma adha
Kunte wandipha ine Mwana iwe suzamva iwe eeeeeeeish
sore kkkk
Kkkkkkkkkk koma kunte😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😅😅abwana
Kmeneko ndye kubweraa am'dala😂😂😂
hahahahahaah keep it up kunte. Tnakusowani nonse
Wathu wathu uyu
Nice kunte
Usamasowe bro umatha ase kkkkkkk pa nzimbe pokhapo unawonjeza
This man😅😅
Ahaa kunte
Kunte Dolo kwambiri
Komatu kuyenda ndi atsogoleriwa sungamve njala eti😂😂😂😂😂😂
Kkkkk kudya ngati akutuma
Umakwana😂😂
Km gute suzayheka
👌👌👌
Kkkkkkk kunte anakonza amwene
Kkkkkkkkk koma kunty ndi 1
kkkkkkkk umakwana kkkk😂😂😂
🎯🎯🎯
Kkkkk kunte ndiwe mlomwe Kod?😂
Km ichi 🤣🤣
Katundu
Umakwana 😂😂
Mmmm osamatero
😂😂😂😂😂😂amazing😅😅
Umakwana Kunte...uzitulutsa tulutsa tnakusowa
Kunte is back ❤
Iiiiiiiiiiih Kunte😂😂😂
Great one😂
Aaaaa kunte😂
Koma iweyo udabwera
Kunte ndiotopesa🤣
🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Kunte ndi Juice😂
Salad ameneyu🤣🤣🤣🤣
Kunte comedy ndi one pamalawi pano,koma ada avala golf shirt ya red wo amandiwaza kwambiri ndipo amatha
Kkkkkkkkkkk kma eya
Kkkkkk
😂😂😂😂 km KUNTE
Kkkk umatha kunte
Kunte is the best
Muthu wakulu kwambili sopan
Kkkk 😂😂😂 km
Umatha kunte kkkkk
Kunte ndi deal
Kunte is great
Kunte😂😂😂😂🎉
Iwe ass😀😀😀
Kunte😂😂😂😂😂🤣🤣🤣guys iiii
Osamukhuza Ali pheee ATI gilaundi nuts tu hehehe
Munthu wamkulu 😂
😂😂😂😂
😢😢😢😂😂😂😂