Ngati Ndimawakonda A Chakwera Pofunika Ndidziwauza Chilungamo - Ben Longwe

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 27 янв 2025

Комментарии • 96

  • @oskidooscar7468
    @oskidooscar7468 13 дней назад

    Guy's Ben longwe tiyen tisamutaye nso akubwelamo uku ndikupepesa kwachikulu more fire anibe

  • @oskidooscar7468
    @oskidooscar7468 13 дней назад

    Ndayamba kukukondanso Ben longwe

  • @Maxielyies
    @Maxielyies 14 дней назад +3

    Anatha awa, zaiwe Ben Longwe tinasiya kumvela bcoz tinazindikila ukape wako

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 14 дней назад +1

    Wayiwona Ben Longwe wekha kuti chilungamo kulibe 🔥🔥🔥🔥

  • @greatalfredlaijah4474
    @greatalfredlaijah4474 12 дней назад

    achisiru a Ben longwe, angakuveleni inu ndi chisiru, kuteleko tindalama tomwe inawapasa mcp tatha Pano akufuna tina

  • @PeterMponda-i9b
    @PeterMponda-i9b 14 дней назад +1

    Genuine Activist, let's welcome our prodicle son, Sir Ben Longwe, thank you Almighty God/ Allah,

  • @MosesNyasulu-c3x
    @MosesNyasulu-c3x 14 дней назад +3

    Tinasiya kuvera zaben longwe

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 14 дней назад +1

    Apapa mukuganiza kwanga ndawona kuti ben longwe bolankoni apapa chifukwa pamene dzikulakwika tidzilankhula, pamene pali bwino tinenepo, izizi ndizomwe DC amanena nthawi zonse.Ben ndikugwilizana nae 100% pa mfundo zonse wanenazi moti akapitiliza izizi akhala mmodzi wa profesional activist. Zomwe akunenazi ndizomwe anthu tikudandaula mmalawi muno.Koma ndimafuna ndimukumbutse kuti msewu wa ku lilongwe si wa cikangawa afufuze bwino×2. Koma ndimuyamikile apapa walankhula chilungamo chifukwa ndizomwe dzikucitika dziko muno mo fire!×2 comradres ben longwe awuzeni dzikoli silibwino timakunyadilani tieni tigwilane manja kukoza dzikoli.

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 13 дней назад +1

    Longwe ndi savage.

  • @MarySinjirani
    @MarySinjirani 14 дней назад +3

    Mwachangu changu thamangira ku chipatala Ben sizili bwino mmutu mwaso konokera amene muli naye pafupi mutenge reni ku zomba mwachangu

  • @ThokozaniBondo-em9fr
    @ThokozaniBondo-em9fr 13 дней назад +1

    Wayamba kubwelamo Ben longwe ❤❤❤❤

  • @meke1308
    @meke1308 13 дней назад +5

    This guy is slowly slowly turning his back towards MCP, mwina amutaya nayenso. Believe me, soon he will be speaking against MCP in full swing.😂

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 13 дней назад +1

      Wawona yekha chilungamo

    • @RelaxCool-dp9jn
      @RelaxCool-dp9jn 12 дней назад +1

      😂😂😂😂😂 ananamidzidwa ndalama sanampatse

    • @meke1308
      @meke1308 12 дней назад

      @ Is it! I see🤣

  • @RajifAbdull
    @RajifAbdull 13 дней назад +1

    Mbudzi yamuthu iyi Mbeni longwe mbudzi

  • @MustaphaChimangeni
    @MustaphaChimangeni 13 дней назад +1

    Welcome Ben reality talkings is what we believe

  • @RasheerdWinnes
    @RasheerdWinnes 13 дней назад

    Ben Longwe ndinu nokha mwatsala olankhula mosanyoza komanso opanda mbali osati agonda nkhutu enawa akuchita kutukwanawa opanda fundo

  • @EthelKspito
    @EthelKspito 14 дней назад +2

    😂😂😂😁😁😀😊 this is a Ben longwe I know hi change any time like kamirioni kkkk amulowesela ya seka pakamwa

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll 13 дней назад

    Ndipo mbuyakoyo wavomereza yekha kuti walephera nanga iweyo ndindani

  • @jafaliKazembe-v3f
    @jafaliKazembe-v3f 14 дней назад

    Ndiganiza beni longwewe udapengapo nsewo ukunena iweyo ndi uti

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx 14 дней назад +1

    Mr Ben longwe nenan kut mcp yalephela bas kapen muopa kuphedwa inuo ndimuthu wabwino koopsa koma Mulo anakupepelesan bwelelan ku job yanu

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 13 дней назад

      Akuopa amufinya a kubwera little by little akayankhulitsa amu tapa 🙌

  • @MussaRafael-d4q
    @MussaRafael-d4q 13 дней назад

    Ben longwe ndiwsmidala uyu

  • @ThomasMaxwell-ks7yi
    @ThomasMaxwell-ks7yi 14 дней назад

    Telela nyani tinakusowani osamasowa❤❤❤❤ mkolongo

  • @Mosa-b6g
    @Mosa-b6g 14 дней назад +2

    Tidasiya kumvera za awa

  • @VictorBanda-ec6km
    @VictorBanda-ec6km 14 дней назад +2

    Ben Longwe wazindikira kuti MCP ili pa ulendo akufuna akonze ubale ndi Mbali inayo kuti mwina adzakhale pa mtendere

  • @GitfIobodo
    @GitfIobodo 13 дней назад

    Chakwera chemene wapanga chadzeru ndikumpha chilima

  • @Lastonebottone
    @Lastonebottone 14 дней назад

    Onyenga mwana wake uyu hat chi inamupasa judo

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov 13 дней назад +1

    Pakwamba nkhamutemwana uyu still nichali nayo ma audios yake yakale kweni pakati apa chikawa chindele welela mwana wa kwithu zani pa unenesko

  • @jamestembo6724
    @jamestembo6724 14 дней назад

    Amufinya Ben longwe ku mcp akufuna kubwera ku dpp mumukane ndichisiru Chaben longwe

  • @marshacee8315
    @marshacee8315 13 дней назад +1

    Umphawi sizinthu mukukamba ziti inu anthu sakumva takolokosa mphuno mwakomo mamina iwe

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 14 дней назад +1

    Mulibe mfundo..nthawi ya Bingu mafuta anasowa inde Koma nthawi tichepe osati Mene zilili Pano nde zimene kulankhula APA zopanda nzeru..chakwera walephera kulamula ndipo anthu alankhula pa 16th sep

  • @jamesphiri4204
    @jamesphiri4204 14 дней назад +1

    Akumapanga zitukuko mumakwawo mokha Lilongwe and Rumphi

  • @saidichirwa5456
    @saidichirwa5456 14 дней назад

    Iwe ndiwe wa bodza ,za ngokukanika kuti unene zoti wamutembenukilaso chakwela wakoyo.Misewu ukunenayo mu town ya Lilongwe si process ya chakwelayo ayi.Iwe unali ku SA ufunse onse tidali kuno ayi.

  • @fysonmatayisa9275
    @fysonmatayisa9275 14 дней назад

    Lero mwayankhula mfundo man well articulated

  • @MalikMulolo
    @MalikMulolo 14 дней назад +1

    Ben longwe weni weni amaneyo sopano

  • @SamLee-j7p
    @SamLee-j7p 13 дней назад +1

    Akatero waigendera patali kkkk timing guys

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy 13 дней назад

    Bilimankhwe wa Muthu uyu nibe

  • @happychimtedza3873
    @happychimtedza3873 14 дней назад +1

    Mwatembenukaso apa 😅😅😅😅

  • @DadTshepo
    @DadTshepo 14 дней назад +2

    Anibe Ngwelo Chawapana Chitseko😂😂😂😂😂

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 14 дней назад +1

    EMPTY TIN......... ...... NOISE
    TADZIKANGOTHUDZULANI DZITHUPHYA UKO WAPANGA CHANI KANGAUDE WAKOYO.

  • @dinchisale
    @dinchisale 14 дней назад +1

    Pajatu mankhwala otalikitsa moyowa ukawamwetsa amasokoneza mutu,

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 14 дней назад

    Beni Longwe ndi Bilimankhwe yemweyo akunyoza boma yemweyo kuyamikira boma ndiye uli mbali yiti

  • @VictorJulio-v4s
    @VictorJulio-v4s 14 дней назад

    Chisilu iwe bwanji osayamikila kwanu ukuyamikila kulilongwe magesi akuzima sikundisiku chimanga anapempha Mai Joe's Bandacho kuteleku achisilu wakowo ukuona Ngati ndife tomwe wangonyelanso osaseta pita ukasete

  • @ClementMunyolowa
    @ClementMunyolowa 14 дней назад +2

    Kuti ma big atuluse ayenera kutero

  • @FelixKChisale
    @FelixKChisale 14 дней назад

    Kulankhula kwabwino kumeneko izo ndiye timati ndale ulemuwanu inuyo mukhoza kumuthandizadi president inuyo zabwino zomwe akuchita achakwela muzitero komaso zoyipa muzimulangiza zikomo

  • @MikeManyamba
    @MikeManyamba 13 дней назад

    Awatu apenga kwasalaku

  • @LukeMapukusa
    @LukeMapukusa 14 дней назад +4

    Kape uyu chitukuko chake chiti from China 🇨🇳

  • @KaumaNtora
    @KaumaNtora 14 дней назад

    Kodi iwe Ben longwe ndimayesa zana lonweli waunyoza chakwelayo ndiye leroso ukumusapota aaaa koma iwe bwanji kodi iwe sidzikuyenda mmutumo aaaa😅😅😅

  • @IdahKadewere
    @IdahKadewere 13 дней назад

    Akuyakhula chochi lero chifkwa chakwera anachosa udindo nthawi imeneyijatu amajiyila chakwera koma dziko abale😅😅😅😅😅

  • @Godwin-xy9rg
    @Godwin-xy9rg 14 дней назад

    Chamba wasutacho nchokhwmisisa wapenga basi

  • @MussaMasuku
    @MussaMasuku 14 дней назад

    Amutaya uyu amuona kuti ndi chitsiru

  • @MustaphaCassim-t7g
    @MustaphaCassim-t7g 14 дней назад

    Ben zooonadi chakwera wapanga zinthu kutenga ndalama yoti angathe kugula fuel ndikupanga asilika akunja kut aphe skc kudzudza amw .

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll 13 дней назад

    Aku user ngat tissue, uona kut upanga bwanji

  • @Jafari-s3c
    @Jafari-s3c 14 дней назад +1

    Iweyo moti ukumalimbabe mtima kumatulutsa tima vn zoona?, ndiye zotembenukazo chakwera wakoyo sanatembenuke?

  • @aishamustafa4410
    @aishamustafa4410 14 дней назад

    Iwe ukufuna kuyaluka chisilu chamunthu

  • @BobJoshua-q5n
    @BobJoshua-q5n 13 дней назад

    openga uyu

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx 14 дней назад

    Chopepela Ichi kod Malawi ndi lilongwe bas kuno palibe chomwe wapanga Khan yamafuta wapangisa kut iyeo asowe

  • @MarcusMarcus-w9w
    @MarcusMarcus-w9w 14 дней назад +1

    A big man but afool

  • @SydneyNyasuli
    @SydneyNyasuli 14 дней назад

    That brother

  • @MussaWilliam-q3l
    @MussaWilliam-q3l 14 дней назад

    Abeni dzimenedzo mwadziwa liti shemu bro

  • @EliasNgoma-k5r
    @EliasNgoma-k5r 14 дней назад

    Mfundo zoyalidwa bwino in a mature way go a head

  • @WilfredKazembe-i6q
    @WilfredKazembe-i6q 14 дней назад

    I will hate " MCP" all my life kupha sikhani ayi mmene anaphela " Hon clement chiwaya" i will hate MCP ever

  • @MaxwellChiwaya-i8q
    @MaxwellChiwaya-i8q 14 дней назад

    Akudwaladi uyu mankhwala amuchulukira

  • @dinchisale
    @dinchisale 14 дней назад

    Beni ndiwe chitsiru kape

  • @mustafailanga2585
    @mustafailanga2585 14 дней назад

    Smangeni mboliyako pamodzi ndi chake wakoyo

  • @LukeshadrickShadrick
    @LukeshadrickShadrick 14 дней назад

    Dzana analankhula zamzeru. Ndinanena ine kuti awa ka Mitac Katha. Ndiye kuti awaponyera ka 2 Mita. Ali pa pay low awa

  • @WhiteMmadi
    @WhiteMmadi 14 дней назад

    Mboli Yamato nice don't tell us nonsense

  • @RelaxCool-dp9jn
    @RelaxCool-dp9jn 12 дней назад

    Anagwela mu Asidi amwenewa mcp kkkk tinasika kale

  • @Tamandakabisala
    @Tamandakabisala 14 дней назад

    Vuto iwe ulindinzeru koma ulindimbali ndipo ndiwe chikangawa

  • @ThaboyEst
    @ThaboyEst 14 дней назад +1

    Nzeru mulibemo umu mmmmm uchitsiru winau

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 14 дней назад

    😂😂😂

  • @MercyNkhoma-b6h
    @MercyNkhoma-b6h 14 дней назад

    Ben Longwe ndi chameleon 😂😂😂

  • @EmmanuelGodfreynkhoma
    @EmmanuelGodfreynkhoma 14 дней назад

    Chitukuko chake chiti achitsilu Inu

  • @PrinceThom-pe6ie
    @PrinceThom-pe6ie 14 дней назад

    Monica chakwera ndalama yomangira school yapamwamba azitenga KUTIKO?.Monica chakwera akugwira ntchito KUTIKO?

  • @FosterPhandama
    @FosterPhandama 13 дней назад

    At least today 😂

  • @ChristianMalingamoyo
    @ChristianMalingamoyo 14 дней назад

    Vinyo watha kapolo iwe

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 14 дней назад

    😅😅😅😅😅uyu ndi munthu onvetsa chisoni mmmmm

  • @YassenYasin-v6o
    @YassenYasin-v6o 14 дней назад

    😂😂😂😂chakwera palibe chimeneapsngs kupozakupa andu ku chikangawa komazo njala kudula zindi deyle aaa achakwra ulendo bazi😂😂

  • @PatumaPhiri-o7g
    @PatumaPhiri-o7g 14 дней назад

    Kkkkk alibe mbali

  • @SamukLungu
    @SamukLungu 14 дней назад

    Ukondiye kubwera asati zija unarikare apa tikukonda

  • @enerstmakochera3956
    @enerstmakochera3956 14 дней назад

    Apa nde wavomeledzano kt with MCP zinthu zavuta

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz 14 дней назад +1

    Koma kweni kweni awa Ali mbali it kkkkk

  • @GeraldMukhuna
    @GeraldMukhuna 14 дней назад

    Fisi ndi fisi koma adawa maluzi akawamenya akumenya yobela chimwendo chenjelan angakubeleni 23milluon ku Bt Ali pa creuza kkkkk ndichilombo ichi

  • @PaulChombo
    @PaulChombo 14 дней назад

    Tamangodya mabazi aise boma ili yaononga dziko

  • @ImpalaSite
    @ImpalaSite 14 дней назад +1

    Iwe Mtumbo wa Mai ako nachende iwe stupid

  • @beakab2378
    @beakab2378 14 дней назад

    Chakwera HAS DONE NOTHING. Ndanena mokweza. Useless Ben longer muthera limodzi ndi mcp yakoyo

  • @simonchirwa5953
    @simonchirwa5953 14 дней назад

    you're just making noise