he is really alive ...am touched with this inspirationan song keep it up in Jesus name.!only wishing that one day I go sing with you the chitheka family.....
Ndimadalitdika ndikamawonela nyimbo za uzimo, ndipo ndikupenpha kwa a amalwi wonse amene a mayimba nyimbo za uzino kuti apitilize patsogolo ndi ambuye mulungo wathu awathandize,zikomo kwambiri
Thank you Lord for setting my child free.Ndinu wamoyo Yesu.
Chimene ndidziwa yesu wanga ndinu wa moyo , mulipo mumandiona mumandimvetsera nthawi zonse
Indeed my Jesus is alive, he doesn't sleep nor slumber
Mulipo mumandiona mumandimvetsela nthawi zonse...,. Powerful. I love this song....
he is really alive ...am touched with this inspirationan song keep it up in Jesus name.!only wishing that one day I go sing with you the chitheka family.....
Ndimadalitdika ndikamawonela nyimbo za uzimo, ndipo ndikupenpha kwa a amalwi wonse amene a mayimba nyimbo za uzino kuti apitilize patsogolo ndi ambuye mulungo wathu awathandize,zikomo kwambiri
Imandidalitsa nyimbo iyi anthu amulungu!!!!!
Ndiwamoyo indeed..i sing this song with tears in my eyes every time and it has been my everyday prayer..may God bless you Chitheka
Yesu wanga ndi wamoyo ndithu
Ndiwamoyo, I Love You Ministers
One of my favorites
Yesu wa wina nkhondoyo
Kunena zoona chitheka family music band mumandisuntha ndipo moyo wanga mwaupanga kukhala osithinka chonde pitilizani kutidalisa.
Maso anga samakuonani manja anga sangakugwireni chimene ndiziwa yesu wanga ndinu wamoyo
Yesu ndinu wamoyo
Nice song grace
😢this song
zoona yesu wathu ndwamoyo" chitheka mumathA
Amen
NDIMALITSIKA NAZO NYIMBO ZANU KWABASI
wow
Can you pls put more chitheka songs.
will do that soon
Thanks
Chitheka is blessed
yesu amandikonda
Drug land