Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Beni ulongwe tizimukhululupira chifukwa anali kuboma konko, pomwe amumana chibunz waagalukira ndiye apa timvano zenizeni
Kulankhura kwa Beni longwe nkofewa nkamwa ngati mwana obadwa kumene,kulankhura kwao nkokhara ngati mkamwa muli minga nde kuti amasuke atambasule lirrime ngati kuti akuopa ndi minga kuwabaya,salankhula mobooleza
Ben longwe simunthu omumvera kulankhura kwake,satha kubooleza ali ngati mwendo wina uli uko wina uli uko sadalirika
Zoonadi nkhaniyo mukambayo anthu tikutsatani ambili enawa majelas❤❤❤
Well expounded waiting for the next episode
😂😅ben longwe nzeru ulibe
Zoona Ben Longwe Mcp yamumanadi chibanzi
Ben longwe wayamba chibwana usamale ife tikulila
just wait for 2025 chakwera ndazake akukalowa anapha chilima ndiazake this time a malawi sitikugina
From South Africa
Uladi musa Amubwilitsa dothi ku MCP, achikaulitsa chimakonda kupita ku zipani zolamula kutsata unduna Uku wakumana ndi mchewa change golo. Andale adyela chonchi kumawatelo ndithu
Very good brain storming
Koma Mayi Yolamu Aja unawakoka zokokakoka zija,,,
Inu tinakutulukani kale mulibenso nfundo
Ukuonesa uchitsiru wako Ben Longwe zopusa zokha zokha
Zoduka mutu zokhazokha udali kuti ndi maganizo ako opusawo anthu alira atopa kapanyo ngati iwe uzikasokosela pano uziwuza anthu pepela
University of Hard knocks 😂
Pa Malawi padzadza anthu ozungulira mitu monga a Ben Longwewa. You fail to wonder kuti peni peni wayima pati?
Awa angotitayitsa nthawi .ndachitsiru
Wakutuma ndani usamale zopusazakozo ugaluwako
Ine Ben Longwe ndinamutuluka kalekale since anayamba kupanga za Mcp ndie apa or mukubweranso after kumanidwa chiguma ndi lazalo koma fanz inakutulukani man u better stick one side cos ur comfusing us ndi dyera lakolo
Inutu dyela lizakuphani man
Vuto lolowa uku ndi uko Zimavuta .Timvele ndani munali Chete nthawi yonse ija abale.Any way Only God knows