USAUVER S10E05 - LIKE FATHER LIKE DAUGHTER

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 1 дек 2024

Комментарии • 714

  • @eddingtonkapenuka1432
    @eddingtonkapenuka1432 2 дня назад +92

    Usauver has officially replaced Tikuferanji. We need it on national TV now. Anthuwa ntchito akuyigwila heavyyy💥💥💥💯

  • @phirimathews234
    @phirimathews234 День назад +11

    You deserve to be on tv now , thanks my people from Malawi, representing zambia,

  • @chifunirotchawango
    @chifunirotchawango 2 дня назад +50

    🤣🤣🤣😂😂😂😂 Gani fans let's gather here

    • @Francis-rz6fv
      @Francis-rz6fv День назад +1

      Gani ndi 1 amwene.kkkkkk

    • @Reen748
      @Reen748 День назад

      Akatundu😊 nd Gani nd Patricia

  • @MphatsoMvula-k6e
    @MphatsoMvula-k6e 2 дня назад +43

    By public demand idzikhala ya 1 hr episode please 🙏🥺

  • @BlessingsHendry
    @BlessingsHendry День назад +10

    19 years amandiwaza takondwa eeee umatha iweyo ndi one mofayaaaa🔥🔥🔥🔥

  • @MusaMgogo
    @MusaMgogo День назад +8

    Ndimangomwetulila ndekh nkamaonel mafilm aanthu amenewa😀

  • @EstherGunduze
    @EstherGunduze 2 дня назад +17

    It's Gani's calling for me😂 ati sistez🗣️, mulaaa🗣️ jah man😂 nde mazila nkudzasweka😂😂😂😂

  • @chikondiphiri7077
    @chikondiphiri7077 День назад +2

    Albert tamuluza basi😂😂😂 . Koma zomwe wayamba Gani akuthamangitsapo ndithu😊😂😂

  • @macjoy943
    @macjoy943 2 дня назад +20

    Ma shadow akumatithera nthawi aaaa😮

  • @iamcrakie
    @iamcrakie 2 дня назад +15

    Ati ndikatenga chicken ikafunika rice🤣🤣🤣🤣🤣

  • @IreenBanda-g5b
    @IreenBanda-g5b 2 дня назад +6

    Zamasilipasi a patirisha tikambabe lets focus zamwana opezayo😂😂😂😂😂

  • @lilliana_es
    @lilliana_es 2 дня назад +10

    Its the consistency for me,,, Good work Sangie and team 😍

  • @DebraChimbaka
    @DebraChimbaka 8 часов назад

    Albert wabalalika mulamu wamusokonoza mutu😂😂sanjie ,gani, angozo 😊🎉🎉🎉

  • @atupelesikwese3263
    @atupelesikwese3263 2 дня назад +10

    Tiwonele zimenezi,
    Ofunikanso izituluka daily ndipo 😂😂

  • @ThokoChilenga-sm1bo
    @ThokoChilenga-sm1bo 6 часов назад

    😂😂Hyphen wapangidwa harnessed....naye anyanya kuoneka bwino nditimanyazi take tabodza😅

  • @tamanichilala209
    @tamanichilala209 День назад +1

    Koma Patricia ndiwetu wamtopola obhebha, naye Ngozo baibulo lamukomera zedi, nkudzati Gani and step daughter eeeh! Komaso bartender uyu eeh 🙌

  • @InnocentKasiya
    @InnocentKasiya День назад +1

    Piksy iweyo ndiwe actor zoonna .. Ndi mayiwo mmakwana 🎉🎉🎉🎉🎉

  • @MemoryChingola
    @MemoryChingola 14 часов назад

    Ati Solomon akundipanga inspire 😂tk akuzatenga ya ndiwo kwa step dad🎉komanso gani penapake aaaah ...the whole crew is fire

  • @daniellatapwata6826
    @daniellatapwata6826 2 дня назад +10

    Kmaso mwana omupeza wa ganiyi eeeeee azuzika naye😂😂😂😂😂😂😂😂😂💔Zoona akawauze bambo ake omupeza kut ngouma....

  • @Lawrencenkhoma-b2s
    @Lawrencenkhoma-b2s День назад

    Pandisangalatsa kwambiri pa Solomon akundipanga inspire hahahahahahaha ndipamasilipasi amene akukakamilidwawo hahahahaha

  • @BlessingsMaloya
    @BlessingsMaloya 2 дня назад +2

    Albert zayambikaso uku mnyumba muja,☺️☺️ nde wakumana ndi Ng,aluli Edo eishiiii ii, bad influence😂😂 kkkkkkkkk akuti mwaziwa bwanji nanga iziso ndanena ndine😁😁

  • @BlklilSis
    @BlklilSis 8 часов назад

    Ati a shadow, iyi inali plan yanu isati yathu🤣🤣🤣..... Hiii koma tonde maluzi amamchapa

  • @SparrowBanda
    @SparrowBanda День назад +1

    Team ngauzoo 😂😂😂😂 akuti Solomon akumulimbikisabetu mpaka pano nde pat hmmm kaya

  • @KondwaniKandulu
    @KondwaniKandulu День назад +4

    Usauver is now the best comedy series

  • @ChifundoKabuka-k7d
    @ChifundoKabuka-k7d 2 дня назад +4

    Silipansi yomwe amakonda sangie abale😂😂💔🙌

  • @DysonAmos
    @DysonAmos 2 дня назад

    ati Solomon andipanga inspire🎉😂😂😂 kma ngozo kkkkk,Gani's act never disappoint❤

  • @LovenessChinyama-xs4ke
    @LovenessChinyama-xs4ke 2 дня назад +21

    Koma Tonde amapempha ngati sionenepa eeeh🙌🙌😂

  • @IvyMhura
    @IvyMhura 2 дня назад +5

    Patricia watchena ma Slides 🤣🤣🤣🤣

  • @izahakageorge9573
    @izahakageorge9573 2 дня назад +1

    Kmano amuna Hyphen aaaah atayatu Yesu awa ooohooohaaa #MUCH LOVE GUYS

  • @doreenluhana
    @doreenluhana День назад +2

    Kuchita kuona kuchedwa for the next episod 😅😅🎉🎉

  • @smithchalemba995
    @smithchalemba995 14 часов назад

    ati ndimatha kuphika....atonde thobwa mmalidziwa inu mmene aphikila😂😂😂😂

  • @freedommuyaka8597
    @freedommuyaka8597 2 дня назад +3

    Solomon akundipanga inspire 😂😂😂😂

  • @EstherGunduze
    @EstherGunduze 2 дня назад +5

    Ati "u r such a gentleman"😂😂😂 zauhule😤😂

  • @BENMALEMA-x6p
    @BENMALEMA-x6p 2 дня назад +13

    Ati ndigula bwanji zinthu zoti ndili nazo 😂

  • @MemoKadaleka-wc5nb
    @MemoKadaleka-wc5nb День назад

    😂 😂 😂 Aaah ndimava kukoma koopsa Patricia ndi gani wakoyo

  • @loveartscreatives
    @loveartscreatives День назад

    A Gani ndinu a busy tisakubisireni😂😂😂😂 Patricia usamalalate kwambili😂😂

  • @ColletaPhiri
    @ColletaPhiri 2 дня назад +2

    Ati bola inu koma anzanu aja anatibweresera ma braa😂😂😂

  • @PelvinNazombe
    @PelvinNazombe 2 дня назад +1

    Patricia Patricia Patricia how many times did l call you 😂😂😂😂😂silipasi yabwanji imeneyo usandikomole wamva 😂😂😂😂

  • @Gracendau-d3l
    @Gracendau-d3l 2 дня назад +1

    Koma ine Patricia ndi ngozo ayi zikomo 😂😂😂😂😂amwene gani ndi mwana wawo😂😂😂😂

  • @TaoKathumba
    @TaoKathumba День назад

    At aaaa kma alendo kkkkk sangie my favourite. At m' bale wake ndi mmodzi kkkkkk

    • @gondwechisomo
      @gondwechisomo День назад

      Chonsecho m'bale wakeyo ndamene waswa dzila limodzilo😂😂

  • @DennnisGogoda
    @DennnisGogoda День назад +1

    Koma ma traffic lights 🚦 aja😂😂😂Iwetu iwe ukhalike

  • @reinamlongoti9286
    @reinamlongoti9286 День назад +1

    Ati vuto lake ndikatenga chicken ikafunika rice🤣🤣🤣

  • @EMM_KAY_KIM
    @EMM_KAY_KIM 2 дня назад +3

    Gani pamsana pake ndithu😂😂🙌🏽

  • @user-m1ss-th0ko
    @user-m1ss-th0ko День назад +3

    Mtebe 😂😂😂😂😂😂he is naturally a comedian 😂😂😂😂😂😂becoz no!!!!

  • @SaraBinalison
    @SaraBinalison 2 дня назад

    Kma Albert ati iii
    Nde ati akufuna mwana
    Ine Ndikuwona ngat nkazi ali ndi mimba ya wina 😂😂😂😂

  • @dylessmwanguku5958
    @dylessmwanguku5958 День назад +6

    Y'all effortlessly funny eehhh😂😂😂😂bartender machine!😂

  • @gondwechisomo
    @gondwechisomo День назад

    😂😂😂😂😂imagine Tonde anakakhala step father wa Takondwa😭💔

  • @ClaraChisale-no7fr
    @ClaraChisale-no7fr 18 часов назад

    Inu simumakumana ndi mayanga mwamtenderee 😂😂😂😂 step daughter uyu atimvuta

  • @jeanmaele3528
    @jeanmaele3528 2 дня назад +4

    Koma Albert Ali mumayesero🙌🙌🙌😂😂

  • @HesekiahChunga
    @HesekiahChunga День назад +1

    Edoooo mmm too much trick questions 😂😂😂😂

  • @kherereluckson4343
    @kherereluckson4343 2 дня назад +1

    Ati ndigula bwanji zinthu zoti ndilinazo 😂😂😂

  • @preciousnamakhwa
    @preciousnamakhwa 2 дня назад

    Mmmm Albert ndy wagwa munsampha bac akufun a azidya kuwiri 😂😂😂😂😂

  • @21rocket.
    @21rocket. 2 дня назад +1

    Ndikatenga chicken ifunika rice ... 🍚 😂🔥

  • @MerryMpakeni
    @MerryMpakeni День назад

    Kkkkkkk gàni zakuchibwezi zochita Kuba Kwa sister 😂😂😂km anthu enawa ovuta kulera😂

  • @Malawi227
    @Malawi227 День назад +2

    The best comedy in malawi ❤❤❤❤

  • @MercyMbeleko
    @MercyMbeleko 2 дня назад

    Ati usakanamizire kusokeratu😂😂 Mulamu nae Eesh🙌

  • @ayaowansongo6436
    @ayaowansongo6436 День назад

    Kod ma Eddo onse ndia chonchi 😅😅
    Tirinaye eddo wathu kunoku koma2 aribe 2koloko kuphurisa nkhan😅

  • @RaphaelMpekansambo
    @RaphaelMpekansambo 2 дня назад +1

    Koma team yachina tonde palibe wabwino 🤣🤣🤣🤣 onse ndizombayokhayokha🤣🤣🤣🤣

  • @jamesbwinja8707
    @jamesbwinja8707 2 дня назад +2

    Koma Gani akwanitsa kulera mwana omupeza wanzeru ngati ndondochayu😂

  • @valentinomolosen
    @valentinomolosen 17 часов назад

    Beautiful TV series as of now in Malawi... pakafunika
    bodyguard wa shadow am here

  • @mirriamchisala7622
    @mirriamchisala7622 2 дня назад

    Kmatu a edo ndi bad company mmmmmh 😂😂😂ati usakanamizile kusochera 😂

  • @chitchohistorical1036
    @chitchohistorical1036 2 дня назад +1

    Albert ndi more vibes😂🤣✨🔥🔥🔥

  • @Mariam-v8w5g
    @Mariam-v8w5g 2 дня назад +22

    Team Patricia gather here😅

  • @ChikuBulambo
    @ChikuBulambo День назад +1

    Koma abusa ngokhomelera eee🙌🙌

  • @DysonLyton
    @DysonLyton День назад

    Koma ganizani wandiseketsa mpaka thumbo kuwawa🤣🤣🤣🤣

  • @LeticiaNgaiyaye
    @LeticiaNgaiyaye День назад

    Koma barman Edo amakonda mabodza mmmmh kkkkkk amakonda azimva mabodza a mmakomo mwa anthu zimankomela😂😂😂😂

  • @TsuzenThomas
    @TsuzenThomas 2 дня назад

    Koma Takondwa ati sinanga mwangochoka simunasiye yandiwo 😂😂 Patricia kutchena kwabwanj uku 😂😂 Albert mayesero akunzembera 😂 Edo ndye iiii mchoyankhulitsa 😂😂 Tonde yambeu yamuwawatu zed 🤣🤣

  • @fatimamalinda6038
    @fatimamalinda6038 День назад +6

    Edo nd bad influence 😂

  • @ThomasMangochi
    @ThomasMangochi День назад

    Komatu nde muuumatisiya mmalele bwanji muzitulusa awir😂😂

  • @YusufAjida-t8r
    @YusufAjida-t8r 2 дня назад

    Koma agani ndi ndiwo zakubazi Mpaka zipitlila ndi mwana alinaye uja 😂😂😂

  • @LM-gz5pk
    @LM-gz5pk 11 часов назад

    Katakondwa kamandbanda 🤣🤣🤣 at inu ndye ouma 🤣🤣

  • @johnmthepheya3700
    @johnmthepheya3700 День назад

    Mulendo wasanduka Jahman
    😂😂
    Gani usationjeze

  • @Aaron-MW
    @Aaron-MW 2 дня назад

    19:42 ati usakanamizire kusochela😂😂, Eddo amatha🔥😂

  • @ChisomoKapanda-jg2uf
    @ChisomoKapanda-jg2uf 2 дня назад

    Mlamu wa Arbert wamunayo eeeee akumusowetsa mtendele 😂😂😂

  • @ShexywkuLilongwe-p2s
    @ShexywkuLilongwe-p2s День назад +1

    Like daughter like father 😂😂 kma a2 ma ticket ndy akuny'ambad. We'll back soon

  • @Stella-jd3dy
    @Stella-jd3dy День назад

    Ka takondwaaka ngakhale sitimakakamba Koma ndika dolo heavy😂

  • @HassaniAnubi-dz3nw
    @HassaniAnubi-dz3nw День назад +1

    Man Edo at mumakonda power bank😂

  • @ChristopherMatemba-m4g
    @ChristopherMatemba-m4g 4 часа назад

    😂😅 ati eeeh inuso ndiye ndinu oumati

  • @winfridakamwana
    @winfridakamwana День назад +1

    It's the slides a sangie for me😂😂😂

  • @morgankalendoh5901
    @morgankalendoh5901 2 дня назад

    "you are such a gentleman. Arbert 😂😂🤣.
    ❤️Mutivesa kukoma guyZ

  • @Ecclesiastes709
    @Ecclesiastes709 2 дня назад +1

    Gani kufuna kutenga chakudya ndi cha 4koloko chomwe mpaka madzila munthu watenga kale nyama eeeeh

  • @OliveChirwa
    @OliveChirwa День назад

    Koma tonde amavutika mpaka kusowa ndiyogulira popcorn, ndeamaneneredwa chilichonse kkkk umphawi sizinthu, koma nthawi ikumandichepera mashadow akumationongera nthawi aaa

  • @IshmaelSmart-l8v
    @IshmaelSmart-l8v 2 дня назад +1

    Ccta wake ndi makinadi eeee😂😂😂

  • @MercyMsiska-d5m
    @MercyMsiska-d5m День назад +1

    Ati like daughter like father abale Gani vizungu 😅😅😅😅

  • @FonexfestonInnocent
    @FonexfestonInnocent 2 дня назад +1

    Ndimwa ice 😅 like father's like daughter 😂

  • @LabaniHenry
    @LabaniHenry 2 дня назад +2

    Gani pamenepaja chete ndi mayi azake 😂😂😂😂

  • @ivyfrankie-jf2eq
    @ivyfrankie-jf2eq День назад

    Kma Ngozo kupangidwa inspire ndi Solomon zitha bwino😂😂😂

  • @RashidKanjoka
    @RashidKanjoka 2 дня назад

    Mpaka ndakakamizika kuti ndikhale ndi bundle😂😂😂😂

  • @jackmoyo9169
    @jackmoyo9169 День назад +1

    Komatu ngat Albert ali opoira choncho in real life ndye ayisotu

  • @nunuluwayo9525
    @nunuluwayo9525 День назад

    Vuto lake ndikatenga chicken ikafunika rice 😂

  • @raconteurreuben6027
    @raconteurreuben6027 День назад

    Shado sanaonekemo akusakabe ngini yomw sing'anga anamusowesa 😂😂

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov 2 дня назад

    Dzina ganizani nde ummm akuganiza molakwika kwambili imene waiyambayo akuthothapo ubwele kuno ku joz uzizathamanga kkkkk

  • @CeciliaBiyombewe
    @CeciliaBiyombewe 14 часов назад +1

    Koma gani wayamba Kuba ndithu 😂😂😂

  • @IvyMhura
    @IvyMhura 2 дня назад +2

    Komanso Tonde umadziwa kupemphetsa eee🙌🏽

    • @RACHIE-zs5sk
      @RACHIE-zs5sk 2 дня назад

      😂😂😂😂😂 mpaka amamumana 😂

  • @MirriamMalefula
    @MirriamMalefula День назад

    Kkkkkkkkk akut ndife asangalare 😂😂😂😂

  • @EstherEmuson-lj3lq
    @EstherEmuson-lj3lq День назад

    Kma zilipoo mmmm tonde alibe ulesi bwanji kupepha kotani uku kkkkkk

  • @InnocentKenamu
    @InnocentKenamu День назад +1

    Komatu nkhani ya Solomo yavuta 😂😂

  • @SinoyaKalima
    @SinoyaKalima 17 часов назад

    It's M'bale wawiyotu safa gagaga kulimba for me😂

  • @ChikwanjeJames
    @ChikwanjeJames Час назад

    Ngt ndapanga follow yonse because of Hyphen mandiwaza

  • @MusaCasimu
    @MusaCasimu День назад

    akuti dzida dzasowa Kaya dzapita Kuti kkkk❤❤❤❤❤❤❤❤ I like it