Gani samatha kukwiya guys🤣🤣 you guys are the best 🔥 🔥 A shadow kadziko mkakang'ono aka muthela mmanja mwa anthu ohooo🤣🤣 Chili mmanja hane 🖐 Best friend?🤣 My Belita is very stressed 😢 🤣 fafandede sau kam'busa koumira kaja🤣💔🤣💔🤣💔🤣Black amayenda ndi Beauty di🤣💔🤣💔Albert mwayamba kubhowa aaah🤣🤣🤣 Mahope Ngozo is always on point ndi mkazi wake Pat🤣 Have faith magaye passport ituluka.
Zinthu zimayambira patali Che Nkope amaseketsa mkalasi with his jokes ku secondary school. Piksy amatiyimbitsa ma desk in class. Lero you are celebrities 😂. Congratulations
Km banja la a ngozo nanu pangani zitheka tsiku lina tizakuoneni muli nchikondi😂😂can't wait to see Patricia akugwira ndevu za angozo hahahaha km pazachema
Leroli ndiye ndaseka, my best scene a shadow achotse milu milu, komanso Albert wabhowa heavy aaaa. Uyuyu ndizungulira nkhonde sichikondi ayi. Wavulala Albert pilizi angozo muthandizeni mnzanu sizoona ayi
Ati sindinagwirise ntchito zida Zina ndi Zina kkkkkkkkkk this time guys mwaphika honestly I like you guys Gani the best l, shado, Patricia mumandisuntha guys
Please don't forget to subscribe and share
Koma camera improve
Apa mmene zuonekeramu mufuna muphe character ya ganizani...sibho koma pakati munamuchotsa ganizaniso mu.uchotse??..
Zafuta ndinyemba
Season finale??😮😮😮😮😮
Subscribed & shared.
You guys are very good at what you do, thank you for entertaining us.
We need more of such longer episodes in the next season
You guys are really good. The characters are all unique and everyone has amazing skill and they are funny in their own right.
Thank you for adding some more minutes I enjoy this series
Gani samatha kukwiya guys🤣🤣 you guys are the best 🔥 🔥
A shadow kadziko mkakang'ono aka muthela mmanja mwa anthu ohooo🤣🤣 Chili mmanja hane 🖐 Best friend?🤣 My Belita is very stressed 😢 🤣 fafandede sau kam'busa koumira kaja🤣💔🤣💔🤣💔🤣Black amayenda ndi Beauty di🤣💔🤣💔Albert mwayamba kubhowa aaah🤣🤣🤣 Mahope Ngozo is always on point ndi mkazi wake Pat🤣 Have faith magaye passport ituluka.
😂😂😂😂😂
This is my first time to watch this. Guys you are so good
That part when the shadow MP said "zinazotu ndiza new1, ndipatseni mask"😂😂😂😂😂
#usauver🔥🔥🔥
Guys inuo youre so creative... Kusayankha fon kwa Albert mpaka ndapanga catch ma emontions 🙌.... Chikondi chija chimapeperesa sometimes
You guys are really good. I just wish I had the financial capacity to sponsor the next season because I love watching you guys. 🔥🔥🔥
Thank you so much for adding more time
This is beautiful............i really enjoy watching you guys and you are very very good
😂😂😂😂 koma guys!! I can't wait for the next season. Ine nde fan weni weni from the start! From the very first episode! You are doing a great job
We are together my deer😂😂😂😂😂
straight up @USAUVER..... Season 8 was lit guys keep it up and keep the fire burning!
Koma Patricia kukokomeza nkhani🤣. It's so nice to see how much the show has grown. Keep it up guys!
Zinthu zimayambira patali Che Nkope amaseketsa mkalasi with his jokes ku secondary school. Piksy amatiyimbitsa ma desk in class. Lero you are celebrities 😂. Congratulations
Km banja la a ngozo nanu pangani zitheka tsiku lina tizakuoneni muli nchikondi😂😂can't wait to see Patricia akugwira ndevu za angozo hahahaha km pazachema
Tsiku limenelo ndiye olo benz adzamupatsa. Ieo koma azilalata limodzi
This has been a great season! Keep it up guys. Matimvetsa kukoma💃💃
This is great Need longer episodes like this in the next season
Ineyo koma I would really like to meet Gani in person tizacheze amatha😂😂😂😂
Olo ine 😂
Ndipo exactly ganizani he's perfect
Kkkkkkk gani amandiwaza nane kkkk ndipo ndewu ija ndikanalowelera 🤣🤣🤣
The tumbuka guy though😂😂😂
Mupange ma t-shirts a usauver enaso tigule ife❤
Tili pano kudikira ma usauver t-shirt
Nice one,, we love this. keep it🔥🔥 we want "Pakati" in the up coming season9🙌🏾
Ndipo we miss that guy🖐️
Leroli ndiye ndaseka, my best scene a shadow achotse milu milu, komanso Albert wabhowa heavy aaaa. Uyuyu ndizungulira nkhonde sichikondi ayi. Wavulala Albert pilizi angozo muthandizeni mnzanu sizoona ayi
The picture quality today is fire nice work guys
Whenever the shadow visit MR tonde amakhala achapa😂😂
I always enjoy this serie, ndipo mudzipanga panga ma episode atali chonchi
I'll miss you guys 😂
Please come back soon.
Usauver without shadow singabhebhe😂😂😂😂😂
Sangie is unpredictable, sungakambe naye zocheza akutembenukira😂😂
I can't trust Sangie in real life 🤣🤣🤣🤣🤣
Broo!!!😂😂😂
Sangie ndoopsa😂😂
Sangie ndioipa
Mkazitapetu zedi 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
You see. Now I see her in video songs, am like aah no don't take her seriously guys, I know Patricia very well😂
Guyz this is dope,don't keep us waiting for season 9
Iyiyi olo itayikidwa 100 mins ikuchepa 😂😂😂😂😂iyi ndi fire 🔥 kwambiri 😂😂😂😂mumayitha guys ❤❤❤❤
Shadow episode iyiyi nde wazigwila😅
I love this series heve❤️❤️😊
Big up guys 🔥🔥🔥🤗
Ati sindinagwirise ntchito zida Zina ndi Zina kkkkkkkkkk this time guys mwaphika honestly I like you guys Gani the best l, shado, Patricia mumandisuntha guys
Komatu sangie ulongosoke iwe mmmmmm ayi...I think ngozo anazigunda mmm 😂😂😂😂
Best season ever looking foward yo another 1❤
Iyiii ndiye ili bhooo ili mwala mwala ndaikonda keep up guys
season 8 inali nyatwa ,gani patricia ndi berita u did your best season 9 sikuti muchedweso ngati mmene munachedwera 8 ti
Gani my favourite 🔥💯... looking forward to season 9 🔥🔥
Sangie AKA patricia Eeeeee ndiwa ntopola kkk kumufunsaso mwini shop ngat akufuna madzi 😂😂😂😂🙌🙌 ai zikomo
mR ngozi ngozo paja munauza madamuwo kuti galu azaziwika kutheka. Anaiwala takumbuseni kuti pakati pa arbart ndi madam awo galuno ndindani kkkk muthu kuthawa chifukwa akukondedwa kkkkk big up gayezi ndimakunyadirani
Koma this is my favorite series in Malawi 🔥🔥.
You can say that again and again
We can now watch it alito bit longer.. Big up guys
Yoh this is a top notch episode 😅😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂 next season we need more 30 min episodes netflix here comes malawi
Sangie kkkkkkk akufuna ndimuthangitse m'bale wanga 😂😂😂😂
Anthu akunva inu bolako mwaonjezera nthaw love you guys ana osamba kma ngozo nd Patricia tikufuna tione baby iyaaa😂😂😂😂😂
A shadow ndi puloblem 😂😂😂
This is one of the best guys keep up the good work 🎉🎉
Albert Ali nchikondi mpaka kukanika kuyakha Fon ya nyemba😂😂😂😂
A Godfrey Mtondee mwatinyamula heavy... Fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
This is nice, yaitali bwino episode
Komaso, Belita nde Ali Ndi chi shop tu 😍
Kuyimilira muyimilire zisankho osati mipanda yaeniake😂😂
Belita ndi Dorothy shonga akunjoya🤣😂😂akulandira ma 500 hundred
Koma Shado amatha kwabasi😅😅😅😅 ati tima children inu timadya ndimafupa omwe🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Wow! You rock guys😂...ashadow ati issue 🙌🙌...when is season 9 coming? Can't wait
Maguy Gani munantenga kuti , uyuyu ndi mbambande kkkkkkkkk
You guys have talent in doing shows🎉
Koma chinanchina eee mu episode iyiyi shadow waziona 😂😂😂🙌🙌🙌 ma issue milumilu 😂😂😂
Love your work guys keep it up
Gan ndidolo ati angokwrra mpanda akagigode pakhomo😊😊😊
Issue iyiyi yikuyenela kuyikamba amekabule kkkkk i can't stop laughing ....a shadow zawavuta sure
ndewu ndindewu olo miyala mpeni game ndikutibulana kuti winayo adziwe kuti ndewu mkuvala zilimbe 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Tsopano Patricia Angozo alakwa chaniiiiii nkhani yatembenukaso 😂😂
Kkkkk koma guys mumakhala serious Mwainswa Iyiyi Alorbet akuchendwa Ndi Mkazi kkkkkk amatipusisad adzimaiwa
Neba wa mtebe ali NyAtwa ,,. good one guys
l love couple ya ngozo mukuitha guy's 😁
😂😂😂😂😂 koma ndaseka kuiwala kuti ndakwera public transport eish Hahaha ee
I love this series ❤
Excellent work guys
your still teaching ❤❤❤
KHANGATI Ntebede ndi zeze zawo ndizofanana, anyamata ama fafandede🤣🤣🤣🤣
Komatu chiganizo chokwela mpanda kuti mukagogode chitseke agani muotchedwa nazo 😂😂😂
Komano isiyen pa tv pg Angauzo
😂😂😂😂😂😂 ati chakuwatu,,,,, it's Mashasi amwene
i love this ❤
Albert mpaka kugona pa miyendo ??Ndevu mmanja mwa adona,,,,Finalle indeed😂😂
Fire shadow keep it up you rock guys😂😂
kkkkkkkk ok ashado kuwatelo kkkkkkk koma osanama guys ndimakunyadilani kwambiri keep it up ok.
The best drama group
Albert waluza bizimisi kamba ka nyu catch kkkkkk. Koma ganie nd 1 eeeish
Thanks we can finally watch it a little bit longer
Eeee koma guys this series eeee mwakonza ndipo l😅😅
Komatu Albert wafikapo olo za business wasiya sakupanga nawo😂😂😂😂😂
Ng'ombe igwera bwanji mudzenje😂😂
Sangie aaahh umfusa bwanji munthu madzi mu shop yake yomwe😅😅😅😅
Koma guys please do something tikudikilabe ya full
Anyway love you all ❤❤❤
Koma Jededaya nde akukupopa kumbali kuno 🤣🤣🤣🤣🤣🤣 wamatemba daily lol
Mandi mvetsa kukoma saname🔥🔥🔥🔥😆😆🙌
Km uyuu mukut Shadow 😂😂😂 amatha heavy 😂😂😂
Alabati apa nde wafikatu
Gani amandiwaza😂😂😂 can't wait guys
Gani udalira mwala😂😂😂😂
First love imakhala yovuta
Inuyo Nde mmandimvetsa kukoma guys keep it up
ka shadow akakhaulitsa, ine mphaka chisoni🤣🤣🤣🤣🤣🤣
I already see the new updates with the reflector etc, also Tonde ndi Shadow wabheba
Guys mumatha, keep it up. Mumatinvetsa kukoma heavy.
Can't wait for season 9!
Now I see Sangie in video songs, am like aah no don't take her seriously guys, I know Patricia very well😂