Maggie Mangani - Mundiyendere (Official Music Video)

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 7 янв 2025

Комментарии • 34

  • @marynkhata9707
    @marynkhata9707 Год назад +1

    Zikomo maggie mangani nyimbo yamatanthauzo iyi ambuye mundiyendere

  • @catherinegama786
    @catherinegama786 9 дней назад

    M'ndiyendere
    M'ndiyendere
    Mnachita bwino kuzilimbitsa baba nyengo zanga'zo
    Mnachita kuyiwumitsa mitima ya abale anga
    Mnachita kuyiwumitsa mitima ya ana anga
    Mnachita bwino kuyiwumuitsa mitima ya ondithandiza
    Kuti mbuye mkandiyendera
    Mkasintha nyengo zanga
    Ndisatame mkono wa nyama
    Ndim'tame yehova.
    M'ndiyendere

  • @MaryMudiwale
    @MaryMudiwale День назад

    Amen mundiyende musithe nyengo zanga

  • @madasaopa
    @madasaopa 24 дня назад

    Nyimbo yachilimbikitso. I like the song. Mundiyendere Mbuye Wanga.

  • @MercySKayange
    @MercySKayange 29 дней назад

    Ambuye ndiyendereni👏

  • @BlessingsChilenje-o3l
    @BlessingsChilenje-o3l Месяц назад

    This song eeee imandilimbikisa heavy💪🔥

  • @BerthaChisoni-t3z
    @BerthaChisoni-t3z 18 дней назад

    Zikomo ambuye adzikusogolela ndinyimbo imeneyo imandilimbikisa

  • @Lloyd-gd6pu
    @Lloyd-gd6pu 24 дня назад

    Ambuye sinthani nyengo zanga ndipo mundiyendere ine

  • @docuslungu9127
    @docuslungu9127 Месяц назад

    Nyimboyi yandipasa chirimbikitso Cha chikulu kwambiri

  • @florakunashe4006
    @florakunashe4006 4 месяца назад

    Thank you sister Maggie for this song. Life may seem hard, we may not undertand, but all the things work together for good for those who love christ Jesus.

  • @sunganipakonda8282
    @sunganipakonda8282 4 месяца назад

    Amen ndathokoza kwambiri nyimboyia ndayipeza 🙏

  • @ZelifaMwale
    @ZelifaMwale Месяц назад

    Ndipo ndimadalisika ndi nyimbo iyi

  • @OlayjerempondahMponda
    @OlayjerempondahMponda 4 месяца назад

    Nyimbo yopasa chiyembekezo pa Ambuye

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 4 месяца назад

    Nice message ❤❤

  • @LiahRestoration
    @LiahRestoration Месяц назад

    Yehova mundiyendere 🙏🧎

  • @ForesterForester-g4x
    @ForesterForester-g4x Год назад

    Amen ambuye mundiyendere kuyimba kwabwino

  • @jacqlynpeter5041
    @jacqlynpeter5041 3 месяца назад

    Mundiyendele ambuye

  • @MukhozenjiKalimanjira
    @MukhozenjiKalimanjira 9 месяцев назад

    Imandisuntha kwambiri

  • @naomiewiscot8458
    @naomiewiscot8458 15 часов назад

    ❤❤

  • @MaryChasokera
    @MaryChasokera 2 месяца назад

    Tikakhara ndi chikhulupiliro atiyendera

  • @pacharonyirenda8098
    @pacharonyirenda8098 4 месяца назад

    Mbuye mundiyendere

  • @FortuneKasolota
    @FortuneKasolota 2 месяца назад

    Nice song mama

  • @joycegama2014
    @joycegama2014 4 месяца назад

    THIS SONG KEEPS ME STRONG ALWAYS

  • @ritaelos8181
    @ritaelos8181 11 месяцев назад

    Amen mai busa❤

    • @AnitaNdovi
      @AnitaNdovi 4 месяца назад

      Ndipo bid nyimbo us wimp kwambiri😂😂😂

  • @MphatsoMlotha
    @MphatsoMlotha Год назад

    Amen nic song

  • @omegahbwanali6218
    @omegahbwanali6218 5 месяцев назад

    My favorite 🎉❤

  • @NastanzioNyaka
    @NastanzioNyaka 29 дней назад

    Zilibwino

  • @nalogamagalleta9312
    @nalogamagalleta9312 9 месяцев назад

    🙏🙏

  • @AliceGelevaziyoKhoma-ne6wq
    @AliceGelevaziyoKhoma-ne6wq 8 месяцев назад

    Y