Nyimbo iyiyi yatuluka Iye Atamwalira T. Chibade

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 19 окт 2024

Комментарии • 116

  • @Yabwata
    @Yabwata 3 месяца назад +9

    My my my my best best ❤musician in malawi is thomas chidade not astanic awa ena iyaaz .. miss

  • @REXCHARLESKAJAWO
    @REXCHARLESKAJAWO День назад

    Mwana uyuyu ineyo ndimamufira heavy ❤❤❤,🔥🔥

  • @MartinMisomali-tk5mf
    @MartinMisomali-tk5mf 3 месяца назад +4

    Ine ngat Pali nyimbo zalokolo zomwe ndimavera ndiza Thomas chibade ndipo sindizasiya kuvera paka ndizapite koko

  • @SaviourjamesBanda
    @SaviourjamesBanda 15 дней назад

    Nice music brother I love you❤

  • @francismuwa2535
    @francismuwa2535 3 месяца назад

    Thank you very much. I have been looking for this song

  • @JohnAlexNthulinga
    @JohnAlexNthulinga 3 месяца назад +2

    The best of the very best Mr Chibade the Legend

  • @salafinamhone-rd1ku
    @salafinamhone-rd1ku 3 месяца назад

    Compose a song like Thomas Chibade did and Lucius did these were speaking for Malawians through music, legends never die

  • @MadalitsoIbrahim
    @MadalitsoIbrahim 3 месяца назад +3

    Koma mwati satuma zigawenga zikamugwile chibade kumanda komweko😅😅😅😅

  • @BlessingsChipetuka
    @BlessingsChipetuka 3 месяца назад

    ngati kuli nyimbo zomwe ndimazikonda kwambiri moti everyday ndimatha kumvera×5 ndi big man amenewa koma dziko lapansi RIP my king

  • @CharlesMagumbwa-kp6rt
    @CharlesMagumbwa-kp6rt 5 дней назад +1

    My Legend and my friend continue Rest in peace

  • @phillipchabu6331
    @phillipchabu6331 2 месяца назад

    May his soul continue resting in peace. He was one of my favorite artists in Malawi.

  • @KondwaniNguleti-x1q
    @KondwaniNguleti-x1q 3 месяца назад +1

    My best musician ever may his soul rest in peace

  • @MathewsMacdonald
    @MathewsMacdonald 3 месяца назад +1

    Best song indeed

  • @JoshuaMkandawile
    @JoshuaMkandawile 3 месяца назад

    Always you was in sweet sound Chibade❤❤❤❤❤

  • @ZephMbeleswa-n8m
    @ZephMbeleswa-n8m 3 месяца назад +1

    The best song T chibade rest well

  • @MaharaWuss-kv8rh
    @MaharaWuss-kv8rh 3 месяца назад +1

    Madala hit munapha iyiyi heavy size kukan my his soul rest in peace until we meet again on other side
    Rip Thomas 😭😭

  • @EricBotha-g4t
    @EricBotha-g4t 3 месяца назад

    Very strong messages from our late musician Thomas chibade May his soul rest in peace

  • @josephykwendah2210
    @josephykwendah2210 3 месяца назад +1

    Chibade unali mutu oganiza ❤❤❤❤❤

  • @MoosaSame
    @MoosaSame 3 месяца назад +1

    My best musician ever forgettable continue rest in peace bro

  • @zayedmitawa8345
    @zayedmitawa8345 3 месяца назад

    Best song composer Malawi ever had,RIP Legend

  • @ngozo07
    @ngozo07 3 месяца назад +2

    We shall never have him again,, Legend

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 3 месяца назад +1

    Beautiful song RIP

  • @SimeonAbraham-u2j
    @SimeonAbraham-u2j 3 месяца назад +1

    Very nice song

  • @LuciousKotamu-dh5uq
    @LuciousKotamu-dh5uq 3 месяца назад

    The best song like this one

  • @RichardMdala-ml4hx
    @RichardMdala-ml4hx 3 месяца назад

    Nice song from the lost talented musician.

  • @Senifala
    @Senifala 3 месяца назад

    This man was my best ..even ndigone osadya but kungovela nyimbo zake ndimakhiluta ....like I wasn't having a stress for the food....may his soul rest in peace 😢

  • @JohnChibanda-h6b
    @JohnChibanda-h6b 3 месяца назад +1

    Nice song

  • @JimmyMpinda
    @JimmyMpinda 3 месяца назад

    Best artist

  • @rabisonpias5131
    @rabisonpias5131 3 месяца назад +1

    Chibade was a prophet. And sees from far..!.
    Just that He was attacked by a Satan blindly, and lost the way.

  • @ChimzyChimzy-i9e
    @ChimzyChimzy-i9e 3 месяца назад +1

    He was gone with his talent and wise 😭😭😭😭😭😭

  • @ElizabethKazambwe
    @ElizabethKazambwe 3 месяца назад

    Eishh koma Thomas eishh ayi ndithu imfayi eee ai ine ndikusowa chonena may your rest in peace

  • @Yabwata
    @Yabwata 3 месяца назад +1

    Plz ngati mulinazo tumaniko zinandi plz nyimbo zake uyu

  • @PetroKachingwe-jf7dh
    @PetroKachingwe-jf7dh 3 месяца назад

    Nice song
    Rest in peace

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy 3 месяца назад

    Good massage

  • @RichardBoscco
    @RichardBoscco 3 месяца назад

    Eish chibade continue rest in peace . Ndipo tiika pa repeat

  • @kingnavitcha6243
    @kingnavitcha6243 3 месяца назад

    Awa anali atate pamayimbidwe ur soul may continue rest in internal peace 🕊️

  • @FortuneGwadiyo
    @FortuneGwadiyo 3 месяца назад

    Uyuyu anali captain ndipo mpaka kalekale dziko tidzamukumbukira ,anabwera kuzalankhula chilungamo munyimbo zake R.I.P

  • @EvanceSungani-cv9jk
    @EvanceSungani-cv9jk 3 месяца назад +1

    😢😢😢😢😢 koma infa kutenga anthu otilankhulila😭😭😭😭😭rip legend

  • @FunnyDimSum-hk1so
    @FunnyDimSum-hk1so 3 месяца назад

    Please nyimbo imeneyi taito yake ndi Chan please

  • @douglaskayira8362
    @douglaskayira8362 3 месяца назад +1

    The gap is too huge to be filled..........

  • @davidmumba3543
    @davidmumba3543 3 месяца назад

    Oweyz loving you chinkumba rip

  • @YoweliPhiri-qu6ez
    @YoweliPhiri-qu6ez 3 месяца назад

    Title please nduisake ku Vidmate

    • @CharityChanzah
      @CharityChanzah 3 месяца назад

      Ulendo wa pa ndege mwaononga ndlama zingat

  • @BensonLitta
    @BensonLitta 3 месяца назад

    Nice song ❤❤❤❤❤

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope 3 месяца назад

    Nyimbotu Koma izi osati achina Zeze ndi a jetu ndi ena otero

  • @isaacchirwa9518
    @isaacchirwa9518 3 месяца назад

    Basi moyo ndi choncho, iwo kudwala kupitisidwa ku south Africa, president waku south Africa kudwala kupitisidwa ku Kenya or UK, waku UK kudwala kupitisidwa ku Japan 😮😮😮😮😮

  • @EvanceRazaki
    @EvanceRazaki 3 месяца назад

    Respect Thomas chibade

  • @blessbless6929
    @blessbless6929 3 месяца назад

    Pakanakhalatu mwayi omavota kuti ena amene anafa abwelerenso uyuyu ndikanamuvotera azadzudzulebe komanso Matafale ndikanamuponyera vote. Osati ena amayimba zachamba aja

  • @MacdonardMapala
    @MacdonardMapala 3 месяца назад +2

    Eeeee ayaaa mamamama haha

  • @Mohammed-sk1fy
    @Mohammed-sk1fy 3 месяца назад

    Anapitad km uthenga ndiomwe anatisiyira CHIBANDE again rest in peace 😭😭😭😭😭

  • @LastenWesele-wq8jh
    @LastenWesele-wq8jh 3 месяца назад +1

    👍

  • @ChimwemweMfungwe
    @ChimwemweMfungwe 9 дней назад

    Anali mwana oganiza bho kwmbr km yifaa mulungu yekha

  • @ThokozaniMoyo-v5r
    @ThokozaniMoyo-v5r 3 месяца назад +1

    Aimvere chakwera

  • @StevieKanavent
    @StevieKanavent 3 месяца назад +1

    Luso lanu lizavuta kuiwara Rip Chibade

  • @Kapoloma-qv9gm
    @Kapoloma-qv9gm 3 месяца назад

    Legend

  • @YoweliPhiri-qu6ez
    @YoweliPhiri-qu6ez 3 месяца назад

  • @AmujeMwamad
    @AmujeMwamad 3 месяца назад

    Power 💪💪💪

  • @emmanuelkakhongwe
    @emmanuelkakhongwe 3 месяца назад

    Real men never dies

  • @samuzymkwanya8490
    @samuzymkwanya8490 3 месяца назад

    Uyu analikatundu pa compose

  • @AgnesLapukeni
    @AgnesLapukeni 3 месяца назад

    Uyu anali katundu ndipo dzumuwake uziwusa mutendere 😢

  • @JuliusMandala
    @JuliusMandala 3 месяца назад

    Kod zikutibwanji kumeneko chibade wamwarira aa 😭😭😭😭😭😭

  • @GiftChitsulo
    @GiftChitsulo 3 месяца назад +1

    Chibade tizakulila pakana kale

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 3 месяца назад

    Uyu Anali freedom fighter wachinsinsi guys mzimu wake uwuse muntendere ndithu

  • @Aubreysekeyah
    @Aubreysekeyah 3 месяца назад

    akanakhal moyo akanamumangstu😂😂

  • @ChimwemweGausi-jy3kv
    @ChimwemweGausi-jy3kv 3 месяца назад

    RIP chibade

  • @samuelmabulesse1267
    @samuelmabulesse1267 3 месяца назад

    Chibade chibade 😢😢😢

  • @AmigoSanudi
    @AmigoSanudi 3 месяца назад +1

    Uyu anali oyimba zinangotivuta

  • @PraiseMasinga
    @PraiseMasinga 2 месяца назад

    Rest well

  • @JameMirward-vm4dm
    @JameMirward-vm4dm 3 месяца назад

    Continue Rest well ❤️‍🩹 legend 🎉😢

  • @Symon-v2c
    @Symon-v2c Месяц назад

    Wa bwino sakhalisa pa dziko

  • @djgvBeatz
    @djgvBeatz 3 месяца назад

    rip lengend

  • @dysonmasiye5736
    @dysonmasiye5736 3 месяца назад

    Ndaikonda kwambiri nyimboyi....otsutsa boma simungatiuze zochitanso ai, munali mommo koma matama too much, ndalama munkangowana nokha nokha kukudzudzulani simunkamva. Adad anu aja munawakhumbatira ndipo simunawalole kuti adzimva kulira kwa anthu ena popeza anali adad anu okha lero bwa? Ndiye inunso amene mukulamulira lero mukumatilankhula ngati pamipandopo munadziikapo nokha dikirani muone zomwe zichitike next year, mutiliratu inu. Ife timaika atumiki pa mipando komanso kuwathotholapo akamatitenga ngati ife ma zoba...Pano muli busy kumatiopseza dikirani muone zomwe tikupangeni 2025. Tikkapo ena omwe alibe mifunda ndithu...

  • @BrendaEnerst
    @BrendaEnerst 3 месяца назад

    koma umu munali chilungamo chanyoooo eee rip 😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @medicoastkzn
    @medicoastkzn 3 месяца назад

    Abwino sakhalitsadi mzimu wake uwuse mumtendele

  • @JummaGhama
    @JummaGhama 3 месяца назад

    Rest piece my legend

  • @RodneyWandani
    @RodneyWandani 3 месяца назад

    Yoooooooooo

  • @cacksygustarf6260
    @cacksygustarf6260 3 месяца назад

    RlP dolo💔😭

  • @StazioChitsulo
    @StazioChitsulo 3 месяца назад

    Continue rest in peace Legend 🩸

  • @Jozdee
    @Jozdee 3 месяца назад

    😢😢😢😢

  • @yusufbakali
    @yusufbakali 3 месяца назад

    It's true

  • @solomonphiri6336
    @solomonphiri6336 3 месяца назад

    Crip chenkhuma

  • @sayidimisessa
    @sayidimisessa 3 месяца назад

    Nzimu wa Thomas R,I,P

  • @mailos.laisoni7001
    @mailos.laisoni7001 3 месяца назад

    Rest peace bro

  • @randettaclaan
    @randettaclaan 3 месяца назад

    abwino sakhalitsa pa dziko MYSRIP

  • @eliaskhumalo
    @eliaskhumalo 3 месяца назад

    😭😭😭😭😭 RIP CHIBADE

  • @JamesOsman-cz9cw
    @JamesOsman-cz9cw 3 месяца назад +1

    😢😢

  • @timothylipenga8413
    @timothylipenga8413 3 месяца назад

    IFA sithawika gulani makhwala muike mzipatala

  • @HamiltonwaNamuwah
    @HamiltonwaNamuwah 3 месяца назад

    Anali akatundu awawo ndithu

  • @PeaceMaker-p6j
    @PeaceMaker-p6j 3 месяца назад

    Very sad

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson1443 3 месяца назад

    RIP MR CHIBADE

  • @BlessingsChunga-hx6cv
    @BlessingsChunga-hx6cv 3 месяца назад

    Muli uthenga

  • @HallimaMakwinja
    @HallimaMakwinja 3 месяца назад

    Ulemu wanu Achibade zoonadi uthengawu ndiwazoodi big

  • @dysonmasiye5736
    @dysonmasiye5736 3 месяца назад

    Daily tikumaluza anzathu a luso eish...

  • @NOVABOUY
    @NOVABOUY 3 месяца назад +1

    ANTHU A LUSO ANALI OMWEWA NDITHU

    • @wittinessnkhokwe
      @wittinessnkhokwe 3 месяца назад

      Zoona boss nt ati gibo lantos ndiye ndaniso kaya

  • @SinetLapuwa
    @SinetLapuwa 3 месяца назад

    Iyi nde ipite kwa pule

  • @ChilekaMoyenda
    @ChilekaMoyenda 2 месяца назад

    R lp

  • @nditumenichagunda4192
    @nditumenichagunda4192 3 месяца назад

    Rip

  • @JuliusMandala
    @JuliusMandala 3 месяца назад

    Ngati zatero kurira kwanga kosarekeza

  • @SamuelChalire
    @SamuelChalire 3 месяца назад

    Ndi

  • @bandacharles82may
    @bandacharles82may 3 месяца назад

    Palibe amayikidwa kumwamba tonse timayikidwa nthaka

    • @AmossAkbar-bt1ks
      @AmossAkbar-bt1ks 3 месяца назад

      Mawu akulu awa ndithu, anali wachikulire chibade

  • @JosephyGeorgejanuary
    @JosephyGeorgejanuary 3 месяца назад

    Nice song