Palibe mfundo yomveka amtanyiwa tamapangani zanu basi man kapena Muli pa ganyu paja ee Ndawonaso kt banja lanu lidye ndekut mmawa uliwonse mwabwebweta, mbuzi
Awanso nde kaaaya koma akuluakulu enawa ndevu ali nazo koma? Antanyiwa zoti Saulosi ndi amene adawasankha a usi to be his vice mutu mwanumo zilipo koma? Misonzi yaboza imeneyo aaaaaa kulira kwa umbuli kumeneko? Mizimu 9 mukuyinenayo ndiimene yayamba kukantha achina kaliati ndazinzaeo kkkkk
Kodi akumbumbawo alibe maso ndimakutu? Mukuona ngat mrs skc sakumudziwa Usi? Bwanji mukuwachitira zinthu kampeni yanu basi imfa ya chilima? Kodi mfundo zotukulira dzikoli ndikumangokamba za imfa ya skc? Tapedzani mfundo zoti anthu amve kuti dziko lizabwelera mchimake.. sizolimbana ndi a usi zo apa
Usi is still a member of utm ,sanatulukepo utm iweyo ntanyiwa ndiwe chitsiru paja ndiwe osaphunzira chifukwa chake ukukakamila zopanda mutu
Km nkhan yokhunza kutenga maguyz achipani amayenela kuziyendesa bwino koz ngt ukuzisata bwino bwino team yomwe yawina ku convention iyo imakamba zokut alliance inatha ndie kt palibeso chokhalila pamodzi mcp nd utm
Mtanyiwa ndigalu kwabasi mumuwuze komwe ali. Kunamiza aMalawi kuti Chakwera wamwalira. Mtanyiwa akapelekele zangozi yandege. Osangotchuka pa social media
Kwa ineyo i just believe kuti what goes round shall comes round not matter what ? Full stop pati
Iweyo ntanyiwa ndiwe uli ndi vuto usi is right bcoz he is a member of utm
God Have Mercy On Malawi 🙏🙏
Usi ndi mfiti wangokalamba koma alibe mzeru. Mulungu akukuonani Mr Usi ndipo akukanthani
Micheal Usi , Yudasi . No umunthu , no manyadzi and cowered
Iweyo nde ukusowa zochita antthuwo akumukonda usi yo😊
Galu wacchabe chabe mtanyiwa
Zazi😅 kabambe wachotsatu nkhope ya chilima
Koma ndiye atanyiwa boza muzareka liti manyazi bwa muzingoti mawa mwanena ichi mukuna aliyese avotere yomwe inuyo mwafuna ?satana ndinu mukuonanga dziko ndimaboza anuwo amalawi akutulukani naniso munasankha chipani chani aliyese Ali ndi Chisankho chawo topani atanyiwa mwayamba ndikale
Galu iwe mtanyiwa usasocheretse athu.. usi is UTM member and there is no problem kuonesa makaka ake..
Iwetu ukuoneka ngati utha kukhala savage oyamba pamasavage onse Ali kumalawi kuno
Savege ndi usi ngati usi anali ndi nzeru bwanji anakana kupita ku Coveshoin kuti akawine ngati anali mamuna ukuu ndiye kudzedzedukandithu
Good idea from Ntanyiwa!!!! Research Usi's PHD, BUT BEFORE THAT, RESEARCH YOURSELF FIRST!!!! "Who is Ntanyiwa ?"then " Who is Usi???"
Palibe mfundo yomveka amtanyiwa tamapangani zanu basi man kapena Muli pa ganyu paja ee Ndawonaso kt banja lanu lidye ndekut mmawa uliwonse mwabwebweta, mbuzi
Ndipo chitsiru chake chomwa madzi ometeratu, chomagwirisa ntchito makaka A UTM pa Za MCP ndichani ? Wasala pang'ono chinachake chimuchitikira Amenei sure 👌
Mulungu wake satana anganve zantanyiwa😢😢😢
Wamabodza unatinamiza kt chakwera wafa nanga uyu akuyendayu ndi mzukwa? Kape iwe
Kkkkkkkk ndiwe wa DPP ???
Corad ntanyiwa mofaya uchitsiru wa amicre usi anautenga pamene abambo ake mdi amake amkapanga zila lake chikhala kuti anadziwa kuti mwanayo adzakhala chitsilu chochi bwezi atango taya
Awanso nde kaaaya koma akuluakulu enawa ndevu ali nazo koma? Antanyiwa zoti Saulosi ndi amene adawasankha a usi to be his vice mutu mwanumo zilipo koma? Misonzi yaboza imeneyo aaaaaa kulira kwa umbuli kumeneko?
Mizimu 9 mukuyinenayo ndiimene yayamba kukantha achina kaliati ndazinzaeo kkkkk
Amen Ntanyiwa
Kodi ntanyiwa ulimbalitiii Ada?
Uwu ndiye uchisilu, Kom. Manganya chimutu chachikulucho
i believe now, kut mr ulis umunthu ndiwochepa, becoz munthu wopa mulungu amakhupira chimene uli nacho.
Back to sender
Usi is still a UTM member so kuvala nsalu ya chipani chake palibe vuto. Uchitsilu wanuo muzikauza anthu osaphunzira azako Galu iwe mxiiii
Ambuye onesan phamvu yanu pa zomwe akuchita usi nd chakwela
Uyuyu Ali mgulu la chikangawa chikumusangaratsa ndi chiyani
Ndipo Mai usi ndiokondwa ndi ifa ya chilima tonse tadzionera amalawi
Ussi is the educated savage, embicile
Iwe usi anakuwuza kuti atuluka mu UTM naweso ufuna ku ntchuka
Umasowa zochita kumalimbana ndiusi uzipangazako
Kodi iweyo chikukukhudza ndichiya kapolo iwe ulimphamvu zoyimitsa munthu chitsilu
Iwe wa DPP chikukukhuza ndi chani ku utm kkkk
Kodi akumbumbawo alibe maso ndimakutu? Mukuona ngat mrs skc sakumudziwa Usi? Bwanji mukuwachitira zinthu kampeni yanu basi imfa ya chilima?
Kodi mfundo zotukulira dzikoli ndikumangokamba za imfa ya skc? Tapedzani mfundo zoti anthu amve kuti dziko lizabwelera mchimake.. sizolimbana ndi a usi zo apa
Ndiwe mbuzi
Zomvesa Chisoni 😢
Ndimfiti ameneyu
Iweyo osaphatikila
Usi Rest in peace
Usi wachita njengunje
Cadet iwe
Anthuwo ndi omukonda michael Usi, kungoti mmutu mwanu akulu munadzadza congress. Ndipo wakuyankhani kuti udindo alibe nawo ntchito.
Ukulakhura zinthu zopanda mutu
Usi ndi mfiti chimunthu choipa kwambir zausatanic basi
Michael usi ndi galu