A JOYCE BANDA KUING'ALULA KOMALIZA 7 September 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 16 сен 2024

Комментарии • 59

  • @mohamudmohamed2714
    @mohamudmohamed2714 3 дня назад

    ❤❤❤❤ mashaalah kofunika ndithu

  • @Vascomw
    @Vascomw 9 дней назад +2

    Aaaaaa zaziiiii mayi wopusa uyu za anagulitsa dege

  • @Mustapher-fb4qp
    @Mustapher-fb4qp 9 дней назад +3

    Grece chimga anati kubwera chipani chamwazi mai njoice d chakwera buchillll

  • @Mem21mem
    @Mem21mem 9 дней назад +1

    PP my Vote

  • @AnorldKamponda
    @AnorldKamponda 8 дней назад

    Akabaza nde zichani so aaaaaaa aaa.

  • @masoyaonamunkhondya9074
    @masoyaonamunkhondya9074 6 дней назад

    Just unite with UTM , forget about the past forward shall be gain by Malawians

  • @JohnFrank-cg1yh
    @JohnFrank-cg1yh 8 дней назад

    Madam joice banda,bwanji summulangiza chakwera zinthu sizikuyenda iye angoyendayenda kumaononga ndrama anthu akuvutika

  • @thomaschipinda6952
    @thomaschipinda6952 8 дней назад

    Ati funani wina, ine ndi ndani kuti ndikane, za ziiiii

  • @juniortsegula3847
    @juniortsegula3847 9 дней назад +2

    Mai ofoyira uyu. Kugulisa ndege ya new one kusiya yokutha yomwe yatiphera abale athu😢😂

  • @MveraNambala
    @MveraNambala 9 дней назад +1

    Hiyaa kangoneni mai kwanu munachita kapumeni

  • @georgeraphael8198
    @georgeraphael8198 8 дней назад

    Mai oyipa mtima,kupha,kuba,kwa nthawi yochepa dziko linaonongeka

  • @EdsonChiwereChieere
    @EdsonChiwereChieere 9 дней назад +1

    Mcp my vote 😂😂😂😂😂 mulirad chakwera mumuva kuwawa anthu aulesii inu alomwe 😂😂😂😂

  • @christophermandala1840
    @christophermandala1840 9 дней назад

    Ankakuvotereni ndani mfundo zake zimenezo?

  • @gwatandingo9502
    @gwatandingo9502 6 дней назад

    Zilibwino kwambili mama😂😂😂😂

  • @GodfreyKampezeni
    @GodfreyKampezeni 8 дней назад

    Mesa munari limodzi

  • @GiftSoko-w4h
    @GiftSoko-w4h 9 дней назад +1

    Koma nyumba ndiye munamangadi mama to be honest may God bless you

    • @ThokoLungu-tq6pw
      @ThokoLungu-tq6pw 7 дней назад

      Zoonadi munthu sakoma zonse kma Joyce mmm amaesesa than chikangawayi iiii

  • @KikaImran
    @KikaImran 8 дней назад

    Zoona kuzitama kugwetsa kwacha? Bingu was agreat leader ever.

  • @NikolasNanawe
    @NikolasNanawe 8 дней назад

    pp my vote 🗳 ❤❤❤

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e 9 дней назад +1

    More fire 🔥 ❤❤😂😂

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 9 дней назад +1

    Mai ife tikufuna economy yochita attract investment mdziko osati zogawa chimangazo.tikufuna ife a Malawi tidzidzathandizanso maiko ena ndi chimangacho.osati kumatiuza za zaulere

  • @FloraMweza-u7y
    @FloraMweza-u7y 9 дней назад

    Tisamveso kuti mwagwirizana ndi chikangawa pls yimirani panokha mai

  • @KikaImran
    @KikaImran 8 дней назад

    Unite with DPP Malawi akuwawa uyu ee, zinthu zakwera, inu mama munakweza salary mwamphavu

  • @LobertSamuel
    @LobertSamuel 9 дней назад

    Mesa kodi mumalamulira nonse

  • @BrianMuleke
    @BrianMuleke 9 дней назад

    Azungu akuti! kkk

  • @Kabwilachikangawa
    @Kabwilachikangawa 9 дней назад

    KOMA AMAI AWA MXIEWWWW

  • @JustinLipipa
    @JustinLipipa 9 дней назад

    Mmmmmm anali limodzi ndi Chikangawa, anthu awa ndamene akuononga Malawi.

  • @AnorldKamponda
    @AnorldKamponda 8 дней назад

    Kodi Mesa akuti nanga zotukwana ai? Kkkkk Mai uyu anamila basi

  • @HappinessKapombeza-ut9mo
    @HappinessKapombeza-ut9mo 9 дней назад

    Pepani MAI JOYCE BANDA,Kodi dzumvekazi ndizoona?😞😞😞😞😞...

  • @BennettNjedza
    @BennettNjedza 9 дней назад

    Fundo zabwino zedi

  • @Felix-j3f7y
    @Felix-j3f7y 9 дней назад

    Akulankhula kwa oduka mitu anzake. Kuyamikira kugwetsa kwacha? Cash gate ija sakukambako bwa?

  • @MusaLion-os1lx
    @MusaLion-os1lx 9 дней назад

    Koma amai mutsamakambe zakale takambani zapanopa chifukwa mukukhala ngati simukuwona bwanji inuyo ndi A MCP paja tisamale naye uyu guy

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480 9 дней назад

    Tiwona zithu next year 😂😂

  • @user-qh2sl4tw4b
    @user-qh2sl4tw4b 9 дней назад

    Koma kusisa marata osati kumagira athu

  • @Blessings-b7h
    @Blessings-b7h 9 дней назад

    Palibe cha mzeru chomwe mungauze mtundu wamalawi mkuvera fundo zanu.Inunso ndi panja penipeni ndipo ndalama zomwe mwapangira msonkhano umenewo mwachita kupatsidwa kuchokera ku mcp.

    • @BrightZionga
      @BrightZionga 9 дней назад

      Kkkkkk chilungamo ndi mwano

    • @user-wl4nd7ic1s
      @user-wl4nd7ic1s 9 дней назад

      Ndipooo this country being ruled by mzimayi, forget about thatt, the Malawians can't do it again that mistake!!

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 9 дней назад

    Zapanga in ndi chakwera mm xandinyasa, pan ndikuyembekeza bpp utm ,afodi not pp

  • @GodfreyKampezeni
    @GodfreyKampezeni 8 дней назад

    Chipani chokuba

  • @FatsaniYusuf
    @FatsaniYusuf 9 дней назад

    😂😂 awaaa ndie ayi

  • @MonikaDArabie
    @MonikaDArabie 9 дней назад

    Cash gate ina bweretsa mkw 1000 malawi akubaso inu ngati mcp

  • @user-gs9vr1lc9d
    @user-gs9vr1lc9d 9 дней назад

    Kulimba mtima kokabanako ndalama CASH GATE

  • @Chilinga_P
    @Chilinga_P 9 дней назад

    Unagulitsa ndege iwe nkusiya ndege yakutha yomwe inatiphera wathu uja....
    Palibe chanzeru kumadzudzula MCP pakuti ukudya nayobe...
    Nkhani yopempha kuli mnzako Usi nayenso ati amatha kupempha...
    Anyway, you don't love Malawians... forget about becoming a president even in times of accidents...

  • @LutMgogodo
    @LutMgogodo 9 дней назад +1

    Awa akufunika saport basi pawonkha sagawine

  • @bisweckchimphamba8497
    @bisweckchimphamba8497 9 дней назад

    Your speech seems like you're attacking Peter Munthalika,osamunena nzako amene akulamulira panoyu bwanji

  • @patrickkapinga7091
    @patrickkapinga7091 9 дней назад

    Cash get tawonera paiwe simungawine or mutatani mesa unali kwachakwera sibasi mwabwerako

  • @RaphiqueYusuf
    @RaphiqueYusuf 9 дней назад

    Osati mbutuma zinazi nkhalamba zikuwonekazi,tikufuna azimayi olimba mtima ngati ameneyu, amunanu tatopa nanu.

  • @RodwellChisambo
    @RodwellChisambo 9 дней назад

    Mayiyu palibe chomwe angathandidze kudziko lamalawi she don't have economic wisdom ndipo she is fundoless

  • @user-wl4nd7ic1s
    @user-wl4nd7ic1s 9 дней назад

    🤣🤣 Your speachh is full of emptyness!

  • @thomasmcbanda9794
    @thomasmcbanda9794 9 дней назад

    Ndipo osamukhulupilira maiyu akungopusisa amalawi pp ndi MCP azagwilizana anthuwa kuvotera pp ndekuti wavotera MCP beware maguys

  • @LobertSamuel
    @LobertSamuel 9 дней назад

    Mesa kodi mumalamulira nonse