BON KALINDO LERO KUING'ALULA __30 December 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 2 янв 2025

Комментарии • 102

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 3 дня назад +2

    Asafuna asiye kkkkk born kalindo alibe nazo zoti ky ndiwe ndani kwanu Koko

  • @OwenMindozo
    @OwenMindozo 2 дня назад

    Hon. Bon Kalindo, please do not afraid lot, God is with you through His son Jesus Christ.

  • @MdalaBonomali
    @MdalaBonomali 3 дня назад +4

    The DC number one❤❤❤❤❤

  • @MayamikoPangani
    @MayamikoPangani 4 дня назад +3

    Fire mabomba😂 Booon kalindoooo

  • @JacobMsukwa-q6v
    @JacobMsukwa-q6v 3 дня назад

    I can not sleep without submitting my comment😂😂but anywa these guys nthaw yawo yatha

  • @JosephKasiyeni
    @JosephKasiyeni 3 дня назад +2

    Go ahead Mr Dc

  • @NelsonSingano
    @NelsonSingano 2 дня назад

    Alinyodoooooo❤

  • @HassanBabujr
    @HassanBabujr 3 дня назад +2

    Ukali wanu The Dc❤❤❤❤

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl 3 дня назад +1

    Respect u Mr Born kalindo 🔥🔥

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 3 дня назад +3

    *iweyo ndi hero koma DC❤*

  • @Mirriumkamwendo
    @Mirriumkamwendo 3 дня назад +3

    Kkkkkkk nde ati akuukusakani inuyo kuti mwalakwa chani

  • @BeatriceProfessor
    @BeatriceProfessor 3 дня назад

    😂😂😂😂koma manganya ngati mwana wakhanda zochitika zake ati Anitana ati ndipite ku L,L ati ndikayakhe mulandu ine sindipitako 😂😂😂😂🙌🙌🙌🙌🙌🙌

  • @BrightenBilly
    @BrightenBilly 3 дня назад

    Umakwana Bon Kalindo. Uwakumbusenso kuti JCE ya a Chakwera ilibe Certificate, ma Certificate a JCE sakupangidwanso. Akungozunza ana kulipira ya JCE Certificate kulibe.

  • @DanielKandiero
    @DanielKandiero 3 дня назад +2

    Ulemu wanu uncle

  • @ChrissyScot
    @ChrissyScot 3 дня назад +1

    Go ahead Mr Dr

  • @GabrielJosua-r2y
    @GabrielJosua-r2y 4 дня назад +1

    Muthu wamnkulu Yehova mwini zonse mphavu ndi zolengedwa zakumwamba ndi dziko lapasi akutetezeni kukupatsani mavumbulutso ndi masophenya akuunikira dziko lanthu.Jehova akupatseni moyo wamphavu ndi wautali. Amen🤍🤍🤍🕊️🕊️🕊️🐫🐫🐫🐘🐘🐘🕺🕺🕺💪💪💪💯💯💯🙏🙏🙏

  • @JerrySaliwa
    @JerrySaliwa 3 дня назад +2

    Good man ❤

  • @AshraffMachika
    @AshraffMachika 3 дня назад +3

    The DC🤘🤘

  • @MaureenNgoma-p7l
    @MaureenNgoma-p7l 3 дня назад

    Nzake wa winoko 😂😂😂😂

  • @DadTshepo
    @DadTshepo 3 дня назад +1

    Mwana Owopsya kwambiri From Njeza Village TA Mabuka Box 76 Malawi Southeeeeeeeeeern Africaaaaaaaaaaaaaaaaaa

  • @DadamdokoEvancemkandawire
    @DadamdokoEvancemkandawire 2 дня назад

    DC ngat uyo ndizani mkanayamba kumsina khutu before kummenyera pa galu chifukwa mkaz sa minyera pa gulu ndiye usi uyo myakhurane ngat mzanu

  • @Harrychokanda
    @Harrychokanda 4 дня назад +4

    Zoona the DC....mmalo molimbana ndi ma real issues... manyaka a govt

  • @BenjaminKapale-k1f
    @BenjaminKapale-k1f 3 дня назад +1

    zimenezi ndizitsilu kwambili ma plan awo kumangoganiza zopha anthu basi pam.nya pawo

  • @Rab2sope
    @Rab2sope 3 дня назад +1

    Awa ngamisala the good thing aliyense akudziwa

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 4 дня назад +2

    Tatulutsani ndodo DC muwakutumule anthu amenewa afika pokwana

  • @YamikanimboweJay-t6l
    @YamikanimboweJay-t6l 3 дня назад

    Chopusachi hahaha ufuna chani akupase chani kkkkkkk fundo zakutherani pitan mzikalima inu

    • @MoosaChirwa
      @MoosaChirwa 3 дня назад

      😅😅😅😅😅iwe ndiye ovesa chisoni Moti ungafane ndi kalindo iweyo

  • @SimonChuungula
    @SimonChuungula 3 дня назад

    Always behind you
    The DC

  • @JrAlfeoLungu
    @JrAlfeoLungu 3 дня назад +1

    Kkkkkk ndipo Michael Usi ndi chisilu

  • @JosephyKadenga
    @JosephyKadenga 3 дня назад +1

    Koma ukooooooo!!!!!!!!!!! anthu atha mapulani awa angogwidwa

  • @AlicePondani
    @AlicePondani 3 дня назад +2

    Great man

  • @BrightNdau-q7o
    @BrightNdau-q7o 3 дня назад

    A Usi akutisokonezatu bwana DC auzeni the truth,convention adakana pano akunyoza UTM this is not good bwana DC

  • @Maxielyies
    @Maxielyies 4 дня назад +5

    That's our president the Dddddd Cccccc, proud of you always ❤❤❤❤

  • @WilsonMbendela
    @WilsonMbendela 3 дня назад

    Kayekaye

  • @JulietMunthali-g9b
    @JulietMunthali-g9b 3 дня назад

    Bravo kalindo😂😂😂😂😂

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 3 дня назад +1

    Ine ndimanva bwino kwambiri ndikamanva kuti MCP ikugawanikana.

  • @SulaimanaFelix-r2k
    @SulaimanaFelix-r2k 3 дня назад

    Kkkkkkkkk auzen agaluwo ndi anyanio

  • @ZameersurathAnnubi
    @ZameersurathAnnubi 3 дня назад +1

    Ndipo ngati malawi muno muli munthu opanda zelu kumatiso bola wamisala ndiye ndi manganya pasana pake mbudzi

  • @andreabanda7838
    @andreabanda7838 3 дня назад +1

    Ngati anthu akukana report ya ma commissioners, kodi ma elections a September,
    a Malawi azalora?

  • @MariaDandazaraJSDmoio2024e
    @MariaDandazaraJSDmoio2024e 3 дня назад

    Tikukudziwitsani kuti kumeneko kuli munthu anabela mavoti kuno ku mozambique monu ndiye wathawila kumeneko chonde chonde chonde akuno amutsatila mumuyanganitsitse

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 3 дня назад

    Ngati chigawenga cho, chakwela yo atafike 2025,tikunena pano, Mozambique ili mu seu kuthana naye chakwela yo awona nyenkhwe,

  • @JeneaSambo
    @JeneaSambo 2 дня назад

    Ndipo ndimamkonda koopya

  • @AlexanderYovatiKhumalo
    @AlexanderYovatiKhumalo 4 дня назад +1

    Kuchokela 1st January to 31december mau omanga osapezeka eeee.

  • @Alexchinangwa-k2q
    @Alexchinangwa-k2q 2 дня назад

    ulemu wako boss

  • @elishabanda1332
    @elishabanda1332 2 дня назад

    Awa awa bwampini wa munthu

  • @BlessingsBanda-w1s
    @BlessingsBanda-w1s 3 дня назад

    Koditu muwaonesese, sakufuna kumaononga ndrama coz they know kuti akugwa next year, nde akusinira ndrama kuti mwina azizatuluka Ali ndi kanthu

  • @Rab2sope
    @Rab2sope 3 дня назад +1

    Munthu uyu akuganiza ngati mumutu mukuyenda manyi

  • @HanifuRashid
    @HanifuRashid 3 дня назад

    Bon kalindo bho bho😅❤

  • @AlexKaunda-w7l
    @AlexKaunda-w7l 3 дня назад

    Mmmmmm chimanga 70.000 kwacha chakwera nyini yamako

  • @timothylipenga8413
    @timothylipenga8413 3 дня назад

    Mvura amabweletsa ndi mulungu

  • @MaryJamali-w7t
    @MaryJamali-w7t 3 дня назад +1

    Agwa nayo chakwera galu ameneyo angowutula udindo Pasi akapitilize kugwila tchito chipitu

  • @Andy20247
    @Andy20247 3 дня назад

    Boss mwauze kuti ku Mozambique anthu akuyenda khomo ndikhomo ya anthu omwe amapanga chipongwe

  • @GoodceeDehkasongoh
    @GoodceeDehkasongoh 3 дня назад

    umakwana boni kalindo

  • @IbrahimDailes-j6y
    @IbrahimDailes-j6y 3 дня назад

    Aganiza bwanji zimenezo pomwe anthuwo ndi akupha afiti mwawuzeso akatenge anthu 9 aja awadyetu.timakunyadila mr dccc always.

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 3 дня назад +2

    The DC Bon kalindo number one

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 4 дня назад

    Ondiuza ndiye analipo Koma kusamva nkutu mwanga .

  • @shareefrabison6269
    @shareefrabison6269 3 дня назад

    Umakwana iwe bg mn

  • @Leelee23-e3i
    @Leelee23-e3i 3 дня назад

    As much as there's substance in some of his audios. But why does he keep on endorsing war after elections?😢

    • @symoldicky
      @symoldicky 3 дня назад

      is endorsing war or predicting acording to what is on the ground.kkkkkkk if u have little knowledge about something its better just to use eyes only

  • @RONALDTCHAUYA
    @RONALDTCHAUYA 4 дня назад +2

    Boooooon Kalindo

  • @MussaAli-h4i
    @MussaAli-h4i 4 дня назад +1

    The DC mwana oopsa kwambili

  • @LeonardMbackie
    @LeonardMbackie 3 дня назад

    ❤❤❤

  • @BORNFACESIMBOTA
    @BORNFACESIMBOTA 4 дня назад +1

    Mmmm mcp yathadi maplan

  • @Maxcarcare-g1d
    @Maxcarcare-g1d 4 дня назад +4

    The DC on fire 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 4 дня назад +1

    Zipi yapani kodi kkkkk koma.

  • @JohnMatick-s7l
    @JohnMatick-s7l 3 дня назад +1

    Koma nde satana wawafulamira mmmmmm dziko lapans mvura yasoweratu chimanga chikuuma mmunda

  • @EssauChimpango
    @EssauChimpango 3 дня назад

    Mbambande

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 3 дня назад

    Boma Chimanga likugawa tonse tikuwona ngati Pali nkhani zina za ndale tikumane pa ground

    • @AlfredNazombe-me2ly
      @AlfredNazombe-me2ly 3 дня назад

      Iwenso ndimakusaka kwambiri ndikuthyo Khosi dikila

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj 3 дня назад

      @AlfredNazombe-me2ly panyapako wava ungandisake ine uzifusa zaine

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 3 дня назад

    Chasowa choyankhula akalindo

  • @RaphaelMaunde
    @RaphaelMaunde 3 дня назад +2

    Lilongwe Likuni chimanga chafika K 80,000 ......K 8,000 pa bigiri

  • @Andy20247
    @Andy20247 3 дня назад

    Mzache wa winiko ndalama zamutseka mmaso ndi mmakutu

  • @BazukaChikungaM23
    @BazukaChikungaM23 3 дня назад

    No comment kkkk

  • @MagretMatemba-r7x
    @MagretMatemba-r7x 3 дня назад

    Apenga misala amenewo kkk apule

  • @elishabanda1332
    @elishabanda1332 2 дня назад

    Bodza la munthu

  • @MagieJames
    @MagieJames 3 дня назад

    Inuyo mayankhula chilungamo DDP osainamizile agalu awa akusowa zochita kd DPP itha anthu awa chifukwa chiyani ayaluka chikangawa party

  • @NafeChongo
    @NafeChongo 3 дня назад

    Kod Mesa iwe the DC u was also one of the pipo umat boma lachakwera lizakhala lokoma kwabasi fertilizer tizagula 4. Chakut uli Munda iwe

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 4 дня назад

    Boni Huma kwana kwambili nakunyandila

  • @AdyasiMaulana
    @AdyasiMaulana 4 дня назад

    Tamuwuzeni mwina akuvelani ife talephela kumulangiza mwina nama drama zanu akuvelani

  • @AlexKaunda-w7l
    @AlexKaunda-w7l 3 дня назад

    Sule man ndi akamuna enao ndi atulo

  • @herbertchimwaza-h5b
    @herbertchimwaza-h5b 3 дня назад +1

    The DC

  • @ziyamporoma377
    @ziyamporoma377 3 дня назад

    Mmmm a winiko its you thats seeking relevance ma audio daily opepera okhaokha....galu owuwawuwa saluma aise 😂

  • @TotelaMatenje
    @TotelaMatenje 3 дня назад

    Kuno chafika 80000

  • @MagretMakunie
    @MagretMakunie 3 дня назад

  • @ThomasJossam
    @ThomasJossam 3 дня назад

    The Dc

  • @KazembeFoster-jw1ww
    @KazembeFoster-jw1ww 4 дня назад

    Boss

  • @MaxyMaida
    @MaxyMaida 3 дня назад

    Fader dc

  • @LetiKasusu
    @LetiKasusu 4 дня назад

    Tikapuma kumwamba

  • @JustinGosten-i5m
    @JustinGosten-i5m 4 дня назад

    Iyoooooo

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi 4 дня назад

    Tazionadi🙌

  • @ProsperNdrew
    @ProsperNdrew 4 дня назад

    Kkkkkkkk koma winiko umandisangalasa🎉

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 4 дня назад

    Chakwera ndi munthu oyipa kwambiri

  • @Andy20247
    @Andy20247 3 дня назад +1

    Mzache wa winiko ndalama zamutseka mmaso ndi mmakutu

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 4 дня назад

    Boni Huma kwana kwambili nakunyandila

  • @RajabAssan
    @RajabAssan 3 дня назад

    The DC