I dont know why Malawi has never recognised Chitsitsimutso Choir in a Special way.This choir can sing and knew this Choir when i was in Primary School tikuonera Music Splash mma 2005 if not 2006.Respect to this Choir and Rest well Vice President and the 8 others❤
Very touching song. My prayer that one day we shall know the truth about it. God saw everything what was happening in Chikangawa. Continue Resting Internal Peace. Biyeni
May God richly blesses you. I don't understand the message but the lyrics are good. May God intervenes in the death cases a d if there are foul play He Will revenue whoever are the culprits. Madam Chilima and the family may you be healed in Jesus's name. Jesus is the husband of the widows He will comfort you.Amen ❤
It's my prayer that the truth should prevail and that our Lord God should show us his Majesty by showing us the truth about this dead,,,,may the soul of My beloved Dr Chilima rest in peace!!!
Iwe chifunga Kodi ukuyimva bwino nyimboyo akuti siku lako likazakwana anthu oyamba kukawaona ndi achilima pamozi ndi anthu awo koma ndiye zikoli urinva kuwawa.mulungu akukantha no secret under the son
😭😭😭😭😭😭 Im a Zambian but i still don't understand this death, Sometimes i want to distract myself from thinking about it but reality just dawns in on me that Chilima and 8 others are no more... MTSRIEP 😭😭😭😭😭
Ndine mmodzi wa nkazi wa munthu ofuna kuimira MCP koma tikakumbukira imfa ya Chilima iii ndipo ntima umawawa... Zidalakwika. He was giving a true definition of opposing ndipo true multiparty kukoka achinyamata. Pano tukonda ndale kamba ka Chilima. Anatizindikilitsa kayendedwe kadziko. He had a vibe. Ndale zinabalancer bwino. Osati kumakhala odziwadziwa kuti owina ndi awa noo it was true mpikisano eish. RIP SKC
Amene tikuyembekezela winawake kuti Mulungu amulange,tizikhumudwa kuona kuti ali innocent pamaso pa Mulungu,don't judge when you haven't been told by God what really happened.

What a wonderful tribute song.
May their Souls continue Resting In peace
Zoona. Tsiku lina dzuwa lizawala. Ndipo chifunga chimenechi chizasukunuka. Chilungamo chizaziwika. Pomwe zonse zizakhale pambalambanda.
Chifunga adzimvele mtolo…… lovely song
Koma ndiye 💔💔💔💔😭😭😭
Achifunga inuyo ayi zikomo
Mourning with you our neighbours.
CK, Zambia.
Amen is great song God bless this choir
Choir iyi amene yatisangalatsa bwerani pano
😭😭😭😭😭😭
Very powerful message oone day the sun will shine and the mist will go with darkness..,Amen
Very touching song. My prayer that one day we shall know the truth about it. God saw everything what was happening in Chikangawa. Continue Resting Internal Peace. Biyeni
Aameen 🤲
Powerful Tribute for His Excellency Dr Saulos Chilima ,May his soul Rest in peace 😂😂😂😂😂😂
Best of the best Tribute song.. May the soul of our beloved Veep Rest in peace 🙏
....madandaulo apite kwa iwe chifunga mmmm mwayimba!This is great choir...May God bless this choir n song😭
😢😢😢
Mulungu amayankha msanga pemphero losweka mtima anthu tonse ndife osweka mtima ndi imfa yachilima Mulungu atichotsera chifungachi😢
Very interesting song......I'm very touched....
I love this choir adzakunguka time is coming
Mmmmmm this choir can sing . Chifunga nice tribute. RIP veep
May soul rest in eternal peace. Choir you are nailed it. Explained it in the song. Indeed zipite kwa chifunga
The vocals reminded me of kaliati ndi m'nzake ku mabvuku ccap, Harare, Zimbabwe in the 80's.
Zikomo
Amen Amen
Chizakungunuka tsiku lina chifungachi Mulungu si munthu
Kulira kwathu zipite kwayiwe chakwera!!!!😢 ngakhale watasa iwe pamalawi pano komabe tsikulina uzamusatila chilima 😢😢😢😢
Every one is crying.this is a nice song.
😢😢😢😢 for us who are still in denial. Let's gather here 😢😢😢😢 Lord why
I feel there is deeper meaning in these words in the song, those who agree with me gather here while we are still crying for our skc
Chifunga analakwa
😢😢
Mmmmmm 💔 only God knows y
We are here😢
Sorry😭😭💔💔💔💔keep rest in peace
May God richly blesses you. I don't understand the message but the lyrics are good. May God intervenes in the death cases a d if there are foul play He Will revenue whoever are the culprits. Madam Chilima and the family may you be healed in Jesus's name. Jesus is the husband of the widows He will comfort you.Amen ❤
It's my prayer that the truth should prevail and that our Lord God should show us his Majesty by showing us the truth about this dead,,,,may the soul of My beloved Dr Chilima rest in peace!!!
May God bless this choir Yoo!!
Mmm what a gud song can someone send to chifunga plz
The legendary choir of Malawi Gospel thanks for the messages 🙏🙏🙏😭😭😭😭
Wow! These people can sing....very interesting song, may their souls Rest in eternal peace
Woow my choir 😢😢😢😢😢Rip Mr chilima..... I know you are happy where ever you are...
Powerful choir yes chakwera uzifutse
Kodi nanuso zilizose kumangoti chakwera kupusa basi
Ndiposo aaaaa ine anthu akamalankhula moweruza amandibhowa bwanji🤣🤣🤣🤣🤣 alibe ndiumboni aaaaa mnxiew
Zopweteka kwambiri
Ambuye salakwitsaaa .God knwz the best.😢😢
We mourn your loss with you.God comfort and give strength to the family and a Malawi nonse at this difficult time
Powerful song amen
Very touching 😢. Zambia is mourning with you
Powerful 🔥🙏 Choir imandiwaza iyi 😢
Nice choir yopeleka chilimbikiso ngati atha kunvera bwana chakwerawo zidabwe
Amen amen nyc & strong massage 😢😢😢😢😢😢
My deepest condolences 😢😢😢This song is so special and moving. Befitting a soul such as SKC😢😢😢
George Mbinga.... choirmaster of the year
thus agood song may GOD bless you
Zowawa kwambiri 😢😢😢 RIP Nkhopei sizaiwalika
Wat a song 🔥..chifunga tsiku Lina udzakungunuka
You ndi tails iWeb chifunga sure… dzuwa la Mulungu likadzawala😥😥
Indeed strong advice to Mr chakwera n ua friends
So touching indeed ,may our gud Lord Jehovah God comfort you o Our family
Iwe chifunga Kodi ukuyimva bwino nyimboyo akuti siku lako likazakwana anthu oyamba kukawaona ndi achilima pamozi ndi anthu awo koma ndiye zikoli urinva kuwawa.mulungu akukantha no secret under the son
This is comforting. Thank you so much choir.
Zovesachisoni kuyiwara khalakovuta😂😂😂😂 2:51
George Mbinga machine when it comes to composing. R.I.P Veep Chilima
My prayer.....chifunga one day uzakungunuka. Kudzawara Malawi azawona
😭😭😭😭😭😭 Im a Zambian but i still don't understand this death, Sometimes i want to distract myself from thinking about it but reality just dawns in on me that Chilima and 8 others are no more... MTSRIEP 😭😭😭😭😭
Nice choir God bless you all
All
Lord Jesus Christ my god bless this song ( what's a beautiful sounds like this is a good message to wrong person who did that sheet
Tonse tikudziwa kuti one day is one day chifunga udzakungunuka ndithu ndipo tidzadziwa choonadi😢
It is a soul and touch song
Powerful song
Wonderful song
Chifunga kuuma mtima kwako kwantundu wanji 😢😢😢😢😢 koma ambuye akuone iwe chifunga pazomwe wachita 😢😢😢
I love the song
My legend choir
This is so touched 😢😢 may their souls continue rest in peace 🕊️🕊️ chifunga iwe atitu uli nditsoka only legends understand the meaning of iwe chifunga
Zoona
Komwe uliko bwanji sukuziguguda pamtima iwe chifunga?
Kulira kwathu zipite kwayiwe chakwera!!!😭😭😭ngakhale wapha azako pamalawi pano tsikulina uzamusatila chilima!!!!
Best tribute song of the world
Wakuta thambo pa malawi pano chifunga iwe.. . Anthu kulephela kuona dzuwa😥
Ndine mmodzi wa nkazi wa munthu ofuna kuimira MCP koma tikakumbukira imfa ya Chilima iii ndipo ntima umawawa... Zidalakwika. He was giving a true definition of opposing ndipo true multiparty kukoka achinyamata. Pano tukonda ndale kamba ka Chilima. Anatizindikilitsa kayendedwe kadziko. He had a vibe. Ndale zinabalancer bwino. Osati kumakhala odziwadziwa kuti owina ndi awa noo it was true mpikisano eish. RIP SKC
RIP SKC
Amene tikuyembekezela winawake kuti Mulungu amulange,tizikhumudwa kuona kuti ali innocent pamaso pa Mulungu,don't judge when you haven't been told by God what really happened.
So touching and strong message 😢
Powerful songs
Rest well SKC my hero ,can't accept the fact that you are gone
I love this choir ❤
Wow nice song eish rip our vp😭😭😭😭
Kuyiwarakukhara. kovuta. Abuyeatiyan'ganire 😂😂😂😂😂
Very powerful message in this song 🎵 🎶 🎵
Chining'a mpaka mukwaya anthu muli mmau kukhozi et😂
Kkkkk
Mr chifunga one day it's one day iwetu uzakungunuka 😭😭😭😭
Nice song mmmm amen
Chifunga iweeeeeee asaaaaa 😭😭😭😭😭😭 watisiya pa umasiye wadzaoneni
Chifunga kuuma ntima? Eeeee! Koma zomwe zinachitikazi ndizowawa
Chifunga ichi chitule pansi udindo kubwere dzuwa la yehova 💔💔💔
😂
to God be all the glory!
Kufa ngati
Chitsilu 😢😢
Mimba pantunda😢
Very interesting song rest in peace kras chilima 😱😱
Very nice song and beautiful.Mr Chilima RIP
I deed this is a very toucherble song let his soul rest in peace
Chifunga chakwela....ukumva bwanji ukamamva zotele😭😭😭
Chakwera ndioipa mulungu woziwa kulanga akukanthe
Nice song amen
Chilima was indeed loved by every one. Koma chifunga for real 2025 uzakungunuka
❤ A good song intended for funeral. 😂😂😂
Chifunga means chakwela kuuma mtima kwanji? Nice song. Dzifuse chakwela.😢
Chifunga wagwetsanso kwacha mmmmmm koma a udzakungunuoa day ina
Koma muli massage yamphamvu mu nyimboyi...chifunga chidzakungunuka
😢😢😢 ndipo sikulina kuzawala
😭😭😭 very touching song
Ameeen chifunga hingakule bwanji tsiku lina chikungunuka Amen
This pipo they have talent RIP Dr saulos chilima 😢😢😢
Koma chifunga 😂😂 ayi dzuwa lizawaladi
Chifunga kuuma mtima kwako kwa mtundu wanji iwe,watiliza chifunga😢😢😢
Nyimbo yomvesa chisoni Mzimu wawo anthu onse omwe anapita pa tsiku lowawali mzimu yawo iwuse mtendere😭😭
Amen
Chifunga iwe ukumva kma?