Boma Latha - Samuel Lwara

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 7 сен 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara asserts that due to UTM's withdrawal from the Tonse Alliance, Malawi theoretically lacks a government. The Alliance has been dissolved.
    Ku Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara wanenetsa kuti chifukwa UTM idatuluka mumgwirizano wa Tonse, dziko la Malawi lilibe boma. Alliance yathetsedwa.
    #malawi

Комментарии • 37

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Месяц назад +1

    Boma palibe and we got no president now

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma Месяц назад

    Ma corner onse obela ma vote mcp mwatulukilidwa kale

  • @alickkachepa3801
    @alickkachepa3801 Месяц назад +1

    Chakwela sakonda zikoli

  • @tasmania527
    @tasmania527 Месяц назад

    Awa a Lwara awa sazatha bwino. Ali ndi chimtima chovutika kwambiri. Kaya ndi kukhwima kaya ndi chani koma mathero awo ali pafupi.

  • @BertharrySecurity
    @BertharrySecurity Месяц назад +2

    Boma latha, MCP yikazawina ndiyekuti Abela zisankho

  • @LoveHere-ki8ck
    @LoveHere-ki8ck Месяц назад

    Yagawana zida band 😂😂😂😂

  • @maxwellchilima5440
    @maxwellchilima5440 Месяц назад

    🎉 judiciary it's your role now. Apa honestly boma lathapo

    • @rexnyalugwe4910
      @rexnyalugwe4910 Месяц назад

      Law society of Malawi. UTM yachotsa vote yake, Kodi otsalawo mandate to govern Ali nayo?

  • @user-wd9yd1bg9n
    @user-wd9yd1bg9n Месяц назад

    Thako limozi 😅😅😅

  • @user-um6yo6nc3e
    @user-um6yo6nc3e Месяц назад

    Awabwezele a Dad aja basi...

  • @thomasphiri7799
    @thomasphiri7799 Месяц назад +1

    😂😂😂😂

  • @LucianoKapepuza-sy9wx
    @LucianoKapepuza-sy9wx Месяц назад +1

    Chakwera achoke Ku state house

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms Месяц назад

      Kwambiri big azipita

  • @MikeChingala
    @MikeChingala Месяц назад +2

    Silingathe Ai chifukwa utm inali just a small part of mcp

  • @OssmanAbubaker-t3n
    @OssmanAbubaker-t3n Месяц назад

    Zoonadi Mr Lwara simukunama apa palibetso chanzeru MCP athako

  • @OliverNkhoma
    @OliverNkhoma Месяц назад

    Boma latha palibepo

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp Месяц назад

    Latha boma kumalawi kulibe boma 😂 achakwera agalu chimunduchopa ndamanyasi

  • @BertharrySecurity
    @BertharrySecurity Месяц назад

    Ndipo zakhalabwino kwambiiiiiri

  • @user-wb9ji3oe5o
    @user-wb9ji3oe5o Месяц назад

    Latha boma limenelo ndipo mcp iri mmadzi ndipo achita manyazi

  • @grayakuzikemanda3114
    @grayakuzikemanda3114 Месяц назад

    Mphamvuyo ma MP 4 basi boma latha?

  • @brendachiwamira
    @brendachiwamira Месяц назад

    Apule atilankhule chifukwa sadalowe kunyumba ya chifumu ndi chipani,km akupezeka kumeneko chifukwa Cha tonse alliance.ndiye alliance ndiyomwe yatha.

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x Месяц назад

      Yaaah ndiokuti a Malawi tipange action kaah Kuti tipange referendum

  • @mzondinkosi1151
    @mzondinkosi1151 Месяц назад

    Problem is that you think you are very intelligent. NO. Latha bwanji? Tione ngati latha.

  • @user-jc5tf8jl1m
    @user-jc5tf8jl1m Месяц назад

    Mcp yabisala pa chipande in 2025

  • @PetroMatias
    @PetroMatias Месяц назад

    Boma rathadi basi

  • @YaqoobStandwell
    @YaqoobStandwell Месяц назад

    Mcp yantha kungot yawina ndiye kut yabela palibe wina aliyese akuifuna ndipo or atabela sitizalola kutilamulila ngat akufuna kulamulila azikalamulila nyumba mwake amalawi sakumufuna or akakamile amalawi sakufuna enan or akupatsen kena kake koma nokha mukuziwa chilungamo mukuchiziwa kut palibe wina aliyese akuchifuna chipan cha mcp and achoka or atabela tizachotsa ndimakofi

  • @BrightPhiri-bt6ev
    @BrightPhiri-bt6ev Месяц назад

    Chakwera simbuli ngati iweyo samuel lwara.chakwela salankhula akalankhule chifukwa cha iweyo ndiwe ndati kapolo wadziko iwe kumangokhalira kuchikamwa.alliance siyinachite kutha koma utm yachita kutuluka yokha ndiye boma litha chifukwa chan? Dikila uwone ngati boma lithe.zifukwa zomwe ulinazo ndi mcp ndizaiwe wekha.mesa unkadya komweko ku state house? Siumatisokosela nthawi imene umadyayo bwanji? Panopa anakuthamangisa ndiye uzitipangila phokoso fotsek zako ndithu.

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o Месяц назад

      Hehehe muona kuti mutani Boma latha basi mixeeeeee

    • @BrightPhiri-bt6ev
      @BrightPhiri-bt6ev Месяц назад

      Uko ndiye timati kuzikwata ndi chala maloto a chumba.funso ndiloti kodi president ndani ku malawi? Ngati president alipo ndiye kuti boma lilipo.utm siingathese boma.ufune usafune chakwela ndi president wa boma kkkkkkk

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms Месяц назад

      Ndiwe wakuba ngati chakwera wakoyo mwantha muziwona

    • @BrightPhiri-bt6ev
      @BrightPhiri-bt6ev Месяц назад

      Ndinaba pa khomo pa pako ?? Iwe ndiwe galu eti ndiponso mbuli yamunthu anthunu mmadana ndi reality.akanakhala kuti dzulo muja watula pasi udindo ndi chakwela bwezi panopa kuli chipwilikiti.koma kutuluka kwa utm ndi kaliati sikungasinthe chilichose mufune musafune chakwela 2025 wooooooo ndiponso ndachepesa chakwela 2030 woooooo.msegula mumimba chaka chake ndichino.kulakalaka mutasamuka mmalawi muno.as long muli panthaka ya malawi president ndi chakwela.

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms Месяц назад

      @@BrightPhiri-bt6ev mbuli ndiwe because you don't know what you talking about

  • @joaquegerman2250
    @joaquegerman2250 Месяц назад

    Vinyo watcha tibalalike