Very nice piece. I like your songs and came across this just yesterday but it has won my heart. May God bless the composer, producer, director and the entire choir. Glory be to God
WOLEMEKEZEKA INU ANTHU ENA ONSE A GULU LIMENELI LA MTHAWIRA SPIRITUAL MELODIES... INE MALAWI NZANU KUNO KU DZIKO LA CHILENDO LA SOUTH AFRICA MU MZINDA WA CAPE TOWN WESTERN PROVINCE OF SOUTH AFRICA NDIKULEMEKEZA YEHOVA MLENGI WATHU AMENE NDIYE MWINI MPHAMVU ZONSE... AKUTSOGOLERENI MU MAGANIZO, NZERU, MACHITIDWE ANU A MASIKU ONSE NDIPO AKUDALITSENI NTHAWI ZONSE CHIFUKWA CHA MAYIMBIDWE WOKOMA WOTERE ❤❤❤AMEN.
WOLEMEKEZEKA INU ATSOGOLERI ABAMBO NDI AMAYI.... MTHAWIRA SPIRITUAL MELODIES... NDIMAKUPEMPHERERANI NTHAWI ZONSE CHIFUKWA CHA MAYIMBIDWE ANU WOKOMA WOTERE KUCHOKERA UKO KU MUDZI BLANTYRE (MALAWI) YEHOVA MLENGI WATHU AKUYANG'ANIRENI USANA NDI USIKU, AKUTSOGOLERENI MU MAGANIZO, NZERU, MACHITIDWE ANU A MASIKU ONSE, AKUDALITSENI NTHAWI ZONSE.. ❤❤❤AMEN.
Anthuwa amaimba bwinotu kwambir ❤❤❤
Very nice piece. I like your songs and came across this just yesterday but it has won my heart. May God bless the composer, producer, director and the entire choir. Glory be to God
Zikomo Mr ngati palizina tumizani timakunyadirani Mr👏👏👏👏👏👏👏👏👏
Thanks guys for listening
WOLEMEKEZEKA INU ANTHU ENA ONSE A GULU LIMENELI LA MTHAWIRA SPIRITUAL MELODIES... INE MALAWI NZANU KUNO KU DZIKO LA CHILENDO LA SOUTH AFRICA MU MZINDA WA CAPE TOWN WESTERN PROVINCE OF SOUTH AFRICA NDIKULEMEKEZA YEHOVA MLENGI WATHU AMENE NDIYE MWINI MPHAMVU ZONSE... AKUTSOGOLERENI MU MAGANIZO, NZERU, MACHITIDWE ANU A MASIKU ONSE NDIPO AKUDALITSENI NTHAWI ZONSE CHIFUKWA CHA MAYIMBIDWE WOKOMA WOTERE ❤❤❤AMEN.
Nice video special and perfect song🌹🌹❤️👍🙏
Praise be to God no where to go no where to run indeed only to God. Am humbled 🙏🙏🙏🙏
Amen zili bwn zamphamvu mkokoma kuyimbira mulungu
ilike this Choir to be honest.....taponyani album yoyamba pls called Ntendere.
Yehova ndinu thanthwe langa ndipothawira panga kulibeso kwina komwe ndingapite
A nice song very touching
Mthawira nyimbo zanu ndimazikonda kwabas,
Bwanji kut muposite yija ya *mtendere*
WOLEMEKEZEKA INU ATSOGOLERI ABAMBO NDI AMAYI.... MTHAWIRA SPIRITUAL MELODIES... NDIMAKUPEMPHERERANI NTHAWI ZONSE CHIFUKWA CHA MAYIMBIDWE ANU WOKOMA WOTERE KUCHOKERA UKO KU MUDZI BLANTYRE (MALAWI) YEHOVA MLENGI WATHU AKUYANG'ANIRENI USANA NDI USIKU, AKUTSOGOLERENI MU MAGANIZO, NZERU, MACHITIDWE ANU A MASIKU ONSE, AKUDALITSENI NTHAWI ZONSE.. ❤❤❤AMEN.
Since 2020 I'm still watching this I don't understand the language bt I like the way
God bless you malawian my African
Powerful
The song simply means that : JEHOVA (THE ALMIGHTY GOD IS MY REFUGE AND MY ROCK!!!
Mumakwana takunyadilani
Good one
So inspiring
Super
Great guy's .keep it up
Thank you so much
Beautiful Gospel music 🎶
2023 still watching
Glory to God
Mumatiimira guys may all mighty God bless you and add more skills upon of you 🔥🔥🔥🔥
Dgsryy
I miss home
Amen
Very touching song
Wawooooo
Please bweresani zambiri za Anthu awa amandidalisa kwambi
Good songs
Nice song
Ndathokoza Kwa mbiri
🎉🎉🎉🎉🎉
Zilibwino, koma za kale zija zili kut I tikuzifunanso chonde
Where is old guys I see new
Zilibwino koposa
Sikefa wefu wefu satopa
Tikuthozeni anzathu mulungu akudalen chifukwa chamayimbidwe anu auzimu
Palibe zasopano?
Nice song
Amen
Tikuthozeni anzathu mulungu akudalen chifukwa chamayimbidwe anu auzimu
Palibe zasopano?
Nice song