Thank God for our bishops, the church needs to stand on the truth & proclaim it. We rejoice when persecuted because of proclaiming the truth of the gospel 🙏🏽
Akunama utsogoleri okanidwa ndi mulungu.tiyichotsa ngati mu 1994 musadandaule ikuchoka iyi. Muona kunali Young Poineer ndi Youth League. Analephera.pachipanda ma bishop bwenzi pamenepo.auze Ana a 2000
Bishop Susa allah akudalitseni,allah salephela, ndipo satana alibe mphamvu yoposa ya allah ,alihamudulilah allah wachifundo , allah mutetezeni bishop uyu ndipo chilungamo chiende ngati madzi,,zili poela allah kuti chilima anachita kuphedwa ndi chakwera, allah phulumutsani malawi 🇲🇼
Mndani amachita advise MCP as a party. Ali ndi alangizi opusa mission yopha Chilima sinayende bwino, pano akutuma gulu kutukwana ma bishop nso. Asaiwale kuti Chilima anali ndi 1.4 million and ma bishop nso Ali ndi anthu omwe amawakonda ngati anthu ndipo kupanga chipongwe anthu amenewa ndi kulakwitsa. Ndalama sizigula mavoti. Atengere phunziro pa momwe analuzira Zikhale atepereka ndalama zankhani nkhani. MCP find better advisers
Abusa ndikukumbutseni kuti dziko likanunkha momwe mukunenera Mulungu sasankha munthu wamba amakudzidzimutsani chifukwa amakhala odelereka koma wa pa mtima wake
Ngakhale nthawi ya Dr,H Banda ma bishop atatumiza chikalata ananenedwa, I'm sorry, a kamplepo kuluwa ananena fisi ndi, chakwera wakuba anawabela amalawi kugwilisa ntchito mau oti tikhululukireni ndine mu busa,
Apapa tingoupanga Ulendo waku state house.Asogoreri achipembedzo Cha chisilam ma bishop ndi Akuru Akuru ena amipingo yosiyana siyana. Tatiyeni tigwirane manja tonse polipurumutsa dzikoli.Tatiyeni tisitike miyoyo yathu popita ku state house konko
Ana ena ananyoza mtumiki wa Mulungu nthawi yomweyo Mikango inawadya, DIKLAN 2025 Mulungu achita monga mwa mphamvu zake........ munthu wa Mulungu, sanyozeka!!!
Atumiki amulungu sakhala pati ndidziko ayi awa ndi atumiki amafano amapembedza mafano Mau amati musakonde dziko lapasi kapena zadziko lapasi awa si atuumiki amakhala bize ndi zadziko
aaaa zinalembedwa pati m'bible,chikondi cha dziko lapansi achionetsa pati??,paja mdima umadana ndi kuwala eti?, chanzeru chomwe chiri mu report mliti😢😢😢
Nonsenu amene mutukwana Abishop pachifukwa choti ayankhurapo za imfa yachilima mlungu akulangani kumapereka ulemu ndi bwino
Ulemu ukuyenera kupta kwa Mulungu osati bishop yemwe akupanga zandale chifukwa cha ndalama.
Ndipo inu
Thank God for our bishops, the church needs to stand on the truth & proclaim it. We rejoice when persecuted because of proclaiming the truth of the gospel 🙏🏽
Ma bishop musaope, musafooke, musatope ndipo musakhumudwe imani pa chilungamo chanu komatu chakwela chakwela chakwela ambuye chonde imvani kulira kwa Malawi 😭😭😭😭😭
Koma chakwela sanachite bwino kunena kuti apita kukaona anthu odwala ku Mangochi koma osapita? chakwela ndi mtima wanji?umenewu chakwela waipa mtima kuposa satana chakwela wapitirira satana.
Amewo akutukwana ndi athu opanda nzeru ndipo ndi mbuzi yamuthu ameneyo ndi carward crocodile team zasatanic chikangawa team
Ma bishop sakuwadziwa amenewo ,,,akalemba kalata dziko lonse limadziwa ,,,ndipo kamuzu anachoka chifukwa cha ma bishop akatolika atalemba kalata ,,ndipo kamuzu anali oopsa kwambili koma analimbana naye mkumufoola aaaaa Mulungu atichitile chisoni ndthu
Bishop sunsa osaopa anthu oti akuyendera ndalama zamisonkho zathu awapasa kut anene wabwino zachikangawa mulungu alinanu
Iwe chakwela kumkuyu chimwendo zikhale mukamati boma ndilomweli mukuzina miza kwambili chakwela sakulamulila dziko la malaw pazitsongoleli wose president olempela okanika osanganizila za ife 🇲🇼💪💪
Akunama utsogoleri okanidwa ndi mulungu.tiyichotsa ngati mu 1994 musadandaule ikuchoka iyi. Muona kunali Young Poineer ndi Youth League. Analephera.pachipanda ma bishop bwenzi pamenepo.auze Ana a 2000
Yakwiya ndi mizimu,,akusowa mtendele anthuwa ,,nde mukulimbana nawowo amaima pachoona Ukalimbane ndi ma bishop akatolika kkk akusewela ndthu ,,,
Bishop Susa allah akudalitseni,allah salephela, ndipo satana alibe mphamvu yoposa ya allah ,alihamudulilah allah wachifundo , allah mutetezeni bishop uyu ndipo chilungamo chiende ngati madzi,,zili poela allah kuti chilima anachita kuphedwa ndi chakwera, allah phulumutsani malawi 🇲🇼
MCP MCP!!!! Iyi ipalapatika sure padziko lapansi pano
Zitsiru zikutukwanazo zidali kuti 1992, Ndimabishop omwewo omwe anaphula dziko lino kwa Tembo ndi Kamuzu
Chakwera watipha basi
Akungoonjezera kulakwitsa zinthu, anapha Chilima pano sapota
Ndithu akupasani 90 days kuti mutule pansi udindo ma bishop ake siameneyo samalani pofuna kuyakha kwa ma bishop akatolika afunseni anzanu mbuyomu kuti zinali bwanji mukasitsa volume inu amcp
Alibe dzeru amene akutukwanayo
Aliyense ameme wayankha zonyoza ma bishop Mulungu awapasa chilango chomwe ana amanyoza eliya anawina.period.
Atumiki amulungu amaima pa chilungamo basi mutukwane momwe mungathele koma nkhani ndiyakuti alipo wina mpaka pano alimoyo ndipo anaona zose zomwe zinachitika ku chikangawa patalike pafupike anthu adzadziwa choonadi
Chipani cha mcp chidzathetsedwe chikadzatuluka mboma
Mndani amachita advise MCP as a party. Ali ndi alangizi opusa mission yopha Chilima sinayende bwino, pano akutuma gulu kutukwana ma bishop nso. Asaiwale kuti Chilima anali ndi 1.4 million and ma bishop nso Ali ndi anthu omwe amawakonda ngati anthu ndipo kupanga chipongwe anthu amenewa ndi kulakwitsa. Ndalama sizigula mavoti. Atengere phunziro pa momwe analuzira Zikhale atepereka ndalama zankhani nkhani. MCP find better advisers
TATIUZENI INU A MIDIA MUMAPANGA BWANJI KUTI UTHENGA USIFIKA PAMENEPA MUNTHU AKAYANKHULA TIUZENI NAFE TATOPA NDI BOMA ILI TIKUFUNA KULIUZA CHIRUNGAMO
Akulimbana ndi mabishop akatolika akunamatu ndipo chakwera adikire kalata samaopa ai mitunda iyi
proudly sponsored by the Hon
Musatope kuopa komaso osafoka paja mdima. Umadana ndikuunika
Zoona
Well done c bishop
Mau amati musakhudze odzodzedwa anga nonse mukutukwana bishop choipa chikugweleni modzidzimutsa musakudziwa
Bishop samawopa ndipo amayakhula chilungamo osati azibusa apusa amangomvomera zili zonse mulungu akulangeni azibusa amene mwalandira ndalama zausatanikizo yesaya 29:15 ziulilika posachedwapa mwasala pangono kululika
Abusa ndikukumbutseni kuti dziko likanunkha momwe mukunenera Mulungu sasankha munthu wamba amakudzidzimutsani chifukwa amakhala odelereka koma wa pa mtima wake
Anthu omwe akupanga breifing ndi akuba adya ndalama agalu achabe achabe ati concerned faith leaders akuti?? Zachamba basi.
Chakwela ndifit
Nde mumafuna ma bishop wo azingovomeleza zonamqzo??
Ngakhale nthawi ya Dr,H Banda ma bishop atatumiza chikalata ananenedwa, I'm sorry, a kamplepo kuluwa ananena fisi ndi, chakwera wakuba anawabela amalawi kugwilisa ntchito mau oti tikhululukireni ndine mu busa,
The problem is that even religious leaders are divided: Some are democratic while others are kleptocratic and money- minded leaders.
Ndale nzachabechabe eish!!!!!!😢
@@augustinechibbalazi8897Chilima anapha, bottom line
@@IsabelLuka-i8fzabwino koma Chakwera wationjeza
Vuti la anthu amadana ndi munthu kapena mipingo kapena azibusa achilungamo amafuna onseee adye chibanzi then aphese anthu ochuluka Koma timaenela kuasapota mabishop ngat amenewa awapase Moyo wautali ndiochepa amabwera poela
Chikangawa ndiabale Ako muziona tukwanani Mene mungathele
Ndimanena nthawi zonse kuti mcp ili ndi msanje ndi dpp simwaona? Nkhani njakuti akudziwa kuti APM akhala ndi molalo yochuluka kuposa chikangawayo ndicifukwa anamulesa. Cifukwa panopa a malawi tikufuna APM osati chikangawa ai.Ndipo mcp ili ndi tsoka, yasekeka mmakutu mabishop akunena chilungamo awa koma iwo akuti ai imeneo nde mphamvu ya satanic yo. Lipoti limeneli lija mulibe ciliconse camzeru.Black box ibwele apa itiuze za kucikangawa, adad osadanda inu pa low palibe cingatisinthe maganizo ife 2025 APM ndiyemwe tikukamvotera.Dziko lathu panopa mulungu wakwiya nalo kwambiri chifukwa ca ulamuliro wa chikangawa.💙💙💙💙💙💙💙💙💙.
It reminds me about the "myth of the cave".
Titukwaneni akatolikafe, September ndi pompano mutifuna
Osadandaula mulungu wathu ndiwamoyo ndipo yense yemwe akunyoza ma bishop mulungu awalanga ekha ndipo awonekera ng'amba ndipo tinakafinya ma kolona
Anthu ku Malawi mmadana ndi chilingamo ,munthu akuyankhula chilungamo koma kunyozera
Ndi pamene timadziwa kuti boma likugwa.
Thanks Mr 🙏
❤
Mofire Mr bishop akunama
Mbusa km iwe ulemu wanu kukhuzika km uku
koma yeah 😰
Mau amene nd m'ganene nd zikomo ambuye
Ndipo inu😢
Ukumva kupwetekadi nanga si ulikudzuwa
Zitsilu za atsogoreli a mcp asatanic afalisi ....
Apapa tingoupanga Ulendo waku state house.Asogoreri achipembedzo Cha chisilam ma bishop ndi Akuru Akuru ena amipingo yosiyana siyana. Tatiyeni tigwirane manja tonse polipurumutsa dzikoli.Tatiyeni tisitike miyoyo yathu popita ku state house konko
Kodi abusa shumba anadyabanzi??
Angoti ziiiiii alikuti kodi
Koma chakwera akuposa Idi amini
Nkhondotu izi zimayamba ndi azibusa
Ngati ali ma dolo atukwane pop
Apapa tudikira akubanja basi chete
Anawapusisa chifukwa cha makhwala nyanga zithumwa akulu amenewa
Ana ena ananyoza mtumiki wa Mulungu nthawi yomweyo Mikango inawadya, DIKLAN 2025 Mulungu achita monga mwa mphamvu zake........ munthu wa Mulungu, sanyozeka!!!
Akutukwana ndindani
Keep on
ONSE MUKUNYOZA MA BISHOP PAMTUMBO PA AMANU
Loud and clear
Mizimu apa yakwiya zayambapo
Mmanja mwako game charger ukunena zoonadi ziuze zitsiruzi
Zilimbwino aliyense azimvele yekha chiluñgamo chizaziwika
ashh life is hard
Tsiku lizakwana
A sign of the fall.
Zoonad auze
Chilungamo ndi chowawa ,
Atumiki amulungu sakhala pati ndidziko ayi awa ndi atumiki amafano amapembedza mafano Mau amati musakonde dziko lapasi kapena zadziko lapasi awa si atuumiki amakhala bize ndi zadziko
aaaa zinalembedwa pati m'bible,chikondi cha dziko lapansi achionetsa pati??,paja mdima umadana ndi kuwala eti?, chanzeru chomwe chiri mu report mliti😢😢😢
Baibulo liti limenelo, bishop susa is number 1 mumalawi muno ,ndinu nokha bishop wachilungamo phulumutsani 🇲🇼
ruclips.net/video/T_MuVQmZYq4/видео.htmlsi=2aiWDnoHtKEoKbSa
Zip animal zotukwana
Ma bishop
UDF
DPP