ULENDO AMALAWI TIVOTELA SATANA WABWINO ........ BRIAN BANDA NDI ANZAKE AKUTI ONSEWA PALIBE M'NGELO

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 18 сен 2024
  • ULENDO AMALAWI TIVOTELA SATANA WABWINO ........ BRIAN BANDA NDI ANZAKE AKUTI ONSEWA PALIBE M'NGELO
    Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
    Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
    Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
    #MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika

Комментарии • 17

  • @MaxwellChiwaya-i8q
    @MaxwellChiwaya-i8q 7 дней назад

    Times sikondera chipani chilichonse ngati aja Ali ku mibawa ndi mbc

  • @MaxwellChiwaya-i8q
    @MaxwellChiwaya-i8q 7 дней назад

    Mulungu apitilire kukudalitsani

  • @VeroMaster-lo1mu
    @VeroMaster-lo1mu 4 дня назад

    Better devil yemweyo

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 7 дней назад

    Ine makosana inu mumakwana ngati Pali program yoveka nde ndinu madoda

  • @MPHATSOEMMANUEL-v6x
    @MPHATSOEMMANUEL-v6x 9 дней назад

    😂😂😂 eshi

  • @frankkumwenda6012
    @frankkumwenda6012 10 дней назад

    Bravo guys mukuchita ntchito yayikulu Ku unikila a Malawi, ngati pali Boma lingayamike ndi la Tonse munalimenyela nkhondo ndinu achina Brian ndi gulu lanu.

    • @AdamsPhiri-h1y
      @AdamsPhiri-h1y 8 дней назад

      Boma ili munthu wolimbikira awona kusintha guys osamadikira zopasidwa at tiyen kumunda Tikalime basi

    • @AmosScott-z9x
      @AmosScott-z9x 7 дней назад

      Man anthu akulimbikila km zinthu sizikuyenda

  • @EarnestKazembe
    @EarnestKazembe 10 дней назад +1

    Mizwanya yosatenga mbali polankhula,ndiye tiyeni tizionere tokha.

  • @eliaskachali-xn2ve
    @eliaskachali-xn2ve 8 дней назад

    Koma Satana uyu wa chikangawa ndiwausilu,amadicha ndalama zambili Ku asogoleri osiyana siyana ,pamafunika Kuti Nagari wadicha ndalama alandile Koma asamuvere agwile ntchito mwachulingamo

  • @RichardRomoliwa
    @RichardRomoliwa 9 дней назад

    😂😂😂 koma mjedo wakoma ma guys.

  • @ArnoldWachepa
    @ArnoldWachepa 10 дней назад

    Komadi tsongoleri akakhala wakudya utsi onse omusatira amakhala okudya utsi.zoona Wanda.

  • @IshmaelWadd
    @IshmaelWadd 10 дней назад +1

    Nkhaniyo ndiyoonadi tikavota basi tichose satanic yi

  • @aliemohammed5853
    @aliemohammed5853 10 дней назад

    Chakwera ndi galu

  • @AdamsPhiri-h1y
    @AdamsPhiri-h1y 8 дней назад

    Apopo mkunena zowona koma ngakhale zovuta Zina kuno kumuzi fetelezayo ndiyet tikumatha kgula kwambiri NDipo zinthu zolimidwa ziyende chocho 3 yrs ikubwelay miyoyo ya anthu amene amalimbika ntchito awona kusintha eytu

  • @ChisomoBanda-g5s
    @ChisomoBanda-g5s 10 дней назад +1

    🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉😂😂😂

  • @RichardRomoliwa
    @RichardRomoliwa 9 дней назад

    😂😂😂 koma mjedo wakoma ma guys.