Komatu ndi bwino kukhala chete mukalandira ndalamazo ku mcp ko kusiyana ndi kuchosedwa ulemu wanu polandira maphumzo chifukwa anthu ndi okwiya kwambiri ndi mcp
Ndikuona ngat chaka cha mawa udf will regret,,,udf once combined with MCP in 2009 and bingu got 60 % and above so do that and will see😅😅😅😅😅😅,udf nkachaniso
Mwayakhulana mwzelu bwana boma ndomweli
Ulemu wanu John Dzuwa
Komatu mwapusa adadtu akalamba angofuna kuchotsa mcp ndiye inu a udf mukadzakhala nomber 1 mudzakha vp ndiye pot mwatelo chabwino yendan ndi mcp muluzila limodzi
Komatu ndi bwino kukhala chete mukalandira ndalamazo ku mcp ko kusiyana ndi kuchosedwa ulemu wanu polandira maphumzo chifukwa anthu ndi okwiya kwambiri ndi mcp
Akulu musataye nthawi .....udf singawine payokha .....Udf ndi chipani chachi g,ono kwambili ......akulu nzelu mulibe komanso muziziwa kuti dpp ndi udf ndi amozi ngakhale ntundu onse ndi akumwera ....inu mukuyankhula zopepela apa
Chakuti Chake alibe nzeru or pang'ono mmalo moti mupite kwa APM akuolosen muli bzy kulandila ndalama ku mcp sigwila imeneyo
ndiye ndi ndan amene akukakamizan Kuti inu mulowe or kukhala sapota wa DPP ..ka 500 kwacha mwalezela nako nanga akanakupatsa Zen zen
Galu ndinu nonse a DPP pamodzi ndi ma supporters onse simukuganizaso or pang'ono kwanu kungosokoneza UDF ndi zipani zosusa agalu inu
MUNTHUYU AKUCHITA KUDZIWIKILATU KUTI NDI PENSIONER ALIBE CHILICHONSE AKUFUNA NDALAMA KU MCP UMPHAWI BASI
Ngt kuli chipani chomwe chapanga chtukuko ndie MCP 1 njala paliponse 2 kudula kwa zinthu 3 ngongole zambri mbiri eeee ayesesa boma ndilomweri
Kununkha nkamwa mmmm
Uyu akunena nzoona
Akugula iwe a mcp
Mmm mabodza basi mukatero mwadya banzai, Bingu ndamene anachituluka chipani cha UDF ndikupanga chipani chake mukamayankhula Pena mudzichitako manyazi ntchito kunyoza chipani cha dpp osapanga zanu bwanji manyazi akugwireni ndithu
100%
Mwina anali ali mwana mkumbuseni
Mzanu amupha pomwepo inuso mukufuna mupite komweko ai zikomo pitani mukaziona konko
iiiiiii dziyenda wekha akuti udziyenda ndi dpp ndan pangan zanu amkolo
Koma umbuli osankha zigawo ndi wainu alomwe ayao ndi anthu ozindikira kwambiri tsopano
Poti wati 'iweyo' khala ndi njala yakoyo
DPP imafuna kuthesa UDF yathu
Mbudzi iwee
Mbuzi iwe waukape iwe
Ndikuona ngat chaka cha mawa udf will regret,,,udf once combined with MCP in 2009 and bingu got 60 % and above so do that and will see😅😅😅😅😅😅,udf nkachaniso
Mpata ulipo olongosola mavuto anu koma Mcp ndi chipani cholimba nokhanokha akumwela mukunyozana Alomwe okhaokha musamale pamenepo mukamayambana Mcp idusa moyela
Koma dzinandzi dzitipwetekesa mutu yidzi awaso akuti chani awa aaaa😅
Chamba akulu inu kwanu kwatha Kale musaononge future ya ana akubadwa pano
Pitani
Dpp ikutha kuposa malatani udf bolani dpp kamtundu koipa malubino kufa momvetsa chisoni sitinaiwale palibe kuwina kuno dziko lathu not for dpp
Mbole yako iwe masikini ulibe mfundo
Miseu yake yomweyi ya tchaina ed
I just west my data to open this nonsens voice
Iwe misewu ukunenayo ndi China aid, si ndalama za MCP ai anthu akudya chitedze suziwa zaziii
Kodi DPP I atenga ndrama zawo kumangira misewu, ndiponso kuyambira kare njala ku Malawi chaka chilichonse osati chifukwa cha chakwera ayi
Miseu yake yomweyi ya tchaina ed