Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Azinzanga nde akita wafaaaa kamba kokonda akasi😄😄😄You have made my evening,inu ndi dolo basi.More love and respect for you from Lusaka Zambia 🇿🇲,,,, komano mundipatse unamba foni yanu because I lavuzi you Che Mandota 💝
King of comedian chemandota,, nice acting yofusira yokhayi ndiwe Dolo... 🙏🙏🙏🙏🙏♥️
😂😂😂 mandota uzangosowa ngati nkhalago ya chikangawa
I can't stop laughing 😂 😂 😂 😂 😂
😂😂 opani akasi mwatani kodi mwapelekedwatu apa ngati Samson 😂😂😂
Kungoona chimbina ,,,nambala mwaperekeratu,,,, kukonda mitala basi😂😂😂😂
Mbambande
Kukufunika kukubandula mandota I loves u mandota kkkk keep it up.
Kumupha
Monga nzika ya malawi 🇲🇼 I'm proud of u brother more ❤
Kupanga ndalama ndiwovuta ndiwakuba ameneyu alandile chilango chokwanabwino Kuti ena atengelepo phuzilo
I respect you bro mandota inuyo mudafikadi kwanyadila wawojo
Very super
Akupanga reverse transaction?Kungwira ndpolice case wakuba ameyo
😂😂😂 ati tisonkherane😂 ndiye munali mutafika or basi munaona kuti simubetsa😅
Akufuni kachilango ndithu achele ameneyu
Koma mandota sadzatheka ok kupeza kumumpha bas chifukwa wakuba amasayina
Mbambande wakulu mumakwana kufela mbina basi
Apa ndiyedi actor wafa 😂😂❤
Mandota ulibwino kwabas ukadzasiya kupanga ma comedy udzandigulise mkanjowo
Kumupha basi nigalu kuposa iweyo
Kkkkkkkk inuyo nde nthawi zonse mmathera mmavuto ndithu🤣
Madoooo😂😂😂 mfumu mandota sopano😂😂😂 talent at its best💯💯💯🔥🔥🔥........... inuyo muzangosowa koma😂😂
Umakwana mandota ❤❤❤
Panandi panand zitheka popano tifika 100 000💪🔥🙏
Awatu ndi chemavuto kkkkk kutoite kugwidwa lero si izi mu minbus😂😂😂😂😂😂
Abro inuyo umakwana mulungu akupatse moyo wautali.❤
Mandota ndi dola ngati ching'ani ng'ani
Ine imandisangalasa ndi jeket kuvalira mkanjo
Kumuotsha 🔥💪😂 fadah ai zikomo ndiinu one
Brother chemandota mumandivesa kukoma ❤❤❤❤
Umakwana Che Mandira usazafe uzangosowa
Ngati akupanga reverse transaction akangogwidwa ngati mmene akugwilira apamu basituuuu iwe moto kuti bhuuuu kukuotcha chifukwa nayo police ilibe chilungamo ndie kumangootcha basiii or kungomudula manja waberawo
Adha iweyo ndiwe dolo kwambiri
iwe ndiosafunika petrol, kungokusonkhezera jacket yakoyo basi 😅😅
😂😅 koma mumatha amwene 🤣
Che Mandota ndidolo km mkazi wasokoneza business Cash munaphulir boss
Great
Koma ine amandiwaza ase.
Focus inavuta. Mandota.. kuhasa basi za uhule ayi..
Mandota amakwanila😅😅😅😅
Palibenso wina iweyo umathaChe Mandota I lafus u tu mach
Changu pamalo Malawi wavuta uyu! Mumayitatha chemandota
Abwezetu ndalamayo ameneyo komanso apasidwe kachilango kabwino
Kkkkkkk... Kumtengera ku police bass
Mpaka ka mnyamata kogulitsa chamba or mantha munalibe , koma mandox ndie ndi mafia
Che Mandota inuyo ndi one.Mwapusitsa Kondakitale ndithu 😂😂😂😂😂😂😂Keep it up
Kkkk kumuotcha basi hiyaa
Matimvets kukom inuy Mr Mandot
Mandota umatha kkkk
Ndaona mulibe mbeeete😂Mandota ndi dolo❤
Kd mundu wamkulu inu zi udya mukumatilangisa kt kt tisiopa akasi udya inu??? Nanga inuyo bwanji 😂😂😂😂😂😂
mandota muli ndi luso kkkkk😂😂😂
Akazi amapha iwe ukunama akazi amapha iwe aaaaaaa
Kkkkk Mandota ndi dolo Koma apa sizinamuthere bwino
Mashallah mandota zeru ya bhobho
😂😂😂😂😂😂😂😂😂 how can I vote you bro? I didn't get a link for vote maso award so let me have the link inbox
Voting has not started yet
@@CHEMANDOTACOMEDY ok fine my best comedian
Kkkkk ndingangomungwila
Umakwana mmesa 😂😂😂😂mmesa
Eeeee! Chemandota wakhala pang'ono afa ndithu, aaaaaa pamene paja ndipoyenda champenii?
Actor wake nthaw inayake ndofoila😂😂🙌
Koma iweyo umaganiza bwanji Ase🙄😂🙌👏
Eeeeeee koma bwana mumatiphunzisa ndthu. Ulemu wanu boss
Kkkkkk bwanawe kuchotsa ma hope alipompo😂😂😂😂
Bro 🤣🤣🤣😂 number one
Nice big koma ma contacts a blue associate sakuwoneka tingawapwone bwanji?
Kususuka inu achemandota adzakuphetsani azimayi 😅😅😅😅
Yosokherana mwagwa nayo tu❤
Ndikhozo kumumagitsa
Mwandizangalaza kwambiritu😂😂😂😂
Kulibenso kumalawi kuno
Mbambande iweyo umatha katundu wa Boma
Nice
Wakuba osamusekera kumuwotcha Basi kut ntundu wumenewo usapitilire
Amatipereka ndi azimayi omwewa
Very nice
Chee mandota inabwela usazafe uzangosowa 😂
Ndikhoza kumupititsa ku police
A Mandota ndinu big basi! keep it up
Ndimafuna ndikhale oyamba kupanga comment koma eee anthu muli pachangu 😂❤❤❤
Kumudula ziwalo kuti likhale phunziro kwaena.
Ndwe doloo...bra Ndo
Mandota umandisangalatsatu hvy kkkkk
Uyoyo kumamuwonetsetsa sali bwino nkomwe😂😂😂mandotayuuu
Aphedwe basi😊
Umatinvetsa kukoma😂😂
Hahahaha akazi ndi weakness yathudi ndipo sitingathawe
Mandota😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Nice one
Chemandota tabwali wamkulu😅😂😂
Pafunka kunjatitsa😢😢😢😢😂😂😂😂
Mumatiimilila a mandota kp it up
Km uyu sazathekaso ai aaaaaa.......chemandota chemandota
🤣😃😃😂 ma babe amaphetsa
Kkkk ndigameyetu koma
Nice🎉MAn
Nawenso fikiii kuulura aaaa 🤣🤣🤣
Azatiphe ndazimai omwewa
Kungophwasula basi😂😂
this one is crazy 😆😅
Mandota ali bhoo
Azinzanga nde akita wafaaaa kamba kokonda akasi😄😄😄
You have made my evening,inu ndi dolo basi.
More love and respect for you from Lusaka Zambia 🇿🇲,,,, komano mundipatse unamba foni yanu because I lavuzi you Che Mandota 💝
King of comedian chemandota,, nice acting yofusira yokhayi ndiwe Dolo... 🙏🙏🙏🙏🙏♥️
😂😂😂 mandota uzangosowa ngati nkhalago ya chikangawa
I can't stop laughing 😂 😂 😂 😂 😂
😂😂 opani akasi mwatani kodi mwapelekedwatu apa ngati Samson 😂😂😂
Kungoona chimbina ,,,nambala mwaperekeratu,,,, kukonda mitala basi😂😂😂😂
Mbambande
Kukufunika kukubandula mandota I loves u mandota kkkk keep it up.
Kumupha
Monga nzika ya malawi 🇲🇼 I'm proud of u brother more ❤
Kupanga ndalama ndiwovuta ndiwakuba ameneyu alandile chilango chokwanabwino Kuti ena atengelepo phuzilo
I respect you bro mandota inuyo mudafikadi kwanyadila wawojo
Very super
Akupanga reverse transaction?
Kungwira ndpolice case wakuba ameyo
😂😂😂 ati tisonkherane😂 ndiye munali mutafika or basi munaona kuti simubetsa😅
Akufuni kachilango ndithu achele ameneyu
Koma mandota sadzatheka ok kupeza kumumpha bas chifukwa wakuba amasayina
Mbambande wakulu mumakwana kufela mbina basi
Apa ndiyedi actor wafa 😂😂❤
Mandota ulibwino kwabas ukadzasiya kupanga ma comedy udzandigulise mkanjowo
Kumupha basi nigalu kuposa iweyo
Kkkkkkkk inuyo nde nthawi zonse mmathera mmavuto ndithu🤣
Madoooo😂😂😂 mfumu mandota sopano😂😂😂 talent at its best💯💯💯🔥🔥🔥........... inuyo muzangosowa koma😂😂
Umakwana mandota ❤❤❤
Panandi panand zitheka popano tifika 100 000💪🔥🙏
Awatu ndi chemavuto kkkkk kutoite kugwidwa lero si izi mu minbus😂😂😂😂😂😂
Abro inuyo umakwana mulungu akupatse moyo wautali.❤
Mandota ndi dola ngati ching'ani ng'ani
Ine imandisangalasa ndi jeket kuvalira mkanjo
Kumuotsha 🔥💪😂 fadah ai zikomo ndiinu one
Brother chemandota mumandivesa kukoma ❤❤❤❤
Umakwana Che Mandira usazafe uzangosowa
Ngati akupanga reverse transaction akangogwidwa ngati mmene akugwilira apamu basituuuu iwe moto kuti bhuuuu kukuotcha chifukwa nayo police ilibe chilungamo ndie kumangootcha basiii or kungomudula manja waberawo
Adha iweyo ndiwe dolo kwambiri
iwe ndiosafunika petrol, kungokusonkhezera jacket yakoyo basi 😅😅
😂😅 koma mumatha amwene 🤣
Che Mandota ndidolo km mkazi wasokoneza business Cash munaphulir boss
Great
Koma ine amandiwaza ase.
Focus inavuta. Mandota.. kuhasa basi za uhule ayi..
Mandota amakwanila😅😅😅😅
Palibenso wina iweyo umatha
Che Mandota I lafus u tu mach
Changu pamalo Malawi wavuta uyu! Mumayitatha chemandota
Abwezetu ndalamayo ameneyo komanso apasidwe kachilango kabwino
Kkkkkkk... Kumtengera ku police bass
Mpaka ka mnyamata kogulitsa chamba or mantha munalibe , koma mandox ndie ndi mafia
Che Mandota inuyo ndi one.
Mwapusitsa Kondakitale ndithu 😂😂😂😂😂😂😂
Keep it up
Kkkk kumuotcha basi hiyaa
Matimvets kukom inuy Mr Mandot
Mandota umatha kkkk
Ndaona mulibe mbeeete😂
Mandota ndi dolo❤