This movie made me to shade tears😢. Mrs Phiri(Deputy Head teacher), Fatsani and Grannny made me to cry unstoppable. At first I thought it's real then I realized that it's just a movie. Honestly this is a masterpiece thing 🙌. Nsaname yandisuntha ndithu and yabwenzeretsa chikondi changa pa anthu osowa ndi opanda mphamvu.
Kaya vuto Ndine kukonda kulira lira koma nde ndaliradi. Alot of Malawian's are going through this because of unsatisfied guruz in authority. Kudos to Fatsani, her friend, Nambewe, Madam deputy, a head, gogoz Film munakazinga iyi❤
Vuto lathu a Malawi ndi ili kukomda kugwilitsa nyimbo nyimbo za mayiko ena apa ndi kuthandauza ku sound pamene tikuwonela video,koma chikhalire tili ndi nyimbo zabwino kwambiri chisanzo Bambali mkandabile,Arani Namoko ,
Amene tabwera without any link let's gather here 🔥🔥
Kuno
Ife kuno..yadza yokha... maphuziro tipanga mawa relo tionere😂
@@portianahkalonga bola asawide😂
@@Allie196eeh 🤣😭🙌
@Allie196 ife sitidalira link 😂
Amene tangokumana nayo let's gather here🎉
Ifee😂😂😊
We here 😂😂😂😂
I like the lady who was looking at Fatsani in the market. I felt her passion for Fatsani.
Finally after so many years of waiting😂
Amene tatulusa misozi pokumva chisoni ndikukhuzidwe together here 😢😢
This movie made me to shade tears😢. Mrs Phiri(Deputy Head teacher), Fatsani and Grannny made me to cry unstoppable. At first I thought it's real then I realized that it's just a movie. Honestly this is a masterpiece thing 🙌.
Nsaname yandisuntha ndithu and yabwenzeretsa chikondi changa pa anthu osowa ndi opanda mphamvu.
ndipo the way ndalilira ineyo.....am jxt realising now that i was on a movie
@@EvieShoeeeeeeeiiiiiiish koma ndi movie yabwino ndinso yophunzitsa
Amene tangofikira kupanga comment tisanaionere let's gather here
Ifeeeee
Finally after years, nafe taonerako🎉
Finally movie ija yapezeka after long tine 😊😊 koma yokhudza kwambiri 😢💔
Anyone who dropped a tear somehow let's gather here.. we have too much sympathy
Its very emotional❤😢
Am sleeping in tears 😭
Just remind me of my story way back...Glory be to God..
Watching from mauritius island great movie hats off really apreciate it💗💗👌👌
Who cuts onions when fasan was speaking 😢
Finally amane takumanizana nayo mwangozi let's gather here😂
Ine pano
Ine pno
😂😂😂😂we here ndimasaka zina nangoti nayoni gululu
Kungoti gululu osanenaso kuti achita post
The quality, story line and characters of this movie is absolutely outstanding. 🎉❤
Am watching but I feel so sorry to my self this movie is so touchable ❤ I love it alot
Eeeh😂🎉🎉❤ Finally I have Been Searching for This Osayipeza....As if Anali ma Drug🙌😅
😂😂😂😂 komatu nde tidalipo ambiri omaisaka sakatu
It touches My heart
Fatsan movie mumaichedweselanjj film yogwesesa misonzi ukamaiwonela eishiii😢😢😢😢
life has a deeper meaning,am so touched by this big up
I like it so much this movie let's go people's to gather comments on here ❤❤❤
Kuyamba kuionela uku🙌🙌
Watching from south Africa nice movie big up Malawi
I really cried at the end... So touching 😢😊
Kumapetoku so touching
I don't know why 😂😂😂😂 but I have cried throughout the movie😢😢😢😢😢
😅😅😅😅😅
Finally on RUclips 🥳🥳🥳❤️
ndalira at the end mmm so touching😭
Same to me😭
Ndavumbuluka ndekha ndi mapiko anga❤
Kungoti gululu ndi Fatsani mpakana ndapanga check katatu kuti koma ndiyomweyidi eeegh, finally ndiionere
Inesotu
So touching let's learn to be a blessing to others 😢
Nambewe is a natural❤😊
A nambewe mumatha Inuyo 😂😂nice movie
Finally the move i was waiting fore its here😊🔥💃
Finally atipatsa tionereko😅😅😅😅❤🎉
Life its not easy 😢😢😢 God help us
nice video
Let's support this and put Malawi on map
The truly Africa movie with good content 🔥
i cried as i was watching this movie😢😢
So touching 😢😢
Finally eh eh
great movie 🔥🔥🔥
Finally
Kaya vuto Ndine kukonda kulira lira koma nde ndaliradi. Alot of Malawian's are going through this because of unsatisfied guruz in authority. Kudos to Fatsani, her friend, Nambewe, Madam deputy, a head, gogoz
Film munakazinga iyi❤
❤❤ndpo kukazinga osat masewera
Finally 🔥🔥🔥
Finally eshii
Finally 🔥🥳🥳🥳
LUKI I SEE U, THAT'S SOME TOPGAME ACTING SKILL THERE❤
Next please I love it
Finally tionere Fatsani pano
Ndipo movie kuchita kuibisa ngat chamba
Nankha imachedwa pat
Movie yabwino kwambili🔥
Downloading I will watch later 😊
Muzindikila yachotsedwa ohoo 😂😂😂
Nice movie, so emotional
Ndangolowa RUclips gululu ndi movie ndakhala ndikuisaka now for free ❤thank you so Much...
Dis movie it makes me feel
Cry the little girl hw she's
Survived, so sad😢
Eish after kutizuza finally tionereno mwaufulu😂
Nice movie
😭😭😭 end in tears
Chikondi and Anambewe very good actresses. keep it up🎉
@@ChimwemweLivuza kaya amachedwa nayo pati
Great film❤
Finally🎉❤. Itasowa pa RUclips pano
Eeeeeeeeh the Lord has fone it finally 🥳🥳🥳🥳
😅😅😅😅
Nambewe🔥🔥🔥
Ndilowe nawo ndimafuna kwabasi❤❤❤
Kungoti gululu nayo movie yachimalawi ndikaionela ndikaweluka
I will come back to comment
Pangolin uja watulukira 😂😂
I cry 😢😢😢😢
😢😢😢eiii this movie
Biggie up MAlawi❤❤❤❤❤🎉🎉🎉
May the good Lord remember the poor and blessings follow them daily no
Wonderful big up guyz
Big up to my country ❤
Wow great latest movie
Eishiii zachisoni kwambiri 😢
Movies at first ndikayinena but to be honest yoh this something else
Vuto lathu a Malawi ndi ili kukomda kugwilitsa nyimbo nyimbo za mayiko ena apa ndi kuthandauza ku sound pamene tikuwonela video,koma chikhalire tili ndi nyimbo zabwino kwambiri chisanzo Bambali mkandabile,Arani Namoko ,
Film yolilitsa iyi iiiiii..so iwas crying like a baby ... 🤦🤦🤦🙌🙌🙌
Koma ndiye mumkabisadi joker tuu,,zilibwino kwambiri ❤
You guys are doing good keep it up, muli mphuzilo labwino kwambili
Aaaaaaarg chikhumbokhumbo choonera Fatsani chinatha 😂😂😂😂 Komabe ena aonerabe ... Atlist ndapanga view , like and comment 😂😂
😂😂😂😂Ndipo tinachita kuiwalako abale
Woww❤❤
Film inabwera kudzakhazikika
Nice movie ❤
Finally😂😂
Misozi kutseka yeka mumaso 😢😢😢😢 next movie please ndizophusitsa
Amene taonera ndipo talira😭😭🙌
Ndiika comment nkaonera yonse,😂😂😂😂
Omg movie
Movie ndakhara ndkuisaka iyi eehhh😂😂
Muli bwino next movie yesani kuti iziwala alot of hated Medina MA movie, but big up Malawi
Change your quality settings to 1080 or 4K
Finaly😂
Ngati kutulo tioneleko Fatsani😂😂😂
Nice
Wow
Tinayisaka kutopa finally mwatipatsa thanks
Fatsani wandililisa abale people go through alot uphawi sizinthu😓🥺
Waivumbulusa ndan movie yobisidwa ngat nyaupe 😅😂
Mpaka fatsani anakula pano
Mposo
Sizot let's gather here aliyense wabwerera bando wake
K😅😅😅😅
😂😂😂😂😂mposo