Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Amenewo anangovala makaka a UTM koma si a UTM, amenewo ndi a Manganya
Mayi Banda nanuso mukufunaso chani koma mpando umenewu mmmm auaaa
Nanga aphedwa Ku chikangawa analakwanji
A UTM mtsogoleli wawo ndi Mayi Patricia kaliyati . Avala mkakawo ndi aganyu amanganya
Kaliyati adatuluka yekha ife sitinatuluke sakakamizana izi zopusa basi
Palibe akupanga nsanje,, a Utm enieni sangapezeke ku Mcp,,amenewo ndi a usi
Si a utm amenewo angovala zovalazo
Inu ayi muli limozi ku mcp
Zikuoneka kuti ngakhale azipani zina amayikonda msaluyi chifukwa ndiyowala komanso yowonekera patali. Musawaletse.
Apule amangotero kuti ulendo ofunikira koma anthu akumudzife tingovutikabe, ayi zikomo
Okuba Chikangawa kullikonse angapite pobwerera amatero Koma a Malawi akadikilira zomwe apule anena zosatira zake 0 out of 100%
@@KingDavedNkhata koma ndiyetu 0 out of 100 ngati bodza mmmm awa akutionjeza kwabasi
Si a UTM mcp imeneyo
A MCP amenewo sizoti tizimva zopeperazo
How do we differentiate that this is UTM supporters or not? Kaliyati is a racism leader, utm is a party for Malawians ,
Utm idagawikana munya boma ndi lomweri
Uchisilu wanu si a utm bwanji kodi usi akupezeka ku utm ngati ogwirizira ndiye Pali anthu omusatila nsanje bwanji