Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza za kuzima kwa magetsi ndi nthawi yomwe tiri komanso komwe tikupita

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 18 сен 2024
  • Mu utumikiwu, a Twaibu akufotokoza za vuto la magetsi mogwirizana ndi nthawi yomwe tiri ndi komwe tikupita. Mkati mwa izi, afotokozanso zina zambiri zoti okhulupilira tidziwe.

Комментарии • 16

  • @yohachimwaye5859
    @yohachimwaye5859 Год назад

    Amen

  • @shakiraamin625
    @shakiraamin625 Год назад +1

    Thank you for opening our eyes so that we should be really ready for Jesus is really coming, may living God bless you and your family

  • @filipegabrielsulemaine9799
    @filipegabrielsulemaine9799 Год назад +1

    Amém 🙏. Deus nos proteja para ganharmos a vida eterna

  • @PetroKachingwe-jf7dh
    @PetroKachingwe-jf7dh Год назад

    Thanks mtumiki Twaibu
    Ziphunzitso zanu zolamitsa
    Pitilizani kutiphunzitsa
    Amen

  • @thomhenry1127
    @thomhenry1127 Год назад

    Yesu abwela posachedwa

  • @markbanda7434
    @markbanda7434 Год назад

    Amen abusa

  • @jeffmalizan9878
    @jeffmalizan9878 Год назад +1

    A twaib ine ndiye ndimachita kuchalira each and every subject yanyuwani ina iliyose koma ndimakuoemphani kuti zina zomwe munangotilonjeza muziizpitiliza

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Год назад

    Ai zikomo brother twaibu

  • @ElinaMambo-tb2cm
    @ElinaMambo-tb2cm Год назад

    One phe kuverera nichidwi, kuyembekezeraso maenje 8 amene anasala nde Pali kii ya gate muulendo was chikhristu chonde mtumiki was Mulungu tikumbukireni.

  • @user-yh2ze3yp3b
    @user-yh2ze3yp3b Год назад

    Ndifuna kukufunsani Inu mtumiki Twaibu Ahmidu kuti,Kodi nkhani ya kukhwimira munthu kukhala ndondocha abathwa ndikumawagwiritsa ntchito zosiyanasiyana,ndiye timamva kuti amangotitengera munthu uja mwamatsenga chimene timakaika ndi china chachabe olo Chanthochi,ndiye ndiye tatambasulani mtumiki kuti Kodi zimayenda bwanji kwenikweni,Kodi anthu aja akumatulukira pambuyo poti wakhala kumanda Kwa zaka Kodi akubwera aja ndi anthu Eni Eni kapena zifanifani kapena ziwanda za Satana tithandizeni mtumiki please

  • @FelixMadeya-d5b
    @FelixMadeya-d5b 9 месяцев назад

    Mtumiki pitilridzan ku phunzitsa za thawi yakumapeto, panonso tayamba kumva za ulenje wa anthu omwe akumagula Tiana ta nkhuku uku akugula anthu

  • @preciousmkute4041
    @preciousmkute4041 Год назад

    Following

  • @reginamhone
    @reginamhone Год назад

    Mulungu wakumwamba apitilize kukudalisani ndikutiululila zobisikaxo kt ife tiziwe za izo zili kuza.

  • @chamunolwaluciano5381
    @chamunolwaluciano5381 Год назад

    yosamaliza tu iyi😑

  • @luciapita
    @luciapita Год назад

    maliizani za maenje16