Dan Lu feat Lazarus Mccarthy Chakwera - Chakwera (Official music video)

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 2 дек 2024

Комментарии • 172

  • @HawasharifYasinpn-b1x
    @HawasharifYasinpn-b1x Месяц назад +4

    Machende anu amene muti boma ndilomweli

  • @peterjcndolo5644
    @peterjcndolo5644 Месяц назад +7

    Iyiyi wakunga Lufan🔥🔥

  • @OmegahKatanda
    @OmegahKatanda 2 дня назад

    Koma ukamati sakuchoka mmmmm ine kumva kukoma Pali ponse❤❤❤❤❤❤

  • @mthawisakaunda
    @mthawisakaunda 10 часов назад

    Kufuna ndalama bas. Inampachka yesu

  • @CEEVUN265
    @CEEVUN265 Месяц назад +4

    I will be watching this video ka 5 patsiku and boma ndilomweli sitikusinthaa

  • @dalitsokaelama360
    @dalitsokaelama360 20 дней назад +1

    kkkkkk ase nyimboyi wapha ngakhale ukutama munthu olakwika,,,koma chorus iri super

  • @christophergibson72
    @christophergibson72 Месяц назад +2

    Iwe umati!!!! ndimafuna yoonela iyi ifika 1 milion

  • @wisdom20mkango49
    @wisdom20mkango49 Месяц назад +2

    Dan more fire.... Atsegula mmimba otsutsa wo😂😂😂😂 2030 woooo

  • @Bvumbwefarms
    @Bvumbwefarms Месяц назад +4

    Zonvesa chisoni a dan nyimbo mpaka siku olo osakwana 10k views

  • @hendrixbanda5111
    @hendrixbanda5111 Месяц назад +2

    Uyuyu akupweteka gulu 🔥🔥
    Cadet mpatsen panado 😂😂

  • @GiftWhayo
    @GiftWhayo Месяц назад +2

    Mmatha kupeka nyimbo fada 🔥🔥🔥

  • @modiseusi4412
    @modiseusi4412 Месяц назад +1

    Amene mukuti ifika 1milion
    Wait idzafika Next year nkadzamugulira phone mwana wanga mwina adzapanga nawo view.....
    7.8k in 24hrs
    Iyiyi ikafika 100k mundifunse, ndili kuseliku.....

  • @jaffalipeace
    @jaffalipeace Месяц назад +4

    Very powerful song🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @AyameWiski
    @AyameWiski Месяц назад +2

    Pamtumbo pako Dan lu NDA agogo Alonso pat

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 26 дней назад

    Koma achakwela musamale akufuna kukulandani zitukuko. Aku. D. P. P

  • @ibrahimmeemzy9754
    @ibrahimmeemzy9754 Месяц назад +2

    Mboloyako iwe galu pamotsi mcp ndi chakwera atsanu akufutika ndi njala inu galu basi🤞

    • @FloridaOssy19
      @FloridaOssy19 Месяц назад +1

      Or mutukwane ifeyo tili nganga pa mbuyo pa Dan lu 🔥🔥🔥❤️🔥

    • @christophergibson72
      @christophergibson72 Месяц назад

      Bwino osadzimangatu bigy

  • @emmanuelkamwendo2295
    @emmanuelkamwendo2295 Месяц назад +1

    Boma ndilomweli sitikusintha antaaa!!!!🎉

  • @uladieawali2490
    @uladieawali2490 Месяц назад +2

    Pantumbo pako ndthu nthawi yomweyo

    • @PRECIOUSMKUTE
      @PRECIOUSMKUTE Месяц назад

      😂😂😂😂😂😂polani moto

  • @clarencevallerah3135
    @clarencevallerah3135 Месяц назад

    misewu mbwembwembwe nanga CHINA AID akfunapo chan hahahaha 🤣 Dan lu kufoila kwakonso aaaaa

  • @thompsonchimphango5076
    @thompsonchimphango5076 Месяц назад

    Boma ndi lomweli chete!

  • @YusufuUsumani
    @YusufuUsumani Месяц назад +2

    Chikangawatu achoka ovota ndife chigawenga chakupa chakwela chikangawa

    • @CathyJambani
      @CathyJambani Месяц назад

      Akuona ngat ndife zitsilu aonaso

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy Месяц назад

      Azingodya ndalamazo ,, DPP boma 2025 ndipo palibe kuchosera tatopa ndi khadza za namapwala chakwera

  • @ChimwemweZgambo
    @ChimwemweZgambo Месяц назад +1

    MCP ikupitilizaaaaa, tati sakuchoka Chakweraa🎉🎉🎉❤❤❤

  • @PeterTambala-c8r
    @PeterTambala-c8r Месяц назад

    Chakwera ndi munthu uyu tiyeni timupase vote MCP yabwera bas

  • @WitnessKatangala-u1l
    @WitnessKatangala-u1l Месяц назад

    Dolo katatu🔥🔥🔥Komaso boma ndilomweli inu aaaa

  • @samsonmtumbati4855
    @samsonmtumbati4855 28 дней назад

    Ugwa nayo olo chimodzi chanzeru ndiboma lolepheralalo

  • @vanessamalangizo7639
    @vanessamalangizo7639 Месяц назад

    Umakwanira iweyo 🥳🥳🥳🥳🔥🔥🔥🔥

  • @MpapalaKOSEKO
    @MpapalaKOSEKO Месяц назад

    Achokatu ameneyo wakhadzayo

  • @MADALITSOKALUSA
    @MADALITSOKALUSA Месяц назад +1

    Mbambande kumenya kugwetsa

  • @PeterTambala-c8r
    @PeterTambala-c8r Месяц назад

    Boma ndilomweli bas musapase mikango ya njala 💪💪💪💪💪💪💪💪💪

  • @MphatsoLangtonLilemba-w1i
    @MphatsoLangtonLilemba-w1i Месяц назад +1

    Ndiye zipezeka kuti cadet apanga view, osadziwa kuti akuthandizira kk

  • @allanphiri2368
    @allanphiri2368 Месяц назад +5

    Chakweraaaaa! Chakweraaaaa! Kutchaya kugwetsaaaa!!

  • @SteveSpeack-u2s
    @SteveSpeack-u2s 15 дней назад

    Amwene nyimbo ndizija munamenja ku Dpp zija bs apa or palibe chanchitikapo mwina chamzeru chanchitikapo kudyeredwa mkazi bs chamzeru chomwe ndawona ine

  • @MichaelchapitaKumphata
    @MichaelchapitaKumphata Месяц назад

    Boma ndilomweli bs Dan lu sakunama ayi guys

  • @PreciousMitambo-hb1lj
    @PreciousMitambo-hb1lj Месяц назад +4

    Iweyo unadza. Wabweretsa mpungwepungwe ku blue camp 🔥😄

  • @PiliraniKhwipira-g3u
    @PiliraniKhwipira-g3u 14 дней назад

    Mmmmm nyimbo yosakoma

  • @elvisnjoka8428
    @elvisnjoka8428 Месяц назад

    Boma ndilimene lilipoli❤

  • @EmilyMandala-j3f
    @EmilyMandala-j3f Месяц назад

    Palibe kholo limafuna mwana wake avutike😌

  • @HASCKHUSTLEFIRST-yy8fs
    @HASCKHUSTLEFIRST-yy8fs Месяц назад +1

    Mapwala malume anthu akufa ndinjala😂 fertilizer 100 pin this year athu akadya kwan

    • @PRECIOUSMKUTE
      @PRECIOUSMKUTE Месяц назад

      Polani Moto chief 😂😂😂😂

  • @RobenAlik
    @RobenAlik Месяц назад +1

    Chikangawa yomweyo mwati

  • @PociahMack
    @PociahMack Месяц назад

    Boma iloooo cadet kumva kuwawa chakwera sakuchoka

  • @modiseusi4412
    @modiseusi4412 Месяц назад

    Tikumane kuseliku
    Kuli AMEN ya KELL KAY
    13.2K
    IN 1HR
    😂😂😂😂😂😂😂

  • @chisomomsungama
    @chisomomsungama Месяц назад +1

    Chakwera 🔥 Chakwera 🔥 Chakwera 🔥

  • @danlufani
    @danlufani  Месяц назад +4

    Simene kulili 😂🎉

  • @MaikNkhoma
    @MaikNkhoma Месяц назад

    ❤❤❤❤❤❤azoona

  • @YankhoChiwaya
    @YankhoChiwaya Месяц назад +1

    Sakuchoka!!😍

  • @Yoxym
    @Yoxym Месяц назад

    Mafuta ngambwi ngambwii😂😂😂😂

  • @fabianoedward9245
    @fabianoedward9245 Месяц назад

    Aise umatha kuimba

  • @mazyjohn-hd7dh
    @mazyjohn-hd7dh Месяц назад

    Tafika kale ife😂 Boma iloooo

  • @FAIBARMWSANSOT-q8o
    @FAIBARMWSANSOT-q8o Месяц назад

    Ili mwala🔥🔥🔥

  • @SightNgwira
    @SightNgwira Месяц назад

    Maliro akatuluka sabwereranso ❤❤❤❤. MCP ✊✊🔥😂

  • @PetersMalunga-i2t
    @PetersMalunga-i2t Месяц назад

    Apa nde bolaninso Mitengeri Choir' tu 😂😂

  • @MadalisoMapemba
    @MadalisoMapemba Месяц назад +2

    Pa ntumbo pako iwe kape iwe uzimvela wekha ndachakwelawo

    • @PraiseMkandawire-oq3ig
      @PraiseMkandawire-oq3ig Месяц назад +1

      Ngati sukufuna kumvera osangochokapo bwanji umburi ukuphani😅

    • @PraiseMkandawire-oq3ig
      @PraiseMkandawire-oq3ig Месяц назад

      Wow nice danlu big up can't wait to dance😂😂

    • @Isac-y3z
      @Isac-y3z Месяц назад

      ​@@PraiseMkandawire-oq3iguzinvela wekha pamene iwe uli kokuno kuwonela 😂😂😂adha yinuso ndi akape bwanji

    • @TrinityChiwaya-s9e
      @TrinityChiwaya-s9e Месяц назад

      Mwagula ufa?

  • @EzraAndrea-t1u
    @EzraAndrea-t1u Месяц назад

    Dolo kwambri iweyo

  • @MuhammadInack
    @MuhammadInack Месяц назад

    Dan lu mapwala ako ndi chakwera wakoyo😢

  • @ezramwale100
    @ezramwale100 Месяц назад

    Boma ndilomweli ndipo enanu bwerani mulandilidwa ndithu

  • @JosmanMw-di5vl
    @JosmanMw-di5vl Месяц назад +2

    Mapwala anu😢

  • @Madalitso-v2w
    @Madalitso-v2w Месяц назад +1

    Boma ndi lomweli

  • @chisatisworld1
    @chisatisworld1 Месяц назад

    Apa ndiye wamenya wagwetsadi

  • @StellaKaunda
    @StellaKaunda Месяц назад

    Boma ilo 🥳😂

  • @CharlesChitanh
    @CharlesChitanh 7 дней назад

    Boma boma

  • @GaliGaliMalawi
    @GaliGaliMalawi Месяц назад

    Nyimbo yabwino kuposa lodzani zanu🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳

  • @dalitsochikhwasa8723
    @dalitsochikhwasa8723 Месяц назад

    Iweyo unabwera Tonse Ndia MCP koma chifukwa cha chamba ndi mankhwala ozunguza ubongo

  • @KamandoDavid
    @KamandoDavid Месяц назад +1

    Machende ako

  • @Alexkalonga-t9s
    @Alexkalonga-t9s Месяц назад +1

    Nazon ili ndi dziko pwanga be careful

  • @JohnSoweso
    @JohnSoweso Месяц назад +2

    Lozani zani was a powerful song
    Composition of the song
    Lyrics
    Sound
    Message
    It touches a lot
    This kutchaya kugwetsa , it's out class

  • @kgmkwanda8271
    @kgmkwanda8271 Месяц назад

    Ine phe kudikila cos ovotawo ndifeyo

  • @ManickYoungster-m5k
    @ManickYoungster-m5k Месяц назад +1

    Kape iwe

  • @SulaimanaSalad
    @SulaimanaSalad Месяц назад +3

    Monsemuja umasowa yojambulisira 😂😂😂😂😂😂 iwetu ukhaula akangochoka galuwakoyo pampandopo

    • @JaneNthala
      @JaneNthala Месяц назад

      Ndikufuna kuseka kma basi🙄🙄🙌🏼

    • @christophergibson72
      @christophergibson72 Месяц назад

      Tikuti sakuchoka mu sova

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy Месяц назад

      Chomwe chikunditsangalatsa ndichoti MCP sinawinepo payokha since 1994 until 2020 ndiye tiwona ali dolo ndindani 2025

  • @AyamiPhiri-f6r
    @AyamiPhiri-f6r Месяц назад

    🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @masmphanje
    @masmphanje Месяц назад +13

    Iyi ifike 1 million views bas🗣🤸‍♂️🔂

  • @WycleafDuncan
    @WycleafDuncan Месяц назад

    Bola Musazalire mukuyandama mu thobwa losapyalo

  • @KondwaniKautsi
    @KondwaniKautsi Месяц назад

    Mboli yake galu ameney

  • @verabenjamin7420
    @verabenjamin7420 Месяц назад

    More fire Dan lu 🔥🔥🔥

  • @GraceangelMdala
    @GraceangelMdala Месяц назад

    Song of the year iyi🔥🔥🔥🔥

  • @Kingwimuzy
    @Kingwimuzy Месяц назад

    Iwe ndi shasha adah

  • @MervisBerthaNyanda
    @MervisBerthaNyanda Месяц назад

    Chakwera my vote ❤

  • @Isac-y3z
    @Isac-y3z Месяц назад

    Ifé timadikila mbali yakuno🎉❤🎉🎉

  • @TasleemahDaud
    @TasleemahDaud Месяц назад

    Zizaoneka

  • @willoseven7579
    @willoseven7579 Месяц назад

    Katundu wa boma

  • @Hawkins_Witkid23
    @Hawkins_Witkid23 Месяц назад +1

    Official video kukanika kufika 10k video in 2 days
    Very sad my people
    2025 zizkhala choncho Pamene mcp ikuzasowa boma

  • @kondwanihenry2901
    @kondwanihenry2901 Месяц назад

    Boma ndilomweli lakuphali

  • @juniormedsonlungu1129
    @juniormedsonlungu1129 Месяц назад

    Kutchaya kugwesa BOMA LOMWELI KULIBE ZOSINTHA 🔥😂🤣

  • @MussahMbawalalah
    @MussahMbawalalah Месяц назад

    Boma ndlomweli bas

  • @edgarbanda7484
    @edgarbanda7484 Месяц назад +1

    🔥🔥🔥🔥🇲🇼

  • @IssacMateyo-u2d
    @IssacMateyo-u2d Месяц назад

    💓💓💓💓💓💓

  • @futuremoyo5714
    @futuremoyo5714 Месяц назад

    Yeah sakuchoka

  • @rafiqlimbilira940
    @rafiqlimbilira940 Месяц назад

    Kkkkkk
    Lozani zanu ife tione

  • @AgnessOffice-k6n
    @AgnessOffice-k6n 3 часа назад

    ❤❤

  • @rodgersdamison2313
    @rodgersdamison2313 Месяц назад

    Akhalitse Chakwera

  • @FastonBwanali-qe9qw
    @FastonBwanali-qe9qw Месяц назад

    BOMA LENELILI💥💥💥💥💥💥💥💥💥 page yanu pano yadusa 421K

  • @IdrysaApanachilipo
    @IdrysaApanachilipo Месяц назад

    Chikangawa sikuluza 😅

  • @gabrielmaluwa1038
    @gabrielmaluwa1038 Месяц назад

    Muzaiona mathelo ake

  • @justinchabwera5380
    @justinchabwera5380 Месяц назад +1

    Keep fire burning

  • @noelwilfredmandevu8274
    @noelwilfredmandevu8274 Месяц назад

    BOMA ndi lomweli

  • @MaxwellStoby-ku3wo
    @MaxwellStoby-ku3wo Месяц назад

    Boma sitingasinthe Chibwana ayiii

  • @FrankFirstMw
    @FrankFirstMw Месяц назад

    Tikuti sakuchoka

  • @KositaHaloon
    @KositaHaloon Месяц назад

    Ok chabwino ndava

  • @chikumbutsokachali4094
    @chikumbutsokachali4094 Месяц назад

    Akuva pain kuseliku❤️

  • @omaligeorge4296
    @omaligeorge4296 Месяц назад +1

    Kwacha zoti ikugwa dairy sunenamo Kodi kuti zinthu zikudura ayi sunenamo Kodi

  • @Geoffrey-k6o
    @Geoffrey-k6o Месяц назад

    Chipani chafukooooo