ZOOPSA IZI CHAKWERA ZAMUTONG’OLETSA MASO POTI ZIKUMUDIKILA PA ZOMWE WACHITA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 16 сен 2024

Комментарии • 50

  • @user-co6sc8om5n
    @user-co6sc8om5n 10 дней назад +8

    M'MALAWI WENIWENI SANGAVOTERE MCP MALAWI CHIKANGAWA PARTY YASATANIC

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 10 дней назад +2

    Abusa muuzeni uyu chikangawa yi Ambuye Yesu akumusiya poyera inu anapanga zoyipa kwambiri. anayiwala kuti maso Ambuye amamuona pamene amapha chilima munthu wosalakwa kom inuyo Ambuye azikutetezani inuyo Abusa❤❤

  • @GeorgeBanda-x6l
    @GeorgeBanda-x6l 11 дней назад +5

    kumawauza kumene anthu sakuwafuna cz munthu amene anawalowetsa m'boma ndi amene anamupha uja

  • @GiftKananji
    @GiftKananji 11 дней назад +7

    Akuti akuyesela zobela ma ballot paper apitisidwa ku south africa kuti azabere 😂

  • @lacksonkim9622
    @lacksonkim9622 11 дней назад +6

    Kuyankhula Koma uku ❤❤❤❤❤

  • @user-gx8or3yz9u
    @user-gx8or3yz9u 10 дней назад +5

    Malawi chikangawa party ng'ona partys

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 10 дней назад +3

    MCP means malawi chikangawa party 😂😂😂

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko 10 дней назад +1

    Kuswakuswa koma mwachilungamo😂😂😂😂

  • @user-qf7ko2dd5g
    @user-qf7ko2dd5g 11 дней назад +2

    Good meditation pastor

  • @AbudulJohn
    @AbudulJohn 11 дней назад +2

    Ine Sidik Mia ineso anandithandizapo ndili kwa Ngabu mpaka ananditenga ku mpaka ku Walisa farm kukawona anali munthu wa bwino kwambili

  • @AtupeleChitenje
    @AtupeleChitenje 10 дней назад +2

    Ndipo apa nde anapanga mistek yaikulu anyatu

  • @user-ws9sy7pp3w
    @user-ws9sy7pp3w 10 дней назад +2

    Malawi Chikangawa Party nick name yake (ng'ona party)

  • @BenjaminGasten
    @BenjaminGasten 9 дней назад +1

    DPP vote yanga

  • @AngolanChinga
    @AngolanChinga 10 дней назад +1

    Mr shumba musalile even ifey tikulila paka pano za chipani chakupha ngat chimenechi mulungu ndiwamkulu akuona zimene zikuchitik chakwela 2025 akuchok Mu Mphavu ya mulungu inshaallah

  • @Thewarrior7093
    @Thewarrior7093 10 дней назад +1

    The next government should just deregister MCP for all the crimes they have committed against the people of Malawi and for mismanaging the economy of our country and made Malawi poorer and useless in all of the world

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i 9 дней назад

    Tchera kumwezi nkhanga zaona ,kupezeka kugidwa mwayankhula mwamphanvu Malawi Chikangawa party 😂

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 10 дней назад +2

    I thank you for such a speech Reverend.I suggest if all religious leaders in Malawi could call H E and discuss how to redress the current problems Malawians are facing.

  • @JohnAssan-dn1he
    @JohnAssan-dn1he 7 дней назад

    Osaopa pastor mulungu alinanu

  • @ThomsonChipwele
    @ThomsonChipwele 11 дней назад +2

    Zoona mawu amenewo ineso ndikuti chandelier amalawi osavotela mcp

  • @IsaacMusa-py2jm
    @IsaacMusa-py2jm 11 дней назад +3

    Mau amphanvu 🙏

  • @berlz12k
    @berlz12k 7 дней назад +1

    Anapanga mistake kupha chilima and ambiri ozindikira anamutuluka uyu sangawine olo,anthu Ngati afika kudya chitedze ingawine?akhalamo okhaokha agalu amenewa..mcp 2025 ou”😡💩🦧

  • @KhonzoBlose-wq7zm
    @KhonzoBlose-wq7zm 7 дней назад

    Mulungu akudalitseni pa uthenga wanu wachikondi kwa Amalawi

  • @Thewarrior7093
    @Thewarrior7093 10 дней назад

    Chakwera ali Maso tudzuuuu diso ngati nkhwezule galu wachabechabe oononga dziko lathu la Malawi 🇲🇼.

  • @WillieKalipinde
    @WillieKalipinde 11 дней назад +1

    😂😂😂 Malawi Chikangawa Party (M.C.P)

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo 7 дней назад

    Chakwera Mulungu anamusiya kalekale ndi chifukwa chake Malawi ali mmavuto opsa werengani 2 mbiri, 15: vs 1 mpaka 5

  • @KaliyapaSeeter
    @KaliyapaSeeter 10 дней назад +1

    Nde mwati mcp ikuyimira chani😂😂

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 9 дней назад

    Palibe angavotere mcp palibe

  • @rhodamaunge-uq5dz
    @rhodamaunge-uq5dz 10 дней назад

    Amen pastor

  • @Donald378
    @Donald378 9 дней назад

    Ine wamangochi kom sindingavotele mcp

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali 10 дней назад

    ❤❤❤❤❤❤ kung'alila kwabwino ndithu ❤❤❤ Mr chikangawa azipita kukasiya

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 11 дней назад +1

    Mdipo asatana awq

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr 9 дней назад

    Masamu ake akugwiritsa ntchito am'ma 60s

  • @user-gm9xj1wc2m
    @user-gm9xj1wc2m 11 дней назад +1

    Ok bwana

  • @MalizeniOliviaBridan
    @MalizeniOliviaBridan 11 дней назад +1

    Mawu mfiti zimenezi

  • @user-ol4cf2oh5u
    @user-ol4cf2oh5u 10 дней назад

    Anangowona kuzichita 💔 akanadzapikisana ndi chilima or akanadzathesa gwilizano myb akanawina

  • @ernestphiri5507
    @ernestphiri5507 10 дней назад +1

    Abusa mukunena zoonadi

  • @FebbieNjewa-g3k
    @FebbieNjewa-g3k 10 дней назад

    APM my vote

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 10 дней назад

    Mcp thawi yawo yatha panakakhala kuti ali ndi umuthu anakasiya pansi kuti ena apitilize kuti zithu zibwerele ngati kale koma Allah akuona zikuchitikazi ndiye thawi yake ya Allah ikakwana palibeso kususa ma comrade tikuvuka kwambili ndi dziko rathu

  • @jamessheki4293
    @jamessheki4293 10 дней назад

    Ukakhala oipa anthu amakuthawa

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 7 дней назад

    Komaso no one can join mcp ngati allowance awa ulendo basi

  • @philipoga2401
    @philipoga2401 10 дней назад

    mboli ya make chakwera or sidik miya anachita kumuphaso sinali corona

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti 10 дней назад

    This is 2024 Century.

  • @rhodamaunge-uq5dz
    @rhodamaunge-uq5dz 10 дней назад +1

    Ku mpoto
    0%

  • @user-xt2gu9yt9q
    @user-xt2gu9yt9q 10 дней назад

    Ndipo malawi weniweni sangachongele mcp aataaaa kupha 2 much

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y 10 дней назад

    Mulungu walankhura kudzera mwa mtumiki wake 😅😢

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 10 дней назад

    🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤸🤸🤸🤸🤸kumeneko M C P

  • @EnockMunthali
    @EnockMunthali 10 дней назад

    Ali ndi manganya yekha

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 10 дней назад

    Ulemu wanu mung'aluleni basi

  • @KenMalasa
    @KenMalasa 10 дней назад

    Km mcp abalee