Salute dc,,,you are 1in a Billions of people here in Malawi,,,Popanda inu a dc aah boma lingamatidode kwambiri,,,Mulungu apitilize kukupatsani Moyo wautali kufikira mudzakhale Minister or advisor wa dziko 2025 Salute Dc
Koma ine a born kalindo ayi zikomo,u ur one in a million aaah ayi zikomo,,,kkkkkkk oh uyu wazobwirabwira ayi tamva bwana mulungu akhudze malire amoyo wanu dc
Ndipo ife mpaka three yrs ndlama zamalemu mayi MA fees mkumasowa magesiwo ndemusanene tinangokataya Ku escom ndlama mpaka three yrs bon kalindo your God sent
Nkhani ndi yoti wa pension akuyenera azipasidwa ndala yake yose azithandiza pakhomo pake,ine ndili ndima cousins Anga omwe bambo awo anapangidwa chipongwe Ku sanje anaotchedwa ndi Moto mnyumba anali a police atangopangidwa transfer kumene,ndalama yawoninatuluka koma Kuti akazi awo ndi ana awo apasidwe zikuvuta kwambili ana ose 5Ali pa school mzimayi yekha atani kuthamdiza kwake kupita kuboma Kuti athandizidwe amawauza Kuti ndalama imeneyo Ina mutigaile Kuti mupasidwe ndalama Zanu komaso simutenga zose Kodi kukhala kwanji uku Malawi ulamuliro uwu ndiye okanika wankhaza greedy pasogolo amangoganizila Za mimba zawo ndi achibale awo they don't care Za mavuto anthu ena

Osafooka Born kalindo our president the real man the DC🔥🔥
🔥🔥🔥 km ndie atiphaaa
,atiphaaaa! Hmm zogwetsa mphwayi
The DC big up boss
Koma ine a born kalindo ayi zikomo,u ur one in a million aaah ayi zikomo,,,kkkkkkk oh uyu wazobwirabwira ayi tamva bwana mulungu akhudze malire amoyo wanu dc
Kkkkkkkkkkk the DC mwana oophya kwambili amene akuzunguza boma lachakwela
Kma ka ma drama uyuuuu😅😅😅😅😅 Dziwe thank you for good job
Koma chakwela anakulakwilani chani akupepeseni
Yalero yandiwaza pamene amati km uyuuu😂😂
I like the way momwe opposition yathu ikugwilira ntchito.mudekhe momwe mwadekhelamo coz amalawi tinanyanya kutengeka ndi zinthu zopanda pake
Ndipo ife mpaka three yrs ndlama zamalemu mayi MA fees mkumasowa magesiwo ndemusanene tinangokataya Ku escom ndlama mpaka three yrs bon kalindo your God sent
❤I love you the DC
The DC ❤❤
Kuswa kuswa
9:27
The DC 🔥
Ulemu wanu bwana Dc
The musamati dziko la Malawi km muziti boma lachakwera boma lakupha
Love this 🎉
U did it nkhani ya MRA komaso Toll-gate,why not force the government to do the same pa nkhani ya pension the Dc?
Dc big up the fighter
Ayi akugwira ntchito kwambili akumenyera amalawi ufulu kwambili
Pangolin 💪💪💪
Lipase moto kalindo
❤❤
Yankhulani boss,
Salute
All the best The DC
The DC coming wave after wave 🔥🔥🔥
Ndipo Chakwera has failed this country🙌🙌🙌🙌
Nkhani ndi yoti wa pension akuyenera azipasidwa ndala yake yose azithandiza pakhomo pake,ine ndili ndima cousins Anga omwe bambo awo anapangidwa chipongwe Ku sanje anaotchedwa ndi Moto mnyumba anali a police atangopangidwa transfer kumene,ndalama yawoninatuluka koma Kuti akazi awo ndi ana awo apasidwe zikuvuta kwambili ana ose 5Ali pa school mzimayi yekha atani kuthamdiza kwake kupita kuboma Kuti athandizidwe amawauza Kuti ndalama imeneyo Ina mutigaile Kuti mupasidwe ndalama Zanu komaso simutenga zose Kodi kukhala kwanji uku Malawi ulamuliro uwu ndiye okanika wankhaza greedy pasogolo amangoganizila Za mimba zawo ndi achibale awo they don't care Za mavuto anthu ena
Ati wazobwirabwira😂😂😂😂
Uthenga omveka bwino kwambiri amenewatu atikwana sitikuwafuna.
The DC kung'alula kung'alula 🔥🔥🔥🔥
Bg up mr bon kalindo
Uyu nde. Atiphadi eee waonjeza ndipo dziko lino adaliloza ndani 😂😂 misoz yosatha ndipo Malawi yemwe angavotere chakwera NDI mfiti ndithu ndipo Ali makolo anga kapn bale wanga kuvotera MCP ndimuda kwambiri coz azawo adalamulira dziko km sizidafike pamenepo km AMBUYE atikondere kubwera mpulumutsi osati MCP eeeee kupha kuba ndi kuononga pomwe afikapa even satana akudabwa nawo
Kkk 🔥
Kabwirabwirayo nde eeee kkkk wanyaynya hvy
Kalindo the DCC umakwana🤣🤣🤣🤣🤣
Yes Escom yavuta
😂😂😂😂 uyu atipha 😂😂😂😂
Dcccccc bon kalindo
Komatu dzoona chifukwa emcp chilowelen m,Boma Palibe chilichose chkuyenda ndiye aloweso atimaliza
The Dc Bon kalindo good message ❤
More fire 🔥 Booooon kalindoooo
Kkkkkkk Jahena km!!!!
Following
The DC ❤❤❤❤
Mbava za chabechabe
Kalindo umakwana😂😂😂😂😂
Takunyadilan mumatipasa chilimbikiso
Yaankhulani abwana, perfect
Chakwera has failed than any president we had before. America kuchita kuwagwira ndikuba Komanso kuchita kunena Kuti Chakwera and his party has failed.
Zikomo kwambiri munthu wamkulu
Kabwira bwira kkkk
❤❤❤❤❤❤❤❤ dc ndiye wan
Akti akabwira bwira 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Akanuna pa chilungamo
😂😂😂😂,,kabwila bwila
Kkkkkk kma ndaseka ati kma uyuyu uyu atipha
Akuthandiza the dc❤
Hmatiyimirira adara dc
Akamanena kuti Malawi ndi dziko loopa Mulungu aaa zodabwisa ndithu
Koma chakwera ay ndi tu mulungu amuone chakwera kuono nga dziko
Report yandege bwanji????
Ali siliyasi poimila anthu osauka ,wakeup malawi
The D.C
Udapenga iwe ukat bakili muluzi utiyo ukumunenayo uja anthu amafa ndinjalawa
Panopa wazindikila kut multiparty si abwino kamuzu anakuuzani kale koma kusanva
Nice guy
😂😂 The DC iwe ndi one
Follow you DC
Awine adzidzatani dzikuwanyerazi
apat bon kalindo nkhani zakuthera!! palizinthu zina zimalakwika olo mabanjamu koma chilichose kumangoloza president!! we know you are funded by DPP
Dc
DC fire
😂😂 SC
Koma kalindo kkkk kkkkkkk
Kkkkkk the DC
The dc
This is too much!!
kkkkkkkkk
Dangerous Child
To that extent america giving us that warning
Tourism Minister saying 12 billion for what what what shame on u 😅 who voted for these idiots
Kodi ACB yilimo mmalawimu?
❤❤
Dc
Koma kalindo kkkk kkkkkkk