A POLICE AYANKHURAPO ZOKHUNZA MLANDU WA AKALIATI NDIPO AKUTI AKAONEKERA KU COURT MONDAY PA 28

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 26 окт 2024

Комментарии • 117

  • @DennisTobias-b4r
    @DennisTobias-b4r 7 часов назад +4

    Mozadusa mmbali chakwera ndi Big suspect ndipo anamupha chilima ndipo mwini wake chilima Ali ndi umboni

  • @JacquereenPereira
    @JacquereenPereira 4 часа назад

    Ananenatu Kalindo Antanyiwa kuti Athu Ambili amangidwa mix Akaliyati chakwela angofuna kuphimba khani yandege iye ndiamene ana pha chilima

  • @dinchisale
    @dinchisale 9 часов назад +8

    That's indeed good idea I support it

  • @ManMen-kp2ze
    @ManMen-kp2ze 8 часов назад +3

    Apolisi, ngati munali musanafufuze za mulandu wa a Kaliyati nde mmamumangilangi, Patu mwamulakwira chiire, coz it's already more that 48 hours now, Malawi Why? Our police, why,

  • @YousufuJohn
    @YousufuJohn 8 часов назад +4

    Mcp ndiyakupha yankhanza si chipani chakuti mpaka kumachisekelera fokof

  • @GodfreyKadzombe
    @GodfreyKadzombe 3 часа назад

    Kuti aphedwe Chilima adatsekula khomo kuti akuphawo abwere munyumbamo ndi Manganya bambo a sikono koma thawi yamuthela

  • @AdenaGuest-g4b
    @AdenaGuest-g4b 6 часов назад +2

    Mapwalaakeameameneyo

  • @bornwellyona6447
    @bornwellyona6447 8 часов назад

    Am Pastor Yona ,its good to live the political party members out in team because it must be neutral

  • @giftkayome3568
    @giftkayome3568 7 часов назад +2

    Ndiye akanapanga Kaye kafukfuku kenaka ndikumanga munthu because her rights are also violated as we know kuti anayenera kukawonekela ku Court pasanathe 24hrs.

  • @VitumbikoKaunga
    @VitumbikoKaunga 9 часов назад +1

    Munthu akamumanga pamafunika anene chomwe alakwa nde azikhara asoziwa chomwe alakwa😢😢😢😢

  • @AdenaGuest-g4b
    @AdenaGuest-g4b 6 часов назад

    Asalemelapakati

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 9 часов назад +3

    Chifukwa chiani a police amatamangila kumanga munthu asanafufuze zomwe munthu wapalamula.? Malawi yikuluza ndalama zambiri za boma, for nothing. Zitsilu!

  • @Milanzi-nb5fv
    @Milanzi-nb5fv 8 часов назад +2

    Muthu anapha munthu nzake ndi futi koma osamangidwa koma akunanga munthu oganizilidwa kuti amafuna apalamule, no sense

  • @MasterNkhono
    @MasterNkhono 5 часов назад

    Sizithauza kathu zimenezo ayakhula akubaj

  • @khanilapozo-fj5tq
    @khanilapozo-fj5tq 9 часов назад +3

    What kind of the case is this? Arresting some then investigating?

    • @BrendaJailosi
      @BrendaJailosi 8 часов назад

      Kaya mwina malamulo adziko anasintha mmmmhu

  • @bornface4786
    @bornface4786 5 часов назад

    Komano ndikanandano kuti mnyamata wapatawa ya MTN uja akumane Naya akamapanga kafukufuku coz zikuoneka kuti iyeyo ndi eye witness

  • @BlessingsUndih
    @BlessingsUndih 8 часов назад +1

    Akuyenera akhaulisidwe pakafukufuku wadege chifukwa akudziwapo kanthu

  • @Dickies-mk8cd
    @Dickies-mk8cd 6 часов назад

    Chakwela sindinafune kutulutsa mau awa, panyini pamkazi munthu oipa kwambiri iwe.

  • @PatrickLysonPeter
    @PatrickLysonPeter 5 часов назад

    Aku banja a kwa Chilima akhalepo pa zakafukufuku.

  • @Dickies-mk8cd
    @Dickies-mk8cd 6 часов назад

    Mcp mukungotayapo mavoti apa, yachikangawa siinathe mwayambanso iyi?

  • @StevenTembo-mb7rm
    @StevenTembo-mb7rm 5 часов назад

    Kalaya ndi chakwera mapwala anu nonse

  • @MveraNambala
    @MveraNambala 5 часов назад

    Mmm zchisoni chipani chooipa zedii

  • @EdwardMathuwa
    @EdwardMathuwa 8 часов назад +1

    Mbole zanu a police a mcp ndi president wanuyo chakwela

  • @ChrissySalimu
    @ChrissySalimu 8 часов назад +1

    Km zoona mutasowa zochita kumugwila zimai kumakamuzuza Ku ndende mulandu musanaupeze zoona mmmmm mudziwe yesu ndiophuzila ake

  • @BlessingsMarley-l2x
    @BlessingsMarley-l2x 6 часов назад

    Ndikanakonda mukomitiyi mukhale munthu umozi wa kubanja popanga kafukufukuyo

  • @Muhamassa
    @Muhamassa 6 часов назад

    Achakwela amwalali😂😂

  • @DavidMtambo-e3b
    @DavidMtambo-e3b 8 часов назад

    Akutanthauza chan ma pioneers a chakwera wa, si apolisi a ife amalawi koma ndia chakwera.

  • @DennisTobias-b4r
    @DennisTobias-b4r 7 часов назад +1

    Muyamike kuti mulungu anasiya kuulula kwa aneneri ngati ngati kale mukanaona inu, kafunseni mfumu David inapha uriya muhithi pomuika pa malo pathina nkhondo kenako anaona ngati plot yatheka koma mulungu anamuuza zonse anapanga, themberero kwa oyandikana ndi oipayo mwazi wa chilima

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 7 часов назад

    No sense, an professional mcp police why can't you arrest chakwera who killed 9 people including vice president.

  • @supa4dupa
    @supa4dupa 8 часов назад

    Mulando waboodza ,kubvutitsa basi.Police ypo manga munthu pali be umboni wa mulandu,Mulungu akulsngeni kubviutitsava opposition,nrhawo yanu izafika.

  • @JeremiahKapundu-j1p
    @JeremiahKapundu-j1p 5 часов назад

    Umbuni sungapezeke pokhapokh a independent

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 7 часов назад

    Akupha awa MCP kwathandidza kulowa boma mistake ya UTM

  • @ManMen-kp2ze
    @ManMen-kp2ze 8 часов назад

    I COULD BE HAPPY IF ONE FAMILY MEMBER WAS INCLUDED IN THIS COMMISSION OF INQUIRY, EVEN ONE MEMBER OF uUTM

  • @AmosScott-z9x
    @AmosScott-z9x 9 часов назад +1

    Apolice mukanangosiya kupemphera kumwamba chanu kulibe mwatanganidwa ndi za dziko

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr 5 часов назад

    This is not independent body in Malawi.

  • @Dickies-mk8cd
    @Dickies-mk8cd 6 часов назад

    Mcp ndichipani chomvetsa kwambiri

  • @JafaliChiwimbi
    @JafaliChiwimbi 9 часов назад +1

    Tawelengani chichewa ife zikukanika kuno 😢😢😢

  • @MikasHsiwwh
    @MikasHsiwwh 6 часов назад

    Pakhalabwaji chilukgano pamene mugulumo mulioipaokhaokha

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 6 часов назад

    Akalaya machende anu chomwe mumuzuzira kaliat nchani

  • @ChrispineJonathan
    @ChrispineJonathan 7 часов назад

    Angosankhana okhaokha a mcp bwanji osatengako akubanja pali chinyengo apa

  • @TinaKazembe-l7d
    @TinaKazembe-l7d 8 часов назад

    Kodi mukamangobwereza bwereza , adzuka , ? Poti aliyese Ali ndi ifa yake ,

  • @Chikwawa
    @Chikwawa 9 часов назад +1

    Kodi a police amadziwa malamulo pa ufulu wamunthu?Kapena akuyendela malamulo akamunzu.?

  • @HassanTwaibu-c6h
    @HassanTwaibu-c6h 8 часов назад

    aaaaa agulu akupa inu apolice anthu osachita bwino

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d 8 часов назад +1

    Koma ndale zaku malawiiiii

  • @IanAllstal
    @IanAllstal 7 часов назад

    Komatu mukuzichotsera ma vote ok tieni Nazo Ngati Ndinu ma Doro osathesa mavuto tirinawo mziko Muno

  • @VitumbikoKaunga
    @VitumbikoKaunga 9 часов назад

    Zoona nkhuni ina ija ya aromwe amati usi ndiwakupha ndiwakuphadi 😢😢😢😢😢😢😢😢

  • @ShakiraJackson-x8w
    @ShakiraJackson-x8w 8 часов назад

    Yes it suppose to be like that akanema nawo azikajambura live

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali 9 часов назад +1

    chonde a Peter chimalaya musamugwirire mzimayiyo kumeneko a Peter chimalaya

  • @KondwaniHara-i2v
    @KondwaniHara-i2v 7 часов назад

    Why not to put his wife so that she can have some pictures

  • @RuthJopilo
    @RuthJopilo 8 часов назад

    Amaiwala kuti kunali anzawo kunjaku alikuti?kuchita kulitenga dziko ngati lambuyawo.

  • @CharlesChagudubuka-rm6bh
    @CharlesChagudubuka-rm6bh 9 часов назад +1

    Police State!!!! Ikadakhala mbewu,tikanakazinga yonse kuti ana athu mbewu imeneyi asazaioneso,coz it's not Police service

  • @SimonNyasulu-m6s
    @SimonNyasulu-m6s 7 часов назад

    Simon nyasulu rumphi tifunan tiziwe ife

  • @ChrispineJonathan
    @ChrispineJonathan 7 часов назад

    Akubanja palibe bwanji?

  • @ChikondiMusaya
    @ChikondiMusaya 5 часов назад

    Mbuzi zawanthu inu apolisi

  • @mansonchinkhuzi
    @mansonchinkhuzi 7 часов назад

    Kodi madokotala aku central aja anawawuza chani akubanjawo

  • @trustDaud-gu6ke
    @trustDaud-gu6ke 8 часов назад

    Iwe chakwela tamutuluseni dzimaiyo bwanji kodi chamba eti

  • @AnthoniohMazengera
    @AnthoniohMazengera 8 часов назад

    Zazi ndale zaumbuli 😂😂😂😂

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 9 часов назад

    Manganya
    Chakwera ndi nduna zake athu awa ndiakhaza chifukwa cha ndale kumumanga muthu basi koma thawi ndi nyengo ikubwera pompano musamatenge ngati dziko ndi rakwanu nonse a mcp thawi ndi nyengo ikubwera
    Osaopa osatopa osafooka Allah alipo

  • @CrispineBetha
    @CrispineBetha 9 часов назад +1

    Plan yamanganya iyi mothandizidwa ndi chikangawa

  • @AustinBornface
    @AustinBornface 9 часов назад +2

    Tili pompano ndipo tidzaonana

  • @mishecksipolo7153
    @mishecksipolo7153 8 часов назад

    Which one is which ?investigation before or after arrest? Mukuwuzana a mcp nokhanokha or the Nation ,that communication is useless,trying to fool Malawians

  • @EmmanuelMponda-ig9bm
    @EmmanuelMponda-ig9bm 9 часов назад

    I a good idea azijambula chilichomnse zithandiza kuulura choonadi

  • @GradinaNgalande
    @GradinaNgalande 7 часов назад

    Ine,kanakonda wakubanja mozi akhalemo mukomitiyo

  • @munikabambe7625
    @munikabambe7625 9 часов назад

    Ambuye, musamayankhule ngati mkazi kapena ngati ndinu mwana, these guys arrested her without evidence hence just wanted to punish her...

  • @MacleansKatungwe
    @MacleansKatungwe 9 часов назад +4

    Zacbibwana, why arresting someone without finalizing type of case committed. Zanuzo musatiuze our parents used to tell us that MCP ndi yankhanza koma kusamva kwathu.

  • @JonathanMunthali-n3c
    @JonathanMunthali-n3c 9 часов назад

    Namia ndiufulu wanu msapiteko ntchito yomenyera ufulu yikukwanila kokalumbira mukadyako chibazi

  • @MikeBatson-d6k
    @MikeBatson-d6k 6 часов назад

    Panyapanu inu musiyeni kaliyatiyo

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 9 часов назад

    Koma police yaku Lilongwe yachukatu pita chimalaya ndianzake umbuli ulipo

  • @VioletMbale
    @VioletMbale 7 часов назад

    Ngati sanapalamule amafuna kupalamula nde mwamumangila kut amafuna apalamule? That is nonsense

  • @HardwickKaunda-o7j
    @HardwickKaunda-o7j 7 часов назад

    Kodi wandale akalakwa asamamangidwe? Kwachuluka ma saveg

    • @robenallie6985
      @robenallie6985 6 часов назад

      3day without charges malawi police useless

  • @JustinPhiri-kq2bb
    @JustinPhiri-kq2bb 8 часов назад

    Wathuyo akangodwala olo kungodula moyo wake muzatimva

  • @DennisTobias-b4r
    @DennisTobias-b4r 8 часов назад

    A chakwera musaduse mbali mesa ku state House koko, asanavuvuzidwe za ngozi ya ndege chakwera ayankhe yemwe anamuuza kuti ndege inafika ku mzuzu ndipo anaibweza ndani, anamuuza chakwera kuti inaomba Phiri ndiyani, kenako mkulu wa asilikali anamuuza kuti ndege sinafike ku mzuzu ndani ndipo inagwera kuwilira moti asilikali sanakafike, Mr mkukuyu Black box la munatiuza kuti mwalisunga liri kuti nankha lipoti la ku Germany akuti munalibe Black box, pali wamkulu Ali ku mwamba akuona zonse ndipo akuyalusani, thanks bakili muluzi popanga kafukufuku wa a China gadama ndi ma friends ake inalibe chinyengo ndipo Malawi anakhutira, Zikomo Joyce banda pa kafukufuku wa malemu bingu a libe chinyengo koma izi ai sipazakhalabe chilungamo, choona chitadziwika chakwera ndi mcp members akazatuluka boma

    • @LeonardNapwanga
      @LeonardNapwanga 6 часов назад

      Ndale it's a dirty game.
      wishing u (Akweni) all the best
      Davil is a liar!!

  • @FiskaniLungu
    @FiskaniLungu 7 часов назад

    Poor government

  • @MildredLongwe
    @MildredLongwe 9 часов назад

    Aaaaa kma ndipo kwanukhaditu

  • @KefatiKozekan
    @KefatiKozekan 8 часов назад

    Koma ine sindipeza Iwo ngat orakwa pazimene arankhurapozi

  • @patrickjaenda8288
    @patrickjaenda8288 8 часов назад

    zoona yudasi usi osalankhulapo kanthu

  • @JamesMwale-o6i
    @JamesMwale-o6i 8 часов назад

    Aboma akakamizika ndiye mzovuta kuwa va

  • @AdenaGuest-g4b
    @AdenaGuest-g4b 6 часов назад

    Zauchiziru

  • @Dauson-j5i
    @Dauson-j5i 9 часов назад

    Ndichifukwa chani anamanga mayi patrisha kaliati akuziwa kuti kafukufuku wa ndege akhalanso akuchitika konseku ndikubvunganyiza

  • @WestonGawaza
    @WestonGawaza 8 часов назад

    Akweni atuluke akapange mavoti awo

  • @MariaNkhata-i9q
    @MariaNkhata-i9q 9 часов назад

    Sakufuna kuti amayiwa akapikisane nawo pa convention ya utm

  • @RebeccaChikalenda
    @RebeccaChikalenda 8 часов назад

    Kma ndye bora iri ndronukha bwanj

  • @Chikwawa
    @Chikwawa 9 часов назад

    Olo mumusunge mpaka kufa kwanu, kuti mutchuke.

  • @JonathanMunthali-n3c
    @JonathanMunthali-n3c 9 часов назад

    Mfumu inailiyose imasapota president

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 7 часов назад +1

    Aaaa ndale dzabodza idzi

  • @KondwaniZuzanani
    @KondwaniZuzanani 9 часов назад

    Dziko linoo linamvuta ndinthu

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 8 часов назад

    Mulandu ulipo tidikire court Monday

  • @TenganiObety
    @TenganiObety 9 часов назад

    A Limpompo Bakili Muluzi TV ananena musatiputsise

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 8 часов назад

    Monday Ndikuti ndizaboza mukupekela milandu yaboza

  • @SovietMzungu
    @SovietMzungu 9 часов назад

    Ndale si tipangila maliro

  • @dyba-x9w
    @dyba-x9w 9 часов назад

    Vuto longothamangira kumanga munthu pasanapezeke umboni weniweni munthu asanamangidwe

  • @annembepula
    @annembepula 8 часов назад

    Mwamuzumza munthu wa mai kulakwa

  • @FlorenceMasangalale
    @FlorenceMasangalale 9 часов назад

    Zomwe akunena avarerazo tagwirazana nazo zikhara pa air

  • @TenganiObety
    @TenganiObety 9 часов назад

    Samalani ndi namiwa sikukbwela chilungamo uku

  • @ruthmissi7766
    @ruthmissi7766 9 часов назад

    Hmmmmmm bt why guys

  • @MadalitsoNansansala-wm2rk
    @MadalitsoNansansala-wm2rk 7 часов назад

    😢😢😢😢

  • @SelemaneAdamo-r3v
    @SelemaneAdamo-r3v 9 часов назад

    Its so sad

  • @GoldenNamanguya-q9u
    @GoldenNamanguya-q9u 9 часов назад +2

    Zufuna pajatu akweni amamutamandila chikangawa ndiye lelo asamadandawule

  • @IsaacChandawira-q9b
    @IsaacChandawira-q9b 8 часов назад

    Police ndinchito Yao yomanga anthu ngat kaliyat musamutae ameneyo galu wamunthu

  • @JoeBanda-gk4ss
    @JoeBanda-gk4ss 9 часов назад

    Malawi wanunkha uyu