Mr usi wosayiwala chinthu chimodzi choti muwaphunxitse ma department onse a boma kuti wogwila ntchito azilankhula bwino kwa anthu wofuna kuthandizidwa.anthu wogwila ntchito za boma uko kumudzi amachuluka mwano zeedi samalankhula bwino ndi anthu .
Thanks for the visit kmano ndikuona ngat mafumso a mkulu anapangidwa raise aja ndamene anali chifukwa chokhacho chimene tikadat kupezeka kwao was very important
As for me the devil is the devil even if cooking food and give it to the poor,, ntchito ina iliyonse yomwe sasana angapange singamusinthe, ndi satana basi Michael Ussi ndi munthu woyipa intima ngati imfa adagulitsa mwazi wa a Chilima yudas wa lero
Why driving licences are only printed or issued at the regional level not paying attention to the high demand for these? Same with the Passports. Look into these issues very carefully. Come to Zambia and other neighbouring countries, there is nothing like what you are doing out there. Remember we are not in 1921.
The music in the background is very irritating. Please stop using background music in these videos.
Good job Dr usi anthuwo akuzuza anthu ngati dziko si lawo anthuwa muwaphuzise
Mr usi wosayiwala chinthu chimodzi choti muwaphunxitse ma department onse a boma kuti wogwila ntchito azilankhula bwino kwa anthu wofuna kuthandizidwa.anthu wogwila ntchito za boma uko kumudzi amachuluka mwano zeedi samalankhula bwino ndi anthu .
Ddr😢😢
Big up VIP my vote
Thanks for the visit kmano ndikuona ngat mafumso a mkulu anapangidwa raise aja ndamene anali chifukwa chokhacho chimene tikadat kupezeka kwao was very important
i will vote for whatever party this guy will be, he is the best
Those are tbe most corrupted gvnmnt institution ever with outdated admin machines and poor nertwork systems......
Every monday nertwork kulibe
Respect bwana vp
Usi is a fault finder, when one is busy answering to his question he pays less attention whilst looking for the weak link.
He must visit all the Home Affairs departments also plz
Km mukuyenda mwachangutu,,,big up VIP
Go ahead to check amain government offices
Imeneyo ndiye ntchito ya vice , keep it up Mr vice , timakukondani
As for me the devil is the devil even if cooking food and give it to the poor,, ntchito ina iliyonse yomwe sasana angapange singamusinthe, ndi satana basi Michael Ussi ndi munthu woyipa intima ngati imfa adagulitsa mwazi wa a Chilima yudas wa lero
Back ground song its disgusting inu muzikula foolishh
Good job VIP
Kodi ma garasiwo amakhwepa?
Why driving licences are only printed or issued at the regional level not paying attention to the high demand for these? Same with the Passports. Look into these issues very carefully. Come to Zambia and other neighbouring countries, there is nothing like what you are doing out there. Remember we are not in 1921.
Mr vice president MULUNGU anakuikani ndi cholinga, Ambuye apitilize kutetezeni ndi kukupatsani mphanvu ndinso Moyo wautali
Big up my president ndinu nokha ndaona chikhulupiliro
Mopermpha avice president please tithandize kuti apolice asayime musewo umodzo same road eg from Mzuzu to Nkhata-Bay mupaka 7roadblock. And onse akufuna kukubela ndalama kodi mwini galimoto apitundula chani, nanga anthu especially driver alandila ndalama zichoka kuti
Too late to implement SKC reform s!
Iwe unali kuti
Remove the background song
Malawi can't change ndizochitika za anthu amaudindo like ku Emigration shame
Tapitan ku ma passport ko inu
Nice one
Anthu amenewo ndizithunwa zotunidwa ndi satana.zabwera kuzawononga dzikolo .
Vice president Immigration ndi Road traffic mwaikila kumbuyo konseko ziphuphu
Uyu atakhala president zinthu zitha kusitha
Tsono za ku immigration bwanj sanaonetse 😂 akukondera galu ameneyu
mwachita bwino bwana kuwayendera amenewa ndipo muzibwerabwerako kumeneku coz mmmm kumachitika zopusa kwambir
Komatu bwanawatu asangoyendatu things need to be changed
Ka short ati chani . Spite ku immigration
Nice
Azawo zimayenda km zamaenda ma office km awa ndikudabwa nawo bwanji asangot akufuna allawasi bwanji akutitenga ngat sitikuziwa
Munnthu ndi Munthu basi sayamika
ma process a kumeneko amatalikadi bwana
Ptrzani kuedera ma office Aboma,maka Kuma migration office kuli cinyengo kwambiri, very very corpution
I like micheal usi and I will vote for him as running mate kenako president uyu awatutumusa ambiri ndipo anthu azigwirano ntchito
Bola kuyenderaku kubweretse kusintha
Koma zitithandiza?
Remove background music please
Lero umayenda mbamva zokha zokha
Nde mukozetu zinthu.
Too late
Iweyo udali kuti ?
Or mupange bwanj tikawonana ku conversation bas
Convention
Kukakhala zotani ?
Ma reform a SKC ana block aboma la MCP mesa ndiwomwewa
Ndiye tikamati Usi ngwa MCP mukumakana patipo
Ntchito za boma sizimayima chifukwa wina kulibe
Kkkkkkk
Amalawi timalimbikila kapena kusamalila zinthu tikanva kuti tiyendeledwa ndi akuluakulu
Koma tchito ilipo
Bwerani kuno ku capital chinyengo chili kunu ndalama zikungoyenda mma buti a Usi fufuzani kuti katagale aneneyu akuchokera pati
Ma licence tikulipila zambili kuposa zopita ku Boma
Kd inu tamugulileni magalas asamahvuke kumaso please amatipangotsa manyazi 😂
Zako izo ulimbana ndi mabwana
Pitani ku lilongwe bwana
Mwaziyamba mochedwa zinthu zavuta kale komanso zinayenera akayambe ku lilongwe akuopako chani
Iwe udali kuti pamene amachedwa ?
Anthu ena amasaka kupunthidwa
Madala usi
Ku immigration alankhulana muchitsitsi Ife sitinamve chilichonse Koma uku akuchuluka nzeru machende ake
Iwe uchedwa ndi kunyoza , mwina mulungu amakudalitsa ndikunyozako !
Sikono amusiya kuti 😅😅😅
Alikunyumba kkkk😊
Kutha kwa dziko.la.malawitu uku koma a malawi simukuona zigonani
Iwe umaona ngati ndiwe wamuyaya ?
respect bwana ntchito yabwino kwambili
Opusa uyu ndale basi akungoyendera kummwera basi
Iwe ochenjerawe wapangapo chian ?