TV yasala kumalawi kunotu nde ndiyomweyi basi, Times TV ija nde ayimaliza kale,atsekesa program ya Kwagwanji,hot current yosakoma ingobwela kuzalankhu za Neef zoti amalawi ndalama sitinatenge agawana okha okha, A Brian Banda ndi awo angozungilili kumangobwela ndi ma exclusive opanda ndi nchele omwe' Anyamata a Times tv atha basi kkkkkkkk ndalama ndiyowopya keep it up bwana,ukugwila ntchito yotamandika,koma try to come back with your voice. Good luck
Voice message yanu ndiyomweyikuyifuna osati izizi
Voice ija muli uthenga
Missed your voice boss man nkangowona ka notification ka bakili TV u run like nobody business
Welcome back, strong man 💪💪
Best Chanel in Malawi
Moyo waziko lapasi mng'onyenga
We need your voice message sir bravo
Musamasewe chochi brother
Ipondeni fadah ❤❤❤
Best TV 🔥
Best TV
Best TV ever in human history
We love you ...
Best Tv.....makwanà. Inuyo Brother❤
TV yasala kumalawi kunotu nde ndiyomweyi basi,
Times TV ija nde ayimaliza kale,atsekesa program ya Kwagwanji,hot current yosakoma ingobwela kuzalankhu za Neef zoti amalawi ndalama sitinatenge agawana okha okha,
A Brian Banda ndi awo angozungilili kumangobwela ndi ma exclusive opanda ndi nchele omwe'
Anyamata a Times tv atha basi kkkkkkkk ndalama ndiyowopya keep it up bwana,ukugwila ntchito yotamandika,koma try to come back with your voice.
Good luck
Timakunyadilani brother man Allah azikutetezan
Best ever tv
I like Brass bank song yo , mmm, imandifikapo....
Campaign anthuwa anayankhulatu, koma mmmm,
Best TV 📺 ❤
Chikape cha president ichi zintchito ngat mwana wa primary
Ndimamva kukoma ndikaona nkhani zanu daily.long live b tv
Chaaaa ndipo Inu chakwera ayi zikomo tikapuma kumwamba basi
We need more vedio munasowa kwambiri
Welcome back
I lov u bro
Bwana voice yanu tikuyifuna
Ine mbalame ayiyo ndiye sifunas kumva
Ulemu wanu brother
Am watching u
Mc Hendie =Chakwera
Ntchindi zikukhumbika, vakutuka yayi, vilekeke Lamulo lindazomerezgepo kutuka, ntchindi ziweme
Boss mwasowatu zoganiza zinayamba kumandichulukila mmutumumu
Best president ever in africa
Back to the sender
Mungoimilatu u president ungakwanise brother
Zaziiiii zenizeni
Tachioneni chill mbwe chikumwetulila ngat chamisala kukamwa ngat bwantasa iyi ndi mbuzi bambo
Kodi mwasiya kulankhula,
Zakhala bwanji,mukuwopa kupangidwa trace kapena iti
Cool umatha
Muthu wankulu mwasowatu or odios brother tidziwe kuti mulipo chonde
Chistilu Cha president we ever had tachioneni mmaso mothinamo
Sure
Zomvetsa chisoni pa Malawi
Za ziiiiiii!
Bwana tikufuna mau anu plz mutiyakhule chifukwa pakatipa pachitika zambiri
Ndipo m,busa uyuyu umuthu mulibemo mulungu adamuchotsela ulemelelo ndithu ndipo sindimafuna ku muona
Wandale aliyense ndiwabodza,iwe umati ayiwale zimene adalankhula mbuyomo?,akukumbukila
Kumeneko nde awononge twenty million mk
Ine cholowelele akulu sindimafuna kunverà speech yawo ndimunthu owukila dziko lathu lamalawi ndipo ngt kwamuku kuli moto ndipo akawochedwe ndithu tili ndidziko la ufulu ndintendere koma namondwe ameneyu anabwera ndikuusokeneza ntendere relo amalawi akunvutika ngati isziko lowo 😢😢
Chakwela ndi chitsiru akutizunzila anthu
Zulule iyi fit galu wachabechabe
Uyu nde mgule weniweni
Eee bwanawa atipha batsi
Koma mukusowatu boss bwanji
Nkhuku ya njiru sikuswa mazira mudziwe nonse asanje chi mtima choipa mulinacho
Anthu mumapita kutchalitchi kukamva mawu a chinthu chomwe chikukubelani ndalama, azibusa ambili ndimbava chintsanzo chakwela anasiya kulalikila atawina loto.
Mbudzi mbava
Apa nde mwasowa zoyikatu big, mwangotithera bundle basi.
Kungosowa siku limozi osatiyankhula baba ife tima kugunda poti satana akukusakani, mumatiyimilira ndithu, Mulungu akusungeni mmanja mwake
Vuto 2020 palibe amadziwa Kuti tikuombera fiti mmanja ..pano NDI izii alibe mchisoni chimwe Kuti anthu akulili tsiku NDI tsiku gure wamkulu wen wen
kuwombela mmanja nzoduka mutu zomwe ifetu sitidya mpunga othila chizungu nje
Musamasowe big
Ulemelero wa kanthawi kochepa....
Yes akuziwadi ndi bambo wake satana tamuwoneni
Ndipo satana ndamene akudziwadi
Amalawi ena adakali ntulodi ndithu mmalo motukula myoyo ya amphawi mmalawi nkumangochedwa zauchitsiru ma satana
Zinthu Zina zikuyenera kukwanilitsidwa monga mwa malemba koma tsoka alinaro munthu yemwe akukwanilitsa izi
Kwamusalira kanthawi kochepa
Why Satana yekha kodi mwamuda mbiri chakwela kumunthu kwambiri kumapangitsa kupha munthu
Nyasi izzi😅
TV yanga ya siku ndi siku b tv
Wabwera iweyo no fear
Ah never seen a self contradiction president like him😂😂😂
Nthawi nkachitsiludi 😂😂😂😂
Achakwera ine akundinyasa kwambiri
Zangovuta kuti amaemda pa galimoto, how I wish if he was using a helicopter 🚁 munyengo yozizilayi ndipo yachifunga kk😂😅
Zazii
Ukanama sikuchedwa kucha
Opusa uyu nyani
Koma ndiyeditu akudziwa ndi satana
Satana akamuwonga munthu samangomusiyira pomwepo ayi koma amamuphatso😭😭😭😭🥱🥱
Ndikamamuona pule uyu zikumangondinyasa heavy
Ndikape kwambiri
Mbuzi ya president nyau bagamoyo chakwera moyende
Mbuzi
Kkķkkkķ🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 zoonadi akuziwa ndi Devil
Phangila
M'busa wakuba
Azibusa onse ndi asatana
Why arresting you pomwe you're saying the truth 😂😂
Cadets ukumva bwanji?😁😁😁😁
Timakunyadila man kwambiri
Munthu oyipa uyu
Uyu atimalize basi tatsala patipo nanga
Ndi mbudzi
😂 ndaseka mutu wa nkhaniyi koma ndie devil
😂😂😂😂😂 Ndipo
President ndemweyu
Kwacha yafika toilet paper
Zachibwana basi
ulemu ndiofunika, tiyeni tidzilemekeza akulu akulu. nsanje ndiye yakula
Palibe za msanje apa koma azikumbukila kutukula ziko lake osati banja lake
Zazi basi
Awa anatisaukisa basi
😂😂😂😂😂😂
Mavuto abale